Yes or no koma Brian simunthu osewera naye, ndipo atapanga zocheza ndi chikangawa PA ngakhale kuyezeka 🤣🤣🤣🤣
@osygmultimedia98546 сағат бұрын
Mery Chilima alindikuthekera konse koma please sitikufuna kumuluzanso , anthu akulamulirawa ndi Ziphe
@macdonaldkufankomweКүн бұрын
Anjawala, zindikilani kuti kukwatiwa ndi M'busa sizitanthauza kuti nawenso ndiwe m'busa kapena ukhoza kukhala m'busa. Mphatso za anthu zimakhala zosiyana.
@StellaCharmer23 сағат бұрын
Mmmmmmm koma mr brain ine ndiwa mtima ndintha kulipulumusa nkhofitu kkkkk😂😂😂😂
@MiddayDeleza23 сағат бұрын
Ayi Mai chilima asakayimile kuli chikangawa party musaiwaletu musapweteketse Mai chilima
@MpasulavisaSonjoКүн бұрын
Do not drag Mary Chilima into politics, do not dilute party ethics. Let this party be unique. Most political parties in Malawi are regional and family based , this phenomenon has bred economic stuntedness of mother Malawi
@Henry-vw2cz23 сағат бұрын
Mai chilima pitani mukaimile chipani
@MphatsoMwale-it4xdКүн бұрын
Sindikuonapo cholakwika ndi momwe akuyskhilamo ndizona angowapitila mayio eytu big brian
@MERCYMtambo-x1bКүн бұрын
eya ineso ndikuvomereza
@paulnyondo7572Күн бұрын
Koma Brian funso yes or no.😂😂
@godrick-s6wКүн бұрын
Abwere Koma tikuwafuna kwambiri
@ben-v9i1xКүн бұрын
BRIAN tangopitani kwa mai chilima mkacheze nawo timve kumbali yawo