komatu kunena dzowona dpp bola kusiyana ndi mcp achakwela ali ndivuto lokululukila akatangale komaso kuwophwedza amabungwe
@user-is5dl7np9g17 күн бұрын
A chakwera dzanja laremba pakhoma ufumu wanu wayesedwa pa mlingo ndipo wapezeka kuti wapelewera
@JohnFrank-cg1yh17 күн бұрын
Ngati Pali president amene wayenda kwambili ma ulendo opita kunja ndi Chakwera ,osava chisoni kumangoononga ndrama za boma athu akumangovutika very sad dziko losauka wina kumangoyendayenda ngat Malawi ndi england, msogolereli ngat uyu osazasakhaso 2025.
@user-gx8or3yz9u18 күн бұрын
Kunena zoona tonse yalephela mwa dad ndionabe chikhulupiliro kuti ukapolowu udzatha akalowa m,boma
@En-Richboy17 күн бұрын
Agalu awa akunyasaso bwanji APM my vote
@user-sq5dt3bc4u17 күн бұрын
Ndingowona kuchedwa ku vota ndimene ndikuwonela nyekhwe ,,,,chakwera wawonjeza
@salimmkumakumakitombi-yc7pw18 күн бұрын
First comment. kunjamba kunali Ngambwi ngambwi mmmmmmm
Tonse yamupangira campaign mkuluyu, ndipo savutika campaign yake.
@user-ii2sh1mz3r17 күн бұрын
Non of them will be good when it comes to ruling the nation of Malawi, APM and his cabinet were also rude, he was forbidding the citizens of Malawi to enter in their own country, he is also the devil , no one is better than the other
@user-wd9yd1bg9n17 күн бұрын
Stop the nonsense bro, you know the truth but you chose to lie. DPP is better than the so called tonse fuckin alliance
@jackwasili3118 күн бұрын
Adadi pachiwongolero bansi
@eliffagondewe821418 күн бұрын
Apm my vote 🔥🔥🔥🔥
@user-du9qs4tb6u16 күн бұрын
We coming back into power
@ishmaelsiffah990018 күн бұрын
APM ndibeleke
@LINNLYMBETA17 күн бұрын
God can make away where SEEMS TO BE NO WAY HALLELUJAH FORWARD EVER BACK WARDS NEVER ARISE AND SHINE YOUR TIME HAS COME TO RISE UP AND SHINE MALAWIANS ❤🎉🎉🎉
Chakwera ndi peter bola peter zomwe zinkachitika munthawi ya peter mwa chakwera sizikuchitika passport kukwera kwa zinthu kuba zochepa chabe zomwe akuononga chakwera
Which new blood are we expecting? I don't think so, since Malawi is the poorest country which also it's political system is the poorest in the world and whoever inspires to lead Malawi will opt to still money
@user-zi8pj5ey4t17 күн бұрын
Apm my vote
@CharlesKolawo18 күн бұрын
Adad woyeeeeee❤
@Uncle_B26517 күн бұрын
Maguyz nthawi zina zinenani chilungamoo awaa aonjeza kwambili ,,palibe boma losaba koma awaaa Ali very dager anthu ambiliiii akuvutika,,mavenda ogwila ntchito tonseee tikuliraaa katundu pasika daily akusitha mtengo mmmmmmm too much MCP
@JamilahChinyama13 күн бұрын
Chakwera thakati wakulu better last days not now
@user-mh4ht6tk2h18 күн бұрын
A pm my vote
@user-nf3ik3ff6y17 күн бұрын
Peter❤ 2025
@ThoccoBondo-mx7vt16 күн бұрын
2025 ikuchedwa bwanji
@beinhardkausiwa710716 күн бұрын
Dpp my vote
@user-lw4hw9ce4w18 күн бұрын
Mwandibandulira madolo atatunu bola kuzavotera better devel which is DPP
Anthu adali ndichikhulupiliro ndi tonse alliance kuti zinthu zisintha koma aaaaaa tidanyika nsima mmadzi pavuto pamavuto anzake komanso boma ili its the whole waste ever Apm my vote❤❤❤❤❤
@user-nj5vu8cd5l17 күн бұрын
Galu peter muthalika kupha malibino peter kuba nepotism galu chimbwe galu ndithu racist president andingwere uko galu iwe nyasi yakuba
@Mahmoodwargison-op2gm18 күн бұрын
Kumalawi kuno anthu andale omwe amatha kulakhula zoti zintha kupindulira amalawi ni ENOCK CHIHANA & ATUPELE muluzi anyamata awa aima pa fedro system of government osati zomwe alakhula apita
@user-dq9oe8sp8k18 күн бұрын
Bro andale ndokoma mkamwa Onsewa zawo mdzimodzi
@user-ux5md4cy3d17 күн бұрын
Mulamuloro wa DPP ndamangamo nyumba ine koma izizi za ose alayasizi palibe ndigalozepo iyaaa
@christophergibson7213 күн бұрын
Panopa azakoso akumanga plus magalimoto
@PaulKaunda-lj8vr17 күн бұрын
Komadi kunali munthu ndi dziwa chakwara kanyela wayamba
@Mike-du7zt18 күн бұрын
Kkkkkkk choose for better devil nxt year eti
@ancientnkhata113718 күн бұрын
Achina Billy Mayaya anaziona that time eish . Pakufunikadi better evil
@temwamfunejere15 күн бұрын
SKC vote
@osmanwanja373317 күн бұрын
Dpp and udf boma 2025
@Wiliam-jj8bn17 күн бұрын
Let Dpp rule again. Chakwela walephela ndinthu
@StevenSinoya18 күн бұрын
New blood? Where from? If it is from the same Malawi, mmmmm you are lying.