MCP imakugwiritsani ntchito kuno muononge DPP, mumati mukufuna Nankhumwa akhale mtsogoleri wa dziko. Lero Nankhumwayo ali ndi chipani chake mwamuthawa. Dyera siyabwino a Botoman.
@StarleckChafudzika-p6e2 күн бұрын
A Botoman angokhala munthu wokula mtima waphuma wosayamika m'mene akuyankhuliramo angopita ku mcp ko chifukwa nkuyankhula kwawo is praising the current administration.
@henryphiri61002 күн бұрын
Pitani ku MCP akulu. Manganya group. Lets wait and achitsiru mwaziona lero zimenezo nthawi imene unali ku DPP sunkaona mavuto amenewo. Ma bank ayamba kubera anthu lero. Zidakuvuta kulorera Mutharika apa ukutiuza zolorerana