Iwe ngodwala bwanji..... don't include kamuzu mukhani yako...he is the only guy that did good for Malawians ukafunse agogo ako...osati mbuzi zako Za dpp zo😂😂😂😂😂4get guys dpp will never come back muulamuliro
@bernardnyirenda763914 күн бұрын
K@@wisdom20mkango49
@TrysonChimenya4-fm8nt17 күн бұрын
Malawi tikapusa tipitilira kuvutikabe President wanji wosapanga regret Mukamakavotera MCP kawiri zanu izo, Kodi bwanji sakutiuza percentage ya zomwe atipangila out of Promises????????? Time to vote for president based on region will no longer help us ....... Ine ndiye ayi Chakwera, Chilima akagwere ndi anthu onama zedi Komanso what we should know this is political battle, sangabwere poyera nkumatiuza kuti eya 2025 tizaluza that's why even those small small parties are promising that they will win come 2025. Uku nkulira kwanga ndatha ine wanu amalawi anzanga
@LovelyAzaleaFlower-uc8vr16 күн бұрын
Ndipo you have said the truth anthu awawa mukut a MCP waaa God will give them a severe punishment
@user-gk3bb8dx1m17 күн бұрын
Apm my vote
@user-nj4ob8jw6y16 күн бұрын
Your president is another Bola Tinubu of Malawi, sorry he has pasted his sell by date, u can even ask Namalomba.
@EmmanuelChiweza15 күн бұрын
Chabwino
@VincentChikondano17 күн бұрын
Stadium sinadzadze or half nde simungadabwe?
@user-vh1cq5gs5u17 күн бұрын
Koma mmene akumuyang'anira Anthu ake amene wabwera nawo kuchoka ku lilongwekowo akuwawona chifukwa akumuysuysatu zoti akhoza kuwinaso
Am a boy who belong to both two sides Lomwe and Chemwa because my dad from kasungu in Santhe and mom in thyolo Thomas .u like it or not .am a solution.
@user-rl8xs2kf1o17 күн бұрын
Kodi Ali ku kapeni 😂 ayiwala zomwe apitira mbuzi za anthu
@user-cq1wv9nq4y16 күн бұрын
Aaaaa ine mmene ndanvera ma speech awo kumeneku nduona kuti uyu unali mnsonkhano wa ndale wa mcp not mwambo okumbukila Kamuzu asamatinamizepo apa olo aja akuti achimwendo aja kulakhula kwanji kumenekuja ati akutchula Peter Munthalika ati sangatenge boma aaaaa zugwirizana chani ndi mwambo okumbukila malemu Kamuzu??? Eeeee koma guys ku Malawi mmm ayi zikomo
@petertaulo801417 күн бұрын
Mbuzi ya munthu sitha kuyankhula
@davidmalasa991213 күн бұрын
Kamuzu sadamange stedium iyi ndi sir geofry cobby
@DannielOnions-fy3dc15 күн бұрын
God knows what comes next
@EmmanuelGasiten-fo5dr17 күн бұрын
Apule kuyesera kubayibitsa anthu ku Kamuzu Stadium, eti anthu kumangoyang'ana osabwezera kkkkkk! Koma m'Malawi anakonza ndithu.
@JackMvura-ik2td17 күн бұрын
Sanje akulu ndinu afiti eti mumadya matewera kwanu eti demeti or pitala angafike gulu limeneli mbuzi
@LamseyLazarous-dl5qd17 күн бұрын
Anthu akeso ndiwomwewa anali zulo ku DPP
@inessmsiyambiri851717 күн бұрын
Izitu sizinali za chipani
@user-mh9se5to6k16 күн бұрын
Kkkkkkkk zoonadi big
@user-jw5rx9ze8k16 күн бұрын
Koma chakwera mwati ali ndi nzeru? Ndikuona ngati chomwe akuyankhula sakuchidziwa.
@ElvisSpesho16 күн бұрын
Makamaka chisilamAchakwera amadana nacho limodzi nd anthu akulilongwe,bas zingo khala zamutundu,tsopano msilam ndye ali paliponse,azichemwali anu onse anakwatiwapo ndi msilamu tili ndi anatu mwa kabudulamu, kuphiri la njudz,kwamasumba,ndye nkhondoyo ife tingo ona kucheedwa,kt tikuonetsen
@spargomw17 күн бұрын
Kwasonkhana zipani 9😂😂😂😂 Peter dzana lija aliyekha koma kunali chiguluuuuuuu❤❤❤❤❤
@user-jr7bq8sw6t16 күн бұрын
Ndipo ine utu sindimamva mfundo zzomwe amayankhula Koma mukuti olo ulaliki wake unali omveka bwino bwino?
apm.my vote baba palibe ncanzelu ndikunva.mwainu.sakho.hvy
@LovelyBlini-cu3iu17 күн бұрын
Akudalira kuba awa
@user-xi2jz8ru1w17 күн бұрын
Komasotu big wa samata kusanga or wa kazi awowatu kungo kala ngati nyapapitu
@YohanePatrick-lc2lq17 күн бұрын
Bt niya azungu
@user-vm7iz6oz6r16 күн бұрын
Ndipo atakuvotere ndan
@user-lk8kj9zv6x17 күн бұрын
Nyawu razalo
@geoffreykankhomba15 күн бұрын
Ovota ndi anthufe kulankhula uku its like ma vote muli nawo mnyumba mwanu ,sitinaiwale ñjala ,kukwera kwa zinthu kubvuta kwa chakudya ,kukwera kwa chimanga mpaka 60 000 zomwe sizinachitikepo mu History ya Malawi ,ziwani kuti anthu ada nanu kukhosi kuyambira ku primary school mpaka ku collage ,ma civil servants ndi Ena onse ,aphunzitsi ndi ena onse ,kufikira munthu wakumuzi sakufunanso kumva dzina la tonse alliance and MCP tionana September 2025 ndipamene mudzaziwe kuti Amalawi anatopa nanu
@BaldwinBanda-gd9zo11 күн бұрын
Chakwera ndiwe mbuzi yamano pasi
@user-xs3nj1es1r16 күн бұрын
Peter Mutharika awinaso🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@yassinmpangiwa17 күн бұрын
Apm my vote 😂😂
@mussahkachere233217 күн бұрын
Kom amalawi nd anthu onvesa chison kwambil 😂😂😂..anthu tikuvutika km still kuiimbila mmanja zinthu zopanda sogolo..
@preciousthafungaunje663117 күн бұрын
Osaiwala kut amalawi Fe Tu tangofuma kumudyela munthu kma awa antha
@Eric-gb9ms17 күн бұрын
Eti makamaka azimayi chosecho usiku azikagona nd njala
@Hastings-on9is17 күн бұрын
Sindikuziwa kut anthufe timaganiza Chan,, mpaka kululutira garu ija koma😢
@MavutoNgoma-kk6lq17 күн бұрын
Garu yamuthu çhakwera
@patrickscott908616 күн бұрын
Ndizona tizivutikabe bas muziba ndalama muzilemba job aku banja lanu
@DevisChikapa17 күн бұрын
Ameneyi ndi galu kwabas
@davidkadyakapita883616 күн бұрын
Zaziiiii Chakwera ndi chitsiru kwambiri
@ChrispinJohnson-py5ie17 күн бұрын
madala mukunama mwalaphela mulibe nzeru olo mfundo mulibe
@ChrispinJohnson-py5ie17 күн бұрын
kape chilichonse choyankhula kulemba basi kupanda nzeru galuu
@MustafaLikaomba17 күн бұрын
Kodi ameneyu amalembela ndani
@Randy-er2xo16 күн бұрын
Ukunama ase ng'ooo udye ndalamazo komaliza wopusa iwe
@user-lv4qd4pm1e17 күн бұрын
Chakwera my vote wina afune or asafune mcp pachiongolero
@giftjamali820416 күн бұрын
Muthu ukamati nkazi uyu ndimukwatila umakhapa kuti madongosolo onse ofunikira manja wapanga Apure akukunaminzani pls konzani nyumba yanu yokapumila