Chilima akuyenela kubwelela ku dpp ndipo akhoza kukhala ndi ubale wabwino ndi amalawi komanso azakhala president otsatila pambuyo pa a Peter muthalika kusiyana ndikupitilila ndi mcp palibe angapange chanzeru koma hot current iyi ma guys mukukamba chilungamo zedi from durban south africa
@stevenbanda240919 күн бұрын
Mbavayo, lkhale konko ku alliance, UDF and DPP, Musa lore ku joiner ndi UTM leader.
@danielmsowoya910721 күн бұрын
UTM ikasiyana ndi MCP, MCP should forget that it can win on her own. It's better to stick to their initial agreement failure which they are out of power come 2025!!!
Chili a abwerere ku dpp ngati akufuna kukhala piece of mind
@SolokingChimzy-yt7dj17 күн бұрын
Zoona che Fatima...that's only the truth koma akabwelelaso akhala peace of mind komabe mtendele wake ukhala osakoma
@mozykavalo735218 күн бұрын
Amalawi aaaa tizingokhalila mcp utm dpp dzikoli anzelu ndi okhawo lets allow God to choose magufuli for us as nation not za dpp analephela kale amenewo ine nduona kuti its God who can giv us a leader like magufuli
@PrinceKachimanga20 күн бұрын
without UTM...MCP should forget kulowa m'boma...one a chakwera saadziwa kuyankhula😂😂😂😂😂😂😂😂
@JoshuaNyirongo21 күн бұрын
Noise vs news
@DysonMuwata21 күн бұрын
These gentleman are mabomba. Amaganiza. Bravo wonder , Chunga and Pankuku
@goodbossmw246820 күн бұрын
bushit ,onse aturuke(utm&mcp)
@DanielChikoti14 күн бұрын
Chilima my Vote whatever. He changed the mindset of many people. Chilima Chilima Chilima!!!!!
@user-dl1dg4yz1j21 күн бұрын
Anyapapi mwadya za MCP akatero. Bring back Brian Banda
@FrancisStima-sc7zs21 күн бұрын
UTM ndi MCP isatayane Ngati akufuna ipitilile kulamula kupandaapo ai DP P ndibwanawao osewa
@greysondymon89015 күн бұрын
Forget about winning . Their unity will remain a casualty.
@HarrisonHara21 күн бұрын
Amukhomelera chilima koma paja sataya Mtima nkatundu ameneyu😂😂
@chitanibenito110921 күн бұрын
A chilima ali ngati wa khungu yemwe ndiwongosatira kuli konse komwe owona akupita, this tym also he will b used koma zoti akhale ndichiyembekezo choti mikango ya mcp ingampase mpata ayiwale izo ndiye ayiwale.
@StivinMabandi21 күн бұрын
❤dpp piter oyeee
@OsmanOsher-sh6gp21 күн бұрын
Popanda UTM ku MCP , tiyiwale kuti MCP ikudzalowanso m Boma believe me
@africahasani-gl2nq20 күн бұрын
Chilima ndi munthu modzi ozakonetsa kwambili dziko la malawi
@user-nj5vu8cd5l21 күн бұрын
Utm my future my vote
@isaacmsumba12721 күн бұрын
UTM 🔥
@godfreykhungwa831619 күн бұрын
SKC is the Main character that's why he is always on people's mind en thought,,,,,,come rain or sunshine SKC & UTM is the next president MALAWI....!!!!!!!
@kondwanichiwanda22 күн бұрын
UTM my vote
@shaddaimaonga583221 күн бұрын
Brian banda & kasakula miss you guyz pa show imeneyi
@UmarAjussu20 күн бұрын
UDF AND DPP ❤
@user-qg4it7my9n21 күн бұрын
hot hot mumakwana watching from cape town malawi waora ndi mbuzi za atsogolerizi
@SamuelMukhura20 күн бұрын
you are right my vote is for Chilima
@RobertLuka-wy9cl21 күн бұрын
Mcp utm palibe angauze amalawi alephela basi
@samdiverson973319 күн бұрын
Apm only hope for Malawians chilima ummmm sanazipeleke Nsembe ku mtundu wa amalawi
@NumbDee21 күн бұрын
Ndamva kukoma kwabasi
@wanangwamwafulirwa883916 күн бұрын
Program yokoma kwabasi.....komano Brian Banda akakhalapo....bwezi zakomesesa
@rafiqlimbilira94020 күн бұрын
Munagwirizana kuti lero muvale Uniform pa program yanu😄