Amene sakumukonda chawezi ndi mbuzi kwaine chifukwa ndikatunduu
@kaphika2 күн бұрын
Munthu wankulu Chawezi, keep it up Dr. Usi ali busy kugawa chimanga APM anawawuza a Malawi kuti azidya mbewa ndi ziwala, Boma lilibe ndalama 😢😢
@billymhoni95272 күн бұрын
Usi sitikumufuna ku UTM Mutengeni ku MCP PLEASE...
@NikolasNanawe3 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤
@PatrickBanda-q7u3 күн бұрын
Chawenzi ndi mbatata ya munthu tikuwona pa 16 September kuti ulowela kuti bwanji osadzudzula cabinet ya Chakwera bwanji? Ma minister 31 poorest country ngati Malawi
@billymhoni95272 күн бұрын
Kufunafuna kuti utm isweke mukumaupondatu
@billymhoni95272 күн бұрын
Utm nde mukusowa nayo mtendere...
@Mrjafman3 күн бұрын
Awa ndi ma praise team
@billymhoni95272 күн бұрын
Anthu ake inu Ayambitse Chipani chake ....
@billymhoni95272 күн бұрын
Inu Usi Anazungulira kuti .....UTM IS STRONGER THAN BEFORE
@PaulKasongo-yc8xy3 күн бұрын
I went to xcul with guy chawezi
@AbdussalaamJulius3 күн бұрын
Chawezi ndikatundu
@Dainaphiri-v8e4 күн бұрын
You say about museum koma anthu akufandinjala shem
@zondwayochipeta47503 күн бұрын
Guys inu mumakwana hvy ❤
@JoshuaNkhoma-u1i3 күн бұрын
Achewezi nzeru zakutherani koma sindikudabwa ndalama zamagazi zimazunguza mutu. A Usi anayitanidwa kuti akakambirane ndiye ngati Usi wakana mumafuna kuti chipani chipani? Simukuwo a kuti usiyo anachita mwano?
@MohammedAllie-d3s3 күн бұрын
Panyini pamanu
@emmanuelmuyilaa3 күн бұрын
Chawez ali mbali ya usi, i see no sense in him.. Why kumuyikira kumbuyo munthu woti akuziwa bwinowno zomwe usi akupanga is wrong..
@PatriciaMumba-qm7pq3 күн бұрын
Palibe amene amakukonda iwe ndiwe wautsilu iwe sumawona
@zondwayochipeta47503 күн бұрын
Ine ndimawakoda ndizako izo
@AHAMADUJRAminie-c6q3 күн бұрын
Machende anko iwe palibe amakukonda iwe
@BacksonLevi3 күн бұрын
Aaaaa inu inu mulichiwalo chotani zazzzz gt simaikonda musamanele tose sitigakonde zomwe inu mumakonda chirugamo mchabwino iwe wasiru garu