Mulungu wamphamvuzonse landilani mizimu ya abalewa amene mwawayitana kuti abwere pamaso panu Ambuye chifukwa Cha ngozi ya ndege mizimu ya abalewa iunse mumtendere osatha long live professor Arthur Peter Muthalika God is chosing you again ❤
@JonesChingaya-yf4gg11 күн бұрын
APM deserves a big credit, we love you adad long live.
@user-qb4pj5yy5b11 күн бұрын
Its good that people have come back to their senses APM ali moyo unlike Bingu, timazindikira ubwino wake atapita, long live APM
@JackMvura-ik2td10 күн бұрын
Kodi a pm alowa UTM kapena akangolowa ndimutu kufuna mavote
@DAMZYLINJE11 күн бұрын
❤❤❤❤❤Ayi ndalila ine motsozi tsikana iwe Mulungu akudalitseni ndiwo anse omwetso ine ali mu mtima mwanga
Mopandanso kukayika Chakwera ali ndi mangazi mmanja mwake a anthu amenewa afera pa ndenge imeneyi kuphatikizapo olemekezeka Mr R Kasambara onsewa aphendwa ndi MCP anthu oyipa kwambiri
@FahadiFalaji11 күн бұрын
Ameen
@user-lw9su5om5z10 күн бұрын
Eeeesh zosayenda ay
@user-ol3ty1dj1u11 күн бұрын
So bad😢😢😢😢😢😢😢😢😢
@PaulChaleka-lb4vx11 күн бұрын
Chilima anali chiyembekozo cha a Malawi and Peter adamupanga chipongwe chilima povera omuzungulira as result Dpp idagwa as kuthamangitsana otsala lack of democracy, bcoz mphatso ya utsogoleri inalipo mwa chilima that's why anali ndi value pa ndale sadaonetse kupupuluma kulikonse pano zapha legacy ya mcp which means mcp no more chance to win
@MebleNgulinga-hi6rg11 күн бұрын
Amen the truth will come out
@MaxwellChiwaya-tv7kn11 күн бұрын
Komadi ulemu upite kwa Peter eeeeeish
@augustMag10 күн бұрын
Father Kimu you are true man of God may God bless you 🙏🙏
Na munthu wa Catholic odzavotela Congress ndi opusa.
@worldfamous_2310 күн бұрын
APM woyee!!! Let me see if you delete this comment 🤣🤣🤣🤣
@user-un6qv6sj3h10 күн бұрын
Koma sadamuphe komanso peter sadamunyoze chilima paliponse
@JustinLipipa6 күн бұрын
Koma samaphatu anzake paja
@worldfamous_236 күн бұрын
Maybe someone reading the comments is unable to interpret ( KZbin interplate gets it wrong sometimes). These 2 agree that it’s okay to steal, openly be corrupt, be nepotistic as long as you don’t say anything bad about your opponent, or try to kill somebody. These 2 people in my comments will vote on the next election. The biggest fight should be tackling ignorance, until then we will still be no where as a country.
@worldfamous_236 күн бұрын
We’re deleting comments now, what happened to freedom of speech 🤣🤣