ZOCHITIKA ZA BRIAN BANDA 🙌🙌🙌🙌

  Рет қаралды 23,518

HOT 265

HOT 265

16 күн бұрын

Пікірлер: 95
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
DPP ndimbambande zedi guys eeeee mpakana Nkhokwe😂😂😂😂😂😂😂 eeee Bomaaa ilo😂😂😂
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂Namalomba atiii Chakwera ayambiretu kulongeza kaya timbale timasipuni Chakwera ayambiretu kuchotsa tiakatundu take APM wanyamuka akubweraaaaaa😂😂😂😂 DPP bomaaaaa lokoma zedi ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 15 күн бұрын
Uyu si si nsokhano ai km chivomelez
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 15 күн бұрын
😂😂
@user-el8to1te3l
@user-el8to1te3l 15 күн бұрын
Hahahaha
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂Chivomeleziditu chofuna kuzawola Chakwera ndi Chilima 😂😂😂
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
​@@patriciacraiton-sf5vu😂😂😂😂😂😂😂😂Eishiiiii chilungamo koopsa zedi mmm😂😂 DPP ndichipulumutso chaife a Malawi
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 14 күн бұрын
@@user-uc1pd1tc2x kkkkkkk exactly bro eish
@frankiechasokoneza5802
@frankiechasokoneza5802 14 күн бұрын
Khamu la anthu ili likundikumbutsa nthaw ya Bakili muluzi
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
A Peter senderaaaa senderaaa tilowenso m'boma ❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
😂😂😂😂Brian Banda akuti anthuwa mwatenga kuti?😂😂😂😂😂😂😂😂😂 osamasewera ndi DPP uzafa chidudu ili ndi boma loopsa zedi limatha APM ndie mankhwala a dziko la Malawi ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr 14 күн бұрын
Mcp ikadzangochoka mboma ndidzagona panja 💃💃🥳🥳 Suleman l like and love you, wangoyenera kudzakhala next president mu dpp 💙🔥
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
Ndipodi zoonad kwambiri brother wanga
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
Suleman kutsogoloku azakhaladi president
@lovenesskampira
@lovenesskampira 14 күн бұрын
Suleman ndi dada ameneyo samapanga nawo Dpp boma 2025!!!!
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 15 күн бұрын
Ndipo ndizotheka ndi adad❤❤❤
@VailetnyirendaShamah
@VailetnyirendaShamah 15 күн бұрын
Dpp woyeeeeeeee moto uyoooo kuti buuuuuii ife ana adadi❤❤❤❤❤🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤
@LongiMtimabii
@LongiMtimabii 15 күн бұрын
🔥 🔥 🔥 🔥 apm uja ndi mtunda wina wina
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
😂😂😂Ndipo ndi phiri Linalina zedi brother mmmmmm Peter Munthalika abale eeeeeee😂😂😂😂😂😂
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
APM my voteee ❤❤❤❤❤❤❤
@user-xm3zl5cg6x
@user-xm3zl5cg6x 13 күн бұрын
Ndipo MCP ndi ana awa akulila ndi nkozo awonaso kwacha unja Ali ku dpp ku MCP kuli kwada
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
Apa Prophessor Arthur Peter Munthalika boma watenga basi
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
Peter Munthalika azawina opanda opikisana naye, ndipo a MEC asazazichedwetsenso kumawerengera mavote chaka chammawa sure😂😂😂😂😂😂😂😂
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
DPP pachiongolero wina afune asafune ❤❤❤❤❤❤❤🔥🔥🔥🔥 okuba wa MCP akupachira soon❤❤❤
@user-te3ps3kf2t
@user-te3ps3kf2t 14 күн бұрын
Boma la tsakho lidzipita ,Lokondela anthu a ku Lilongwe
@BenissoneErnesto-eh6zs
@BenissoneErnesto-eh6zs 15 күн бұрын
Adad oyeeeeeeeeee
@user-cy7gd1go6y
@user-cy7gd1go6y 15 күн бұрын
Koma ine ndendikufa kukoma week ino bwanji apm 💪🔥🔥
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
Inenso brother mmmmmm❤❤❤❤
@NyalekeBanda
@NyalekeBanda 14 күн бұрын
Dpp yawo a kale
@user-ty9fv2qe5o
@user-ty9fv2qe5o 14 күн бұрын
Adadi amakwana 2025 boma
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
Bomaaaaaa iloooooooooooooooooo
@SEASERHASSAN
@SEASERHASSAN 15 күн бұрын
Peter muthalika ndikatundu omanga ndi wire kudula ndi graender
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
Adad woyeeeeeee
@ElizabethMajiga
@ElizabethMajiga 14 күн бұрын
Anthu okanda ziko lawo akusiyanisa posatengela tundu kapena Dela koma kunena chilungamo,Malawi salibwino kumavomeleza abale
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 15 күн бұрын
Emen ambuy chitilan chifundo Malawi
@VictorBandah-fj2ut
@VictorBandah-fj2ut 15 күн бұрын
Koma eeee kuli zinthu...amalawi samachedwa kutembenuza mcp angwa nayo
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 15 күн бұрын
M cp yikawonachocho yizimangirira DPP hoooooo yeee
@MarikoYakobe
@MarikoYakobe 13 күн бұрын
Adadi woyeeeee 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@user-du9qs4tb6u
@user-du9qs4tb6u 14 күн бұрын
We are getting back into power adad woyeeeeeè!!
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 14 күн бұрын
Apm Moto moto
@user-kf2zv2zo8e
@user-kf2zv2zo8e 14 күн бұрын
Dpp mbava
@user-nx7yz4qo8f
@user-nx7yz4qo8f 15 күн бұрын
Adad❤,akumva pain Dan Lu imba bro😅
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 15 күн бұрын
Takonzani bwino tikumango chita manyazitu pa nkhani zaku Malawi,ma wairesi onse kunja kuno akungo kamba zaku Malawi OLO tina tchona kunja Koma kwanu nkwanu zochitisa manyazi basi panopa mbiri Siri bwino
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
Zoonad kwambiri panopa Malawi Waipa wayaluka zedi Mbiri yoipa ilipaliponse Maiko akujawa komanso adzungu akudandaula zaulamuliro wa Chakwera Ndi Chilima
@sthoramexjrsa902
@sthoramexjrsa902 15 күн бұрын
Sure man ndikatundu
@owenskabazanechiumia3543
@owenskabazanechiumia3543 15 күн бұрын
Koma ndiye eeee Undipondera mwanadi Anthu atopa ndi MCP
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd 15 күн бұрын
Exactly
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 15 күн бұрын
Signal yaperekedwa apapa
@alfrednazombe
@alfrednazombe 14 күн бұрын
Wina ndiye kungopasidwaa ka data nkumanyoza kkkkk shame kom kudeen kulibe phwanya kkkkk kufoila bwanji kkkk ndala wankulu kumadya data kkkk wake up guys kkkk
@homeremedys3748
@homeremedys3748 15 күн бұрын
Ane Matumbi wamaso ngati tengetenge wajoina MCP
@FaroukSaliem
@FaroukSaliem 14 күн бұрын
Aka joina chifukwa alibe kalikonse mesa zaphweka ku mcp
@InnohLukah.1998
@InnohLukah.1998 15 күн бұрын
Brian..you mean za ndegezo siunamve kkkkkk
@trynessmsowoya4187
@trynessmsowoya4187 15 күн бұрын
Koma Brian eti ndenge yatani😂😂😂
@user-mg9ie2pi3d
@user-mg9ie2pi3d 13 күн бұрын
Vote my m p
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 15 күн бұрын
Muntharika ndi madala, take or leave
@user-dq9oe8sp8k
@user-dq9oe8sp8k 15 күн бұрын
My vote
@PaulKaunda-lj8vr
@PaulKaunda-lj8vr 15 күн бұрын
Koma kupusisidwa chakwara mutu ngati galu 😂😂😂
@SameKaposa
@SameKaposa 15 күн бұрын
😂😂😂😂
@SmithLikoswe
@SmithLikoswe 14 күн бұрын
Apm my vote
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
Malawi guys wafikapo, Chakwera ndi Chilima awononga dziko. Mumadziwa maiko akunjawa amalawi tayaluka ndipo tikunyozedwa koopsa kuti dziko losauka lotheratu la president osaphunzira opanda mnzeru osadziwa kayendesedwe kadziko. Mpakana adzungu ambiri achokachokako ku malawi coz cha ulamuliro. Kudura kwa zinthu atii sangakwanitsekoyi. Adzungutu mmmmmmm malawi wafikapo MCP mwatipha ndipo mukutichititsa manyazi koopsa, mpakana adzungu ena akuti ngati kuli chipani chozindikira cha anthu ophunzira odziwa za economy ndi DPP. Ma president ake anawatchula ati Peter Munthalika ndipo anena kuti mmene waonongeledwa malawi akufunika Peter Munthalika DPP ndipo tizaipatse nthawi zonse zizakhala bwino. Adzungu amenewa agulitsa manyumba awo ndima company awo awiri coz chakuonongedwa malawi ndi MCP
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 14 күн бұрын
Dpp my vote
@johnfrancis4671
@johnfrancis4671 10 күн бұрын
Zopasa mantha
@alexsumani6823
@alexsumani6823 15 күн бұрын
Agalu ena. Amfiti kumati anthu ena achoka kimpoto mmagalimoto
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj 15 күн бұрын
Mulungu adalise adadi bassi phamodsi ndi Malawian yyonse 2025 mashall Allah 🤟🤟🤟🤟from estan cap sauth Africa live now
@user-zg9jv5ns1c
@user-zg9jv5ns1c 15 күн бұрын
Bola MCP ichoka m'boma basi
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n 15 күн бұрын
Dpp oyeeeeè
@sidreckrashid9327
@sidreckrashid9327 15 күн бұрын
Koma tiwona zinthu
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 15 күн бұрын
Welcome to DPP
@user-mh4ht6tk2h
@user-mh4ht6tk2h 15 күн бұрын
DPP 2025 boma iloooooo
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 15 күн бұрын
Chakwera asinyera manyi amimba😂😂😂 kusikosera❤❤
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 15 күн бұрын
Chakwera wakomoka komwe aliko
@user-rl3os8ex1w
@user-rl3os8ex1w 15 күн бұрын
Zamabig
@CharlesBanda-kv8bh
@CharlesBanda-kv8bh 13 күн бұрын
M0ti munthu lero akhoza kumachemerera dpp,misala kapena kulodzedwa. Mudzalira dikirani
@ErnestManyera
@ErnestManyera 11 күн бұрын
DPP 😂😂😂😂
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 14 күн бұрын
Ineeee ndie kunva kukoma koopsa zedi eeeeeeee APM ❤❤❤❤❤
@GrecianWyson
@GrecianWyson 15 күн бұрын
Congratulations to my DPP
@AbrahamLLoyd-xb2xc
@AbrahamLLoyd-xb2xc 15 күн бұрын
Chipani changa❤
@sungananigondwe2807
@sungananigondwe2807 14 күн бұрын
Muzakhumudwa mukazaluza
@user-jo2zi6po8s
@user-jo2zi6po8s 14 күн бұрын
Kuvotera dpp nde Bola kuvotera chikomeni
@jeuzywandasigner4908
@jeuzywandasigner4908 11 күн бұрын
Ndyetu muzilongezelatu nonse ndi MCP yakoyo chaka chammawa chisadathe cz APM ikulowatu ndiye mudzasanzatu zamagwava😅😅😅
@user-eo2ol3ww8h
@user-eo2ol3ww8h 15 күн бұрын
analephera 6yrs
@frankbanda7333
@frankbanda7333 15 күн бұрын
Waboza iwe
@solomonlapson
@solomonlapson 15 күн бұрын
Kulephera umakudziwa koma
@user-nx7yz4qo8f
@user-nx7yz4qo8f 15 күн бұрын
Akakuyeze m'mutumo
@Annie-ls7po
@Annie-ls7po 15 күн бұрын
Chimene analephera ndi chani
@Annie-ls7po
@Annie-ls7po 15 күн бұрын
Aaaaaa kukutha wadya banzi
@wilisonbornface4282
@wilisonbornface4282 15 күн бұрын
My vote
@AffectionateGeyser-fm7dl
@AffectionateGeyser-fm7dl 13 күн бұрын
Dpp my vote
A CHIMWENDO BANDA KUSAMBWAZA DPP KU DOWA🙌🙌🙌
27:59
Super sport🤯
00:15
Lexa_Merin
Рет қаралды 19 МЛН
How I prepare to meet the brothers Mbappé.. 🙈 @KylianMbappe
00:17
Celine Dept
Рет қаралды 47 МЛН
Bro be careful where you drop the ball  #learnfromkhaby  #comedy
00:19
Khaby. Lame
Рет қаралды 36 МЛН
NKHANI IJA YAFIKA POVUTA KWAMBIRI🙌🙌🙌
30:26
HOT 265
Рет қаралды 22 М.
BRIAN BANDA LELO PA 6 MAY,  KWAGWANJI KUMUZUKUTA  DR CHILIMA 🙌
34:37
Village champion
Рет қаралды 29 М.
MOSES KUNKUYU EXCLUSIVE INTERVIEW
56:13
Zodiak Malawi
Рет қаралды 23 М.
Mbiri ya Joyce Banda
16:55
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 52 М.
Mkangano wa Kamuzu Banda ndi Samora Machel.
29:19
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 178 М.
HOT CURRENT/=ACHILIMA ALOWERA KUTI?
27:28
HOT 265
Рет қаралды 21 М.
ZOMWE ZIKUCHITIKA KU DOWA🙌🙌🤣🤣
12:48
HOT 265
Рет қаралды 6 М.
Super sport🤯
00:15
Lexa_Merin
Рет қаралды 19 МЛН