MAYI WINA WAGONANASO NDI DOCTOR WA PRESIDENT KU STATE HOUSE

  Рет қаралды 94,052

TIDZIWE TV

TIDZIWE TV

Күн бұрын

Пікірлер: 120
@stevenbanda6665
@stevenbanda6665 5 ай бұрын
Watching live from Haiti.I like the song
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 7 ай бұрын
Koma nde kuyalukatu boma la chisembwere ngati ili sinaliwonepo yohh Keep it up Mr ntanyiwa more fire
@MatemangaMoyo
@MatemangaMoyo 5 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂
@BessieTembo-r4o
@BessieTembo-r4o 4 ай бұрын
Iwe ntanyiwa ndiwe chitsiru galu satanic akuphesa
@mbaliehaward947
@mbaliehaward947 Жыл бұрын
I like the song
@wilisonbornface4282
@wilisonbornface4282 7 ай бұрын
Watching form South Africa
@StellaMangani
@StellaMangani 11 ай бұрын
Mmmmmm zamabodza izi ndinu macadet inu 16:40
@HassanantonyHaxy1
@HassanantonyHaxy1 6 ай бұрын
From nsanje boma Limpopo fm ❤❤❤❤🔥
@argentchilanga3246
@argentchilanga3246 Жыл бұрын
Takunvani a Limpopo FM nkhanga zaona poti mayi Wina wadyesa nyemba Kwa dotolo was apresident kkkk
@OsmanSaizi-v8y
@OsmanSaizi-v8y 5 ай бұрын
Mmakhwana adah
@victoriabanda7828
@victoriabanda7828 Жыл бұрын
I like Bakili muluz, amapeleka ma umboni, pankhani zake
@HopefulCoralReef-tx4vx
@HopefulCoralReef-tx4vx 10 ай бұрын
Zoona zake man
@daviechannel8603
@daviechannel8603 5 ай бұрын
Mmmmmmmmmm mavuto 5:51 5:55 6:10 6:26
@SHUREIMSULAIMAN
@SHUREIMSULAIMAN Жыл бұрын
Ayaluse moto kuti boooo😊
@Mark.P1u3
@Mark.P1u3 6 ай бұрын
Mark pastor 9:14
@VaidaSidreck
@VaidaSidreck 2 ай бұрын
Nthanyiwa ndikuchita kukusalila kudya
@VaidaSidreck
@VaidaSidreck 2 ай бұрын
Adani asakuone
@VaidaSidreck
@VaidaSidreck 2 ай бұрын
Adaniasakuone❤
@ChristinaStambuli-q3e
@ChristinaStambuli-q3e 3 ай бұрын
Chikakhala chisembwerecho mdiye Mcp nkudya kwake ..koz akuti even mbumba za Kamuzu zinkadyengedwa nda youth myp kalero kumisonkhano yogonera konko mhuuu
@fredalbert6998
@fredalbert6998 6 ай бұрын
More fare🔥🔥🔥🔥 tili pambuyopanu
@chiphalechima831
@chiphalechima831 Жыл бұрын
Nice one song
@EdisonNakulenga
@EdisonNakulenga 6 ай бұрын
Awadiaziwada ofunikila motobasi ahebili 12:29
@asivenathilitye7268
@asivenathilitye7268 7 ай бұрын
Continue is a good story
@felixmtwana
@felixmtwana 6 ай бұрын
Continue telling the truth
@LysonMkomadzinja
@LysonMkomadzinja 5 ай бұрын
Amene amadana ndi limpopo ndi chitsilu
@KamizaElizabeth
@KamizaElizabeth 5 ай бұрын
From kasiya Lilongwe Limpopo Fm
@agnesmkanthama5327
@agnesmkanthama5327 6 ай бұрын
Mmmmm nanga mpachisanu, kwa a banje, cha MMA 4,😮
@leonardjika2100
@leonardjika2100 Жыл бұрын
A NEW THINKER WISE WILL GOVERN OUR LAND SO HELP ME GOD
@KondwaniMwasinga-rs6kv
@KondwaniMwasinga-rs6kv 7 ай бұрын
Limpopo FM keep it up
@WakalalaMtiozi
@WakalalaMtiozi 6 ай бұрын
Ndiyakhepo pa mayi akunedwayo malemba akunena kut . Wawuze athu zomwe wawona ndimaso wosati zakuva ndiyena ayi kid chikakhala chabodza wukwanitsa kwawuza athu ones amen wawuzawo pepani baba yakhulani zowomwe mwawona ndimaso
@KhefasKhembo
@KhefasKhembo 6 ай бұрын
10:09 10:10 10:11
@JohnChibalo-wf8gr
@JohnChibalo-wf8gr Жыл бұрын
Kustate kwasunduka ku ndagala chifukwa chotenga mahule osalimba nsalu nkumamagwira ntchito lero ndiidzi nyumba yolemekedzeka ikungomveka zausiru zokha zokha kodi nthawi zija simungamakambirane zosisa mitengo ya zinthu zomwe munkalonjedza zija kapena mwalephera kusisa ? 😂😂😂😂😂😂
@veronicagullo9373
@veronicagullo9373 5 ай бұрын
Inu mwafika potitenga ngati oduka mitu ife neither kuti Patokha sitingaganize
@FloraRonard
@FloraRonard 6 ай бұрын
😢😢😢
@MerryWayson
@MerryWayson 6 ай бұрын
Ai A Cormled Kunotu tadzuka bwino ndithu , Aaaa A MCP mama Mr Chakwera akusaka pofera awapeza amene wawasogozao Chakwera pompano
@alickalick6509
@alickalick6509 Жыл бұрын
LIMPOPO FM moto kuti buuuuuuuu with Comrade MTANYIWA Awululeni ayaluke anthu oyipa a Mcp
@languitoneelias9972
@languitoneelias9972 6 ай бұрын
Nde pali vuto lanji?mwaiwala kuti mkazi wa bakili muluzi anagonana ndi bodygurd inunso ukape bwanji
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll Жыл бұрын
Ameneyu kennako agona ndi a president 😅😂😂
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 6 ай бұрын
Koma azibale ndichani kwenikweni agalu amenewa?
@PiasonWilliam
@PiasonWilliam 5 ай бұрын
Kuseka mopwambwana, zoyankhurazo zopanda nzeru , Za ziiiii Koma Ngati anthanyuwa zili ziwanda ambuye akuoneni kunena zoona mukutinyasa kwambiri kamba Koti zokamba Zanu zilibe umboni.
@MillyKachepa
@MillyKachepa 6 ай бұрын
Koma kuli zinthu 😮😮😮😮
@CharlesBanda-mv6cr
@CharlesBanda-mv6cr 5 ай бұрын
Amudalawa koma akuganiza bwino? 😂😂😂😂 I doubt
@zacariasjoselemessonelemes9562
@zacariasjoselemessonelemes9562 Жыл бұрын
Nkhanga zawona kkkkkk
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness 5 ай бұрын
Koma awaso zaziiii ndiye iweyo zikukhuza pati kodi iweyo siwugona ndi nkazi wako nanga zimenezo amalawi zapindulira chani zaziiii
@Jamesangir-b1d
@Jamesangir-b1d 5 ай бұрын
Aji moyo Mozambique
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k 9 ай бұрын
Kkkkkkkkk km kwathu nkokoma umangovuta ndi umphawi basi
@abelmuyila8723
@abelmuyila8723 5 ай бұрын
Eeeiissshhh!!!! Zosakhala bwino
@PiasonWilliam
@PiasonWilliam 5 ай бұрын
Fullish reporter
@MakawaPartrick
@MakawaPartrick Ай бұрын
Boma lachakwela boma la chigololo boma lachimangawa boma lakupha
@elliousBowman
@elliousBowman Жыл бұрын
Nkhanga zaona!!!!!
@wellingtonmtoso2074
@wellingtonmtoso2074 Жыл бұрын
Innnuu mwatani kodi pezani nthawi nanu mukaloweko kenako tidzamve za inuyooo mmmm
@Kalumbijoyce-hb8gr
@Kalumbijoyce-hb8gr Жыл бұрын
Usatanic wawowo 😂😂
@LehmanManere
@LehmanManere 2 ай бұрын
Ibwegede ndithu
@promisebanda8785
@promisebanda8785 Жыл бұрын
Koma ngt irinyere😂😂😂😂
@MosesSolomoni
@MosesSolomoni Жыл бұрын
Kkkkkkkk ayaluka nayo
@dianandove7031
@dianandove7031 6 ай бұрын
You Malawias you need president like Kamuzu Banda .you dnt have respeck
@Kalumbijoyce-hb8gr
@Kalumbijoyce-hb8gr Жыл бұрын
Chiwandadi chimenecho
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 6 ай бұрын
Kkkk.kodi ndi ciizimba ca a pulezidentwa kuti doctor wao azigona / azichindana ndi animal ogwila ntchito ku state houseku.? Izitu zikhoza kukhala kuti dokotalayo sakhala wina kuposa mwini wake lazarus Chakwera yekha cizimba ca upulezident
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 5 ай бұрын
Even in the USA they do same rituals
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 7 ай бұрын
Osawopa inu nde mumanena zoona Ndi aBakili mulizi TV
@AlickSaid-gj8kr
@AlickSaid-gj8kr 6 ай бұрын
Bakiri muruzi tv
@IssacMateyo
@IssacMateyo 7 ай бұрын
Achitsilu mulibe zochita mukufuna kumanamiza Malawi basi
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 6 ай бұрын
Chitsiru ndiwe pamtumbo pako galu
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 Жыл бұрын
Limpopo FM zikomo moni talandira koma mabvuto onsewa anthu ena oipa anachita kuwasankha
@TadalaBirsonkanjanga
@TadalaBirsonkanjanga 6 ай бұрын
Koma yah
@blacksonpeshes5057
@blacksonpeshes5057 6 ай бұрын
takudyadirani tizikupemperelani kut asakupezeni
@LaynaAdam
@LaynaAdam Жыл бұрын
La 40 limakwana
@Brockbaby143
@Brockbaby143 5 ай бұрын
Ku opposition ndie ndi kowawatsa mutu mpakana maina opanda tanthauzo
@asivenathilitye7268
@asivenathilitye7268 7 ай бұрын
Thaulandndila moni
@DalitsoKaunda
@DalitsoKaunda 6 ай бұрын
Kodi mayi ameneyo wabuyi buyi ndindani abale
@ClementMushele
@ClementMushele 6 ай бұрын
Komano man ngati umanena zoona iweyo ndi katundu umakwanila
@JaneKaphambi
@JaneKaphambi 5 ай бұрын
Kuchedwa kuyamba nkhanizo
@AliAli.aliheassim
@AliAli.aliheassim Жыл бұрын
Nkhanga zoona mumatiimilira
@ImraanJafali-dk7rg
@ImraanJafali-dk7rg Жыл бұрын
🤓🤓🤓🤓 Kwamvuta akutinyasa ife achakwela
@marryphili5419
@marryphili5419 Жыл бұрын
Mulungu aliko atimenyere nkhondo 😜😜
@BerthaMkwinika
@BerthaMkwinika Ай бұрын
Panga zako ndi banja lako, zimenezo sizikupindulira ntanyiwa aaaaaaa za ziiiiii,nde ife zitipindulira chani?
@HarriePearson
@HarriePearson 10 ай бұрын
Chakwera ananyenga kale mkazi ameneyu chitsilu choke alone ena dzamuchima
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Жыл бұрын
Kwachema
@stalickkafera3454
@stalickkafera3454 6 ай бұрын
Za bodza Munthu wamkulu ngati iweyo pali nkhani yoseketsa Mau onyasawo
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 Жыл бұрын
Abale zikuoneka kuti atsirikali athu sidzikudziwika mbali yeni yeni komanso ntchito yawo akuyenera kugwira chifukwa kale a Malawi timadalira atsirikali kuposa police popedza zonyansa zonsezi akuchitazi anayamba kale mogwiridzana ndi mbiri ikufotokodzera
@MillyKachepa
@MillyKachepa 6 ай бұрын
Anawagura akulu akulu a boma nde ntchito zawo sizingaoneke komanso ovutika ndi apansiwa
@ZinawZinawmulu
@ZinawZinawmulu 6 ай бұрын
Mumativesa kukoma amkanga zaona mupitilize kutelo ine Balakasi
@KondwaniMunthali-vf1ws
@KondwaniMunthali-vf1ws 5 ай бұрын
😂😂
@WilsonMaulana
@WilsonMaulana 3 ай бұрын
Tiuxen zowona
@blessingbanda6206
@blessingbanda6206 6 ай бұрын
Usapelekele umboni wabonza Mulungu akuwona zonse
@judgeshonga
@judgeshonga 6 ай бұрын
Chonde muzifika pa point msanga pankhani osamachulutsa zolubwalubwa
@RoseChinseu
@RoseChinseu 6 ай бұрын
😅😅😅😅
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw 10 ай бұрын
Akatero ndinkazi wamweni wake uhule basi zisilu ziyanthu zaku paliyameti ko
@KhefasKhembo
@KhefasKhembo 6 ай бұрын
Koma man mukunenadi zoona kuti anthu agonanadi aaaaa
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o Жыл бұрын
Alomwe namwe tikati panji mazelu muli vizeleza kuyowoya unenesko cha muli vindele
@tingamasi106
@tingamasi106 Жыл бұрын
Imwenso namwe ulichindere chakufikapo
@patrickmandalawe745
@patrickmandalawe745 6 ай бұрын
Komatu zomatchulana mitunduzi sizabwinotu ayi. Chondechonde
@ShadreckLingani
@ShadreckLingani Жыл бұрын
Nthawi yake iiiiiiiiiiiiiii
@thomasnyasulu
@thomasnyasulu Жыл бұрын
Koma boma la MCP imeneyi, laposa la Kamuzu.
@LeonardPetro-ky6dq
@LeonardPetro-ky6dq 5 ай бұрын
Tikumvela ife
@AishaChibwana-b8o
@AishaChibwana-b8o 7 ай бұрын
Ma cadet a lomwe a khutukumve inu usatibowe mulibe zochita koma kupeka nkhani zabodza
@NyirongoMexonyoba
@NyirongoMexonyoba 6 ай бұрын
Kkkkkkkk kuyaluka
@Kalumbijoyce-hb8gr
@Kalumbijoyce-hb8gr Жыл бұрын
Ufitiwawo waonekera
@phillimonzgambo1663
@phillimonzgambo1663 Жыл бұрын
Nkhanga zaona
@triza.kamwanjatalandira446
@triza.kamwanjatalandira446 Жыл бұрын
Koma.abale misonkho yaamalawi ikungowonongeka
@AlinetMatewele-cp7ru
@AlinetMatewele-cp7ru Жыл бұрын
Chofunika.mulungu.amukkhudze
@jordan-m5s
@jordan-m5s 6 ай бұрын
Olandana mkazi sanenera zabwino
@mbaliehaward947
@mbaliehaward947 Жыл бұрын
Chakwela anamunyenga kale mai ameneyu
@UsumanMiles-ik6fw
@UsumanMiles-ik6fw Жыл бұрын
😂😂😂😂😂
@HappyMmenyanga
@HappyMmenyanga 5 ай бұрын
Kkkkkkk
@patassonelucaszovuta3431
@patassonelucaszovuta3431 9 ай бұрын
Tiuze cadat
@MaggieGondwe-vn2wx
@MaggieGondwe-vn2wx Жыл бұрын
Mumativetsa kukoma ankhanga zaona
@IssacMateyo
@IssacMateyo 7 ай бұрын
Bodza kufuna kutchuka awa
@IreenChilingulo
@IreenChilingulo 5 ай бұрын
Zovuta
@ulemuchigoma4899
@ulemuchigoma4899 Жыл бұрын
Fake channel i like Bakili Muluzi Tv he provides evidence
@vuyokazi9540
@vuyokazi9540 6 ай бұрын
Hi
@philimonstepe4795
@philimonstepe4795 6 ай бұрын
Koma nkhani Zina muzitipatsako ma umboni osamayankhula ndiye pot a Malawi tazolowera kunamizidwa
@SoyagaMussah
@SoyagaMussah Жыл бұрын
😂😂😂😂😂 koma nde zovuta bwanji
@Kalumbijoyce-hb8gr
@Kalumbijoyce-hb8gr Жыл бұрын
Washing for south Africa 😂😂😂yomweyo galuwee
Chifukwa Chimene Anthu Amamudera Miracle Chinga
11:55
Sam Malvitha
Рет қаралды 267 М.
CRUISE 5 MAFUMU MATIKI
1:14:37
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 160 М.
My scorpion was taken away from me 😢
00:55
TyphoonFast 5
Рет қаралды 2,7 МЛН
Ogulitsa Ziwalo Xa Anthu  Agwida Ku Thyolo.
1:27:49
Malawi Lovers 🇲🇼
Рет қаралды 244 М.
NKHANGA ZAONA
21:49
TIDZIWE TV
Рет қаралды 86 М.
Khothi la ICC likumufuna Zikhale Ng'oma; Mbava zovala ma suit ku Malawi
8:01
Ma No. Plate a galimoto 20 za mwana wa Chithyola, anatulutsa ndi Chimwendo.
12:23
EXCLUSIVE WITH PATRICIA KALIATI | 04 JANUARY 2025
1:13:01
Malawi News Update
Рет қаралды 87 М.