Komadi olo zitakhala zopeka he is telling the truth and izizi zikuchitikadi,ife takawidwapo ndalama osadziwa kuti yasowa bwanji,komanso izi za kwa asingangazi nzoonadi ndunena pano ankoloanga ndamisala nkhani zake zomwezi,anasemphetsa zizimba pofuna kupha mayanga mmatsenga,mwatsoka zidakanika,tiyeni titengerepo phunziro,zikomo
mkulu uyu ndiwabodza ndi uja amakonda kukamba nkhani zaku South african uja uyu
@FlorenceMustafa-f1m3 күн бұрын
Ndipo ndiye taphunzilapo apa kwambiri eee
@PatrickChiwaya-cc9ef3 күн бұрын
Jafari kod ukufuna uxitipusisa eti mesa unakumanaso zooopsa pomwe unali pa ulendo opita ku Joni iwe
@Shem22 күн бұрын
Ndi yemweyu inde. 😂😂
@NganoNjazi-r4h2 күн бұрын
😂😂😂😂....ayamba kutinamiza
@RoseFatchКүн бұрын
Super 😢😢
@LazarusChirwa-su7yc5 күн бұрын
Koma kudziko kulizinthu abele mlungu ativele chosoni
@YahyaIsmail-b8o3 күн бұрын
Aise iweyo ndiwonama kwambiri mesa iwe ndiwe unazalongosolanso nkhani ya Ku jons nkhani ya nzako amene anaba ndalama Kwa bwana wanu mkuthawa voice yakenso ndiyomweyinso😂😂😂😂😂
@ChikondiKwengwere3 күн бұрын
Akusiyana
@AlishaYasin-t1xКүн бұрын
Kuterokotu izizi posatengera kuti kaaya amakamba yekha koma zikuxhitika ndithu,iye alingati driver,kapena kuti advisor,tiyeni tizimgotengerapo phunziro bas
@HawaMamo-q2vКүн бұрын
Zowonadi Kaya zabodza koma muziphuzira
@innocentlipita3630Күн бұрын
Koma use standard language the word khwesi ndiye zochani zimenezi