Fanz ya MCP imeneyo 😂😂 zakuvutani a Usi basi, chitseko chakupanani.
@sheedampama1462Күн бұрын
kungodzichotsa ulemu ndithu a usi, pangani zanu amanganya,
@besterlumbe44042 күн бұрын
Osamutengera ku court bwanji naphulu ameneyi
@EstherSangwati2 күн бұрын
Akuoneka azimayi okha okha
@HumphreyKasowanjete15 сағат бұрын
Just kick him out of the party please
@HenryLaidon-pl9ly2 күн бұрын
Mbuzi ya vice
@BreezeBarry2 күн бұрын
Manganya he is Coco loch
@TamandaniKayisi-z8s2 күн бұрын
Alikuti aja amamubakira,mukuona?
@thomasbotha97902 күн бұрын
Usi ndikape chifukwa chani iwe usi umatenga masapotazi a MCP kuwapasa makaka a UTM ndiwe kape usi ukàyakhe mlandu kukhoti
@RuthKaledzeraКүн бұрын
Angoyambitsa chipani chake basi
@JoefreyGongoni2 күн бұрын
Uyu apetsa kabambe muzaimva mark my words
@AchinaKellz2 күн бұрын
Siyibwera nkhwari ndipo kupanda kupanga zimenezi moyo wake uli.......... Panja ndi mcp 😂😂😂
@billymhoni95272 күн бұрын
Kod a Usi owatsatira ndi azimai okhaa??
@mishecksipolo71532 күн бұрын
Mudakayamba kaye anthu adatema a dpp pa blue tour aja. Kenako adzikwanje kuma demo Aja then a Musowa finally
@EsnartGirivin2 күн бұрын
Akapitiliza ofunika kungomtibula 😮😮
@GeorgeR.MafambisaКүн бұрын
Auzeni anthu aku ndirande amupande uyu😂😂😂
@EsnartGirivinКүн бұрын
@GeorgeR.Mafambisa 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@AchinaKellz2 күн бұрын
Manganya 😂😂😂😂sana waonekera mwazi wa anthu umafunika kumwa chilope 😂
@JoefreyGongoni2 күн бұрын
Galu iwe usi usatioatse mseru unapha nawo Chirima bombo kalato. Akutandizani chiani ini uphawi wanuwo
@Blessings_The_MC2 күн бұрын
Game iyiyi ikufunika kumaionera outside box otherwise mmmm tipeperadi
@ernestphiri55072 күн бұрын
Crazy Mr usi
@SylvesterWyson2 күн бұрын
Ameneyi kunkholo kwamache mbudzi yamunthu
@JailosWallen2 күн бұрын
Mayikolo ndiwoombanisa mitu anthu
@Nelie-k4z2 күн бұрын
Agowachosa chipanimo Ayambise chake
@thulanimpphiri68732 күн бұрын
Ife anthu aafupi nthawi zambiri timakhala ndi zeru kusiyana ndi anthu ataliatali koma ka usi zeru kalibe ndichifukwa ku tikuferanji wazeru anali mai sikono kusiyana ndi kausi zija ananena ku bbcc kuti kumalawi wamadirama mupaka vice president mmmmm ndizimene akuchita usi zaziiii ngati mwana
@JamesBrown-gx8my2 күн бұрын
Azigotaya nthawi ameneyo mtaeni
@AchinaKellz2 күн бұрын
ndiye ukalembetse chipani kuti akuvotere kapena kapena akavotere ndani? iwe usanyozetse amasewero uli openga ndiwe, guy's Wise ndi intelligent zosiyana😂
@shadreckphiri17992 күн бұрын
Just make Michael Usi the president of MCP. He is better than Chakwera
@JohnYoweliКүн бұрын
Ngati ndi a mcp.ndiyetu.mcp ili ndi fanzii shaaaaa