THE COURT..(Malawi )🤔

  Рет қаралды 280,520

Malawi News Update

Malawi News Update

Күн бұрын

Пікірлер: 493
@MwaleYankhoKatanga-k3e
@MwaleYankhoKatanga-k3e 2 ай бұрын
The second wife is fully genius,
@gracioussinoya2850
@gracioussinoya2850 2 ай бұрын
Dont forget that she's from ndirande
@ShamilKumwembe
@ShamilKumwembe Ай бұрын
Mahuleee kkkk
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 2 ай бұрын
Chonde tibweleseleni nkhaniyi timve kuti anagamula bwanji so interesting 😂😂😂 Komabe mwanayo akuyenela kumugawilako chifukwa amayiwa anavomeleza mitala linali banja ndithu akanafuna akanakana kuti mitala sakuifuna kangachepe ampaseko mwanayo
@ishmaelimani3779
@ishmaelimani3779 2 ай бұрын
Apatsidwe gawo lawo mayiwo ,komaso ndasangalala mwayamba kuzenga mulandi mchichewa osati kufuna otathauzila tonse ndachewa 😅😅😅
@aminamussa9835
@aminamussa9835 2 ай бұрын
Point of correction, tose ndamalawi
@marianamwanje8968
@marianamwanje8968 2 ай бұрын
​@@aminamussa9835ndiposo yonse ndachewa ndiye kuti chani eti
@EvelynDamiano-zg9kn
@EvelynDamiano-zg9kn 2 ай бұрын
M'bambo akakhala pa mitala amayenera mkazi aliyense azimupangira zotsogolo payekha ndi ana ake..momwe zilili apapa palibe chifukwa chomwe mkazi wamkulu atengere chuma kugawira mkazi wamng'onoyi..angoyamikanso kut ntsungwana uja wanena kut azimusamala brother wakeyo
@JamesMalemba-tx4uh
@JamesMalemba-tx4uh 2 ай бұрын
Very beautiful I need kumva chigamulo
@MadalitsoBokosi-j3u
@MadalitsoBokosi-j3u 2 ай бұрын
Na ngati wakulu adavomera kt ndi mitala ali mwana wa bambo chuma amupase komaso amupase 25% yamwa make 10%nkhani yatha
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 2 ай бұрын
Camera man is 🏃‍♂️ runner
@ganizanizuze7104
@ganizanizuze7104 Ай бұрын
The second wife is very genius
@AnnieChaonekera
@AnnieChaonekera Ай бұрын
Mesa nkazi aliyense amakhala kwao Kodi and abambowo aliyense amamupangira zomwe anakwanitsa? Wantchitoto deserves mpando ophotchoka omweo iyaaa
@HenryLaidon-pl9ly
@HenryLaidon-pl9ly 2 ай бұрын
1st born wa Dzanja from MG 1 uli ndi umunthu coz pa dziko pano uli ndi brother wako mmodzi from MG 2 komanso ndi mwana musamalire, komano zolinga ZENIZENI za MG 2 PA mlandu wu aaaaaa chabwino tiyeni tione kuti MALAMULO akuti chiyani
@TabiahWisick
@TabiahWisick 16 күн бұрын
Fusolanga kod mayi akut chumachili mmanja mwa anaawo akuyendetsandi ana ngat chuma chawo,tsopano nanga bwanji mboniyoikutiso chuma chili mmanja mwamayi awo sangathe kugawa ?
@MwaleYankhoKatanga-k3e
@MwaleYankhoKatanga-k3e 2 ай бұрын
She knows how to explain,this marriage issue
@ChrispoGawani
@ChrispoGawani 2 ай бұрын
Mwanayu ndi wa m'ng'ono akuyenera kusamalidwa aphunzire school yabwino azigona pabwino chuma adzapanga yekha msogolo m'mayi wa mkuluyi wavuta sapereka gawo la chuma komanso bamboyu analakwitsa osalemba will iyeyo ndiyemwe anayenera kugawa chuma adakali ndi moyo azibambo anzanga tiphunzirepo apa nkhani izi always zimavuta kwambiri
@MustafaAmeen-tb6wd
@MustafaAmeen-tb6wd 2 ай бұрын
Ngat nkazi anavomeleza mitala akuyenela amugawileko nzakeyo chumacho, congratulations ku mboni athandizedi mlongo wakeyo kuti naye azafike ngati pomwe ali iyepo
@pridebihalie
@pridebihalie Ай бұрын
Palb chifukwa chogawana katundun( kd munthu wakalimbusidwa nsima Pali chifukwa Choti uzilamulila nsima ya ainake?) Mutayen ameneyo wangotopa nd umphawi aaah 😂😂
@kesterkaunda
@kesterkaunda 2 ай бұрын
This is true story or movie?
@RhodaKalumbi
@RhodaKalumbi 2 ай бұрын
Amen good wafunsa funso labwino mkazi wa mkulu mahule wa ndi anthu oyipa wake kunalibe
@MeltonMumba-rn9mf
@MeltonMumba-rn9mf 2 ай бұрын
Exactly
@patrisiobinalison8476
@patrisiobinalison8476 2 ай бұрын
Uyutu sihule ,mkazi wamkulu pomwe analakwila ndi kuvomeleza mitala
@GiftCMlangeni
@GiftCMlangeni 2 ай бұрын
Mind your tongue remember ngati pali hule ndi abambowo not mkaziyo. Am also aman how can idate wantchito wanga? Mesa amkagwirantchito nde amakapempha banja ngati? Wamkukuyo adavomeleza bwanji mitala nde chitavute nchani kungomugawirako kuti asathe nthawi yaboma? Kungoti ndikupatsa business imodzi or minibus imodzi basi nkhani yatha. Komaso akuiwalakuti chuma chimatha, dzina la abambowo lilindi wamwamunayo, enawo mawanja akakavuta adzamufuna nchimwene wawoyo?? Nanga mayiwa akadzakalamba akaziwa adzakwanitsa zonse zomwe zimafunika mamuna akhalepo?? Mmmmh kuipamtima kukuoneka apa
@McDonaldKanyinji
@McDonaldKanyinji 2 ай бұрын
As long as the first wife accepted that they were on polygamy, the worth is suppose to be shared according to how many kids each wife has......... but not equal..... Court should observe this.❤
@AshleyMbewe-k5z
@AshleyMbewe-k5z 2 ай бұрын
I second with you bro,the rulling is very important
@PaulBambe-m3t
@PaulBambe-m3t Ай бұрын
Where is the ruling. I need it pliz. Give me a link 😂
@CeciliaPaulchidule
@CeciliaPaulchidule 27 күн бұрын
Km kuli zinthu😂😂😂....second wife is so courageous
@gracechingaresearch-b5v
@gracechingaresearch-b5v 16 күн бұрын
Malemuwo asanamwalire anaenera kupangiratu kalikose pamwana wanuyo mesa mukuti anakugulirani kanyumba basi pangani za business sisi😂😂😂 muchedwa mukalilira chuma kubereka mtsikana sichifukwa iwe ungofuna chuma basi
@ShaibuMbwana-h2i
@ShaibuMbwana-h2i 6 күн бұрын
Shaibu mbwana 😂😂😂😂😂
@peterjoshua2595
@peterjoshua2595 2 ай бұрын
I just like the guy who’s sat behind the accused 😅
@hajikasaku6054
@hajikasaku6054 28 күн бұрын
I like second wife she had a good question to first wife
@FrankNyoni-pm3jz
@FrankNyoni-pm3jz 2 ай бұрын
What was the final judgment ?
@PamelaSumbuleta
@PamelaSumbuleta 29 күн бұрын
Koma chigamulo ndie chikuchedwa bwanji kkkkk
@gremmerchris71
@gremmerchris71 2 ай бұрын
Nkazi wachiwiri uziyamika kuti uyu woyambayu anakulola kulowa m'banja lawo komaso pokutenga kuti uzikamugwilila ntchito chokhacho uzimuyamika...usazitenge wapamwamba kwambili kuti wabeleka mwana wamamuna nzakoyo sikufuna koma zidangochitika.. Komaso iwe nkazi woyamba kuti ufike pomwe ulipo dzidatengela nzakoyo kukhetsa thukuta ndikudzichepetsa kwakwe kuti iweyo ukhale umoyo ofewawo muthokoze pomupatsa shop imodzi over time mudzapeza ina basi simple..mukutelo pokuti iye ndiyemwe wasunga nfunda wanu basi
@NedsonKennedy
@NedsonKennedy 2 ай бұрын
The best way is, write willo b4 pass away 😂
@WilsonPhiri-vl1di
@WilsonPhiri-vl1di 2 ай бұрын
Exactly
@IsumailaSalanje
@IsumailaSalanje 2 ай бұрын
Kumupatsa gawo lachuma kukhoza kulimbikitsa antchito kumagwa muchikondi ndimabwana.Mngosokoneza mabanja amenewa
@aminamussa9835
@aminamussa9835 2 ай бұрын
tikudabwa nanu enanu ma comment anu mmalo moyakhula zinthu zomanga zadzelu, muli busy kumunyoza nkazi wachiwiliyu anthu mukuzimvela nokha kuti anavomelezana mbali zose ziwili khani yamitala sono wasanduka bwanji kukhala hule! Chomwe mukumunyozela munthuyo ndichani? munthu pozindikila kuti zapadziko ndazakutha chovuta ndichani kumugawilako gawo lililoselo kuti naye asangalale ngati njila imodzi yoyifunila zabwino business kuti ikhale ndimadalitso pokana zokokanakokana
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 2 ай бұрын
Chuma chigawidwe kwa mkazi wachiwiri chifukwa kumenekonso kuli mwana wabamboyo amayiwo asaphangile chifukwa chakutinso mkazi woyambayo adavomereza kukwatiwa kwamkazi wachiwiri
@GibsonZunda
@GibsonZunda 2 ай бұрын
Koma ngati Pali Ana chuma agawe basi
@DesireMphatsogama
@DesireMphatsogama 2 ай бұрын
Apatsidwe chuma chifkwa kuli mwana komanso akaz akuluwo anavomeleza
@ChimwemweEddimael
@ChimwemweEddimael 2 ай бұрын
Aah ine I think this is just acting why do I see the same faces on different cases or maybe it's only me 😂😂😂
@corretabanda7685
@corretabanda7685 2 ай бұрын
Eyaka ndi acting. Akufuna kuti anthu adzipita ku khoti zikaavuta, komanso anthu tidzitengerapo phunziro.
@MilwardChanza-mr4yr
@MilwardChanza-mr4yr 2 ай бұрын
Mkazi wachiwiri anakakonda anamkagaila ma percentage angat?
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 ай бұрын
Ndipo anthu musamangoti a agawe agawe muli inu mungapange zimenezo uyotu ndi hule apezaso bambo wina kuti abelekele mwana wa nkazi sinanga ali pa business yopangila ana kwa zibambo omwe akufuna ana osiyana m nyumba ine ndikuti asampase....
@owenlingwa
@owenlingwa 10 күн бұрын
Mau ngat kaz chiphwanya 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@glorynkhoma
@glorynkhoma Ай бұрын
Mwanayo athandizidwe bas kms amayi wo ndiopusa kangoona kuti pomwe ndkugwira ntchito pano pari chuma bas ndavomera banja zaziii ndpo musamupase kanthu azikhala konko kumipando yofubwako
@vestarmkandawire6138
@vestarmkandawire6138 2 ай бұрын
Mkazi wa chigololo ameneyo ndi mbuzi,, banja ndi ndalama ndi zinthu ziwiri zosiyana. Mkazi woyamba ayankha bwino kuti adavomereza mwamunayi akhale awose osati chuma. Ndiye huleyo chuma chake ndimwana wamwamunayo. 1 Akumbukire kuti anali wa ntchito wa mayi wamkuluyo 2 wamulakwira kumulanda mwamuna wamwini. Apapa kunena zoona chuma asamugawire ndi wakuba mayiyu. Zikuonesa kuti wapha mwamuna ndiye kufuna chumacho.
@AwufWaria
@AwufWaria 2 ай бұрын
Wolakwisa ndi mayi oyambayo povomereza mitala,chuma chiyenera kugawidwa basi
@FatimaAyami
@FatimaAyami 2 ай бұрын
Mwanvetsa koma inu kapena ndinu achibale a MG1
@macdonaldkorea2928
@macdonaldkorea2928 2 ай бұрын
Inutu ndiodwala, munkhaniyi mwakambidwa zoti wina ndihule? Iwe momwe umkabadwa makolo akowo anakwatirana mwadongosolo? Kumasata nkhani osati mopusa.....
@macdonaldkorea2928
@macdonaldkorea2928 2 ай бұрын
@@AwufWaria nkhani koma imeneyi ndithu.....
@johnssanamah1408
@johnssanamah1408 2 ай бұрын
Vuto lowakhira nkhani pali za uhule apa mesa akuti unali mgwirizano oti ayese zida abambowo amafuna mwana wa mwamuna ndye atafunsidwa amayi akuluwo anavomera kuti vuto palibe atha kukhala pa mitala mwayi uwo mimba mkubwera akabadwe mwana chimphongo ndye kuti mdala Ku khosi mbeeee kuti mission yatheka mwana wa mwamuna wapezeka. Ndye chomuchulira kt ndi hule mumakhala chili chani....?????
@MwaleYankhoKatanga-k3e
@MwaleYankhoKatanga-k3e 2 ай бұрын
The first daughter is coming with some juries and want to run away from this as solution
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 2 ай бұрын
Nkadzi wa chiwiliyo chuma akanapasidwa ndi mamunawakeyo chifukwa chumacho ndi cha kubanja lalikululo mamuna wanzeru satenga wa kwa Nkazi winabkupitisa kwina akanapanga zawo nthawi imene amunawo Ali ndi moyo😢
@josephgondwe5829
@josephgondwe5829 2 ай бұрын
Nkhanizi ndi za kuMalawi konkuno, I like it kuti you are using Chichewa osati zokhala ndi interpreter.
@HaroonHaji-rp4if
@HaroonHaji-rp4if 2 ай бұрын
Malamulo amatiuza momveka bwino zachuma chamasiye mwana wamng'ono komanso ndimwamuna akuyenera kupatsidwa gawo lake koma akharea ndimtsinkhu woyenera ndipo MG 2 sakulakwitsa sichifukwa MG 1 pamene amavomereza mitala anadziwa zoti ali ndi chuma chimene umwini waukulu umakhara kwa ana
@AgnessMaumbo
@AgnessMaumbo 2 ай бұрын
Akafukule amunache ankamuuza kuti amupatsa chuma adzamupatse,vuto la tsikana amasiya chomwe apitira maso muchanya kwa zimuna aeni ake kkkkk,akamaona nkazi akuoneka bwino amaona ngati akumusamala ndi mwamuna nde kumakhala kuti ndipite nane ndizikaoneka ngati amene aja,osadziwa kuti munthu wamayi amazilombikira yekha kkkkkkk,kuphunzitsa kwabwino amene akuonera atsikana aphunzirepo sure
@Idrissa-r2h
@Idrissa-r2h 18 күн бұрын
Ndimadikila chigamulo abale please aaaa ndangoononapo bundle sinzaonelaso izi
@innocentwilfred-b5s
@innocentwilfred-b5s 2 ай бұрын
PA ana atatuwo dzanja alipo mmozi uyu ndiye mwana wamamuna mpaseni zabamboake
@SamboRuphan
@SamboRuphan 2 ай бұрын
Hule ameneyo 😂😂😂eyeyo amachayilila chuma cha bambowo chifukwa chake amakachindana ndi abwana ake 😂😂musamupase kalikonse
@AmosSimeon-i5i
@AmosSimeon-i5i 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 ooooh?
@BrendaMwandumba
@BrendaMwandumba 2 ай бұрын
Ndie malemuwo si hule?
@SamboRuphan
@SamboRuphan 2 ай бұрын
@@BrendaMwandumba onse ndimahule,,,ndiye asavutise kuti amugayileko chuma,, chifukwa iyeso anali ndi nyumba yake,,,,amusiye kazi woyambayo akhazila patendele,,,
@marthachapepa6729
@marthachapepa6729 11 күн бұрын
Share the properties, waiting for ruling
@EstherChokani
@EstherChokani 2 ай бұрын
Zaziiii agawe chani,amkaleka kumpasa chumacho mamunayo alipo bwa mg2 anthu oyipa akhoza kukumpha akhaula
@MikeMwale-bw1xw
@MikeMwale-bw1xw 2 ай бұрын
Umfiti suposa pamenepo,kumakhala ndi umunthu palibe amadziwa za imfa kuti ingachitike mwachangu kwa bamboyo,ndili sure naye gawo lake lipezekapo akagamula.
@GibsonZunda
@GibsonZunda 2 ай бұрын
Agawe chumacho
@PociahMack
@PociahMack 2 ай бұрын
​@@MikeMwale-bw1xw wina wazuzika naye wina kungochoka uko Ali agawe zosathekatu
@MikeMwale-bw1xw
@MikeMwale-bw1xw 2 ай бұрын
@@PociahMack Ayi agawane anapangira limodzi,sikuti wangochoka uko nayeso anali mrs
@mphatsokauta6387
@mphatsokauta6387 2 ай бұрын
@@MikeMwale-bw1xw kungoti kwanthu kuno ma banja samayenda mwadongosolo
@elsontmsukwa4356
@elsontmsukwa4356 2 ай бұрын
Ine ndimaganiza kuti chuma chisungike bwino chingokhara ndimunthu yumozi azichiyanganira kenako aziwapasako azake asowekera chinachake chifukwa akapupuluma kugawana mwana tava ndi wamungono nde mwina nikutheka awagawira koma koma mutu wa business alibe apeza chonse chathaso nde mwanayo azapezachani akakula 😢😢😢😢
@macdonaldkorea2928
@macdonaldkorea2928 2 ай бұрын
Ayi agawane chifukwa azimai okha okha sangamachitire zinthu limodzi
@RobsaiSaidi
@RobsaiSaidi 2 ай бұрын
Bwanji you don't fully finish your court trials... whats the point of not letting us know the judgement. I. USA they finish fully. We love watch such stuff
@HildaMachinjiri
@HildaMachinjiri 2 ай бұрын
😮😮😮 ati ana akazi alibe ntchito nkhani ija waiononga 😂😂
@TabithahLloyd-z4t
@TabithahLloyd-z4t Ай бұрын
Ndipo kuyankhula bwinobwino koyambilira kenako nkudzangosokonezanso ekha 😅
@TabithahLloyd-z4t
@TabithahLloyd-z4t Ай бұрын
I don't think kubeleka mwana wammuna chikhale chitonzo pa anzawo , iwo adakangopempha thandizo la mwana osati mpaka chuma chifukwa mkazi wankulu kuvomeleza mitala sindiye kuti chilichose chomwe ali nacho ndye kuti nkazi wango'ono akhale nazo
@CleemelLucretia
@CleemelLucretia 2 ай бұрын
Is this acting classes?
@WillardPatrick-h9s
@WillardPatrick-h9s 23 күн бұрын
Yes but helpful
@RejoiceKamanga
@RejoiceKamanga 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂 zosekesa bwanji. Mnthu kukhalq wantchito kumasiliraso mwanana wa wolemba ntchito. Uyu anali after chuma mwamunayo. Mkazi wachiwiri sangakhale ndimphavu zachuma ai. And alibeso malo kumwamba woziwika ndikaz woyambayo. Iiiiii kma abale ndimafuna ndilembe wantchito ai sindilemba 🖐️🖐️
@kanyengamatress6130
@kanyengamatress6130 Ай бұрын
Akazi achiwiri skut muzit mutenge chuma chose aiii nkhan ndiyot akugairen gawo lanu basiii awoso akuyener kuperek ndinth
@WillardPatrick-h9s
@WillardPatrick-h9s 23 күн бұрын
I think sanati akufuna chuma chonse, nkona akuti angowagayirako ka gawo chabe
@marianyirenda
@marianyirenda Ай бұрын
Komano walembedwa ntchito mphaka kumasukilana ndi a bwana wosachita mantha mphaka kuvomeleza kuti mukwatilana yikhale mitala ndi mkazi wa bwana mmmmm koma azimayi muzikhala ndi mantha please
@AgnessMakuluni
@AgnessMakuluni 2 ай бұрын
Chuma ndi chamkazi wamkulu no matter kut ali ndi ana akazi okhaokha, wang'onoyo bwezi atamupangira chuma chake asanamwalire
@GiftMoyo-eh8pw
@GiftMoyo-eh8pw 2 ай бұрын
Ndipo wamkulu wandisangalatasa koposa asagaile Chuma icho cos mwachoka Patali Mamie hule linagwa mchikondi bcz Chuma I 😂😂😂😂😂😂😊
@NedsonKennedy
@NedsonKennedy 2 ай бұрын
Sibwino kumangoti MG 2 ndioyipa ngati kuyipa sanakuwone bamboyo asanamwalile mukawone anthu wamba😂 chuma agawe basi, kuthandiza mwana it's not a big deal.
@DesireMphatsogama
@DesireMphatsogama 2 ай бұрын
Komatsu inu omwe mumapanga post muzimalizitsa mpaka kuchigamulo coz timaphunzilira momwemu
@starlonJames-qr4xl
@starlonJames-qr4xl 2 ай бұрын
yes
@ComfortChiombangoma
@ComfortChiombangoma 2 ай бұрын
Zoonadi ndithu 😂
@JoaoLazaroMATABICHO
@JoaoLazaroMATABICHO 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂zowond
@CleJohn-v6z
@CleJohn-v6z 2 ай бұрын
Yes iwe😂😂
@KondwaniGumba
@KondwaniGumba 2 ай бұрын
Ngati adali mkazi wa malemu ndikumuberekera mwana , akufunika kukhara ndi gawo la chuma Cha mamuna wawe. Ndikukhulupirira kuti pakutha pa khaniyi ikomera odandaula.
@IdrissahJames-gu2yo
@IdrissahJames-gu2yo 2 ай бұрын
Zinko nd Anthu ake....koma apopo plz plz 😢 Awapatseko Gawoo la Chumachoo plz plz
@johnssanamah1408
@johnssanamah1408 2 ай бұрын
Mboni yafotokoza bwino zedi moti ndikuona akulandira gawo la chuma brother wakeyu
@mphatsokauta6387
@mphatsokauta6387 2 ай бұрын
palibe kumugawila koma kugawana...100% ya assets yo then awona anthu oyenela kugawana ndangati then aliyense atenge percentage yake. community of property ijayo
@MoffatBinali-pp8hi
@MoffatBinali-pp8hi Ай бұрын
Wang'ononoyo ndiwosusukira chuma zikutanthauza kuti maso ake anali pachuma.chabwino akanakhala kuti waberekanso wamkazi akati chani?
@OviousSili-th5mk
@OviousSili-th5mk 11 күн бұрын
Part 2 ilipo kod ?
@BrendaSinoya
@BrendaSinoya Ай бұрын
Watchitoyo anafoira bamboo alimoyo,akanapempha zake zoti aziyendesa ekha abambowo asanamwalire koma pot mphuno salota
@graciousbwanali5079
@graciousbwanali5079 2 ай бұрын
Gyz if i can have chance to coach people before the court ambiri sibwenzi akuluza milandu❤
@wittinessnkhokwe
@wittinessnkhokwe 2 ай бұрын
Kodi anthuwa anangokhala amodzimodzi tiziti amangoyelekeza ndi zaku court?
@GilbertKuziona
@GilbertKuziona 2 ай бұрын
Ngati mkazi wankulu akuziwa ndipo anavomeleza zamitala ndipo akudziwadi kut kuli mwana kwa mkazi wachiwiri akuyenera kumupasa gawo lake mwanayo
@StanleyChinsewu
@StanleyChinsewu 2 ай бұрын
When we are in that situatio n solve this problem before you die it's about money not marriages today
@dinnakabaghe4246
@dinnakabaghe4246 2 ай бұрын
Iyiyi imakhala Drama koma kuti tiphunzire mmene nkhani amaweluzira mma Court athu, moti muzionera pa MBC TV Monday 5:pm to 18:00. pamakhala nkhani zosiyanasiyana koma anthu ake otenga mbali ndi omwewa. Zikomo
@miryamkatundulu
@miryamkatundulu 2 ай бұрын
Please men before you die, write your last testament and will so that life is not complicated.
@MikeMwale-bw1xw
@MikeMwale-bw1xw 2 ай бұрын
Kodi bwanji programm yofunikila ngati iyiyi adayipatsa nthawi yosakwanira?Tikaonetsetsa chofunika kwambiri ndi chigamulo koma anthu tisanamve chigamulo akupezeka nthawi yatha amatero?konzani tikufuna tidzimva programm yonse bwino bwino osamatisiya mmalere.
@bonfacekantwanje6223
@bonfacekantwanje6223 2 ай бұрын
Akuti akufuna chuma Cha chani? Koma guys😊
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 2 ай бұрын
Kwakoma ndikuno😅😅😂😂😂😅😅
@binwellchunga4986
@binwellchunga4986 2 ай бұрын
Mai uyu wodandaula chuma apatsidwe sitikuti wagawane pakati koma chuma atengeko izi akulankhula Mayi wankulu izi ndizopusa kwambili mamuna wake ngati amatenga maliseche mkumalowetsa ku nyini kwa mzakeyu mpakana ubelekamo mwana sizoti wapusitse court kuti mwana wazimuthandiza Noooooooo uyu chuma apatsidwe basi
@henrymwale8994
@henrymwale8994 2 ай бұрын
Kodi izizi zimakhala zenizeni kapena ndi mwa drama coz anthu ake ndimaona amodzimodzi
@SoniahMussah
@SoniahMussah 2 ай бұрын
Drama😅
@ChifundoBita
@ChifundoBita 2 ай бұрын
Ndi drama yomwe imaphuzitsa anthu zokhudza khothi, malamulo, kuweluza milandu
@PeterJafari
@PeterJafari Ай бұрын
Kodi anagamula bwanji guys ine ndikusaka koma sikupezeka koma mkadzi wang,onoyi akuyenera amupase ngawo lake ndithu
@henrychikuse1543
@henrychikuse1543 2 ай бұрын
Uhule ulibe profit chemwali. Komaso kulibeko mau oti amuna athu koma amuna Anga. Mwana wanu ndiwakuchigololo ndiye mwana wakuchigololo sawerengedwa
@SteveriaNyalugwe
@SteveriaNyalugwe 2 ай бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤
@DavidChapalala-i2g
@DavidChapalala-i2g 2 ай бұрын
Nkhan yabwino kwambiri 😂😂😂😂😂😂 Chumacho ndi cha onse ndipo akuyenera kugawa bas
@ShamirahMakungwa
@ShamirahMakungwa 2 ай бұрын
Munthu utha kuvomera mitala malingana ndinyengo mmene iliri...vuto ndimalemuo coz sitikuziwa kuti ankagwirizana chani ndiwantchito wawo akakhala awiri.kmanso ngati inali mitala mamuna amapanga equal popanga zithu.iwowo kod sanasiye will...
@ShadreckKwelani
@ShadreckKwelani 2 ай бұрын
Second wife agawilidwe mbali yake.
@StellahChisale
@StellahChisale 2 ай бұрын
Kkkkkk kom tiphana😂 unatan kuwauza amunanuo kt akugawilen chomacho asanamwalile, mukufuna kuzumza munthu ot czikumukhudza
@neighbourfilms
@neighbourfilms 2 ай бұрын
Sound track is too loud please
@EliasManthenga
@EliasManthenga 2 ай бұрын
Odandaula munavomela banja ndinso kuwabelekela mwana ,osati chuma ai ngati bambo sadapange gongosolo chafa kwanu mai
@MikeMwale-bw1xw
@MikeMwale-bw1xw 2 ай бұрын
Koma banja mukulidziwa inuyo kapena mukungolubwa?
@SteveriaNyalugwe
@SteveriaNyalugwe 2 ай бұрын
Ndipo mwamunayo akanasiya wilu asanamwalire, ndiye ngati mwamunayo sanamugawire mwana wake alimoyo samamuwelengera. Amafuna mwana osati chuma
@FRANCISLIFFAH
@FRANCISLIFFAH Ай бұрын
odandaulidwa munamvomera kunkhala akazi awiri, kwa m'bambo mozi sono musachuluke mzeru cfk mamunayo wamwalila
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 2 ай бұрын
MG2 kutha mantha mpaka ku khothi kutengela MG1.
@nitafraphael2362
@nitafraphael2362 2 ай бұрын
Please part 2
@LakaniChikweza
@LakaniChikweza 2 ай бұрын
Ati iwowa katundu wawo umachokera kunja,koma ine zanga ndimagula mu ndilande momwemo,😅😊😅
@MikePetros-e7m
@MikePetros-e7m 2 ай бұрын
❤ Mai awa sakuyakhura mwanzeru'!!
@praisechikuni8200
@praisechikuni8200 2 ай бұрын
Azimaiwa akunatipha dala, bola kumangogila munseumu , zazithela kunseu komko
@mussammakwinja5215
@mussammakwinja5215 2 ай бұрын
Kkkkkkkkk nyumba mwa mkazi wang'ono ndi wa mkulu mungafanane Bwanji mwamunayo samapanga dongosolo aaaaaa palibe kugawana
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 2 ай бұрын
Ndipo inuyo palibe kugawana mvuto athu awa akaona kut ukusangalala nawoso amaona ngati azasangalala Palibe Chake amunakewo alimoyo analeka bwanji kupanga dongosolo
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 ай бұрын
Komaso akanankhala kuti mamunayo analibe ndalama sakanavumela kuti abelekele mwana koma mavomela chifukwa anaona chumacho
@TiyamikeKamkwete
@TiyamikeKamkwete 2 ай бұрын
Ine maganizo anga ndikuona kuti despite kuti mwana wawo amuthandiza za school,akufunikilabe ka gawo kake kachuma chifukwa linalinso banja lovomelezeka ndithu...and ngati akuti nkazi wamn'gonoyo apeze zochita zomuthandizila pamoyo wake,,,zikuyenela kuti nkazi wankuluyo amuthandizire nkazi nzakeyo pomugailako ka kapitolo ...
@MableMachemba
@MableMachemba 2 ай бұрын
Gawo lake ameyenera kutenga bambo ake alipo osati pano nde pangano anapangana ndi mamuna pano palibe nde aziti chani mene ankamugulira nyumba ankareka kumugulira nthawi yomweyo
@JosophineKaonga
@JosophineKaonga 2 ай бұрын
Lets work hard guys tisazalilire chuma cha eni😂😂😂
@FastonChidule
@FastonChidule 2 ай бұрын
Chonde ndi pempho lathu kuti tidziwe m'mene ziyendere. Taikonda program imeneyi.
@HannockMesiwni
@HannockMesiwni 2 ай бұрын
Apachumacho chinera kugawidwa ndipo nkhani iyi yikuoneratu chilungamo chake ngakhale mwana wamaiwa wakuluyo akuyakhula chilungamo ndinthu apase gawo lawo amai achiwiriwa
@WelemuSayizi
@WelemuSayizi 2 ай бұрын
Iwe nkazi wachiwiri ndi wopusa chifukwa court imafuna umboni munasaina pati kuti ndikadzafa nkazi wankulu adzakugaira chuma
@MikeMwale-bw1xw
@MikeMwale-bw1xw 2 ай бұрын
Mukunama akanadziwa bwanji kuti adzayanbe kufa ndi iyeyo.
@JoshuaNgosi
@JoshuaNgosi Ай бұрын
Ka nkazi ka ntchito aka ndikamisala.😂😂
@AndyChisunda
@AndyChisunda 2 ай бұрын
Kosangalatsa kankhanika. Poti banja laling'ono lidaziwika ndikuvomeledzedwa ndi banja lalikulu chuma chigawidwe basi posatengera ichi kapena icho.
@yotamumahomed1313
@yotamumahomed1313 2 ай бұрын
Ngat mkazi wamkuluyo anavomeleza mitala ndekut chuma chigawidwe coz iyeyo ngat amafuna kusalimbana ndi aliyense pa chuma chake akanayamba nthawi imeneyo
@ashadokhomzy5781
@ashadokhomzy5781 2 ай бұрын
Yalakwatu apa kaya tidikile final episode kuti zitha bwanji
Usauver S09E02   AKAZANU ASOWA
16:28
Piksy TV
Рет қаралды 230 М.
HAJJAT ZUULAH AYIYE BWIINO OMUKAMBWE, TAATA NISHA EXPOSED
1:27:54
Gossip Live
Рет қаралды 4,6 М.
Osman Kalyoncu Sonu Üzücü Saddest Videos Dream Engine 262 #shorts
00:20
НАШЛА ДЕНЬГИ🙀@VERONIKAborsch
00:38
МишАня
Рет қаралды 2,9 МЛН
Wait for the last one 🤣🤣 #shorts #minecraft
00:28
Cosmo Guy
Рет қаралды 10 МЛН
THE COURT (Malawi)
24:46
Malawi News Update
Рет қаралды 81 М.
BON KALINDO - ANTHU AKUYENDA OKWIYA KALE SAMALANI MAYANKHULIDWE ANU
21:21
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 1,7 М.
Mr Jokes "WACHAKE COMEDY SERIES" episode 6 (Full Video)
15:12
MR JOKES
Рет қаралды 235 М.
JUDICIARY OPEN DAY 2024 LIVE CHE MANDOTA PERFORMANCE
14:19
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 77 М.
Rev Alexander Kambiri preaching at the funeral service in Malomo Ntchisi
30:23
Rev. Alexander Kambiri
Рет қаралды 130 М.
THE COURT (IYI NDE MUSAIPHONYE!!) Malawi
22:07
Malawi News Update
Рет қаралды 66 М.
MILANDU PA OKALA....Episode 24
11:54
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 323 М.
Osman Kalyoncu Sonu Üzücü Saddest Videos Dream Engine 262 #shorts
00:20