HOT CURRENT YA LERO PA 4 August 2024 🤔🤔🤔🙌🙌

  Рет қаралды 26,444

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 110
@Kamwachale
@Kamwachale 2 ай бұрын
I like you guys but to have my comment on what you are saying. However all the mess we face today is our own making based on the choice that we made as citizens. It is not even fair to blame DPP as weaker opposition because by DPP opposing this government, it also means that DPP is opposing the choice that Malawians made through the votes. If Malawi has ever had decent party it is DPP because it gives respect to the wishes of Malawians. MCP is politics and Malawians chose politics and DPP is development and it's up to Malawians to choose development based on comparison between the two.
@BeatriceProfessor
@BeatriceProfessor 2 ай бұрын
Fantastic guys inuyo ndie ndi one respect 💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪❤❤❤❤
@RonnMtafya
@RonnMtafya 2 ай бұрын
Continue being open.Musafoooke musagonje a Malawi.A new Malawi with new mindset needed.
@RonnMtafya
@RonnMtafya 2 ай бұрын
You guys mukunena zoona..Koma adzakutengere ku Chikangawa .Long live so that you continue civic educating us.
@wineskhaneni8669
@wineskhaneni8669 2 ай бұрын
U guys are great, u can really guide
@SoldierWilison
@SoldierWilison 2 ай бұрын
Lelo ndi pamene mwalangula muopa mulungu please continue don't change
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 2 ай бұрын
Times mwezi umenewu mwayambapo ncito wabho love u
@Guttagaard
@Guttagaard 2 ай бұрын
Wonder Msiska ndevu za mwanyi ali hard kwambili
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 2 ай бұрын
2025 kumalawi ngati tikufuna president wazeru achoke mu anthu awa 1 wonder musisya ndevu zamwayi 2 jona 3 Brian banda 4 chunga 6 bon kalindo 7 tanyiwa 8 bakili muluzi TV 9 kaliat 10 njawala Anthu amenewa mumozi atha kuyendesa bwino Malawi kusiyana ndi makape akulimbirana ku mcp.
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
🔥🔥🔥🔥
@JohnfosterNkusengwa
@JohnfosterNkusengwa 2 ай бұрын
❤❤❤Guys all the way from cape Town PA boma PA Athlone zedidi l salute you guys and my vote and my ldea let's build Malawi and let's be not afraid 😊 utm more fire
@DominicNkosi-iq9fh
@DominicNkosi-iq9fh 2 ай бұрын
You guys you best tutors, only that people trust in regionalism.
@RonnMtafya
@RonnMtafya 2 ай бұрын
We need More fire ttv.
@DENSONZULU
@DENSONZULU 2 ай бұрын
Chaka chamawa tivote mwanzeru chonde.... Rest in peace SKC 💔🔥
@AbrahamTembo-z5k
@AbrahamTembo-z5k 2 ай бұрын
MEC, pa nthawipo, 6AM to 4PM ndikuwona ngati nthawi yachepa. Bwanji itakhala 6AM to 6PM?
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 2 ай бұрын
For me the lack of poor governance and the inability to deal with blatant corruption. 4% of development can not buy our vote.
@GiftCMlangeni
@GiftCMlangeni 2 ай бұрын
You people we love you and malawians are proud of you. Congratulations for all the times boad for this programme. Generation shall talk about this radio station and TV.
@RonnMtafya
@RonnMtafya 2 ай бұрын
Let us be patriotic and totally love our nation first.
@JaneBanda-ht4ve
@JaneBanda-ht4ve 2 ай бұрын
Mafuta ayamba kubwera pa njanje after 21 years, ma mega farm ndi awo, zitukuko zochuluka mu zaka 4, ine vote yanga ndi MCP - Chakwera 🇲🇼✅🔥
@RedsonMasamba
@RedsonMasamba 2 ай бұрын
hahahaa its your opinion
@SimenyeSimkondachirwa
@SimenyeSimkondachirwa 2 ай бұрын
Vote for Dpp thing will become better trust
@Cuddy-ol5wq
@Cuddy-ol5wq 2 ай бұрын
That's talking...but is it possible our mp to have two terms as maximum for serving the constituents rather than for life?
@paulmgombebanda-mr19sate
@paulmgombebanda-mr19sate 2 ай бұрын
You have a point aise
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 2 ай бұрын
Tisanamizanepo apa Chakwera yemweyu is a better option pa anthu amene alipowa #boma ndilomweli
@Creslevison-vj2sl
@Creslevison-vj2sl 2 ай бұрын
Kupusa
@famousphiri944
@famousphiri944 2 ай бұрын
Mmm😢
@MakawaBenjamin
@MakawaBenjamin 2 ай бұрын
Big up guys mumatiimilira ❤❤❤❤
@AubreyWilson-j8w
@AubreyWilson-j8w 2 ай бұрын
Kkkk nde fisiyo ndindan😂😂😂
@JanuaryGwere
@JanuaryGwere 2 ай бұрын
Yovotera chaunzika ndizopoyila akupangila aku Lilongwe okha kuno kulibe
@DENSONZULU
@DENSONZULU 2 ай бұрын
ACB tizangoithetsaso ntchito yake sidziwika
@RonnMtafya
@RonnMtafya 2 ай бұрын
Money Must not buy us.Ndalama zinapha Yesu.Akupereka ndalama ngoopsya ngakhale chipani lets avoid them.
@EvansNkumba-q7t
@EvansNkumba-q7t 2 ай бұрын
Me zikhale m'goma I want to imform the general public that we are closed this tv station tomorrow 😂😂😂
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
😂😂😂😂
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
Big up wonder and atsukuluzi mwayankhula mosaopa munthu chilungamo akumva amve anthu akuba mowononga zedi eesh....
@RonnMtafya
@RonnMtafya 2 ай бұрын
We need MAGUFULI type of govt not mabwefu bwefuwa
@ChomboNgosi
@ChomboNgosi 2 ай бұрын
Wonder chakwera ayi pls ndipo sitikumufunaso ndikumuona pls pls
@mandelahindu9226
@mandelahindu9226 2 ай бұрын
Ma brother Aku t tv nthawi zina mumandilowa mmaganizotu mosakunyengelelani inuyo mumang`alula or thelele limandikomela mbamba
@BrightZionga
@BrightZionga 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂 wonder kodi tiana tumakuopsyzani love you guys ❤
@JanuaryGwere
@JanuaryGwere 2 ай бұрын
From 2020 kufika lelo njala sikutha president wachikondi angapase bwanji mwanawake ma contraction aboma zinthu zingayende bwanji kwathu kuno chakwera sanafikeko kuno
@RonnMtafya
@RonnMtafya 2 ай бұрын
Anyanatanu muzigona kutali ndi ng'ona ngakhalenso mikango kuti mupitilize kutigawire
@DENSONZULU
@DENSONZULU 2 ай бұрын
1000% increase bwana 💔💔
@wisdomchilanga723
@wisdomchilanga723 2 ай бұрын
Guys apa mwang'alura😂😂😂❤❤
@SiphiweTonnyChidumayo
@SiphiweTonnyChidumayo 2 ай бұрын
Kung'aluratu😂😂😂😂😅👐Kaliati,Njawala atimile u president we should see them.......Let's try out something new mbuzi zinazi ayi
@DENSONZULU
@DENSONZULU 2 ай бұрын
Zodiak ndinasiya kumvera ndimanvera times ndithu
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 ай бұрын
Amcp inu olo inuyo zomwe zimachitika muulamulilo wa peter muthalika mungayelekeze ndi manyani tili nawowa a mcp wa inu muzikhala ndi manyazi dpp ilowa mboma mufune musafune
@EfeloYovita
@EfeloYovita 2 ай бұрын
mafuta akupezekawo akugulitsidwa ndalama zingati zopusa basi dpp imagulitsa 700kwacha za mcp zakozo kagwele 😅
@KennedyPhiri-c7g
@KennedyPhiri-c7g 2 ай бұрын
Aford basi enawa atarephera kale
@MonicaSembo
@MonicaSembo 2 ай бұрын
Massive
@blessingsmandiwa4840
@blessingsmandiwa4840 2 ай бұрын
Ati tchifiiiiii mubweraso why eeee anyamata inu😂😂😂😂
@AubreyWilson-j8w
@AubreyWilson-j8w 2 ай бұрын
Koma tikaika pa scale between chax and pix Bola pix😂😂😂
@JanuaryGwere
@JanuaryGwere 2 ай бұрын
Moses anapha witika koma uyo akutukwana anthu dziko muno
@TonnytyphorHarawa
@TonnytyphorHarawa 2 ай бұрын
Vuto amalawi ife sitimachedwa ku yiwala, MPC yatizudza kwambiri, apa yikubweraso kuti nyengerera kutipusitsa, amalawi ife tikuononga tokha dziko lathu, MCP yationongera dziko, ndikuputsa kwathu tizawa voteraso....
@JanuaryGwere
@JanuaryGwere 2 ай бұрын
Dziko mulibe ndalama chakudya mulibe koma zitsilu zikuwononga
@ChomboNgosi
@ChomboNgosi 2 ай бұрын
Ndipo brain Banda tamusowa
@EmmanuelMoyo-hy5ni
@EmmanuelMoyo-hy5ni 2 ай бұрын
Dziko lathu kuchita bwino ndi kosavuta koma amtsogoleri ake amakhala kuti akuchokera ku njala,,Check Burkina faso now
@LUCIUSChamwamba
@LUCIUSChamwamba 2 ай бұрын
Apa ndiye kung'aluladi 😂😅
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 ай бұрын
Why u come back killer😢😢😢
@GeoffreyShariff
@GeoffreyShariff 2 ай бұрын
Chilungamo chimawawa eti
@JanuaryGwere
@JanuaryGwere 2 ай бұрын
Mcp kumanga anthu kupha kukondela mtundu ngati gala uyu chimwendo banda akuti anthu ambili Ali ku Lilongwe kumalankhula mopusa
@JanuaryGwere
@JanuaryGwere 2 ай бұрын
Vuto timavotela anthu osawuka munthu anali m'busa analibe kanthu mukuwona ngati
@OswaldKachala
@OswaldKachala 2 ай бұрын
Vote wisely to have a better future Malawi 🇲🇼
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 2 ай бұрын
Koma khan ya amec andinyasa pa programs imoz ,pofuna kukayesa makina ovotelawo ,mmm zobera bas
@Ertyvhk
@Ertyvhk 2 ай бұрын
Guys lero mwabwera bwino kwambiri zowonadi tikudabwa kuti ACB inakafufuzadi ndalama anthuwa akuzitenga kuti .
@paulmgombebanda-mr19sate
@paulmgombebanda-mr19sate 2 ай бұрын
Ati tisavotere Manganya 😂😂😂😂
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 2 ай бұрын
Chakwera sangafuse zimenezo coz iyeyi amaopa anyamata akewa
@Drmuhammadchiwona
@Drmuhammadchiwona 2 ай бұрын
Komaapa ndiye ikubheba
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 ай бұрын
Nkhani ya kuchikangawa mukafuse civo
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 2 ай бұрын
Kkk
@James-o5t
@James-o5t 2 ай бұрын
Tayimilani inuyo tizakuvotereni muzasinthe zinthu osamangodziwa kuimba wizulo
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 ай бұрын
From 1964 all Malawians leaders there shit series 😢😢😢 guy's
@GiftHlungwane-q5o
@GiftHlungwane-q5o 2 ай бұрын
For me DPP was too much better than this fulish Gavernment it is now
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri 2 ай бұрын
Zikanakhala choncho sokanaluza
@RonnMtafya
@RonnMtafya 2 ай бұрын
Let's try a total new crop.MCP is too much of Julius Ceasar & Mcberth Theorems.
@RonnMtafya
@RonnMtafya 2 ай бұрын
Chakwera is painted black he has no courage to denounce evil doers in His party.
@James-o5t
@James-o5t 2 ай бұрын
Phokoso lokhalokha chanzeru palibepo apa
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 2 ай бұрын
Amvele anzake amanena chawezi azimvele anzake amatha
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 ай бұрын
I like kuswakuswa what is chakwera cha satanic
@shotsfired588
@shotsfired588 2 ай бұрын
I believe Usi is Malawi first, I have noticed Malawians are so stuck up to party politics that they can never appreciate anything, every day is politics day in Malawi, no political party will help you because they are from your region, as much as I hate chakwera for the way he was ready to betray chilima before he died, I don’t think there’s anyone better to run Malawi at this moment, unless it’s Bushiri the fake pastor but brilliant hustler.
@Andy20247
@Andy20247 2 ай бұрын
Bravoooo
@StanleyChabwera
@StanleyChabwera 2 ай бұрын
Boma ili kuganiza kukuvuta....
@OwenNyangu-nv1yt
@OwenNyangu-nv1yt 2 ай бұрын
Chakela ubwino ukuchuluka kuposa enawa
@JanuaryGwere
@JanuaryGwere 2 ай бұрын
Palibe boma lalamula bwino
@vukanifracksonchinkonde7324
@vukanifracksonchinkonde7324 2 ай бұрын
Sindingaiwale ma black out a mbweeeeeee
@ShadreckMatenje
@ShadreckMatenje 2 ай бұрын
Guys apa nde tomati zisankho zayandikila kuswakuswa osaopa
@chiwaulaashraf4696
@chiwaulaashraf4696 2 ай бұрын
Eeeeeeee
@Isaiahbotoman
@Isaiahbotoman 2 ай бұрын
Eeeeeee wonder 😂
@DonKapeniZagwah
@DonKapeniZagwah 2 ай бұрын
Koma ndy kuswa kuswa di
@SababaHotel
@SababaHotel 2 ай бұрын
chakwera sakufunika kukhalaso president
@ShaihSalaam
@ShaihSalaam 2 ай бұрын
Boma Lili manja mwa Agalu
@StevieChilinde
@StevieChilinde 2 ай бұрын
Makape Inu;Poyamba mumayankhula Zanzelu koma pano mbola zenizeni dollar sizinthu zinakusinthani makape Inu.
@StevieChilinde
@StevieChilinde 2 ай бұрын
Kodi nkhani ya chikangawa ilipati?Naga Mr.B.Banda alikuti sizikubebaaaa olo pangono.
@UseniMailosi
@UseniMailosi 2 ай бұрын
Agalu wojoyina sipaniwa site chifukwa timavotela wina amalamulila wina
@JuvenileDebwe-bv8ow
@JuvenileDebwe-bv8ow 2 ай бұрын
zimenezo ndiye vuto lomwe tilinalo ma politicians athu ngooipa kwambiri amafuna tikhale owaonbera m'manja ndi 2000 mk
@ImediJames-b4u
@ImediJames-b4u 2 ай бұрын
Thanks you guys
@John-m6b4m
@John-m6b4m 2 ай бұрын
Lero ndye kwavuta osati masewera
@JamesFundi-zn7nk
@JamesFundi-zn7nk 2 ай бұрын
Okay my friend
@Chisomo-h3c
@Chisomo-h3c 2 ай бұрын
Mwalankhulatu lelo takunyadilan
@MisheckAselo
@MisheckAselo 2 ай бұрын
Anthu atopa akung'alura🎉🎉🎉
@BornfaceMakamu
@BornfaceMakamu 2 ай бұрын
Thaw Zina mzachezepo za ku chikangawa
@SababaHotel
@SababaHotel 2 ай бұрын
Kodi brain banda alikuti abale
@FelixGambiza-fp7tn
@FelixGambiza-fp7tn 2 ай бұрын
What's the point of this program bola izangotha
@SitiyaBatwell
@SitiyaBatwell 2 ай бұрын
Awa akungodzikilakola nawo mpira a aaa osabisapo apa
@MaggieBanda-ft5tu
@MaggieBanda-ft5tu 2 ай бұрын
Mukubowa times,mwakwela MCP inu
@VioletMbale
@VioletMbale 2 ай бұрын
Nanuso pamene akwela mcp ndi Pati? Mziyamika these people alibe side
@francis12fombe54
@francis12fombe54 2 ай бұрын
Shunga alikuti ma bwana
@LuciaOsman
@LuciaOsman 2 ай бұрын
Inde inu
@ChristMaunde
@ChristMaunde 2 ай бұрын
Yache madolo
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr 2 ай бұрын
Sindimaliza Nanu mukuoneka kuti mukubowa zokamba zanu bola Chunga ndi Brian Banda apa inu phokoso too much aaa
Enigma Answers Viewers Questions, Guest Houses, Internet, Emojis. PART 7
1:25:20
How it feels when u walk through first class
00:52
Adam W
Рет қаралды 24 МЛН
Хасанның өзі эфирге шықты! “Қылмыстық топқа қатысым жоқ” дейді. Талғарда не болды? Халық сене ме?
09:25
Демократиялы Қазақстан / Демократический Казахстан
Рет қаралды 346 М.
Mom had to stand up for the whole family!❤️😍😁
00:39
MAYI WINA WAGONANASO NDI DOCTOR WA PRESIDENT KU STATE HOUSE
17:36
CHILIBE MANTHA ICHI!
15:35
Shamsdeen Chikwakwa TV
Рет қаралды 1,8 М.
THE COURT (Malawi)
24:46
Malawi News Update
Рет қаралды 81 М.
ATUKWANA BEN LONGWE PA FONI NGATI MUJA ANACHITILA NDI KEN MSONDA
5:47
Malawi Trends TV
Рет қаралды 17 М.
THE DC BON KALINDO 😱😱😱_21 October 2024
16:51
HOT 265
Рет қаралды 8 М.
KWACHEMA KU NKHANI ZA LERO BWERANI ZAVERENI |
21:05
DZIWE TV
Рет қаралды 1,6 М.