HOT CURRENT/ LERO PA 7 APRIL 2024

  Рет қаралды 16,190

HOT 265

HOT 265

Ай бұрын

Пікірлер: 69
@douglastholo390
@douglastholo390 Ай бұрын
Well researched topics and well analyzed with constructive arguments that intend to assist in building the nation.
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Ай бұрын
Tiyamike ndinthu azibambo mwayankhula momveka ngati ali makutu anthu a menewa amvetsere ndinthu🔥🔥🔥
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d Ай бұрын
Ma big zikomo kwambiri polikonda dziko lathu koma choti mudziwe chakwala ndi galu plus ndi wakuba ndiye palibe chomwe angachitepo
@user-zf8hx9cf7p
@user-zf8hx9cf7p Ай бұрын
Big up ❤
@user-pk6vq1cr1b
@user-pk6vq1cr1b Ай бұрын
Thanks guys you always do the best 💯 percent continue to deliver powerful message
@user-xq3vq4yr1h
@user-xq3vq4yr1h Ай бұрын
I blv zomwe ananena kalindo was very true anagula machine opoira nanga tizit chani
@George-zd5le
@George-zd5le Ай бұрын
Ooooh Ambuye thandizani Malawi 🇲🇼 kuchosa president chakwera chifukwa ndiwoyipa wakuba komanso wankhwizi.
@user-fd1tu6ku1r
@user-fd1tu6ku1r Ай бұрын
Boma la Chakwera ndi Tambala Party lalephera
@jonathanmalanda7742
@jonathanmalanda7742 Ай бұрын
A Malawi ofunika kulapa machimo Anu palebe mmalawi Amalankhula chilungamo
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r Ай бұрын
Chakwera azachoka mowawa musiyen even azayesere kuba kwakeko koman mulungu awakatha ndithuuuuu
@mitochilukas9170
@mitochilukas9170 Ай бұрын
Solution chakwela walephera ndi boma lake
@ChifundoNinje
@ChifundoNinje Ай бұрын
Ndipo ineyo sindinaonepo muthu okuba ngati chakwera ndi nduna zake
@StiveKantiki
@StiveKantiki Ай бұрын
Kulibe akuziwa olo apulewo saziwa kanthu angoziwa Kuba basi
@Johnybegood260
@Johnybegood260 Ай бұрын
ndiye chitsiru china chiza votela MCP
@MalawianCamera
@MalawianCamera Ай бұрын
Big up
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Ай бұрын
Even akanakhala kut ndi a DPP okhaokha ndie inu ngat Boma muzingowayang'ana anthu akukhapana??? Mesa timati palibe Ali pa mwamba pa lamulo???? Stupid government ever.
@EstherPeter-cf1vf
@EstherPeter-cf1vf Ай бұрын
Anthuwa onse ali cholinga choti adzabele ma vote chaka cha mawa
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 Ай бұрын
Ndiye ife tikamati ulamulira ukulephera mkulakwa?
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v Ай бұрын
Zikhale ng'oma pamozi ndi Chakwera zeru alibe Kulibwino anthu awiri awa atule pasi udindo chifukwa palibe chimene akupanga
@homeremedys3748
@homeremedys3748 Ай бұрын
The DC Osachita Mantha Tabwelani ndima audio aja this is Democratic country, Mukuopa boma ili ladzitsilu
@Tawina0101
@Tawina0101 Ай бұрын
Anamulanda Foni ku police,,,akuti akufufuzamo
@user-gd3jx7tr1p
@user-gd3jx7tr1p Ай бұрын
Zosezo vuto NDI dpp ndiyomwe ikubweretsa mavuto Ku migration alowesa ndale Malo monthandiza zika zawo
@kennedybanda
@kennedybanda Ай бұрын
Zoonadi anthu akumwalira chifukwa chopanda passport yoti apitire kuchipatala chakunja akalandire thandizo. Boma ili likupha anthu mwachinsinsi.
@OsmanGift
@OsmanGift Ай бұрын
President wathu ndiwopepela
@MmikeeMateyo-kj2pn
@MmikeeMateyo-kj2pn Ай бұрын
Mwachidule kwambili chakwelayo ndi galu komaso mbuzi
@VictorGondwe-zs3vx
@VictorGondwe-zs3vx Ай бұрын
Ndipo ngati a boma amava bwezi akuphuzirapo china chake apa makosana mukumasula osawopa ayi ndipo osafooka tiyeni nazo ndi ziko lathu
@jamesgama5489
@jamesgama5489 Ай бұрын
Inu ndi anthu okonda dziko lanu kwambiri pitirizani kutumikira amalawi
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk Ай бұрын
A MCP anaiwala kuti ukanama sikuchedwa kucha, MCP kunama too much
@user-hg4rm8xn5t
@user-hg4rm8xn5t Ай бұрын
Kwa amene amatsatila za utumiki wa Mr Twaibu Ahamad Alli ali ndiumboni pa zomwe mukunena azibambo inu
@leveltrapper4322
@leveltrapper4322 Ай бұрын
I lost his group link tipangen tiipange follow link bwaa
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg Ай бұрын
Boma kulamulira ngat banja
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Chomwe akuziwa ndikumanga anthu opanda chifukwa akamawawuza chilungamo
@kennedybanda
@kennedybanda Ай бұрын
Chakwera achotsedwe kumene 2025. So Immigration CEO ndindani kusachotsedwa timudzutsira Ayaya.
@user-oe1lg4xo7w
@user-oe1lg4xo7w Ай бұрын
Guys matuvi Ali ku immigration adanyera ndi chakwera nchifukwachake akulephera Kosova mavutowa. Achakwera , azikhale ndi immigration officials atule pansies maudindo
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b Ай бұрын
Mai yolamuwo ndi MDF panopa ili ku mcp siyoziimilaso payokha ai panopa inagulidwa mpakana ndi mec yomweso fundo kachali ndi a mcp amenewo onsewo
@SymonNamalomba-sh3fu
@SymonNamalomba-sh3fu Ай бұрын
Which A president are you talking about
@user-hy6gc6ld9w
@user-hy6gc6ld9w Ай бұрын
Kalumo , zikhale onse anasankhidwatu ndi chakwera okubayi ndipo chakwera pakha sapanganso chiganizo ali ndi anzake komano kodi anzakewa ndiyekuiti amawawuza chani abwanawa chakera ndianzake onse ndi mbava anthu okuba mochitisa manyazi
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g Ай бұрын
MCP simalabadira kulira kwa amphawi bola iwowo zawo ziribwino tikayankhula chonchi aziti tikudananao
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d Ай бұрын
Chakwela ndi zikhale ng'oma ose ndakuba ndi zinkhumba ndi makape
@user-cb2cv9fz7m
@user-cb2cv9fz7m Ай бұрын
Kkkkkkkkk ma big inuyo mumatha kuyankhula mwamzeru, mbuzi za anthu including chakwera mbava yaikulu apite uko,bodza basi
@kennedybanda
@kennedybanda Ай бұрын
Kaku Immigration kaja nde kamapambuka mwano.
@petrooverton6643
@petrooverton6643 Ай бұрын
solushoni ndi chakela chifuka chakela ndiye bwana awo ngati sisitimu yaonongeka bwanji osagula ina
@nnmzakwachamzakwacha9405
@nnmzakwachamzakwacha9405 Ай бұрын
Chakwera has failed beyond. How do you believe in someone on retirement.
@user-nk5mj5ws8v
@user-nk5mj5ws8v Ай бұрын
achakwela adziwa bwanji asakuyendela mene dzikuvutamo ango yangula ali kunyumba ndi nsogoleli ovensa chinsoni
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Vuto ndiloti boma la MCP silikufuna chilungamo alitenga dziko la Malawi ngati family yawo tiwonana 2025 Muli busy ndi kudya misonkho ya amalawi palibe Chimene mukupanga
@ChristopherBaluti
@ChristopherBaluti Ай бұрын
The president is wik
@dorcasmwale6328
@dorcasmwale6328 Ай бұрын
koma mukudziwa kuti anthu akutuluka atanyamula ma fake papers, anthu akutenga ma risk kuyenda opanda passport
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v Ай бұрын
Mavuto ochita kufuna, tamuyitanani Timothy Mtambo kuti akufotokozeleni pa program yanu chifukwa ndi mmodzi amene atifikisa pamenepa ngati dziko.
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d Ай бұрын
Achakwela zoti anali abusa mmmmmmm linali dzina chabe kuba nkhaza many of God 😂😂😂😂😂😂 zaboza galu iwe walephela magilass ngati fulu
@user-ig7dv8rp7r
@user-ig7dv8rp7r Ай бұрын
Makape a MCP azaziona
@user-nw6ie3xx8b
@user-nw6ie3xx8b Ай бұрын
This hot current yinali yachongo no one was giving a space to talk
@AmusedDimSum-hd5yp
@AmusedDimSum-hd5yp Ай бұрын
kalumo ubongo udauma kalekale
@user-ek7mv2vo4f
@user-ek7mv2vo4f Ай бұрын
Kukhapakukhapa
@SynodAudit
@SynodAudit Ай бұрын
kuteteza forex
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Ай бұрын
Chakwera ndi munthu wa bodza kwambiri, ngat amanena chilungamo ndie kut amakanena kwa IMF ndi world bank chifukwa kumeneko ndikumene kuli anthu omwe akuwatumikira.
@SynodAudit
@SynodAudit Ай бұрын
kuteteza forex kkkkkkkkkkkkk
@mchipengule
@mchipengule Ай бұрын
Tikamanena munthu tiziganizila kaye, chifukwa mwina zitsilu mukhoza kukhala inu anthu akuchikamwa. Sitikudabwa chifukwa chingakhale ana a Israel mchipululu amalankhula ngati mmene mukuchitila inu. Anthu mulibe pabwino mwinaso amene mumafuna kuba ndinu mukulankhulanu a Dpp nanga izi zinayamba zachitikapo? Asiyeni azanu agwire ntchito kufikila zitheka. Nanuso a Times mumaonjeza kwambiri mumaoneka ngati azeru kwambiri kapena mumafuna udindo? Tiphuzile kulemekeza a dindo enanu ndinu alaliki pamenepa. Kumbukilani ana a Israel mchipululu tikamayenda njira mumakhala zambiri. Dzisungileni ulemu please chonde.
@ZelinaKisswell
@ZelinaKisswell Ай бұрын
Ulemu umapita Ku ulemu uzake Mesa anayamba ndi kalumo kunyoza nde iwoso atopa zikanakhala KT Iwo amawayankha bwino professionally I don't think bwezi a times akulankhula chonchi
@user-gz9iy7sd7j
@user-gz9iy7sd7j Ай бұрын
A Times akulankhula chilungamo asamanyengerere munthu.
@leveltrapper4322
@leveltrapper4322 Ай бұрын
Zako izooo aseh koza TV yako uzilankhula mwa ulemu wakowo..
@user-cf9yz3ei5o
@user-cf9yz3ei5o Ай бұрын
Gentlemen no .matter how much we can talk Malawi died sometime back economically
@user-hg6qp4hs2m
@user-hg6qp4hs2m Ай бұрын
When sometime back you talking
@shupikayintuwaluwa-5899
@shupikayintuwaluwa-5899 Ай бұрын
N then, as a citizen wat z ur responsibility on that matter
@mabvutochimkondenji910
@mabvutochimkondenji910 Ай бұрын
Chakwera 2030;woo
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Ай бұрын
Mmm ukunama ngati dziko lili lake
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b Ай бұрын
Uzamuwinisa iweo 2030 chakwera basi 2025 mukapitilize kulima uko kuminda yanu ikukudikililani inu abyapapinu
@user-gz9iy7sd7j
@user-gz9iy7sd7j Ай бұрын
Noway Chadwell is going 2025 no matter what come day come sunshine.
@douglastholo390
@douglastholo390 Ай бұрын
Well researched topics and well analyzed with constructive arguments that intend to assist in building the nation.
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v Ай бұрын
Zikhale ng'oma pamozi ndi Chakwera zeru alibe Kulibwino anthu awiri awa atule pasi udindo chifukwa palibe chimene akupanga
Iindaba zesiXhosa @13H00 | 14 May 2024
21:11
SABC Iindaba
Рет қаралды 21 М.
6 às 9 |EDIÇÃO DE QUARTA-FEIRA |15|05|2024
TV Sucessomoz
Рет қаралды 284
Normal vs Smokers !! 😱😱😱
00:12
Tibo InShape
Рет қаралды 26 МЛН
McDonald’s MCNUGGET PURSE?! #shorts
00:11
Lauren Godwin
Рет қаралды 35 МЛН
Useful Gadget for Smart Parents 🌟
00:29
Meow-some! Reacts
Рет қаралды 10 МЛН
DNA Tinashe Mugabe Padare Rachief Mutasa
15:49
TICHKACH MTV
Рет қаралды 16 М.
TIKUFERANJI 01 AUGUST 2015
25:43
Edson Gunsalu
Рет қаралды 329 М.
CRUISE 5 WITH PATRICIA KALIATI
59:03
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 150 М.
Expresso Show | 15 May 2024 | LIVE
Expresso Show
Рет қаралды 802
P9 DURI FAM Kufa kwemapositori #MUKOTSANJERA # Karanganda TV
1:06:49
Karanganda Tv (Waiyepo ere ?)
Рет қаралды 44 М.
Tikuferanji 13 April 2024
25:46
Edson Gunsalu
Рет қаралды 40 М.
Budiriro tragedy : Driver weKombi akatsikwa neKombi yake
39:30
Destiny TV
Рет қаралды 55 М.
CRUISE 5 WITH THOMAS CHENKHUMBA CHIBADE
47:02
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 214 М.