Kangaude: Apolisi anawombela Galimoto ya Andrew Banda kamba koti inanyamula ma Somalians

  Рет қаралды 38,501

Malawi News Update

Malawi News Update

Күн бұрын

Пікірлер: 103
@justinanyirenda6899
@justinanyirenda6899 28 күн бұрын
I've learnt a lot from this story. Let's not risk our lives, this man could have been late by now
@merryMaele
@merryMaele 29 күн бұрын
Great Lessons indeed..Keepon Mibawa with the great .Zulanga.
@MeruMitha
@MeruMitha 15 күн бұрын
so sweet shadi feeding sharuk
@JosephywokondedwawamatitiKamot
@JosephywokondedwawamatitiKamot 28 күн бұрын
Red flags were everywhere koma unasankha kupusa😂😅
@CrytontwalikiManyungwa
@CrytontwalikiManyungwa 29 күн бұрын
Good work Mr Dzulanga
@julianathondoya
@julianathondoya 24 күн бұрын
Uyuu ndi ngumbiii 😂😂😂
@KhulumaniBanda
@KhulumaniBanda 28 күн бұрын
Zili kwa mzako zimawoneka Ngati ngopusa tisalankhulitse ayi
@Nelly-k4j
@Nelly-k4j 24 күн бұрын
Ndipo awuzeni
@haroldmpakiza177
@haroldmpakiza177 5 күн бұрын
Ku Songwe ku Karonga akunenako ndikomwe amakatenga ma Ethiopians, naye Banda ndiwa bizinezi yomweyo
@HassanIzaya-y1p
@HassanIzaya-y1p 29 күн бұрын
Kangaude imakwana kwabmili ndithud 💪💪💪
@PeterwrenClaus
@PeterwrenClaus 29 күн бұрын
Following with interest
@veronicamalisero2671
@veronicamalisero2671 26 күн бұрын
Can't wait for part two....koma akulu Mukanaphedwatu m'boma la eni..mukanatenga ndi wachibale kwa eni kulibe mkuwo apo munakakamizika kumangomvela anthu Oti sumuwadziwa chifukwa munapita nokha amkakuonelelani.komaso Extrail kugulisa pa 6.5 anakupepetulanitu nanu
@LameckManuel-f3q
@LameckManuel-f3q 12 күн бұрын
2023 chinali Chaka chovuta nane nalamdidwa galimoto eeeeee sidzaiwala
@SAUZANDEEmmanuel
@SAUZANDEEmmanuel 28 күн бұрын
Akuluwa kukonda ndalama galimoto abesa
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb 29 күн бұрын
Nanuso ndiwopusa,, this big issue without involving police like serious?? You are so stupid Mr man... Galimoto inalidi yanu or bwanji? Nonsense
@FloraBanda-w7t
@FloraBanda-w7t 29 күн бұрын
Following
@haroldmpakiza177
@haroldmpakiza177 5 күн бұрын
Uyu Banda akunama kwambiri
@RhamaBanda
@RhamaBanda 25 күн бұрын
Kupupwaaa ankolo😅😅😅😅😅😅
@RosinaPatel
@RosinaPatel 29 күн бұрын
Eh lesson learned
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt 23 күн бұрын
😂😂😂 but this guy Ndi mbuzi wezzie kkk the way he thinks aaah noooo
@chemunyapaComedy
@chemunyapaComedy 28 күн бұрын
Izizi sizinali za normal kamankhwala kadalipo
@Nelly-k4j
@Nelly-k4j 24 күн бұрын
Koma anthu oyipa bwanji kumupepetula muthu zoona
@memorychimpesa198
@memorychimpesa198 27 күн бұрын
Man munangochenjera koma ndinu opepera mxiiiew mpaka kubetsa galimoto zoona.
@PeatryNdanga
@PeatryNdanga 27 күн бұрын
Pakumvetsetsa kwa ine mkuluyu akunama nkhaniyi siikumveka
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri 29 күн бұрын
Am touched
@giftchale672
@giftchale672 29 күн бұрын
Akuluwa ndi wopoira
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy 29 күн бұрын
Ndipo akanatha kuphedwa motsavuta
@LameckManuel-f3q
@LameckManuel-f3q 12 күн бұрын
Siopusa koma satana akat akukonde mmmm sizimaenda
@EmanMiles
@EmanMiles 24 күн бұрын
Allah akbalu
@EzekielBanda-r7r
@EzekielBanda-r7r 15 күн бұрын
Mmmmm munthu wakwathu Apapa akupepetulani ndithu galimoto yapita basi
@alfredpatel3984
@alfredpatel3984 23 күн бұрын
Life has a meaning for everyone. God proved to be God.
@sahilujameswadison-r9i
@sahilujameswadison-r9i 28 күн бұрын
Uyu amakonda ndalama kwambirii
@dyanchilongo5088
@dyanchilongo5088 28 күн бұрын
part 2 bwanji
@EdwardPhiri-n1e
@EdwardPhiri-n1e 28 күн бұрын
Umakwana zulanga umatimvesa kukoma kwambiri
@coastersRob
@coastersRob 29 күн бұрын
Koma amwene munapusa motani kodi shaaaa
@lucksonsaka700
@lucksonsaka700 16 күн бұрын
Aaaaaa ndamva nkhaniyi koma Mr banda be careful zomwe munachita apa mnagona kwanbiri kupereka galimoto kwa anthu oti simukuwaziwa kumati akayendese okha mmmmm ayi zoopsa plus kusayina document yoti mukugulitsa galimoto koma milandu ina msanathane nooooo pamenepa munapusa ndithu
@amauzak
@amauzak 15 күн бұрын
Zitha kuchitikira wina aliyense izi
@LucySaidi-o6b
@LucySaidi-o6b 28 күн бұрын
Koma Inu ndiopepela bwanji
@mwalemmercy9249
@mwalemmercy9249 28 күн бұрын
Zamankhwala izi
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt 23 күн бұрын
Mwina panali nkhuzumule sure
@FrankChanza-l3g
@FrankChanza-l3g 29 күн бұрын
Inu galimoto mwagulisa kupusa kwambili mwa onjeza
@AnetBanda-b5i
@AnetBanda-b5i 19 күн бұрын
Koma bwanji nthawi yose yo samapanga involve police????!
@ronaldnyirenda1452
@ronaldnyirenda1452 15 күн бұрын
Part 2 until now??
@EmmanuelMankhwazi-qb4zt
@EmmanuelMankhwazi-qb4zt 26 күн бұрын
first u could hav see the car in malangalanga to comfirm kut yaonongekadi
@ThokozaniBanda-cx7fw
@ThokozaniBanda-cx7fw 28 күн бұрын
Ndichamisala mukucheza nacho lero
@AlasonPaulo-ht7zb
@AlasonPaulo-ht7zb 22 күн бұрын
Koma ndimaziwila galimoto sungangomupasa Muthu osamuziwa inatokhala njingaa
@LovenesskNali
@LovenesskNali 27 күн бұрын
😂😂😂😂😂 anawapatsa mankhwala opusitsa awa si nchina ayi
@ElizaJoseph-q9w
@ElizaJoseph-q9w 27 күн бұрын
Mmm zosayenda
@darlingtonkamanga4858
@darlingtonkamanga4858 21 күн бұрын
Still waiting
@TiwongeWaonanji
@TiwongeWaonanji 21 күн бұрын
Story ndiya bwino koma mtola nkhan iwe umandibowa mafuso umachilukisa kwambili
@JamesJohn-pg4tk
@JamesJohn-pg4tk 26 күн бұрын
Koma zinaz
@lungisanishezi1023
@lungisanishezi1023 28 күн бұрын
Kufoyra kwa bwanji uku
@patriciazacharia8896
@patriciazacharia8896 18 күн бұрын
Abambo opusa awa ndithu
@amauzak
@amauzak 15 күн бұрын
Anthu ena ndioyipa. Zikhoza kuchitikira wina aliyense. Learn a lesson here.
@JescaChimaliza
@JescaChimaliza 28 күн бұрын
Km abambo awa kugna kwabwanji uku 🤣🤣🤣🤣ati dekhan basi 😂😂😂
@MosesMahowe-vn2tl
@MosesMahowe-vn2tl 29 күн бұрын
Nkhana kupusa chaiko galimoto kulonjera nge ninkani mmmmm daily kumpusikani maboza nga Mwana 😂😂😂
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri 29 күн бұрын
Others use juju
@esternchimwala6926
@esternchimwala6926 28 күн бұрын
Careless
@christophermmakiwa7829
@christophermmakiwa7829 28 күн бұрын
Kupereka galimoto kwa munthu osanziwa iwe kusala,kupusa kwa mtundu wanji uku
@KennedyNYiRenDa-s8w
@KennedyNYiRenDa-s8w 28 күн бұрын
Kukonda ndalama Mr Banda ngati hule bwanji wabesa gamoto iyo kuchenjera kopusa uko
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 22 күн бұрын
Kukonda faranga inu
@GanieBwanali
@GanieBwanali 29 күн бұрын
Bro ndinu achibwana kwambiri how can you trust munthu oti mwangopezana kumene😢 mupaka kumusiyila gamoto 😮 look at now 💔🙌
@DannyMkochi
@DannyMkochi 29 күн бұрын
Kodi town yiribe udolo,munthu umaberedwa nyumba yako yomwe
@DannyMkochi
@DannyMkochi 29 күн бұрын
Utha kuberedwa ndimzako omukhulupilira..iyeyo amapanga business munthu atha kubwera pa rank kuzapanga hire galimoto oyendesa kukhala iweyo umakhala ukuwaziwa anthuwo ngati?
@EstherZintambira-sq3yy
@EstherZintambira-sq3yy 28 күн бұрын
Ndipo galimoto sikubwela ndalama sakupeleka mkumati tikugule mkumalandila Tina 75 150 ayi 1mita galimoto kugulisa ngati chimanga aah xtrail 6.3 nde yotchipatu koma Andrew bands aah
@EstherZintambira-sq3yy
@EstherZintambira-sq3yy 28 күн бұрын
Nkhani yomvesa chisoni zedi antamata ameneo osawamangisa bwanji
@gesinasutherland9241
@gesinasutherland9241 29 күн бұрын
nkhani yomvetsa chisoni.koma mumphuzile dont trust anyone..ndipo musadzapangenso..mwatenga mphuzilo
@Nelly-k4j
@Nelly-k4j 24 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😊
@RashidBiyala-x3c
@RashidBiyala-x3c 28 күн бұрын
Kuru uyu akuziwana ndi athuwo asatithelepo data apa
@GrivinBanda
@GrivinBanda 27 күн бұрын
Nthawi yonseyo or kuziwisa apolice
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 27 күн бұрын
My thoughts exactly??????
@BlessingsCperumal
@BlessingsCperumal 16 күн бұрын
Pepera
@RihannaKaliati
@RihannaKaliati 22 күн бұрын
😂😂😂
@ChimwemweMchoma-cz3gc
@ChimwemweMchoma-cz3gc 25 күн бұрын
Komatu kulongosolako nde kumavuta et hahaha mpaka nkhani kumveka ngt yongopeka pompopompo
@mickiaskumbasa136
@mickiaskumbasa136 27 күн бұрын
Ambuye akuthandizile oyipayo achite manyazi
@chimzyPhiri-e2u
@chimzyPhiri-e2u 29 күн бұрын
Wunagulisa galimoto iwe
@Nelly-k4j
@Nelly-k4j 24 күн бұрын
Koma zoona iziii
@DJSuper-zb8jf
@DJSuper-zb8jf 28 күн бұрын
Koma ada awa amatha kulongosola
@Nelly-k4j
@Nelly-k4j 24 күн бұрын
Ndilipano kunvela
@RhodiWhite
@RhodiWhite 18 күн бұрын
Pati 2 ili kuti
@justinanyirenda6899
@justinanyirenda6899 28 күн бұрын
Abambo inu anakuphwisirani mmaso chani?
@Nelly-k4j
@Nelly-k4j 24 күн бұрын
Aaaaaaaa kulakwa
@Nelly-k4j
@Nelly-k4j 24 күн бұрын
Week inotu
@JamesKamtedza
@JamesKamtedza 28 күн бұрын
Taphuzila zambili or zili zosekesa
@KondwaniKandulu
@KondwaniKandulu 28 күн бұрын
Gangata ananenapo kuti Palibe wolemera wopusa, Awa anali olemera opusa sure
@MadalitsoGolombe
@MadalitsoGolombe 28 күн бұрын
Gwamba kukonda ndalama...dekhani
@ziyamikanmakowa5981
@ziyamikanmakowa5981 28 күн бұрын
Muli ndi tulo a bambo inu
@BezaiMwale
@BezaiMwale 16 күн бұрын
😂😂😂😂 Anawadyesa balalikani
@FrankChanza-l3g
@FrankChanza-l3g 29 күн бұрын
Akunama uyu ndi cigawenga
@PatienceMphuche
@PatienceMphuche 29 күн бұрын
Inu angakupusiseni choncho kusaina zimenezo
@VictorireneuPio-d2n
@VictorireneuPio-d2n 29 күн бұрын
Eeeee koma khani yake
@FaziluKenneth
@FaziluKenneth 29 күн бұрын
P
@RobertChikawonda
@RobertChikawonda 29 күн бұрын
Kumachenjela
@JuniorSaine-d6r
@JuniorSaine-d6r 18 күн бұрын
Uyu nd mbatata ndthu ..how can you sign such document 😂😂😂...Ngumbiii yenyen
@k.wazamw
@k.wazamw 5 күн бұрын
aaaaaa koma anthu enawaa
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo 29 күн бұрын
Ndiwe upusa kwambiri komaso mutu wako suyendabwino
@EstherZintambira-sq3yy
@EstherZintambira-sq3yy 29 күн бұрын
Atamwa kale mafuta kk
@mhoneelvin
@mhoneelvin 29 күн бұрын
Zachisoni tisakonde ndalama
@lovemorekasema5506
@lovemorekasema5506 28 күн бұрын
😂😂😂😂 kkkkkk
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 27 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 Abamwa chani??
@EstherZintambira-sq3yy
@EstherZintambira-sq3yy 27 күн бұрын
@chesterphiri7523 a petulo
@FaziluKenneth
@FaziluKenneth 29 күн бұрын
😊p
@Jonas-v8y
@Jonas-v8y 9 күн бұрын
Ukalozedwa sumanunkha, aise ukanafa iwe
TCHUTCHUTCHU | 2 JANUARY 2025
55:11
Malawi News Update
Рет қаралды 3,8 М.
How Strong Is Tape?
00:24
Stokes Twins
Рет қаралды 96 МЛН
Try this prank with your friends 😂 @karina-kola
00:18
Andrey Grechka
Рет қаралды 9 МЛН
MFUMUKAZI | 2 January 2025
28:34
Malawi News Update
Рет қаралды 18 М.
Cruise 5 with Prophet Habakkuk Stanford Sinyangwe
1:06:02
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 103 М.
From poverty to progress: 1 year of cash impact | GiveDirectly
3:49
Michael Usi - Akanaziwa sakananena izi
5:36
Malawi Top Talent
Рет қаралды 2,8 М.
Moyenda Pa Mibawa Tv- Able Zulanga Kucheza ku Monkey-Bay_Cape Maclear
28:16
CRUISE 5 WITH ROSSANA STELLA TURNER
1:18:43
Zodiak Malawi
Рет қаралды 48 М.
Молдавия готовится жить без российского газа
1:13
TIMVETSE | 2 JANUARY 2025
1:17:03
Malawi News Update
Рет қаралды 2,1 М.