Fr Nthalika:Yakwana Nthawi, Tiitanitse Mkwiyo wa Mulungu, Pakuti Anthuwa atisinthanitsira Mtsogoleri

  Рет қаралды 14,246

Ndine Mkatolika

Ndine Mkatolika

9 ай бұрын

Mutu wa Ulaliki: Yakwana Nthawi, Tiitanitse Mkwiyo wa Mulungu, Pakuti Anthuwa atisinthanitsira Mtsogoleri.
Wolalika: Bambo Nthalika.

Пікірлер: 48
@louisemsowoya8235
@louisemsowoya8235 Ай бұрын
😭😭😭 Ambuye bwerani mwachangu mutonthoze dziko la Malawi 😭😭Kam Lord do not delay 😭 Ambuye musakhale chete tikumira
@user-zo3bf3ec3g
@user-zo3bf3ec3g Ай бұрын
No comment 🙌🙌 inu munali oyamba osafusa kumwamba mulungu mukuke ife tichepe❤
@StevenNyozan
@StevenNyozan Ай бұрын
Amen father 🙏🙏🙏
@GreshamKadzembe-tn8cq
@GreshamKadzembe-tn8cq Ай бұрын
Mukulankhula ngati mkwiyowo utabwera mungapulumuketu anthu oyipa a catholic, palibe chimene mungalankhule cha nzeru
@user-xl7ph8bs7t
@user-xl7ph8bs7t Ай бұрын
Amen fr
@StanleyPatrickChiumia
@StanleyPatrickChiumia 22 күн бұрын
Amen
@MaxwellMbesa
@MaxwellMbesa Ай бұрын
GOD bless you keep on preaching Hard Amen:
@lottiethamanga
@lottiethamanga Ай бұрын
Keep on hitting the nail on the Head. Poti ndi satana, sakumva. Keep it up from.
@jessierodgers150
@jessierodgers150 8 ай бұрын
Amen Father Thanks for the powerful message be blessed 🙏
@annembepula
@annembepula Ай бұрын
Amen mumatiyimilila fr yanganso ndachotsa
@PhilomenaChikabadwa-dt6vy
@PhilomenaChikabadwa-dt6vy Ай бұрын
Amen,mau omveka bwino Mulungu apitilize kutilankhula kudzera mwa inu ndi atumiki ena onse olalika kuti anthu adziwe kuti kuli Mulungu ndiye mwini wazinthu zonse .chofunika apa ndikuleka zoipa ,Kuti Mulungu akhululuke ndikupereka madalitso omwe tikuwasowa.
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np Ай бұрын
Amen
@StellaChizombo
@StellaChizombo Ай бұрын
Amen father mau achilimbikitso
@user-zj1xx1ic2m
@user-zj1xx1ic2m 8 ай бұрын
Amen pastor!!!! ❤❤❤
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 Ай бұрын
Inde fada,
@StellaMathawisa
@StellaMathawisa Ай бұрын
Ambuye kumwambako imvani kulira kwathu.tituluseni mu aiguputumu.
@georgesmart3791
@georgesmart3791 8 ай бұрын
Amen mau amphamvu ❤❤❤
@JanetLuis-th5ls
@JanetLuis-th5ls 8 ай бұрын
Amen paster
@corretabanda7685
@corretabanda7685 Ай бұрын
Amen Fr
@JohnChinangwa-r2g
@JohnChinangwa-r2g Ай бұрын
amen. farther
@morisndalama6380
@morisndalama6380 Ай бұрын
Hallelujah
@user-dl8yg8cj8z
@user-dl8yg8cj8z 8 ай бұрын
Uthenga wamphamvu fr
@remsychipani2896
@remsychipani2896 8 ай бұрын
Amen and amen father
@HhhMas
@HhhMas Ай бұрын
Amen father
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 8 ай бұрын
Amen Father 🙏
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 5 күн бұрын
Koma bambo mulungu akudaliseni,,wathu uja siameneyu. ,,inenso Voti yanga ndachosamo
@user-mf1ey3vu6q
@user-mf1ey3vu6q 8 ай бұрын
Mumatimira father
@user-ti2ct8ts8d
@user-ti2ct8ts8d 8 ай бұрын
Great❤❤❤
@FranciscoJendala
@FranciscoJendala Ай бұрын
mumatiimirira father
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 Күн бұрын
Anatisinthisila wanthu siameneyu,,inenso Voti yanga ndachosako
@BennieKanama-yr3sh
@BennieKanama-yr3sh 4 ай бұрын
Mawu amphamvu Mbava izi zikuti langa zenizeni
@andrewmajawa
@andrewmajawa 8 ай бұрын
Bambo, uthenga wanu umatitsitsimusa
@ManifoldPhiri
@ManifoldPhiri Ай бұрын
Wataya njira ya chipulumutso
@greychizaka4088
@greychizaka4088 8 ай бұрын
@user-bh5ni8lk1v
@user-bh5ni8lk1v 8 ай бұрын
Mau amphamvu
@user-hc6sr9eu4k
@user-hc6sr9eu4k Ай бұрын
Uthenga wanu umandisintha fr Kaya Pano mulikuti?
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr Ай бұрын
Amen Father.
@manzunzochicafa4889
@manzunzochicafa4889 8 ай бұрын
Inenso voti yanga ndaichotsa
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
MCPigs ndi ufiti
@MerryWayson
@MerryWayson Ай бұрын
Ndipo mkwiyo wamulungu uitanisidwed Kwa omwe atimphera Chilima ndi anthu ena Aja akanthidwe ndi mkwiyo wamulungu
@user-xe5lb4uf3n
@user-xe5lb4uf3n Ай бұрын
Zoonadi atisinthira Mtsogoleri.
@shupikayintuwaluwa-5899
@shupikayintuwaluwa-5899 8 ай бұрын
Amen
@user-et3sl8vq2x
@user-et3sl8vq2x 8 ай бұрын
Amen
@VeronicaYohane
@VeronicaYohane Ай бұрын
Amen
@chimwemwenkute3839
@chimwemwenkute3839 Ай бұрын
Amen
@ZepharDriano
@ZepharDriano Ай бұрын
Amen
@EagerChicken-qj6xu
@EagerChicken-qj6xu Ай бұрын
Amen
@thesocietynews3181
@thesocietynews3181 8 ай бұрын
Amen
Fr. Elizeo Nthalika: Iye amene adampatsa Zambiri sizidamuchulukire,....
25:45
Идеально повторил? Хотите вторую часть?
00:13
⚡️КАН АНДРЕЙ⚡️
Рет қаралды 10 МЛН
Why Is He Unhappy…?
00:26
Alan Chikin Chow
Рет қаралды 71 МЛН
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔
20:45
Jimmy
Рет қаралды 41 М.
Fr Elizeo Nthalika: Nzeru za Anthu Wamba.
25:47
Ndine Mkatolika
Рет қаралды 2,6 М.
Fr. Elizeo Nthalika: Ukapolo Wamafumu.
14:29
Ndine Mkatolika
Рет қаралды 4,3 М.
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za kuopsya kwa malonda ogula ndalama zakale za siliva
27:03
T.Y. Nyirenda - Mphatso ya Mulungu yaikulu ku Dziko
46:27
Charles Shonga
Рет қаралды 41 М.
Fr. Elizeo Nthalika: Tsoka Malawi kudalira anthu, Kufulatira Mulungu.
28:06
Chaka cha Ukaristia- Fr Joseph Kimu
23:49
Tiyankhuleni Ambuye
Рет қаралды 1,7 М.
Идеально повторил? Хотите вторую часть?
00:13
⚡️КАН АНДРЕЙ⚡️
Рет қаралды 10 МЛН