Adad ofuniks apangise mega rallly. Kuti athu alandile chimanga chifukwa Kunene kwapiita adad animal amabwera NDI chimanga
@MathewsChakhutamadziАй бұрын
Forward ever never backward
@Samuel-c1j1tАй бұрын
VUTO AMALAWI TIMATENGEKA CHIRI CHONSE ANTHUWA AKALOWABOMA THEY JUST WANT TO CONTINUE STEALING WHERE THEY LEFT AND THEY BECOME BILLIONAIRS OVERNITE WHILE YOU AND ME ARE LANGUISHING IN POVERTY PHINDU LAKE NDI CHANI AAAAAA
@kingsleyhopematchaya5184Ай бұрын
@@Samuel-c1j1t sukunama apapa akuona kt adzamalizitse manyumba anayima aja
@IsaaczidanaZidanaАй бұрын
Phindu palibe kaya anthufe mzimu wachidziwitso umatidutsa bwanji,dpp yi akunama
@babranzima8120Ай бұрын
Koma adpp amapangazao komachokudya tinalinacho bwezi pano athu arugula chima chimapezeka sitikulira fundozao ai koma athu ife akumdzi sitingakwanise kugula chimanga patengo wodula fertilizer ndiokwera mtengo athu Salinas pano chaka chamawa kukhalso njala muulaliro wa dpp kunali better
@AmosStambuliАй бұрын
Ndale zakumalawi zomangonyozana basi.
@Paul-z6k4lАй бұрын
APM, NDIYE, OTSUTSA
@SamisonLevison-z5pАй бұрын
A Chisale musazafe chonde muzangosowa,mumatiimilila
Ili ndee boma tinapanga mistek kobas mulilongwe muno
@Samuel-c1j1tАй бұрын
😂😂😂 anthuwa a dpp avutika BOMA NDI LOMWELI MCP 2025 OPPOSITION IKUNGOTAYA NTHAWI
@inessmsiyambiri8517Ай бұрын
Ukamakhuta munthu susowa
@morisndalama6380Ай бұрын
@@inessmsiyambiri8517 Koma ndiye
@AmosManyera-s4pАй бұрын
Izizi uzalembe tikavota bwanji
@OkalekaleАй бұрын
Munatsala ma savage mu DPP,palibe chimene angadzapangenso chachilendo,anthu adzalira,ndali za pa Malawi ndi za mbuli,a Ndale ndi anthu ovota omwe.Ku Malawi kunasokonekela ndipo anthu asadzinamize kuti chipani china chake chidzasintha zinthu,Democracy ndi system ya nyansi