Comment yanga yopanda nzeru kwenikweni: Nduona ngat some songs mukamapanga, mumakhala smunapange your assignments/research well. Mafana aja ndaonerapo some interviews akufotokoza kut crew yao ndi chan and meaning ya dzina lawo kut linachoka ku chiyao chanchan osat the allegations kapena mmene timathanthauzira muja. I feel like the guys have been wrongly judged chifukwa chakusaita kwambiri info ya industry ya ma up and coming. I can even name oimba ambiri analandira some scores cz of kusowa kwanu kwa info komwe mmangokufuna nokhanokha mwa ulesi wanu. Ndinu madolo ndipo mukungoyenera kukonza zochepazo
@harryKamfose-xq6zs4 ай бұрын
duwa la eli njuchi imaziona
@FortuneLizigeni-kd9iv4 ай бұрын
Apa nde mumaonera nokhatu😂😂🤣🤣
@nicksonjohnjumbe83824 ай бұрын
King Hyphen kutulusa mwa mphamvu
@joelchikuse8874 ай бұрын
Komaso musamatinamize mutu wa phyzo uja moti ndi wa hip-hop? 😂😂😂
@happymwachande85114 ай бұрын
Chimwana Chosamba tulutsani ina
@lukepeter82904 ай бұрын
Hyphen bad company anatelo David kalilani aku disa desert eagle 😅
@CollingsMoyo-ym4pq4 ай бұрын
Mfumu hyphen sapala
@temwachikuse47474 ай бұрын
ah ah ma guy, bwezi mwaonesa zomwe zimaphikidwazo to promote his brand ka. mwatani kod? 🥲