Nonse onyoza a Twaibu Mulungu akukhululukileni muzakhulupila pa tsiku lachiweluzo muzakhumba kumpepesa patsikulo
@HarrisonLimbe2 ай бұрын
Ndizoona zimene amanena Br Twaibu mikumanoyi imachitika koma Mulungu amalepheretsa monga nkhani third war akukambirana koma sangachite override plan ya Mulungu sizingachite chifukwa rapture siyinachitiche
@alicesekela90544 ай бұрын
Meaning this was published on 8th May?
@mcsellahntv68964 ай бұрын
Now it makes sense, koma ndiye kuti nkulu wa chipani chotsalachi cha black, red, green akuyenelanso kuphedwatu , sinanga onse anasokoneza
@PatrickAnusa4 ай бұрын
Ai mwina winayo sanalowe muziwa bwanji
@LinleyNjenjete4 ай бұрын
😂😂🫴 Inu wabodza uyu 🚮🚮🚮🚮
@CharlesKachipanda-jz9jv4 ай бұрын
Ngati nayenso anachita panganolotu
@almadinaislamic90914 ай бұрын
Uyuyu machende ake
@inessmsiyambiri85174 ай бұрын
Mmmmmm@@almadinaislamic9091
@AnnetMndelemani3 ай бұрын
Akupatsa zingati????. Apa tizingopemphera kut chilungamo chiyende ngati madzi??¿,Inu munatani kuyitulutsa before pa 10 june.???
@austinallie302Ай бұрын
Ife tidaimvela ngozi isanachitike mu 8 July ndie kuti inuyo mukuimva kumene
@CathrineKumwenda4 ай бұрын
Amen
@MosesMakawa-f5v2 ай бұрын
God have mercy
@EstherchavulankhomaNkhoma3 ай бұрын
Izizi zithakhala zoonadi chifukwa zakumidima
@HandersonBanda3 ай бұрын
😮
@HandersonBanda3 ай бұрын
😮
@Mangwiro-e8r4 ай бұрын
Answer ya oyimba inu mungalephele kuziwa mulibe mzimu wachiziwiso
@inessmsiyambiri85174 ай бұрын
Anthu mukunyoza chifukwa brother twaibu simmamudziwa iye sakuikira kumbuyo munthu koma akunena chilungamo bvuto mwina simmamudatira mwangoyambira pa audior pewani kunyoza
@PatriciaPhiri-r8h3 ай бұрын
Zoonadi, and malemuwa ankadziwa kale za imfa yao remember ma speech awo pa misonkhano yawo.
@joanngrey83852 ай бұрын
Ndi abodza
@KennyThindwa4 ай бұрын
Womwalira sayankhanawo nde zopanda umboni.
@reality61654 ай бұрын
Kodi ngati zilizachinsinsi chifukwa chani anakonza ma website. ??
@AKanjerwa3 ай бұрын
Ma website ameneo salowa winaaliyese amaloweako nd okha okhao
@AKanjerwa3 ай бұрын
adha naoso anali a satanic nde amat anatuluka nde website amaiziwabe nde akamakambilana zaozo a satanic iyeso amatha kulowa nkumakaona nao
@BlessingsGama-j3r4 ай бұрын
Don't leave or forsake us ooh Lord 🙏
@WilsonNedi-s6t4 күн бұрын
Atwaibu amanena zoona koma panopa mutiuza zotani ndimomwe dzikoli likuyendera
@austinallie302Ай бұрын
Anthu ena apa sakumvetsetsa nkhani ndiyakuti Audio imeneyiyi inatuluka Achilima asadamwalire kuthekanso kuti Achilimawo adaimvela fukwa idatuluka pa 8 July enanso adaimvela chilima yo alipo ndie awawa samamuikila munthu kumbuyo kwa munthu amene amawatsatila bwino angandichitile umboni neie enanu mutha kumanenela kusadziwa sinanga mukumvela chilimayo atamwalila kale eyatu anthuni
Mwaonano pamenepo zikanakhala zoona akawanchula enawo ili ndi bodza la mchombo lemde target yanu njofuna kukonza dzina la chajwera kuti tidziti ngosalakwapo mwapala apa anaphedwa skc ndi chakwera
@IgnatiousFote-i7g28 күн бұрын
andale onsewa nd apansi panyanja and olemelawa osamawasilira ai
Mulungu akuzikutetezerani a Mr twaib koma tinakusowani kwambiri
@PatriciaPhiri-r8h3 ай бұрын
Hallelujah
@AlufeyoBanda-cv2we3 ай бұрын
Mma group apa watsap samasowatu Amayankhula
@DanielGeorge-l4h4 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 mwandiseketsa bwanji zako zimenezo ndi satanawakoyo😂😂😂
@DanielGeorge-l4h4 ай бұрын
Tikuuzila ntanyiwa 😂😂😂😂😂
@Mangwiro-e8r4 ай бұрын
Inayenda koma anthu analibe nao bizy
@AlicePondani9 күн бұрын
Prophesy simabwera zithu zitachitika kale ayi,,,
@HildaMbiziАй бұрын
Vya yii
@arnoldsimfukwe624 ай бұрын
Tisiya kukukhulupiliran ndizosatheka Ulosi wapa 8 May ukatuluke lero apo mwanama
@kellitachagona62293 ай бұрын
Ine mukumva kwanga i have heard that this is not a prophesy but zimene waonera ku Lcd
@AlicePondani9 күн бұрын
Ndaononga bundle yanga
@FebbieNjewa-g3k3 ай бұрын
Anthu omwe mukunyozanu simukudziwa kalikonse,,ndiye kuti mwahagana ndi satana tight
@PatriciaPhiri-r8h3 ай бұрын
Kwambiri mmm, sakuvetsa pat? Mulungu atithandize
@FLETCHERBANDA4 ай бұрын
Wina ndi iweyo.
@Blessings-td4cr4 ай бұрын
Mutitumizireko constitution book imeneyi tiwerengeko.
@frezarphiri34804 ай бұрын
Koma .why odiyo iyi yinatuluka pa 8 May 2024 koma bwanji sinayende kwambiri yikuyenda lero why??
@HildaMbiziАй бұрын
Akutuma kuti uphiphilise nkhani za Chikangawa iwe boza lako luta nalo kutali kapusike wabulutu
@JoyceMoloya4 ай бұрын
Mulungu akuwona ndipo Mulungu sakhala chete pq ana ake amene sanalakwe anafela pa ngozi za pqnseu komaso namondwe. Ambuye atithandize ndipo oyipa onse awakanthe.
@jeremiahmalikebu23933 ай бұрын
I would believe only if this video was released b4 the dismiss of SKC ngati mmene adapangira warn wa Bakili Muluzi TV uja kuti mdziko muno mwalowa asilikali aku Israel omwe apangidwa hire ndi MCP.
Wadya ndaalama uyu koma akuzinyenga yekha ife tikudziwa chomwe chinachitika chilima sanafe kamba ka satanik mwanama mmalawi ngopenya uyu
@chiletsokazembe-ri4ic4 ай бұрын
kod inu mesa munati munatuluka satanic? nanga bwanji mukunenabe zasatanic osakambapo za yesu? apatu mwaonetsa kut inu mukanali ku satanic ndipo mpingo wa seventh day adventist ili pamoto wakumwamba
Koma ineyo nkulu uyuyu sindimamukhulupirirayi chifukwa iyeyu ananenakuti anali wa satanic ndiye anatuluka, funso nkumati ngati anatuluka satanic zitheka bwanji kumanena zomwe zikuchitika ku satanic? POPEZA ukatuluka mu system amakuchotsa ,ndiye amakondakuti NDIKUONA LCD . A Malawi TIYENI tisatsate ndi kukhulupirira anthu tiyeni tiyang'ane kwa Mulungu ndamene amadxiwa zonse za pansi pa thambo ngakhale kumwamba panopa anthuwa atisocheretsa masiku omaliza ano
@EDSONNAKULENGA4 ай бұрын
Eeeeeee komatu zizibazi sizabwino
@joegibsonzulu25994 ай бұрын
Shatapu.Kagwere uko ndi bodza lakolo.
@S-rr1eu3 ай бұрын
You mean kut chakwela wapha zake coz anaitana makaka olakwa? Mulungu akutsutsan abusa.😢
@Lawrencenkhoma-b2s3 ай бұрын
Lucias banda Ndy kuti samadwala kkkkkk
@reality61654 ай бұрын
Ndi bodza.la.phwee ili. La Dala dala kuti mudzikambirana . The possibility is there kuti mutu wankhani utha kukhala oona kuti zinachokera mu kachisi wawoyo . komanso zitha kukhala zabodza . Cholinga chake nchaaa??
@quincyswart18844 ай бұрын
Amayooooooo
@PreciousLungu-z3t2 ай бұрын
Koma iyi audio yimaynkhula za ku L C D mmene yinaliri meeting yake
@RaffickAllie4 ай бұрын
Pena ndikutha kukhurupilira cause ngodzi zanyanya abale mmmmmmmmm dairy ngodzi
@clementchipinga98484 ай бұрын
MCP propaganda imeneyi machende anu!
@NovemberMmangathayo4 ай бұрын
Ndimalemekeza twayibu koma na iyiyi mwapala malume