HOT CURRENT WAPA 8 SEPTEMBER 2024 |

  Рет қаралды 3,308

DZIWE TV

DZIWE TV

Күн бұрын

Пікірлер: 8
@LuciusSakamula
@LuciusSakamula 7 күн бұрын
Hot hot current Pali hot big up guys I like 🎥🔥
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 6 күн бұрын
Bayana akunena zoona pa za environment yaku malawi, imagwetsa mphwai munthu kulimbikira
@FisherAction
@FisherAction 8 күн бұрын
Good
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 7 күн бұрын
Good said 👍 guys always mumayima pa chilungamo
@MosesLeckson
@MosesLeckson 8 күн бұрын
Pena pake tiyeni tizivomereza kuti a Malawi ndi olimbikira.Palibe uyo amadalira boma.Timadya,kudzigulira zovala,kudzigulira mankhwala tikadwala ndi zina zotero patokha umoyo mkumayenda.Zosalimbikirazo akuzidziwa ndio malinga ndi anthu omwe amawadyetsao.Tikudandaula kukwera mtengo kwa zinthu ndiye titani ifeyo kulimbikirako kuti zitsike?Asaiwale kuti omweo amatipeza mkumadzatilinjeza ndiye zomwe amatilinjezazo kodi poti akhala pamipando chikhaleso chitonzo?
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 6 күн бұрын
True
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 6 күн бұрын
Boma ndilosalimbikira ndiye anthu alimbikira bwanji?? Pulezidenti kumangoyenda, malo momanga dziko, zomvetsa chisoni, look at what bingu did? Anali serious ndi Boma and anthu nso started doing things differently
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 8 күн бұрын
Chimakhala muchinyengo
هذه الحلوى قد تقتلني 😱🍬
00:22
Cool Tool SHORTS Arabic
Рет қаралды 105 МЛН
Waba zambiri kuposa Yudasi Iscariot; Amalawi akudya zikhawo za mtchire.
7:07
My Expose has saved Ghana Millions of Dollars...Hon Ablakwa
1:27:57
THE KSM SHOW
Рет қаралды 50 М.
BON KALINDO LERO PA 17 SEPTEMBER 2024 |
18:22
DZIWE TV
Рет қаралды 2,6 М.
Oyenda ndi Lupanga adzaphedwa ndi Lupanga
7:53
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 55 М.