Asis speech yanu it's powerful 👏 🙌 a Malawi 🇲🇼 tiyeni tichose matha amene tili nawo dziwani kuti onena chilungamo adzaona mwayi pamapeto amoyo wake
@ProphetessEzinass-qu4ir6 ай бұрын
Iam not politica but this is the truth and awesome people chose to save gods and no justice . Continue to put sense in malawias God bless you
@OwamThoko6 ай бұрын
Powerful massage,I'm a man but you make me feel pain like I'm in labour to gv birth to a baby ,100 % I agree with you,GOD protect you from this ng,ona,n bless you,you are the angel of malawians,keep it up❤❤❤❤ 25:47 ❤
@Eric-gb9ms6 ай бұрын
Powerful message mom god bless you indeed it was painful.
@memoryziyaya25936 ай бұрын
i love the blief dear sis...what a plain tuth ..wow!!i salute u love💥🤝
@josephchitsulo58826 ай бұрын
You make me cry too 😢
@PaulChaleka-lb4vx6 ай бұрын
Michael usi alibe chilungamo and ndidamuona chilima akuzengedwa mlandu olo tsiku limodzi sadapite
@BrianjuniorMaleta-d3y6 ай бұрын
Even address as the utm VP to address for truth or to stand by him
@cynthiakananji16086 ай бұрын
Chilombo manganya
@EmmieZenengeya6 ай бұрын
Akapume Chilima abale😭😭😭
@MaxwellMbesa6 ай бұрын
GOD bless you Sister power full keep on sharing what ever is coming from our party
@AbuBakrIqrah6 ай бұрын
😢😢😢 sister indeed you made me cry a lot
@amoschataika74406 ай бұрын
Abiti ndi Deal, long live Sis
@elvienyirenda-ln3dm6 ай бұрын
Mai zoona zokhazokha mukukambazi. I wish you were here, muthandizane ndi Bon Kalindo.
@andreabanda78386 ай бұрын
Thanx so much madam. This is great for local Malawians. As you keep keep advocating for change. Please factor in the perspectives of the manifesto - such as freedom education, in secondary schools, even in the universities. Eradication of corruption. Change of some elements of sections constitution such as why the VP without real jobs descriptions. Kulira kwanu tonse tikulira. UTM please be strong. It’s only some 13 months to go. People don’t want this MCP thing.
@josephgabriel59416 ай бұрын
I absolutely agree with you. Nothing to subtract or add. You have said it all
@BrianjuniorMaleta-d3y6 ай бұрын
Exactly
@victorauwana72586 ай бұрын
So sad ... Mcp people are not sleeping anymore
@lyiemanganjira97086 ай бұрын
You make me cry also ma'am,,, God is watching Malawi and whatever is happening in Malawi God is there 😢
@CathreenKadwala6 ай бұрын
Abiti God bless you, zitiyankhulirani plz tikanena ife atimangatu
@EmmanuelZiba-qz6ug6 ай бұрын
😢😢😢😢😢 or Zambian 🇿🇲🇿🇲🇿🇲 we are crying 😭😭😭
@WitnessPhiri-zr9uf6 ай бұрын
😢eish zopweteka ndinthu God bless you sister
@EdnaSiyan6 ай бұрын
Very powerful
@AlubiBilly6 ай бұрын
Mcp bolaosamusowetsatu mayi you akulila malilo abwana ake 😢😢😢
@MiliamManda6 ай бұрын
Or aphee adadi wioo komabe tivotela My alipo a my Mrs Mary Chilima siazawinaso a Chakwera 2025 UTM yiwinakale takozeka ife kuwapanga sport My Mary Chilima❤❤
@Mavuto-b4f6 ай бұрын
l agree with you sister,your are tolking the truth, Molingana ndimmene mwafotokozelamu musalolere kukhalabe pa mngwilizano ndi mcp chifukwa a Bwanawa Sanali ku chipani cha UTM ,mubwelele ku gwilizano pokhapokha ngati malemu Saulosi chilima angadzuke kumanda kudzapitiliza mngwilizano ndi mcp not Bwana usi chifukwa akuoneka ngati anali a independent, according to your statement.
@LawrenceMsango6 ай бұрын
Powerful massage sister kumalawi kwaza afiti mudzipanimu there not have future anthu anapita school zakamuzu alibwe kuti mawa kubwelanji
@Agin2pex-ms3di6 ай бұрын
Am touched 😢
@burtonamin59136 ай бұрын
Congratulations sister
@doreenKamwendo6 ай бұрын
Facts dear
@ishmaelsiffah99006 ай бұрын
Tipemphe anthu aku Chilimba asamupatse manganya vote, munthu ameneyu ndi traitor sure
Koma Ku UTM Ku Kuli azimayi okongola heavy...SKC ndi idea for sure mama
@TressLuka6 ай бұрын
You make me cry tòo Aunt 😢😢😢 . Pipo ayi zikomo chikondi palibeee😢😢😢😢
@EdithKachule6 ай бұрын
TRUE WORDS SISTER 😢
@DenisDias-i7l6 ай бұрын
Namwera ❤
@lindamalunjika65816 ай бұрын
powerful
@PrinceBlessings-bv5bs6 ай бұрын
Mwazi wa saulos supita pachabe ai..... Ndipo mulungu sangalore kuti mizimu ya anthu 9 isabale zipatso
@LanceLance-mj4kc5 ай бұрын
We are all crying,& others we don't believ that he is gone for gud
@FrancisDay-br7xb6 ай бұрын
Mzimayi akulira
@ZogoZeko5 ай бұрын
Pano ndithawi yokonda utm
@JudithMaluwa6 ай бұрын
Kkkkkk wandiwaza kufazafaze kukoko basi
@OmegaChingamuka6 ай бұрын
Amene muli nchipani cha UTM munvere uthenga uwu mulungu alowelelepo
@IanAllstal5 ай бұрын
Kunamveka kufuura kupempha thandizo Koma olo ndi moziyemwe otulukira mmm my Biyeni
@umalimaganga6 ай бұрын
I like you ndinu wolimba mtima Mayi👍🔥
@HusseinAdamLidezo6 ай бұрын
Powerful enough
@dingim12346 ай бұрын
Zodanwitsadi zikuchitika ndi Michael Usi. Money root Of evil. POLITICS is a dirty game. Malawi opposition is wealth. Anankhumwa ankati a Chakwera asiye udvinding, later zoo anagulidwa anatseka pakamwa. But who is fearless to
Chilima akanakhala kuti amatikonda ife amalawi bwanji sanachoke ku mcp ataona kuti zimene amafuna sizimachitika personal he was a good guy political zero for me
@eliaskachali-xn2ve6 ай бұрын
Sorry sister , Chakwera galu yeniyeni. Amalawi no vote for MCP.
@WilliamBandaWili6 ай бұрын
Tikavotera Apm basi
@chikondibanda93726 ай бұрын
I like the way you are looking at this issue. I strongly think the party can be rescued. Leaving it in the hands of those on the ground currently will be a great betrayal to SKC. Sober mind must sit down and stretagise and not allow the movement to die. Please within the UTM don't allow SKC to be killed again. Allowing these selfish so called leaders sell the movement,is the same as allowing SKC to be killed again.
@ChikumbutsoJohn-rs4tt6 ай бұрын
Sister what you're talking is true and we were tired with greedy people like Usi, Usi is an carnivorous animal since the time our late Saulos Chilima Ali ndi mlandu wake Usi sanapite olo kuyankhulapo ,now come to imfa yake koma maliro ake sadayankhulepo kalikonse why? Traitor Usi, tisalore MCP ndiyakupha Osaopa Osatopa osafooka no more MCP 2025 God is my evidence
@PaulChaleka-lb4vx6 ай бұрын
2025 ndikuona kuchedwa kt tichotse mcp and chakwera
@Extratremendouszeus6 ай бұрын
Komanso chakwerayo akafere kundende ...he will never be allowed out.komanso Ma boarder onse tidzatseka ...tidzamuvula zovsla adzakhale pa mphepo ngt mmene adapangira chilima
@chrispinekaludzu8646 ай бұрын
Ku America mkokoma amai
@DuncanThambala6 ай бұрын
What do you mean apa mayiwa akuyankhula za mzeru tsono what does it mean ku America mkokopa please yankhulan za nzeru athu tikulira imfa ya chirima
@wonganimwase98816 ай бұрын
Those 9 people were murdered in cold blood.
@Josephiriillovo6 ай бұрын
It breaks my heart mmmm
@CathyKatsokamalanda6 ай бұрын
@@Josephiriillovo😢😢😢😢😢😢
@harrisbanda58916 ай бұрын
Usi is a hypocrite, ndinthira kuwiri amene anampereka chilima mmanja mwa zigawenga za crocodiles dancer mcp patty and dat we know for sure. I had request sister, i need a capital please, der's no one whom I can ask apart from u sister, zinthu sizilibwino mdziko muno
@Shadrick-lq6oj6 ай бұрын
Mahule awa akulila Poona kuti ntanji wavuta
@BensonChilundu6 ай бұрын
Zoona mayi Manganya kapena kuti Micheal Ussi ndi chitsilu nkhandwe yeniyeni ndipo ndi mlomwe nzathu koma kwa ine ndamuchotsa mwa alomwe.Galu ngati uyu sindinamuone munthu wakupha munthu wadyera.Manganya ndi mkoma kuwiri kukonda ndalama,akuti oopa Mulungu plus wa Seventh day heeeedeeeeeeee U seventh day wopusa wopanda chilungamo,ng’alula sisi ndipo usasiye.ubwere ndi ina.