Good lawyer can sort this case with easy ...Mr banda just find a good lawyer to represent you
@NothandoNovey24 күн бұрын
Bwanji kumalawi kuno tingokhala ndi MDF police ingotha basi
@foscohSamboko-uz1ex15 күн бұрын
Apolisi penapake zikavuta timagwiritsa ntchito nzeru osati malamulo galimoto tikukamba apayi ma key ake ali ndi ogula wa ku karonga nde zikuvuta pati kufunsa komwe anatenga ma key ngati iye sanali driver, chabwino mwagwira oganiziridwa oyamba zinavuta pati kupita naye ku courts chabwino mwati mukufufuza nde za change of owner ship chikukukhuzanipo ndi chani? Ineyo mukumvetsa kwanga nkhaniyi inuyo adindo mukuziwapo kanthu koma choonde osamupondeleza mphawi nzangayo
@chisomomakiyi-os9bc12 күн бұрын
Ma somalia munawathawitsa, akukakamiridwa ndi Banda sopano..... zinthu Zake zovuta kunvetsa bwanji......
@hockeymoments958324 күн бұрын
From the responses given by Maurice Chapola, there are indications that it is not going to end well for Mr. Andrew Banda. The police are going to try to make him pay for being pushy. If I were him (Andrew Banda), I would have also involved human rights NGOs. The worst thing that can happen to Banda is being accidentalised. Asamale kwambiri.
@HenryKabowa-n4y18 күн бұрын
Mr Banda munatayilila....
@memorychimpesa19823 күн бұрын
25 million 200, Abanda nivichi kasi 😂😂😂😂
@mphatsolupiabanda691017 күн бұрын
Zinyengo kuMalawi sitikapulumuka
@AffectionateGeyser-fm7dl25 күн бұрын
Koma abale mesa munthu obwereka galimoto anangwidwa and is the one who knows the driver .so u are keeping the car yet the owner is suffering and gal8moto ikuwonongeka
@TachikoMwanamanga23 күн бұрын
Khani zina zimakhala za straight and kuwagwila athu ake sizingavute kma police ikufuna kuzungulila that’s y timati police ingotha tikhale nd MDF basi. Khaniyi ikufunika kuipanga follow tione bodza la police. Police yopanda manyazi
@FreedomSibanda-p9r18 күн бұрын
Koma achina banda kkkkk fundo'less sitigulitsa katundu wosamuona
@MzikaPhiri25 күн бұрын
Uyu akhale mneneri wa National Police akufotokoza mwa nzeru zozama
@hockeymoments958324 күн бұрын
Koma zikulakwika kuti mukufotokoza kwake mwachuluka kuopseza munthu odandaula.
@LastonBiliat-j3y23 күн бұрын
Palibepo nzeru zozama apa nanga munthu ayendesa galimoto angabwere aziti ine ndiuja amayendesa galimoto uja ndnzeru zozama zimenezo kkkkkk
@williamsrenford-fb6de14 күн бұрын
Nanuso kupusa ndi izi munasakha nazo chitsilu chimzanu kukhala president, nanga chomwe akufotokoza chanzeru ndichani pamenepo, kuwopsezako? Uchitsilu eti mxieee
@elishamzomera755325 күн бұрын
Dyela awa
@KampilaAllie23 күн бұрын
Chinyengo chadusa basi Andrew banda akuudzani inu a police information yonse andinso anthu onse amene akukhudzidwa pa nkhani imeneyi why simunapite kukagwira anthu amenewo ndikafunsa in frant of Andrew banda ,inu a police nkhani yoti maumboni alipo mpakana kutenga 2 years mukupanga kafukufuku zoona dzimenezo no no no corruption basi a policewo ali gulu limodzi lodzembedza ma Somalia lo asanamidze amalawi
@LameckManuel-f3q21 күн бұрын
😂amakhala adya ndalama man pamenepo amatha kuwapatsa ma million
@EmmanuelGasiten-fo5dr25 күн бұрын
Afrobalometer inapeza Kuti Police yathu ili pa number one, kumbali ya Zinyengo.
@jonesnezara429425 күн бұрын
kkkkkkkkk zoonazake ndithu
@MosesTangwe-q8o25 күн бұрын
A banda munachepa kaganizidwe.the thing you should do is kupita ku police kukalembetsa statement masiku omwe munagwilizana aja munabweleketsa galimoto aja
@RestarUmi20 күн бұрын
Police ikulandilapo zinyengo apa oyendesa akuziwika nde mungozungulila zungulila zadala akufuna muthuyu amulande galimoto
@RihannaKaliati25 күн бұрын
A police chawakulila ndi dyela moti khaniyo aisate bwino bwinoai km kufuna ndalama osauka singamukomele km olemela tisawaweluze abanda Iwo amapanga business
@MassPastor-bn8ck24 күн бұрын
kafukufuku for how long chonsecho mwini galimoto akuzani komwe adabwerekeketsa galimoto there after mkomwe mukapeze emwe amkayendetsa galimoto. Speech yanu inu a Police ikuchitira umboni report la Aforobalometre. Corruption is today's police shelter
@hockeymoments958324 күн бұрын
Sizili bwino at all.
@ZaynMahomed-y4e18 күн бұрын
Wa police uyu ndikape
@JuniorSaine-d6r24 күн бұрын
Its a lesson kwa anthu amene tikuonerafe...Der is for a proper documentation
@blessingsmtawanga25 күн бұрын
Komaso wapolice uyu mfundo alibe amangochulukisa zonena za ziii mot azingopita pa straight point
Mmmmmmm sorry koma malawi anali kare pano ndichipwisi chamalawi 😮😮😮😮
@IbrahimAlli-x4j20 күн бұрын
Zovuta
@stevietungama977522 күн бұрын
Kodi mmesa banda wanena kuti ma key anabwera ndi mkulu wake wa munthu yemwe anabwereka galimoto that means driver anakepeleka kwa Iwo that means he knows where the driver is
@dexzimba408224 күн бұрын
M police uyu ndio upusa kwambili nayeso alinga ngat a mcp mwini wagalimotoyo ampase bas zantha kusiyana ndi bas
@beatricengoma45276 күн бұрын
Mesa ndiwa MDF Banda uyu?
@HAPPYNATHANGA25 күн бұрын
Osazakhulupilira police guys
@kingsleykamwendo283325 күн бұрын
Banda ndiwatulo koopsa and tulo limenero mmmmmm I don't know how I can describe it chipwaza chenicheni.
@RhamaBanda24 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂ukhaliketu ohoooo
@EstherZintambira-sq3yy3 күн бұрын
Ngokondaso ndalama xtrail ntengo umeneo
@patriciazacharia889625 күн бұрын
Abanda penapake dyera linawavuta
@lovemorekasema550622 күн бұрын
So bluebook ya original a police mumafuna ya chani ? 😅😅😅
@EvanceChiponda-dn8ck24 күн бұрын
Eeee zosayenda auncle
@dalitsomambo932022 күн бұрын
Malawi police service mmmmh manyaka Eni eni
@LastonBiliat-j3y23 күн бұрын
Nanga popeza anthuwa anamunamiza munthuyu kut galimoto ili ku garage
@KondwaniKandulu22 күн бұрын
25 million 200 Thousand for a dilapidated Nissan X-Trail 😅
@MorganBanda-oc2jx3 күн бұрын
Ndikuona kut panalakwika apa ndi mwini gamotoyi Banda yi anawononga nkhani yekha. Amalandira bwanji ndalama gamoto palibe? And ataona kut gamoto sikubwera first time bwanji sanakapereke report ku police?? Uyu ngofooka kaganizidwe.....
@RhamaBanda24 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 25 million 200 😅😅😅😅 akuwelengera
@AlexanderBilliat24 күн бұрын
Following
@ConnexKhomba23 күн бұрын
Tikamat a police si abale athu nde muzitikakamiza ubale aaaa