Mudzina la yesu amangidwe ndipo chakwera a chotsani anthu akukuchitsani manyazi
@joicemartin-ji5zu9 ай бұрын
Kumkuyu amayerekedwA kudzitenga ngati iye ndi mwini dziko waona kumkuyu zomwe amachita Mulungu Watsala ndi ladzaro ndi zikhale ng'oma Mulungu awayalutsa safulumira sacedwa
@JosephMagombo-ex7cx9 ай бұрын
You welcome back 😊
@HappyJohn-vw3ul9 ай бұрын
Umatha big man❤❤
@fredgabrielnyangulu9 ай бұрын
Muwulureni basi timudziwe kuti ndi ndani kapena ndiwomwe ali pomwepowo
@amadichembe40689 ай бұрын
Moni Moni antanyuwa a Saro a dc, a mpepo a njaji ndi ena onse ( a Malawi fest ) mulungu akudalitseni nose
@noahtsamdoka11729 ай бұрын
ndipemphero nyimbo ikhale Billy Kaunda nsampha satchela pamaso pa mbalame simungakole 🤣🤣🤣
@leonardjika21009 ай бұрын
THEY GOVERN OUR GRANDFATHER'S GRANDMOTHERS FATHERS AND MOTHERS AM GOING TO GOVERN THEIR CHILDREN SO HELP ME GOD
@mayesojameskatete9 ай бұрын
Big love brother
@eliffagondewe82149 ай бұрын
Koma ziliko eesh🔥🔥🔥
@user-gu8rx9gq9d9 ай бұрын
I miss you commed ❤ more fore 🎉🎉🎉🎉🎉
@ibrahimjackson-cg6tc9 ай бұрын
Fire 🔥 mabomba
@blessingsnyalo-rp9koАй бұрын
Koma a mtanyiwa😅😅😅😅😅😅
@mayenjefumuАй бұрын
Amtanyiwa ine ndimakunyadira kwambiri ndipo umandivetsa kukoma
@petermasenti20849 ай бұрын
Good work comrade
@amadichembe40689 ай бұрын
Mwadkuka bwanji abale anga apa pa group ya nkhanga zaona ngati mulibwino mulungu akudalitseni nose
@alexjeremanuel25419 ай бұрын
Munthu wake tamudziwa ndi Nan'gogoda ndipo iyeyo ngakhale kumanena kuti ndiwa DPP I think ndikulakwa let us simply say he's an MCP member
@amadichembe40689 ай бұрын
Mwadza bwanji abale anzanga apa pa group ya nkhanga zaona
@yousufjohn9 ай бұрын
Mumakwana big mn
@MorrisMapiriАй бұрын
Limpopo woye!!!!!!!!
@kelvindickson9 ай бұрын
Mumatimvwsa kukoma koma ndikuti kutichosa magwnizo
@AliceChipo26 күн бұрын
Tilinanu limozi Mr Tanyiwa kkkkkkkkkkkkkkkkkkk
@amadichembe40689 ай бұрын
Odi odi kuno ku nkhanga zaona,ndati ndifunseko , Kodi nkhanga zilipo? Moni a munlo,a Ben,antanyuwa .a dc,a Saro ndi ena mulungu akudalitseni nooonse apa pa group ya nkhanga zaona
@IbrahimDailes9 ай бұрын
Timakunyadilani bro
@PatrickNjolomole-vb7jf9 ай бұрын
Tanenani tive
@meganabigail-ye7fw4 ай бұрын
Where are you comlade mtanyiwa
@LysonMtalika-tb6fk9 ай бұрын
Nkhanga zaona, keep us updated comrade 🔥🔥🔥🔥
@mustafahaji25999 ай бұрын
Mumakwana
@sparkdymon34299 ай бұрын
Kkkk mtanyiwa waionela Pali basi ndinakhumwa basi please mtanyiwa khalani nayo pasi makosana awa
@priscillamangata4023Ай бұрын
Comredy mtanyiwa mulungu azikudalisani
@amadichembe40689 ай бұрын
Nati nipeleke moni kwa nonse apa pa nkhanga zaona
@AleksaWilliams-qc6cn9 ай бұрын
Mukupeza bwanji pano?
@jamusnamwino-br2iz9 ай бұрын
koma kukuchitika zithu paka kwasing'anga kkkkkkkkk
...kodi anamachende nonsenu, osangopeza ntchito bwanji...? Kaya ndi zitsiru za MCP, kaya anaPanya a DPP ndi a namitumbo a zipani zina, tapezani ntchito. Some of us are busy building businesses and making our own small economy. Instead of you inspiring the youth to be self sufficient you waste time talking shit. Panya panu nonse. Musamatisokose. We have an economy to build and wealth to create. Zamankhwala zanuzo kapangileni kwanu
@georgednthala-wh3pf9 ай бұрын
Zilibe umboni izi iwe, tht ur cheap propaganda, tamufuse DC, Bon kalindo kuti amapanga bwanji anzako zimenezo, mukuphunzila kumene eti? Ngati wadya chamba kaya ndi cocaine kamwe madzi