KENNETH MSONDA WAPASIDWA NDALAMA KUCHOKERA KU MCP KUTI ADZITENGA INJUNCTION KU DPP

  Рет қаралды 16,509

TIDZIWE TV

TIDZIWE TV

Күн бұрын

Tidziwe tv

Пікірлер: 51
@dysonmasuligama
@dysonmasuligama Жыл бұрын
You are a Star Mr Nthanyiwa I always tune to your FM Radio please keep it up. The sky is the limit.
@replacefruittreenursery
@replacefruittreenursery Жыл бұрын
Very powerful msg brother
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr Жыл бұрын
Program yabwino koma mmayankhula nkhani mwaphuma, ndimopanda ndondomeko, modukizadukiza, easy pofotokoza nkhani. ndesizikomayi but to me l love the program. ❤❤
@JamiraJamirashaime
@JamiraJamirashaime 3 ай бұрын
Kkkkk koma kwachematu 😂😂😂✊✊🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼Winaathawa
@FiannaFiannakaponda
@FiannaFiannakaponda Жыл бұрын
❤❤❤ exactly achakwera sakuwina
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw Жыл бұрын
Kodi naye ken Sonda osazivera chisoni .mutuwo wangosara ngati ana Amabarame osamera mapiko ...
@AnishaMoosa-ej7yr
@AnishaMoosa-ej7yr Жыл бұрын
ATHU akuvutika mmudzimu why osatenga money zo to help people eeesh
@meganabigail-ye7fw
@meganabigail-ye7fw Жыл бұрын
Kodi pricence chitsulo oyimba gospell yu kapena wina?
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga Жыл бұрын
anyamata a ku times adapanga chani achina boni kalindo analikuti aaa
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete Жыл бұрын
❤ big up brother
@jonathanmbewe4246
@jonathanmbewe4246 Жыл бұрын
Eish
@amadichembe4068
@amadichembe4068 Жыл бұрын
Mwadzuka bwanji achimwene,pa nkhanga zaona,pa rimpopo FM radio,
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi Жыл бұрын
Audio ?
@MusaFrackson-n8l
@MusaFrackson-n8l Жыл бұрын
Princess chitsuro wake yemweyu oyimbayu? Anawamba ndale? Abale tandiuzani
@AustinChiyembekezo-cx4mz
@AustinChiyembekezo-cx4mz Жыл бұрын
Henry messaged can do that even ever [dpp
@alexsumani6823
@alexsumani6823 Жыл бұрын
Kodi a Msonda angabweletse kusintha kwanji ku ndale aaa mxiu
@amadichembe4068
@amadichembe4068 Жыл бұрын
Ndakulupilila pa zomwe mumaya nkula pa nkhanga zaona,namva kuti ena amboma akuwafuna ku icc ,
@SymonMwingitsa
@SymonMwingitsa Жыл бұрын
Musachedwe ndi msanje zonse zakambidwa apa ndi za msanje mayina onsewa mwawathulawa mukutathawuza kuti dpp kulibe mwatsa ndinu amtanyiwa mmm inu ndikholokolo amtanyiwa
@kantionsankhulani
@kantionsankhulani Жыл бұрын
Kodi dziko rathu likupita kuti Eish 2:07
@JohnChibalo-wf8gr
@JohnChibalo-wf8gr Жыл бұрын
Lipompo ndi ntanyiwa sitizakhala.muumbuli wakusadziwa
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w Жыл бұрын
Umavumbulusa zobisika bro keep going
@CharlesNtasa-k2n
@CharlesNtasa-k2n Жыл бұрын
Tiyenazoni comred Mtanyiwa
@RuthRuth-h6w
@RuthRuth-h6w Жыл бұрын
Ubwino wake pano chilichonse chikumaululika dzikoli si ladzana lija ,APM bomaaa
@AliAlihasin
@AliAlihasin Жыл бұрын
APM ndi TUPELE more fire
@echitemaemmanuel3370
@echitemaemmanuel3370 Жыл бұрын
Limpopo
@TisaiwaleTewesah
@TisaiwaleTewesah Жыл бұрын
Kod asilikali anthu akugona chonchi kumalolera ziko lathu likupangidwa zonyasazi
@StewardRLikaka
@StewardRLikaka Жыл бұрын
Comred nyimbo izi mutigaila sure
@FiannaFiannakaponda
@FiannaFiannakaponda Жыл бұрын
Agalu amenewo achoke l don't like this man 😢😢😢😢
@mbaliehaward947
@mbaliehaward947 Жыл бұрын
ADPp mu chenjele ndi mamembela anu
@JamiraJamirashaime
@JamiraJamirashaime 3 ай бұрын
😂😂😂😂
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga Жыл бұрын
bomali musapuse nalo tiyeni tizisova mavuto amakomo mwathu kuti enanu mukufuna ma udindo mu zipani
@TisaiwaleTewesah
@TisaiwaleTewesah Жыл бұрын
Mumativesa kukoma kwambiri Mr nganganga pambuyo pano
@mbaliehaward947
@mbaliehaward947 Жыл бұрын
Mr robot amfana wokonda ndege osati kuona mene anthu akuvutikila zausilu chakwela
@AjiliIssah
@AjiliIssah Жыл бұрын
Olo atapanga motani chakwera 2025 wautali
@FranciscoMasuli
@FranciscoMasuli Жыл бұрын
Ken nsonda mbolo yako uwonekera poyera galu
@Pangolinimw
@Pangolinimw Жыл бұрын
Chakwela achoke
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev Жыл бұрын
Amsonda tazimwani ma ARV wo shup it wangosala dzimaso zokhatu tudzuuuu
@mbaliehaward947
@mbaliehaward947 Жыл бұрын
Ayaluka
@MarcoHenryMazombwe
@MarcoHenryMazombwe Жыл бұрын
Iweso nde zolankhula zako zimakhala zopanda nzeru zokhazokhatu
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd Жыл бұрын
Koma limpompo sidzatheka
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu Жыл бұрын
😅😅😅
@MagretMvula
@MagretMvula Жыл бұрын
Chonde a comrade tiyeni tilimbiikile yithane nayo nkhondoyi tatopa naye mkulu uyu a hoke achoke
@kantionsankhulani
@kantionsankhulani Жыл бұрын
Kodi dziko rathu likupita kuti Eish
@AliVuyo-re3cy
@AliVuyo-re3cy Жыл бұрын
Zikoli sililibho kunena zona
@LuciusMowa
@LuciusMowa Жыл бұрын
Akugula anthu Kuti azawavotere 2025 ndiye akukuganiza Kuti amalawi ndioputsa amalawi osavotera MCP ndi tonse alliance ndimbava zokha zokha
@mbaliehaward947
@mbaliehaward947 Жыл бұрын
Zoona
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Жыл бұрын
Yebo butt
@HusseinKachala-ml7ut
@HusseinKachala-ml7ut Жыл бұрын
Tigayileko nyimbozo iwee
@BamusiKadzuwa
@BamusiKadzuwa Жыл бұрын
Zovuta
@kantionsankhulani
@kantionsankhulani Жыл бұрын
Kodi dziko rathu likupita kuti Eish
@kantionsankhulani
@kantionsankhulani Жыл бұрын
Kodi dziko rathu likupita kuti Eish
We Attempted The Impossible 😱
00:54
Topper Guild
Рет қаралды 56 МЛН
VIP ACCESS
00:47
Natan por Aí
Рет қаралды 30 МЛН
DÎROK Û XWÊZA / ŞIRNEX
23:49
PELFİLM TV
Рет қаралды 19
Nyau Dance- Midlands Province Culture Week Celebrations 2022
5:10
Impact Stories Zimbabwe
Рет қаралды 127 М.
APHANA OKHAOKHA A MCP
17:54
TIDZIWE TV
Рет қаралды 8 М.
Landing In Blantyre Malawi - Air Malawi
3:02
Muslim Xplorer
Рет қаралды 40 М.
We Attempted The Impossible 😱
00:54
Topper Guild
Рет қаралды 56 МЛН