KODI MUSOWA WAKU DPP ZAMUTHELA BWANJI KU POLICE? NANGA BWANJI ZIKHALE NG’OMA WATOKOTA IZI PA XMAS?

  Рет қаралды 22,018

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 39
@OftenEliasmaguza
@OftenEliasmaguza 10 сағат бұрын
Nanga mmwambamu mwaikamonso a traffic wo kuti aonesese kuti ngozi za ndege mmapangisa zija musapangisenso Ina?
@JoyceMoyo-mp3de
@JoyceMoyo-mp3de 8 сағат бұрын
Good point zilile ngoma is very stupid
@SHAMILAIMEDI
@SHAMILAIMEDI 8 сағат бұрын
Aaaaaa zauchisilu mmalo komanga azikwanje aja
@clairemyegha4315
@clairemyegha4315 12 сағат бұрын
Anthu asangalala bwanji akudya chitedze
@AbisalomJackson
@AbisalomJackson 11 сағат бұрын
🎉
@jumasingano1950
@jumasingano1950 7 сағат бұрын
kuchikangawa bwanji simunapange kuti musagone koma pa Christmas koma guys
@Dellingsmunthali
@Dellingsmunthali 8 сағат бұрын
Apa mwanena fundo yikulu para wakhutako mpasa galimoto munyako amen🙏🙏
@ThomasShuga-z5p
@ThomasShuga-z5p 10 сағат бұрын
Zikhaleyu ali nzithumwa zotani Kodi munthu akuoneka ngati sing'anga Kumati ndi nduna?
@catherinekadwala3839
@catherinekadwala3839 9 сағат бұрын
Kkkkk zovutatu, zot alindima billion ay ndithu
@EmmanuelSambani
@EmmanuelSambani 11 сағат бұрын
Nsono amamutenga asanafufuze kodi zimakhala bwanji Apolice athu amathamangiraku kumanga munthu zamanyazi.
@josephalfred5138
@josephalfred5138 10 сағат бұрын
Kodi mkuluyu amalankhula Ngati wavumata madzi mkamwa bwanji alibe mfundo
@JosephCompan
@JosephCompan 7 сағат бұрын
ine ndchedzela koyenda wapolice ayeleze awone
@Zebron-kg2qz
@Zebron-kg2qz 7 сағат бұрын
MUMALO momakalimbana ndi TZ
@patriciajangaza675
@patriciajangaza675 13 сағат бұрын
Nde Kodi iwowa sakumanga azikwanje amatema anthu anja bwanji
@SteynMaduka
@SteynMaduka 13 сағат бұрын
Mmmmm mufuna muwapherepo anthu inu asakuziwani ndani, munalephera kuika chitetezo kujaku nde chitetezo panopa mumuikira ndani, munalephera kumanga azikwanje nde mukumunamiza ndani inuyo
@CharlesMukona
@CharlesMukona 8 сағат бұрын
Chimimba Ulibe nzelu khala chete
@JulioChiwalo-t4f
@JulioChiwalo-t4f 13 сағат бұрын
Apolisi kusowa zochita kumangomanga anthu chifukwa chankhani za ndale pamene boma lao la Mcp lolepherali likupereka mavuto oopsa kwa a Malawi
@JosephCompan
@JosephCompan 7 сағат бұрын
zikhale ng'oma ndwe kape kwambiri malo mokonza dzikoli ukalongosole za Christmas kkkkkkk ndalama zomwe tikusangalalira ndzathu palibe chitiletsela kusangalala
@FatsanNyanda
@FatsanNyanda 7 сағат бұрын
Wayambitsa yekha kunyoza
@EsetaGerate
@EsetaGerate 10 сағат бұрын
Kodi zikhare ng'oma kumeneko kumeta kapena dzipere 😂😂😂
@AlumakioChingalu
@AlumakioChingalu 10 сағат бұрын
Uyu anayankhuladi mopusa
@AllieAjeedah
@AllieAjeedah 12 сағат бұрын
A police wo tauzen akatenge Nyanja uko zikutinyasatu ife za nyanja
@clairemyegha4315
@clairemyegha4315 12 сағат бұрын
Kumvesa chifundo abale no nkhani
@MolesBrown
@MolesBrown 13 сағат бұрын
Anthu adpp ndi amisala achioxha ndi adpp simukudziwa?
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera 10 сағат бұрын
Wamisala ndiwe ndi chipani chako cha Chikangawa Congress party.
@AcramJuma-lr6np
@AcramJuma-lr6np 9 сағат бұрын
This is Panyopatic for the trafic Officer, it means we are still Pambolicly ill for Machendment ideas 😭😭MCP
@AdyasiMaulana
@AdyasiMaulana 13 сағат бұрын
Koma mcp abale azikwanje aja mpaka pano sakwamanga bwanji
@patriciajangaza675
@patriciajangaza675 13 сағат бұрын
Azinkhale tikufuna mumange anyamata Anu anja osamayankhulira phuno Pano ayi
@Amina-gg5gr
@Amina-gg5gr 12 сағат бұрын
Zikhalenso ndindani?
@HusseinKalima-f4z
@HusseinKalima-f4z 11 сағат бұрын
Iwe umati zamuthela bwanj?
@HerlbertKaalis
@HerlbertKaalis 11 сағат бұрын
Mukupindula chani inu anthu Amamina mutu
@Christopherchapeta-q2j
@Christopherchapeta-q2j 13 сағат бұрын
Apolice sakumanga aka mazikwanje
@jumasingano1950
@jumasingano1950 7 сағат бұрын
nduna mantaka
@StaffordNgalande
@StaffordNgalande 6 сағат бұрын
Kom kumanga ongolakhula pasokhano azikwanje ai apolisi akugwila chito ndi Mcp vuto ndilimenelo
@ElizaKumwenda
@ElizaKumwenda 13 сағат бұрын
Anthu a mcp ndi anthu amisala onse
@EdwardMagaleta
@EdwardMagaleta 13 сағат бұрын
Anthu woipa
@CharlesMukona
@CharlesMukona 8 сағат бұрын
Apolicio onse pantumbo pamako zitsilu alonda panyelopao
Okonkwo, APC Chieftain Review Media Chat, Rate FG Low In Food Production
47:02
Sigma girl VS Sigma Error girl 2  #shorts #sigma
0:27
Jin and Hattie
Рет қаралды 124 МЛН
번쩍번쩍 거리는 입
0:32
승비니 Seungbini
Рет қаралды 182 МЛН
How to have fun with a child 🤣 Food wrap frame! #shorts
0:21
BadaBOOM!
Рет қаралды 17 МЛН
President Chakwera Arrives In Mangochi
1:59
State House Malawi
Рет қаралды 2,6 М.
'MK Party will do well as long as Zuma is still around'
12:51
Newzroom Afrika
Рет қаралды 16 М.
5 Ways to Handle People Who  Don't Respect You | STOIC PHILOSOPHY
29:24
James The Stoic
Рет қаралды 891 М.
Uthenga wa Khrismas kuchokera kwa President Chakwera (Chichewa)
6:49
State House Malawi
Рет қаралды 3,2 М.
Sigma girl VS Sigma Error girl 2  #shorts #sigma
0:27
Jin and Hattie
Рет қаралды 124 МЛН