GAVANALA OLIMBA MTIMA WANENELATU PA IMFA YA CHILIMA AKUTCHINGA CHILUNGAMO NDI APULE

  Рет қаралды 5,827

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 20
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 7 күн бұрын
UTM ndi imene inawinisa chakwera ndie lero akut aima paokha anthu inuyo ndnu amene simukulifunira ziko lanu zabwno chifukwa zipan zonse palibe chimene chingaime pachokha ndkuwina
@FracksonMadani
@FracksonMadani 6 күн бұрын
Ndiye ngati Chakwera anawina chifukwa cha UTM ingalephere kupambana?
@MathewsChitambe-m6o
@MathewsChitambe-m6o 7 күн бұрын
Adah inu mumatha analysis,mumandisangalatsa, continue notifying us latex news.
@RiteRoderick
@RiteRoderick 7 күн бұрын
Ndipo koopsa amatha zedi❤❤
@JBMkonda
@JBMkonda 7 күн бұрын
Achoka bwanji inu a utm mukukula mtima kuti muima panokha
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 7 күн бұрын
Eti man akukula mtima koma chosecho sangawine. Ngati akufuna kuziwa chilungamo km kaka kt aima wokha
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe 7 күн бұрын
Eti eti ifeee amalawi tooonse ambiri tikufuna dpp utm and aford ngakhale udf kuti agwirire ntchito limodzi ndipo sitikufuna chibwereza aiiiiiiiii pamozi mcp chakwera akagwere basi ndithu kabambe sangawine payekha ai koma pakufunika munthu oziwa zachuma,zama connection ni wena osati zokula mtima aiiiiiiiii
@Alexchinangwa-k2q
@Alexchinangwa-k2q 7 күн бұрын
ndichoncho ameneyo anapha chilima
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i 7 күн бұрын
Anamuphadi sizofunsa
@isaaczuze
@isaaczuze 7 күн бұрын
Chilima anachita kuphedwa ndi chakwera ......munthu woyipa uyu achoke basi
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 7 күн бұрын
Ndipo or mwana amadziwa kut chakwera ndi mfiti
@CourageBanda-d1g
@CourageBanda-d1g 7 күн бұрын
Naweso ndi chanel yakoyi ukumalakhula wekha nkhani bwanji osayika zomwe alankhulazo timve
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe 7 күн бұрын
Kuti nkhoswe ameneyu Kuti achoke pakufunika inuyo dpp utm and aford pangani gwirizano ufd Atupele pawekha sungachite kathu chifukwa simungawathe amalawi tooonse ambiri tiri ku dpp ni APM basi and utm, aford and udf iri ni percentage tochepa ngati 1.5%
@DesireMoyo-y8x
@DesireMoyo-y8x 7 күн бұрын
Mkuchita kulilila migwilizano
@BlessingsNgomba
@BlessingsNgomba 7 күн бұрын
I pray musamayankhule kwambiri. Let us hear from the mouth of a horse
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 7 күн бұрын
NDIPO SAKUNAMA CHAKWERA CHIMUNTHU CHOIPA CHIKUKHALIRA LIPOTI KOMA AKACHOKA MBOMA NDI POMWE PADZADZIWIKE CHILUNGAMO
@PollyLysonLutepo
@PollyLysonLutepo 7 күн бұрын
Anthu omwe safuna kuti Imfa ya Chilima Ifufudzidwe ndi a UTM asatinamidze. Ndicho chifukwa amakakamila kuti aima pa Wokha. Amadziwa kuti akapanga m'gwilizano MCP Yiluza. Omwe anapha Chilima adziwika. Ndiye ndibwino tiime pa tokha kuti MCP yiwine Kafukufuku wa Chilima asachitike. Koma takudziwani chomwe m'makanira m'gwilizano.
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 7 күн бұрын
Ulibe nzeru
@spargomw
@spargomw 7 күн бұрын
Totally nonsense😂😂😂😂😂😂 thobwa nd thelere
Quilt Challenge, No Skills, Just Luck#Funnyfamily #Partygames #Funny
00:32
Family Games Media
Рет қаралды 55 МЛН
It’s all not real
00:15
V.A. show / Магика
Рет қаралды 20 МЛН
Prophet Uyu Walosera Zoopsa Pa Zisankho Zikubwerazi ... Tanvani
27:34
Sam Malvitha
Рет қаралды 102 М.
Prophet Bushiri wamudandaula Steven Kayuni, mnzake wa Kamajekete.
11:59
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 54 М.
Quilt Challenge, No Skills, Just Luck#Funnyfamily #Partygames #Funny
00:32
Family Games Media
Рет қаралды 55 МЛН