Soja kwake kwantha kwasala Kwa inuyo ndiye mulira mpaka liti?,
@hazel-deannkhalamba90703 ай бұрын
Mini Soldier. Your father is proud of you John
@LinessPelete3 ай бұрын
Anali munthu wa luso kwambiri nyimbo zake tidzazikondabe ngakhale iye wapita
@HevenChiwaya3 ай бұрын
RIP sir SOJA Lucius banda ntchito zanu zikuchitila umboni young soja boys still rising!!
@chikhombe13 ай бұрын
Kodi mwambo wa maliro MUKUTI? 😊
@madalitsomakawa97083 ай бұрын
Limenelo khwimbi la anthu mmm odala soldier
@ZayithwaKumwenda3 ай бұрын
More love to soja rest well king let’s indeed celebrate his life❤❤❤
@AlihIbrahim-w6n3 ай бұрын
Mulungu akadamakhala kuti amalankhula live,,,akanatilankhula ndithu,?mwapemphela kumutchula Mulungu kupempha chikhululuko kwa munthu wakufayo then mukubweletsaso zida mkumayimbaso nyimbo bwanji koma A malawi,,,Oh paja mmati kuyimba ndiluso lokupasani Mulungu eti
@doreenkaliati31662 ай бұрын
Ndizomwe ananena mwini wake kuti pa maliro ake anthu azakodwe not kulira Rest Well Mr Banda tidzaiwala koma chikumbumtima chidzakhalapobe mpaka Kale ❤❤❤❤❤❤
@HappyAbyssinianCat-xt2bm3 ай бұрын
Like father like son John umatha iweyo ambuye akuze malire amoyo wanu ana a Lucius Banda, zinchito za soja zikuchita umbon
@BMDMasulani3 ай бұрын
Rest in peace solder ndidanena kuti maliro achibade anali amfumu komanso amene adzafananenae adzakhala solder ena ankabwezamoto mwaona?
@BestMtawali3 ай бұрын
😂😂😂😂zamaliro zatha bas maliro amjune 2024🙌🏻
@macknesschirambo64072 ай бұрын
R.i.p . Soldier
@HawaMkwaila3 ай бұрын
Ñdie muti tonsefe pa dziko tizamwalira anthu onsewa
@kingstonekalonga84353 ай бұрын
Koma maliro anthu olemera ndimavuto bass izi ndizichani able anga 😂😂😂😂😂😂😂😂
@manzyhelp3 ай бұрын
Vuto anthu osauka timalemekeza kwambiri ntenbo
@eunicemacdonaldkaipsa97053 ай бұрын
Kumudxi kwathuso amatero soja wz a musician nde amapanga zimene malemuwo amapanga kutereko akulira ndithu pamenepo 😂
@Jiahmk2 ай бұрын
Iyetu anali oimba samatamba ai so musamasokoneze
@PeterPaulChimaliro3 ай бұрын
Tiyenera kusunga mwambo wanthu ndife amalawi
@IsaacsCapetown-hu8wh3 ай бұрын
Aaa ndezikusemphana ndimwambo wamaliro tu ndinkaona ngati pamaliro ndipolila
Maturity kwanu konko coz they are just celebrating a life of a hero and that's what Soja always wanted and that's y amati aliyense zintchito Zake zimamuchitira umboni
@gracekabango66873 ай бұрын
Haven't you ever seen anthu akusewera mpira pa maliro amunthu okonda or sewera mpira? Music was Lucius's life...and akumulira in that way
@victorbanda90393 ай бұрын
Ana a MMA 2000 zamalilo Kodi mukumaziyendetsa bwanji
@@HannahChingwalu Hannah, maliro timayenera kuwapatsa ulemu ndiife ma Africa not Kuti azilira
@TsuzenThomas3 ай бұрын
Aliyense ntchito zake zimamuchitira umboni n Soja ntchito zake zamuchitira umboni, John was just celebrating a life of his hero nothing more nde maturity kwanu konko
@JumaKachala3 ай бұрын
Zawonjeza kwambir. Mmmm
@oskidooscar74682 ай бұрын
Koma akhristu kkkkkk
@CatherineDesire3 ай бұрын
Ka Isaac kanakali NDI moyo🙄🤔nanga Oliva alikuti?
@VanessahChikuwo-k9c3 ай бұрын
jane nduona koyambayo?
@PatrickMulangala-os4by3 ай бұрын
Odwala akuvutika mu zipatala
@TomasDzifoole3 ай бұрын
Adamtalika alibe zelu.
@PatrickMulangala-os4by3 ай бұрын
Amphawi akuvutikabe
@AnointedElijahPastor3 ай бұрын
It's Malawi now funeral party like Dubai
@DivineSyntaxMw3 ай бұрын
Don't catch feelings but trust me that's what Lucius Banda wanted his funeral ceremony to be like, let people fulfill Soja's desires..
@jogechawa61923 ай бұрын
Anyapala inu Lucius anayimba nyimbo kuti asazalire pamaliro ake but celebrate him
@hazel-deannkhalamba90703 ай бұрын
That's how he wanted his funeral to be. The song talks about it all
@charitykadama33543 ай бұрын
Komanso mwana wakeyu ndi olimba mtima ,akuyimba ndi mphanvu eeh
@hazel-deannkhalamba90702 ай бұрын
@@charitykadama3354 hes celebrating the life of his father
I think tikutaya miyambo yathu, azungu akutipusisa no way you can dance during a funeral in malawi this is hilarious
@HawaMamo-q2v3 ай бұрын
Kodi pachikhalidwe chathu chakumalawi .ndi mene zikupangira panopa kumaliro ngati kuchisangalaro .timaona ngati zili kuno kokha ky SA pano ndi kumalawi komwe 😥😥😥😥😥
@greenmatias83323 ай бұрын
Bro munthu uja anali oyimba osamayiwara nde it's must Kuti pa mwambo wake pakhare ngati show ndi zomwe munthuyo amakonda, even nfumu ikafa anthu amatenga maliro kupita nawo pa bwalo
@TsuzenThomas3 ай бұрын
and also remind them kut aliyense ntchito zake zimamuchitira umboni ndpo Soja ntchito zake Zamuchitira umboni