COMMISSION OF INQUIRY YOPUSA!!! TAMVANI  IZI
6:45
MICHAEL USSI NDI CHIGAWENGA. TAMVANI IZI
16:07
BILLY MALATA WAGWIDWA UFITI  TAMVANI
20:06
9 сағат бұрын
KUMALAWI KUNUNKHA MPHILA!! BON KALINDO
16:52
A BEN LONGWE  ZAWAONEKELA  TAMVANI
6:46
19 сағат бұрын
PHUZIRO LA AMALAWI LOSAIWALIKA
18:07
KUSWAKUSWA LERO BON KALINDO
17:44
14 күн бұрын
TAMVANI ZA  MATENDA A CHAKWERA .
9:02
14 күн бұрын
Kod CHAKWERA Wamwalira? tamvani izi
8:31
MA PLAN OOPSA A MCP TAMVANI IZI
14:26
14 күн бұрын
CHAKA CHA MAWA KULI ZOOPHYA TAMVANI
16:48
Пікірлер
@PhlipsPhi
@PhlipsPhi 28 минут бұрын
Well spoken
@storytambala6088
@storytambala6088 Сағат бұрын
Unawupeza chifukwa, cha ufiti, ayi ndithu zoonadi uyu alibe chisoni ndi imfa ya mnzake ndi mfiti.
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Сағат бұрын
Palibe nduziona apa aaaa mbava zokhazokha iziiii💔💔💔
@AsinasLiomba
@AsinasLiomba 2 сағат бұрын
😂😂😂😂 km aMalawi ndi okwiya zenizeni. Dandaulo limveke basi. Rise Malawi rise
@FrancisChimenya-m9d
@FrancisChimenya-m9d 2 сағат бұрын
Munthutu wayankhula uyu okumva wamva
@FrancisChimenya-m9d
@FrancisChimenya-m9d 2 сағат бұрын
Wise words
@AgnesLapukeni
@AgnesLapukeni 4 сағат бұрын
Mwayakhula zowonadi apa aaaa
@DavidMtambo-e3b
@DavidMtambo-e3b 5 сағат бұрын
Or amutukwane bushiri iyeyoso watukwana.
@DavidMtambo-e3b
@DavidMtambo-e3b 5 сағат бұрын
Bushiri ndi mulungu iyeyo, prophet wanji uyu? Kapena akulanura chakwera ndiongobisalirako koma president ali iyeyo bushiri.
@NdingodyaChisale
@NdingodyaChisale 6 сағат бұрын
Mr DC 1
@BrightNyoni-yd4ip
@BrightNyoni-yd4ip 6 сағат бұрын
📱📱📱🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
@crosbeygondwe5403
@crosbeygondwe5403 6 сағат бұрын
😂😂😂
@YusufJames-f5f
@YusufJames-f5f 6 сағат бұрын
Fact up
@JosephJonson-o4r
@JosephJonson-o4r 6 сағат бұрын
Afisi Afisi enieni awa
@HamzahTwaib
@HamzahTwaib 6 сағат бұрын
Iwowo azingokozekela 2025 akuchoka bc za chibwana bc kumangonama zoona alibeso ndi manyazi choncho The DC akamalankhula aziti amalankhula zonama 😊
@HamzahTwaib
@HamzahTwaib 7 сағат бұрын
Kukuyu ndichisilu inu,, tikamat alephela kulamulasoo boma azilesa zochitika manyadzi
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c 7 сағат бұрын
True story
@NelsonKasanga-b6q
@NelsonKasanga-b6q 8 сағат бұрын
Mawu mawu zoona koma noanduawa akutitola kyampili ,
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 9 сағат бұрын
Zowona kutenga afisi azake inquiry inafunika ikasankhidwe ku parliament only namiwa si fisi mwina asanduka kumene kukhala fisi
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Сағат бұрын
Palibe wabwino apa akuba okhaokha... Namiwa nayeso ndiwa corruption kale🙌🙌
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Сағат бұрын
@@eliffagondewe8214 ya ndavera speech yomwe alakula pule kuti akhala 4 weeks kufunafuna anthu abwino kuti afufuze nkhani ya ndege kusonyeza kut namiwa tisamukulupilire kwenikweni mwina pali deal pamenepa chifukwa inquiry timaganiza kuti ikhala mbali zosiyanasiyana koma ili mukati mwa boma ndikukayika kuti tipeze chilungamo chokwana. Kulumbilisa sitilumbira ku munthu yomwe akuganizilidwa komaso timalumbira kumunthu woopa Mulungu wamoyo.
@agnesKachikunji
@agnesKachikunji 9 сағат бұрын
💯 mulungu God protect you
@axtongilbert8048
@axtongilbert8048 15 сағат бұрын
Mfundo moya thumb up
@charlesmbewe4001
@charlesmbewe4001 17 сағат бұрын
Zoona zimenezi ndipo mopanda kuonjedza ai.
@RobertMakondetsa
@RobertMakondetsa 17 сағат бұрын
Kkkkkkkkk zavuta
@austinvincent1264
@austinvincent1264 18 сағат бұрын
ANTHU ANGODZUKA BAS KUPEKA NKHANI
@MathewsJanuary
@MathewsJanuary 18 сағат бұрын
Kuteloko munthu amene ndioyipitsitsa, m'nthawi iliyose amantchula mulungu ndicholinga choti akazangapanga choyipa tizikayikila Kuti ameneo sangapange zimenezo just bcoz amayakhula za mulungu, koma ayi ndinthu ili fiti.
@FreddieNkhoma
@FreddieNkhoma 18 сағат бұрын
We never know what Usi has been like!!!!!!!
@M.shukriAdams
@M.shukriAdams 18 сағат бұрын
Anthu amantchula mulungu nphanvu yake anayikana
@amoschataika7440
@amoschataika7440 19 сағат бұрын
Well said, big up
@InacioCement-t7n
@InacioCement-t7n 19 сағат бұрын
Exactly your right ngati akukumvani akupepeseseni ana achepa
@McDonaldZingani
@McDonaldZingani 19 сағат бұрын
Muli ndi nsanje inu
@yotamumkandawire-k8j
@yotamumkandawire-k8j 19 сағат бұрын
Iweyo watsala pang'ono kupita Ku mental hospital Ku Zomba.
@GeogeNkhoma
@GeogeNkhoma 20 сағат бұрын
Masukani mbuzi zimve
@JulietKapata
@JulietKapata 20 сағат бұрын
Exactly
@HawaHussein-d4l
@HawaHussein-d4l 20 сағат бұрын
Zikomo comrade ambuye akudalitseni poullula chilungamo
@HarriePearson
@HarriePearson 20 сағат бұрын
Good speech very good
@blessingsdouglas3
@blessingsdouglas3 19 сағат бұрын
Ase uli ndi mau abwino komaso ndiwe olankhula modekha nice
@margetjustin7170
@margetjustin7170 20 сағат бұрын
Zoona munthu wamkulu usi ndi oyipadi
@maryphiri2409
@maryphiri2409 20 сағат бұрын
Ndiwe mfiti apa ukuti ndiwe wamkulu?
@MercyManda
@MercyManda 21 сағат бұрын
Kkkkkoma you
@rhodrickmpumila1820
@rhodrickmpumila1820 21 сағат бұрын
Jealous sibwino amwene , Mesa Inu ndi a DPP ndiye simungazimvese
@OdettaLowrence
@OdettaLowrence 21 сағат бұрын
Amadalira ufiti, manganya machende ako, wayaluka ufiti basi, palibe akumvotere ndithu kalanga ine 🙆🏾‍♀️🙆🏾‍♀️🙆🏾‍♀️🙆🏾‍♀️
@OdettaLowrence
@OdettaLowrence 21 сағат бұрын
Ndi zoonadi usi ndi chigawenga ndithu, chilima anpangidwa upo ndi usi, apatso mai kaliati usi, kod ukufuna ukhale wekha, palibe angakumvotere iweo machende ako usi
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 21 сағат бұрын
Mukunenadi zoonadi Atsogoleri. Mwamvatu inu Azimayi mumatengeka ndi manganya kumuvinira za ziiii
@ChristianMalingamoyo
@ChristianMalingamoyo 22 сағат бұрын
Nkhani njakuti akuti ophunzila alimo muno koma akungoyang'ana
@MacdonaldMakokaDetector-gq2zt
@MacdonaldMakokaDetector-gq2zt 22 сағат бұрын
Zoonadi Mulanje Central ndife omvetsa chisoni. Timafuna udoba doba basi no nzeru. Manganyanso ndani? Kuchitura chipongwe kweni. Udziwanso
@chimwemwemondolo5126
@chimwemwemondolo5126 22 сағат бұрын
We can not mount on this.
@victorkaphaso4663
@victorkaphaso4663 22 сағат бұрын
muli uthengatu umu
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 22 сағат бұрын
Manganya ndi opusa kwambiri, tinene kuti ndi ochenjera, komabso nfiti.
@ThozaChilinjasanena
@ThozaChilinjasanena 22 сағат бұрын
zoonadi chilungamo,
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 22 сағат бұрын
You're right indeed
@georgechinangwa
@georgechinangwa 22 сағат бұрын
Manganya thathauzo lake ndi manganyera chichewa ndikuti osokoneza koma ndi muthudi oipa kwambiri