Because of arrogance and big-headedness, Malawi is being ripped apart. Brian Banda and George Kasakula discuss this in this week’s edition of Hot Current.
Пікірлер: 38
@chriskaidi68714 жыл бұрын
I like you guys your really fight us ndimakunyadilani here in cape town South Africa
@stanleydamalekani71134 жыл бұрын
Grt! izi ndizo timafuna osati zinazi .
@dyelekalokoku71934 жыл бұрын
Thanks alot guys ndinudi mzika za Malawi
@liki-likiladies---lilongwe69634 жыл бұрын
Kkkk koma guys u r making it... Big up guys... This is the only malawi we shall ever have
@williamsbanda92254 жыл бұрын
Yes Mr.Brian you are indeed for the poor citizens of Malwians, anthuwa ndi amodzi akudziwani,nkhani apa so amai away ayi nkhani ndi DPP party with few greedy individuals, koma Mulungu shall take over very very soon,instead of loosing job it shall be something else.
@roxtonmbawa80124 жыл бұрын
No point of correction main Jane Ansah ali nchiwanda not chiwindi matsulani nkhani ofunika deliverance mai uyu
@alexpeteribrameja18194 жыл бұрын
Alex is back in Town
@johanpieterse1944 жыл бұрын
Munakatokota mpaka 2024 hahahaaaa
@amosmbuka69454 жыл бұрын
Amalawi amzanga ziwani izi. Jane is a judge, then onani mmene wakhumudwisira fuko la Malawi. ziwani kuti paziko la pansi palibe judge oposera mwini wake Jahova. she must stepdown. Ngakhale Peter nthawi yake yatha he must stepdown as well.
@williammkhalipi51434 жыл бұрын
Mtambo is playing with u guys and he uses u mtambo tripecee Must fall,if U refuse why others , must,we,re sick and tired of,ur playing dirt, games,, , of politics working with, MCP utm,, we know they gave U better offers
@chesterphiri75234 жыл бұрын
Kkkkkkk safinyika kodi Brian ? Yes asafinyike aliyense
@moyo777774 жыл бұрын
timakunyadiran ma big.....man mumayakuraq chilungamo
@dysonmukhuna64284 жыл бұрын
Ma demo anuwo mukuti peaceful yet mukamachita katundu akubedwa mukaba mukamanga ma nyumba magalimoto mwagula ndiye muzilemba thank God zachani mpila osewela wina mumachuluka nzeru ndipo chili kwa mzako
@danielmpombera99624 жыл бұрын
Ndimakutsan akulu akulu kuno ku south africa
@chebedi4 жыл бұрын
Ndipinde shirt😝😛😝
@davismchenga33634 жыл бұрын
Kkkk true.
@fikiremariwa72524 жыл бұрын
Achokepo Jane pampando plz plz aboma
@nambelasilungwe53144 жыл бұрын
Chomwe akuopa a boma ,akawachotsa a mayiwo or akatulapasi ndekuti avomeleza Kuti chitsakho sichinayende bwino,
@dysonmukhuna64284 жыл бұрын
Mwaswa Japan embassy anthu oipa inu vuto simuatuluka kunja mukati muzituluka mukanaziwa kufunika kwake kwa embassy ndipo simukanaswa
@yamiechikhola67054 жыл бұрын
Jane Ansar mmmmm ndiochimwisa kwambir
@edisonnyasulu95684 жыл бұрын
Kunena zoona muli pa njanji kungoti mulungu alinanu
@beinhardkausiwa71074 жыл бұрын
The damage that is happening in the country is bcoz of one innocent Jane ansah.
@princenoah43904 жыл бұрын
Amayiyo akuopa chani kuusiya udindo. Palibe chimene angaluze akasiya. Koma akupanga mantha ndi a Peter munthalika kuti mwina adzafuna zawo
@sillahnyali54014 жыл бұрын
Apa nde timvera bwino kwambiri a munthalika alibe maso autsogoleri anangokhalapo kufuna kutchuka koma maso mphweya nde mmmmm alibe,Jane ansaah apite akapume ife tione zina
@zamcatahmed49494 жыл бұрын
Koma B B ndi Kasakula ndinu madolo
@louismayiwakuphaameneyorob97364 жыл бұрын
B b ndinu olimbadi mtima chifukwa thawi iliyose akhoza kukuphani ocz panja safuna muthu onena chilungamo
@yufufmapata14704 жыл бұрын
Musamuyikile kumbuyo mp amene uja certificate yogula Vuto lake ndilimenelo
@conductorhlongo89604 жыл бұрын
Jane Ansa ndiokula mtima akakhala wina akanachoka kale kale.Mademosration apitilire ngati katundu akuonongeka akafunse Janeyo ndi amene waononga zinthu.
@stewartkamwendo7354 жыл бұрын
Kumenyana komenyana njovu ovutika ndi udzu......... muzaziwa choona cheni cheni chikuononga malawi onani kachikena malamulowo America ndi dziko lalikulu koma zipani ziwili koma ndikomwe kunachokela kadzina koti ufu ndiye mumuone Malawi wantuyo ndimomwe timautengela ufuluwo ngati zimagwilizana zachisoni kwaife omwe sitinganiza zamawa
@dysonmukhuna64284 жыл бұрын
Stewart Kamwendo zoona izi anthu akuononga ka ziko kosauka aka
@dysonmukhuna64284 жыл бұрын
Eya anyamata inu mukukwanisa ntchito za satana bambo wanu ndi wambanda kuchokela pachiyambi kwake kupha kulanda ndi kuononga zimuonongani Malawi osauka kale
@ComfortNoahJofilisi4 жыл бұрын
Ma guys mmatha inu!
@molanaahmad8614 жыл бұрын
Tingogawana dzikoli kumwela presdent wanu ndi paetarayo , pakati pano ndi kumpoto presdent wathu ndi chakwela . Zitatelo phokoso litha
@innocentbvumbwe50754 жыл бұрын
Guys what you have said is very true if this people can understand your points you have raised here I think zikhoza kuchitira ubwino Kwa a Malawi ochuluka amene akuvutika chifukwa cha Jane
@dysonmukhuna64284 жыл бұрын
Noah Comfort Jofilisi samatha awa brother ma satanic awa
@simonchitenje65754 жыл бұрын
Zowona zake nzakuti Mai ameneyu chiwandachake akufuna kuphesa anthu ambiri ndi mzimai wosabeleka she is satanic woman.we can even see by her face.kunyasa ngati muleme.