HOT CURRENT LERO ACHAKWERA MUGANIZE BWINO MCP |

  Рет қаралды 19,660

DZIWE TV

DZIWE TV

Күн бұрын

Пікірлер: 92
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 3 ай бұрын
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa God bless you all the time.
@simonpaul6567
@simonpaul6567 3 ай бұрын
Tangoyankhulai zoona mcp yagosaukisa dziko bisi pa 4 years
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 3 ай бұрын
Tinasiya kuyikhulupilila Times pano ndi Limpopo fm comred m,'tanyiwa more fire m'tanyiwa
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 3 ай бұрын
Komatu think twice ali ndi mwai kuti samagwidwa , koma atantenga a police kuti akapelereke umboni pa zomwe amayankhula zija apeleke umboni weni weni okhoza kukhumudwa akukana kuti alibe umboni pa zina zimene amayankhula kwa ife zija koma vuto ndilakuti ali ndi mbali ndie zinazi angoyankhulapo mokwiya koma munthu oimilira osauka sakuenela ku khala ndi mbali any government ngati ikuchita bwino mbali zina ayamikile, mbali zina ngati si nachite bwino aneneso, koma kuti timfuse bon kalindo anena kuti boma ili chabwino ya chita ndi chani, akuyankhani kuti ndi zero kufusa alimpopo FM ayankhaso kuti ndi zero. So apa zongooneselatu kuti ali ndi mbali so if you see this guy's akunena chilungamo mbali zonse akugunda eyetu , but sorry umu ndimmeneso ine ndimazionela , koma ndalemekezaso maganizo ako basi.
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd 3 ай бұрын
Exactly!!!!
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 3 ай бұрын
MCP zaka 4 zomwe apangako ndikupha Chilima basi fiti zawathu💔💔💔💔💔
@Geraldmkwewu
@Geraldmkwewu 3 ай бұрын
Prgm lzikhara choncho better pangono lero osamabakira zopoyira bomari lachakwera osapanga zinthu ngt mwadyesedwa Bazi atimes yakhulani chilungamo ziko ndilanu plz
@mathewsmakina7845
@mathewsmakina7845 3 ай бұрын
Ma Tv station apamalawi amapembedza Boma basi ife kuno timamvera Limpopo FM osatizanuzo zomapembedza Bomalo ayi Brian Banda munanchotsa pa Hot current chifukwa samafuna zachinyengo ayi pajatu ndi m,busa weniweni osati ubusawake opha anthu ayi tikufuna Brian Banda abwelere pa hot current tidzayambanso kuikonda TTv
@TheresaNtodwa
@TheresaNtodwa 3 ай бұрын
Azikhale ngati amakanika kuvala bwino okha .angakhale ndinthawi yowasamala apolice .ali bizy kumanga anthu .sakuziwa kuti nthawi yathera angoona ngati adakali chaka choyamba ....APM more fire🔥💪
@JosephNsona
@JosephNsona 3 ай бұрын
Tifunsireniko a wonder ndi apankuku expenditure ya maliro anthu 8 kuphatikizapo amene anali vice president Dr SKC, we are still waiting from Government
@InnocentMlowoka-ew4lo
@InnocentMlowoka-ew4lo 3 ай бұрын
Minimum wage is nothing with devaluation 80%😂😂😂😂
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 3 ай бұрын
Amalawife tinasiya kukumverani kalekale and zimenezo muziziwe from today onwards, inu ndamcp crocodile dance party
@GraceMaida
@GraceMaida 3 ай бұрын
Musawanyengelele agalu amenewa palibe chapanga iwo olo chimodzi koma kupha chilima ndikuba ndalama zamisonkho yathu akagwere afiti amenewo
@ArnoldBanda-b9q
@ArnoldBanda-b9q 3 ай бұрын
0
@ibrahimalfred6539
@ibrahimalfred6539 3 ай бұрын
Pempho kwa ayini ake Chanel itchi zingatheke kuti ma program anu special videos kuti muziika full screen not other side pink then videos izikhala pakati I'm saying this because other people's the got small phone please we love your Chanel
@PetroMatias
@PetroMatias 3 ай бұрын
Sakuyankha mofanana ndimafusoo Ali ndimbali mcp palibe chachitika
@mathewsmakina7845
@mathewsmakina7845 3 ай бұрын
pankuku ndi wa Mcp chimwendo mene akumangozela amalawi angamve kupepesako sitingamva ayi musaipitse Tv yanu ayi lankhulani point yachilungamo kuti chakwela ndi Mcp yakeyo alephera basi ine ndikuwapatsa 1/10 osati 4/10 ayi watimzunza ife amalawi kwambiri
@miltonkanyamula9486
@miltonkanyamula9486 3 ай бұрын
Today's hot current has not been realistic.a pankuku akuwoneka kuti ali bias. Coz analysis umanene the good and the bad But zonse zikuoneka ngati pallibiletu chomwe chachitika. Thats not fair l think Rayana chunga is more analytical than a pankuku.and l have missed him. Chonde timakukondani but you can do better than zomwe analysis yanu ya lero.
@CharlesChipwere
@CharlesChipwere 3 ай бұрын
Palibe chimwe achita away mwina pakuopyseza anthu ndikomwe akwanilitsa kumamanga anthu mudzina lacyber crime
@JUMAHSabiti
@JUMAHSabiti 3 ай бұрын
Very useless 😕 😒 😑 ufulu nawo palibe nanu muzinena ndikutha kumanenako chilungamo
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 3 ай бұрын
Tangonenani zowonga gyz 4 yrs MCP palibe chachitika makape a MCP azipita
@mathewsmakina7845
@mathewsmakina7845 3 ай бұрын
Apankuku musakhale ngati chawezi Banda ayi Kodi kwatsalaku misewuyo aimalizakodi chakachimodzichi kapena mwadyanawo ndalama zamagazi zikungogawidwa chisawawazi musaipitse TTv ifetimaikonda mukapitiliza tikutumizani Ku mibawa muzikayamikira limodzi ndi chawezi Banda
@awardjafar2928
@awardjafar2928 3 ай бұрын
Imagine mene amavalira nachibuluku zikhale ng'oma muja you think angagamgulire wina nsapato
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 3 ай бұрын
Nanunso sixoti muziti ayamba, ayamba chani nawe chomwe akupanga ndichani? 😡😡
@ShadreckMatenje
@ShadreckMatenje 3 ай бұрын
Apamkuku muli Ku rainbow mumaswa mosaopa NDA Aubrey kusakala koma Ku times mukumaopa chifukwa chani. Amsiska muitaneni kusakala azizaswa
@SamuelYakobe
@SamuelYakobe 3 ай бұрын
You're going to loose more customers if you will not caring.
@HaliJana
@HaliJana 3 ай бұрын
CHAKWERA MMUTUMO OKHA MAMINA 2026 NDIZAMUCHINDA MKAZIWAKO IWEYO UKUONA DIKILA UZAZIWA KUTI KHOBWE SI NYEMBA
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 3 ай бұрын
Palibe chabwino olo chimodzi hiyaaa osamangoti cyclone anasokonedza ngt anachitapo kanthu
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 3 ай бұрын
Mwadzya ndalama inu musatipusitse ndinu zitsiru za anthu mukubwera so ngati muyakhula za mzeru zili zopusa zokhazokha
@Lizzie-h1k
@Lizzie-h1k 3 ай бұрын
I repeat..the score is 4% end of story😅😅😅...I do not apologize to anyone..
@EdenNgulube
@EdenNgulube 3 ай бұрын
Mcp siyinabwelele ku zakodza zinthu koma kwao ndi kuba kupha ndikuwononga. anthuwa amadana ndichilungamo ndanena ndanena
@ArexBright
@ArexBright 3 ай бұрын
Kunena zoona chakwera chazelu chapanga iye muzaka 4 ndi kupha amalawi bas kugwesa kwacha kuwanamiza ndi kugulisa amalawi ku Israel bas
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 3 ай бұрын
Iwe pankhuku zonse pa mmalawi wakumudzi zilibe ntchito anthu akufuna azidya katatu wosati zomwe ukunenazo
@NgongireMwakasungula
@NgongireMwakasungula 3 ай бұрын
Mbuli za dyera inu mukuyankhula za mcp kapena tonse muli Malawi momuno inu mbuli zeni zeni limpompo fm mofaya
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 3 ай бұрын
Nkhani ndi limpopo fm not ziwanthu ixixi Zoti zidadya kale ndalamazi😡😡
@SharifMajiga
@SharifMajiga 3 ай бұрын
Times ndiya mcp Anaigula, bakili muluzi tv is the best ❤ ever
@AronAlfazema
@AronAlfazema 3 ай бұрын
Ndizimvela program ya Banda ? Wander dzakoyo ndi kape ameneyo wa MCP
@ProspaMitumba
@ProspaMitumba 3 ай бұрын
kkk hot hot lero ndemwalakhura zanzeru koma 4/10 mwanama amenewo or 2 sanafike ife a pre wo tinatopa nawo
@AllunaBenjamin
@AllunaBenjamin 3 ай бұрын
Atolakhani times mwakomedwa ndi ndalama
@Enock-c9l
@Enock-c9l 3 ай бұрын
Mwayamba kulephela kuyamkulatu mukuoneka kuti mwamezatu banzi
@DalitsoPhiri-sq5nl
@DalitsoPhiri-sq5nl 3 ай бұрын
Ndalama Ali busy kumapeleka kuma fumu akapita ku state house komanso kumangolemelesana ku mipandoko yeti mzipala mankhwala akusowa ku emigration zinthu sizikuyendako machine sakupedzeka tinene kuti zeru zilipo pamenepo
@Lizzie-h1k
@Lizzie-h1k 3 ай бұрын
Kkkkkk....a Zikhale ndi stretegist wa Tonse?? and the score is 4%😅😅😅😅... not 40%.
@chimwemwechiundira6002
@chimwemwechiundira6002 3 ай бұрын
Faka moto. Ndanenandanena!
@JIMMYWATHONJE
@JIMMYWATHONJE 3 ай бұрын
Hot current wodree umafuna kumenyela a mcp compain
@BrightZionga
@BrightZionga 3 ай бұрын
Andevu zamwai mkunena zoona kumakhala kunena kwaumphawi
@GiftMlinde
@GiftMlinde 3 ай бұрын
Talking guys 💪💪
@JuuuKomba
@JuuuKomba 3 ай бұрын
😂zikhale wake uti angaone zamavalidwe
@prophetjacksonmakonda63
@prophetjacksonmakonda63 3 ай бұрын
The coming term they will be a world war 2, they will come with more excuses, let chakwera and his tonse alliance and his administration must go, we dont need chirichonse chokwera mdziko lathu
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg 3 ай бұрын
Inu ndizisilu ngt muli nd zilu musiya kupanga ma program chakwela wapanga chani nyani ameney
@martinsailesi1731
@martinsailesi1731 3 ай бұрын
Kodi masiku 21 wolira atha kale ku boma?
@SamuelYakobe
@SamuelYakobe 3 ай бұрын
Tamva Kale za inu mmalawi akutulukani ngati anzanu aja.
@sweeneykamwendo6251
@sweeneykamwendo6251 3 ай бұрын
BMTV is the best
@Enock-c9l
@Enock-c9l 3 ай бұрын
Mmmmm kodi nanu mwayamba utabwanji ??
@ArnoldBanda-b9q
@ArnoldBanda-b9q 3 ай бұрын
P P
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 3 ай бұрын
A Brian alikuti tisrkeko apa
@vegon357
@vegon357 3 ай бұрын
Dziswe dzimenedzi😢
@AmusedDimSum-hd5yp
@AmusedDimSum-hd5yp 3 ай бұрын
jona ndi wa mcp uyuakulephera kuya kha
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 3 ай бұрын
Mcp palibe yapanga ky kwa athu odya banzi km kunena chilungamo mowopa mulungu awa zawakanika
@BrightZionga
@BrightZionga 3 ай бұрын
0. Pa 10😂😂😂😂 miliri ya chani
@DKMWALE-ew3lp
@DKMWALE-ew3lp 3 ай бұрын
Lost hope
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 3 ай бұрын
Inu ndi angalu kobas mokanene kuli ufulu wake uti
@MosesShaibu-ee8hn
@MosesShaibu-ee8hn 3 ай бұрын
Andevu zamwayi akupatsani ndalamainu a mcp
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 3 ай бұрын
Bakili Muluzi TV.
@DominicNantowa-t4d
@DominicNantowa-t4d 3 ай бұрын
Nkhani zimenezi ife timazinvesa bwino pa Limpopo FM bakili muludzi TV bon kalindo the DC inu tamalambalalani ndi timambanzi mukumadyato kung'alula kung'alula bas chilungamo chimamasula munthu iya.
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 3 ай бұрын
I'll feel you guys keep it up osamakhala ndi mbali poyankhula, koma awa a MCP -wa zinawavuta zambili why achakwela luso la usogoleri waziko alibe mwina kumpingo analiko mwina coz enafe kunalibeko. Waonekelatu kuti ali ndi nzimu ongopempha basi waubusa-ubusa eeh okama yowonda kale in the name of Jesus ziko sili ngapite pasogolo
@ThandiMbewe
@ThandiMbewe 3 ай бұрын
Kupepesa kwa chani poti amaziwa chomwe akufuna ndi kupanga, kodi muli mbali iti????
@ChikondiAbdul-hk9cd
@ChikondiAbdul-hk9cd 3 ай бұрын
Palibe chomwe angapange awoo
@GodiflyNazombe
@GodiflyNazombe 3 ай бұрын
I lespet blian bamba
@IshmaelNesta-rb8dx
@IshmaelNesta-rb8dx 3 ай бұрын
Mau oti ayambapo mumayenera kumayankhula two yrs ago now it's too late kuyamba xitukuko...nthawi Yao yatha kale....soon we are going them OUT
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 3 ай бұрын
Musatithelepo bando yathu apaa, ife timamvela limpopo FM with mtanyiwa alongside bakili muluzi tv komanso Borne Kalindo
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 3 ай бұрын
Cakwera canzeru comwe ampanga mudzaka four ndi kupha chilima imfa zosaneneka
@liz9425
@liz9425 3 ай бұрын
Limpopo FM omwe timamvera imatiuuza zoona!!! Inudi aaaa mwanyambititsidwaaaaa
@GogomphatsoSinosi
@GogomphatsoSinosi 3 ай бұрын
Komano izi amakhala ndi nthawi yomazimvera adindowo kapena tikumanvera ndi kuonera akafa tisiyanji tomwefe
@AllunaBenjamin
@AllunaBenjamin 3 ай бұрын
Atolakhani times mwakomedwa ndi ndalama musatitayise nthawi 17:02
@LuciusLungu
@LuciusLungu 3 ай бұрын
Koma ife tilila mpaka 2025 September. Osati 21 dys yanu iyo 😭😭😭😭
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 3 ай бұрын
Awuzeni kuti azipita asadikire masankho a malawi sitikufunanso kumamva za tonse a liance, palibenso chomwe ayamba nanu musamachite mantha poyankhula , chomwe achita ndi kupha chilima ndi ena komaso kumanga anthu, palibenso chanzeru mukuyankhula mukanangosiya tikufuna anthu osaikira boma kumbuyo iyaaaa
@alexsumani6823
@alexsumani6823 3 ай бұрын
KUSWAKUSWA,kugagadakuhagada 👍
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 3 ай бұрын
Kukhapa Kukhapa kkkkkkkkkk.
@JonathanChinomba
@JonathanChinomba 3 ай бұрын
Munasiyilanji kwagwanji wakasabola uja lachinayi sanakuopsezani amcp
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 3 ай бұрын
Koma ndalama zogula anthu ndi zimene zilipo
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 3 ай бұрын
Chakwera must go.
@simonpaul6567
@simonpaul6567 3 ай бұрын
Jona ndiwe wa mcp kupepetsa kwa chani
@GeraldMustafa
@GeraldMustafa 3 ай бұрын
Lelotu Bola azimvere okha 😂😂
@MikeDael
@MikeDael 3 ай бұрын
Bola lelo Times mwakambako zolongosoka.
@FelixBoss-yn9pe
@FelixBoss-yn9pe 3 ай бұрын
Nde mwati zikhale chani kkkkk
@NelsonMhango-j1d
@NelsonMhango-j1d 3 ай бұрын
Ulemu wanu
@MsondaBanda
@MsondaBanda 3 ай бұрын
Wali kuchitako Mzimba Bridge,
@mayomayo-uf9hu
@mayomayo-uf9hu 3 ай бұрын
kkkkk
@AwaliBlack
@AwaliBlack 3 ай бұрын
Mumasiya pati kuzuzula zithu ngati zimenezi muli bho
@ArnoldBanda-b9q
@ArnoldBanda-b9q 3 ай бұрын
Np
Tensão em Manica: Venâncio Mondlane Desafia Frelimo em Vanduzi
1:17:33
GIANT Gummy Worm Pt.6 #shorts
00:46
Mr DegrEE
Рет қаралды 107 МЛН
SHAPALAQ 6 серия / 3 часть #aminkavitaminka #aminak #aminokka #расулшоу
00:59
Аминка Витаминка
Рет қаралды 2,2 МЛН
iPhone or Chocolate??
00:16
Hungry FAM
Рет қаралды 46 МЛН
It's Topical | Cabinet Announcement Preview
49:50
SABC News
Рет қаралды 137 М.
Malawi appoints Dr Michael Biswick Usi as Vice President
6:54
Customer Care Sn2 Ep 62A
23:00
TRUST FILMS
Рет қаралды 26 М.
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 119 М.
LUCIUS BANDA EXCLUSIVEINTERVIEW - 20 MAY 2021
56:54
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 148 М.
UTHENGA WA A CHAKWERA  NDI UWU  |
25:37
DZIWE TV
Рет қаралды 240
GIANT Gummy Worm Pt.6 #shorts
00:46
Mr DegrEE
Рет қаралды 107 МЛН