My comrade sure man you r the best politician we love you may our lord bless you with long life health life protection n guidance more faya my bro sureman
@EvanceSungani-cv9jk2 күн бұрын
Uyuyu timusalile kudya akhale VP adzachigwira bwino chipanichi who's agreed with me
@MaryPhoyaКүн бұрын
❤❤❤❤❤you are blessed sir
@wideafire978422 сағат бұрын
wamalapu Lapu bwino, ulemu wanu my uncle Suleman..
@0wenNkhambule2 күн бұрын
Suleman number one ❤
@henryphiri61002 күн бұрын
Ndege yasilikali imakhala ndi parachute. Anyamula bwanji vice president opanda zozitetezera mundegemo
@JamesSuman-if2xo11 сағат бұрын
Mtolankhani do not explain amaganizo ako. You are the interviewer. 😂😂😂😂
@bridgetmajor36462 күн бұрын
Dpp my vote mcp out soon
@EliyassYusufu2 күн бұрын
Suleman we love you so much musasiye osawopa akuchepa mcp abwelele kudabwe
@GraceShaibu-i9d2 күн бұрын
sulemani big up osatopa osafoka🔥🔥🔥
@PiliranKaundaКүн бұрын
Ur strong leader mr Suleman
@innocentnamondwe965017 сағат бұрын
man of courage Sammeer
@BenjaYagoloКүн бұрын
Uyu ndi katundu ndipo kulimba mtima kwake kumandi limbitsa mtima kwambiri long live fada
@CharityChirwa-v8vКүн бұрын
Sukunama iwedi ndimpulusi wathu ndawonela mwanawanga snamphuzila papole ndintolakhani koma zakq 5 akusaka chito osayipeza pano mozikakamoza analowa chito ya police zosezi chikangawa i love you big boss sulemani
@DjshukulanGift2 күн бұрын
Mr suleman ndikuziwa kt Apure azasila in udindo ,hope ya amalawi ili pain
@Sumaili-rs2we2 күн бұрын
Zikunika president wa experience well educated and wa integrity with good strategies.
@DominiqueChitimbeКүн бұрын
Good boy big man 💪💪❤
@Chrisy-n1oКүн бұрын
Big up sir
@yamikanijoseph9381Күн бұрын
Nice you are recognizing munthu amakhala mu shock muchitsanzo chanu chomwe, nanga munthu wakuti ndege ikugwa, angakhale ndishock yanji?
@FunaniChagwira-ue5pl2 күн бұрын
Mighty DPP my Vote
@AbdullahSaeed-e7zКүн бұрын
May Allah bless u Mr suleiman ❤❤
@yamikanijoseph9381Күн бұрын
How would you feel Suleman, if someone addressed the president as "you"
This is Bishop Owen M.Tembo, let me encourage you, the Bible says do not afraid God is with you, justice is justice.
@MarryMartin-z6u2 күн бұрын
Big up mr❤❤❤❤❤
@MaqsoodJailos-c6v2 күн бұрын
Following keep it up
@wezimwalebanda-ux4sm2 күн бұрын
Sulemani sindidamuone koma amandiatsa chikoka sir i love you
@AllanChabwela2 күн бұрын
I like this boss
@JaplennthondowaКүн бұрын
This is not interviewing but kukambilana anthu a side imodzi ,,coz chimene ndimadziwa ine akamati interview.. interviewer amafusa mafuso not taking a side And we are following ❤ Just wait en see 😂
@jackalview74912 күн бұрын
Kunkuyu peleka black box
@AlainTemboКүн бұрын
Bwana bigup inu mumakwana
@yamikanijoseph9381Күн бұрын
Za a mtali manja, zisiyeni, kodi munthu waku mec alipo amene bambo or mai ake sadachitepo ndale. Umbuli mukuchitau, kodi iweyo suleman mwana wako sakuyenera kutenga any position m'boma la DPP simply because you were there before. Ndi umbili ukuchititsani izi, bwanji last time DPP IG sanali a northern person for example.
@nokosemakolija-xe9do2 күн бұрын
Am not a journalist koma i think the interviewer needs not to take sides. Let him ask questions oyankhayo aziyankha not being directive
@JaplennthondowaКүн бұрын
Ndipo live
@YasinMmadiКүн бұрын
Mr sulemani pliz dzusaninso anzanu ku parliament mukhaleko kagulu anthu olimba mtima ngati Inu pliz mwina nkuliphula dzikoli pa moto
Suleman tizikupemphererani mufike mu September mulungu akudalitseni
@MdalaBonomali2 күн бұрын
I love this my brother Allah bless him ❤❤❤
@JamesZanelo-iv1wb2 күн бұрын
DPP nayo analindizofooka zake and some of the challenges we're currently facing ......akungopitilra kuchokera ku ulamuliro wa Dpp. MCP ndiye ikungotimaliza basi.Mcp and Dpp nonse ndiamodzi.
@HamuzahBamusi2 күн бұрын
Koma mcp ambuye please kumene kuliko please please please ife akapolo anu simungaawatenge agaru amenewa
@tiwongeluhana92722 күн бұрын
NTSB imangofufuza za ndege zomwe zinapangidwa ku USA koma zopangidwa ku Germany ali ndi bungwe lawolawo lotchedwa Bundesamt für Verkehrswesen (BAV), which is responsible for investigating transportation accidents in Germany.
@MusaJali-bu3cl22 сағат бұрын
Chakwela ndi mbuli yophudzira yosaziwa mayendesedwe adziko
Akulu awawa ndi Dolo hv amaziwa zochita pathawi yake
@anthonynkhoma4265Күн бұрын
Suleman wants to seek punlic sympathy. Za ziiiiiii
@MarryMartin-z6u2 күн бұрын
Zoona ine pay slip yanga yochititsa manyazi😂😂😂 mdulidwe too much. Koma nthawi ya APM ndinalibe ngongore ine😢😢
@ChibakuliAliaКүн бұрын
❤❤
@ChristopherMwase-n7n2 күн бұрын
Ana ake atiwo
@SliviaJosephy2 күн бұрын
Iweyo 😂
@RabeccaMkandawire-i9j2 күн бұрын
Suleiman ndi Chilima 2
@edsonkamba317010 сағат бұрын
Malawi is going back to the dark 🌑 days
@HamuzahBamusi2 күн бұрын
Nde kupanda nzeru kumeneko anyamatawa nde mesa akukunyeressni manyi thumba lachimanga pano 60 nde pamtumbo pamenepo
@yamikanijoseph9381Күн бұрын
Zamabodza izo Suleman, sete zako, have you forgotten munagula ma tractor ku India and you declared them zachabe chabe kenako munagulitsana nokha nokha a DPP, pano matractor mulinawo m'makomo, munagula pa auction ma 50 pin per tractor, lero mukunya mwano oterewo, anthu oipa inu?
Suleman tsogolo lako likuonekera ,si iwe Nankhumwa ai .iwe udxathandixa anthu Dxiko la Malawi tikudxiwa.
@HildaLimbusha2 күн бұрын
Forward with Dpp
@ShareefKalima2 күн бұрын
Ndine ntchewa koma ngoz za kuchikangawa Aliyese sakusangalala nayo mpaka panopa. Ndine wakulilongwe koma ndikuopa mulungu tabwelesan black box anthu akukhulupililan koma apart from that aaaaq M.C.P wakupha
@patriciajangaza6752 күн бұрын
A MCP akudana ndi makaladi , amiya anali nkaladi chilima komaso akuluwa awawa akufuna atsale okuda ngati makarawa
Tikamupatsa 5 years dzina tonse titha 😂😂😂 chikangawa achoke
@AmosShadreck2 күн бұрын
Ee zafika pamenepa mpakana 😢
@yamikanijoseph9381Күн бұрын
Bomali Lili ndi mavuto oti likonze koma bomali silikadakwanitsa kuchita control shock yomwe malemu Chilima adachita go through, when the plane was out of control. Akulu akulu tisamalankhule za maganizo chabe, it doesn't matter how young and energetic we are, akulu akulu ngozi ya ndege simasewera, chinthu chija chimathamanga, imagine accident ya galimoto pa top speed ya convoy ya president, how much possible damage. Ndiye ndegetu imathamanga speed yoposa 400 to 600 km/ h, imagine At 400, and fall down from air,
@jomochirwa2 күн бұрын
Kumalawi kwadzala zitsilu zokhazokha pa ndale.mumangokhala ndi ma propaganda auchitsilu.inutu simudzalowaso m'boma.dpp idawononga dziko lelo mudati mukoza dziko ,zitsilu inu .😅
@PatumaSelemani2 күн бұрын
Tikufuna athu ngat inu
@GiftBello-v1i2 күн бұрын
You are out hope Mr Soleman
@yamikanijoseph9381Күн бұрын
Suleman ulibe umunthu, alubino wasowa kotenga, nthawi imene ija alubino mumachita kusaka in various homes, nanga anjinga za moto mumaundila kwa biwi, ziwalo mumapita nazo kuti?
@PatriciaBanda-e3vКүн бұрын
Sule iweeee
@NicksonKotokwa2 күн бұрын
Eeeee guys mumakwana
@VictoriaKumwenda-k6o2 күн бұрын
Wopembeza mafuno wopembeza pitala not mulungu
@WedsonVinkhumbo-q9l2 күн бұрын
Malawi athu ngati awa sachedwa kuphedwa
@BacksonLevi2 күн бұрын
Ka midiya aka chazeru palibe ofusa manyaka
@ZephMbeleswa-n8m2 күн бұрын
Awawa mzeru alibe malo mowawuza anthu zoti muzapange
@EdwardPatel-f1gКүн бұрын
Iyi si program ya kampeni,. Anu nde mukufuna akambe zomwe apange bwanji.. tazingogwirani maganyuwo
@ZephMbeleswa-n8mКүн бұрын
@EdwardPatel-f1g iweyo nde upanga chani chifukwa ifeyo ndi dairy ku ganyu kupanga mchele awawaso akupanga mchele wawo chifukwa chake akukamba za anthu ena kkkkk
@henryhenry66322 күн бұрын
Aportuguese aku Mozambique othawa nkhondo panyelo pamanu, & peter mathanyula mboli yamake muiwale zodzaphaso ma albino mmalawi muno dzimachende dzanu
DPP wa m'boma chaka chake ndi chino akane akane alole alole
@yamikanijoseph9381Күн бұрын
Choti mudziwe nonse a DPP ndi ichi, boma lililonse likalowa, limaika anthu ake m'maposition osiyana siyana to protect interests of chipani cholamula ngati muja mudachitira inu kuika Jane ansa, Chimulirenji, chisale, etc. simungaike bodyguard wa APM yemwe ali pro MCP, muika wanu amene mwamukhulupilira, ndiye what you say is total rubbish, it's against Machiavellian principles pa politics and preservation of power once attained. Perekani fundo zachitukuko, vomerani zidakuvutani, MCP idawina, chances are high apapa iwinaso, inuyo dikilani mwina next two or more terms. Komaso vomerani boma lanu munali katangale, kulembana ntchito pa chibale, kuba ndi kupha alubino ndi anthu, kudulana ziwalo, mano ndi maliseche, boma losava madandaulo a anthu, ansembe kumasunga mafupa a alubino, mpaka munapha wansembe amene uja kuopa kukuululani. Ndiye apapa tipumeko.
Machende amako iwe ndani angakuphe , ma refugees inu othawa nkhondo ku Mozambique panyelo panu
@JJ-in-the-hut2 күн бұрын
🐊🐊🐊🐊
@henryhenry66322 күн бұрын
@ kumatako kwamako mudzipita kwanu ku Mozambique
@JJ-in-the-hut2 күн бұрын
Is not you who's swearing, i know. Those are Demons that are manifesting in you
@JJ-in-the-hut2 күн бұрын
@@henryhenry6632 demons are manifesting in you, that's you swearing
@DesmondWolhuter-bw2xc2 күн бұрын
Kodi ada inu bwanji maka maka koma umunthu mulinawo zoona busy kumuchendesa mnzanu ngati inu ndi ofula man mmmm dzilemekezeni koma
@GeofreyNkhoma-u8p2 күн бұрын
Sulemani mulungu akutetezen kuzingawengazi adadi akazatenga boma azakusankhe u Vice president ndiwe wazelu komaso olimba mntima
@VictoriaKumwenda-k6o2 күн бұрын
Adpp maboza basi
@AmosShadreck2 күн бұрын
Zimachitika koma dekhani
@WedsonVinkhumbo-q9l2 күн бұрын
Anama pati
@Bbbbwesgtcjoug2 күн бұрын
Ma propaganda abodzawa ife timWadziwa wekha ukufuna kudzipha ukukaloza amzako 😅😅😅😅koma mbuli iyi ulibe mfundo usi ♥️😘 my vote ❤️❤️❤️
@wezimwalebanda-ux4sm2 күн бұрын
pita pa page ya usi omwewo.
@JJ-in-the-hut2 күн бұрын
🐊🐊🐊🐊
@bridgetmajor36462 күн бұрын
Chikangawa uyu koma iweyo ndi Boma la Mcp lakoyo...anthu okupha inu
@Bbbbwesgtcjoug2 күн бұрын
@bridgetmajor3646 ngati DPP chipani cha mwazi wa malubino 20 anthu anafa ku mzuzu
@JJ-in-the-hut2 күн бұрын
@@Bbbbwesgtcjoug albino aja mukapha ndinu ma Lacoste ndicholinga chofuna kuipisa mbiri ya DPP, didnt president Chakwera promise that he's gonna call for a commission of inquiries for albino killings where is it now, how many have arrested so far?
@mishecksipolo71532 күн бұрын
Akapha ameneyu ndiye kupempha nkhondo
@shotsfired5882 күн бұрын
DPP ikuyenera kuwina, koma vuto ndi peter is 85 years old, chisale is a dangerous man once in power people will suffer and people will die, the other problem that’s with every party is the cadets, they give a bad reputation to any party just like UDF had young demons. Sort that issue out and people will fall for you.
@EllahChikwatu2 күн бұрын
Dzaka zilibe vuto
@AllanChabwela2 күн бұрын
that's not a big a problem and him is winning definitely