KODI MWATI KWAGWANJI? LERO ANYAMATA A KWAGWANJI AJA ATULUKIRASO PA TIMES TV KWACHEMERATU

  Рет қаралды 25,332

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 28
@kingsleymsampha2260
@kingsleymsampha2260 19 күн бұрын
We don't have a leader in Malawi. We have just a pastor.
@IshmaelSaidi-i2f
@IshmaelSaidi-i2f 19 күн бұрын
Chakwera ndiwoononga. guys let's fix Malawi now
@SteveKanongwa
@SteveKanongwa 19 күн бұрын
Ineo chakwera uyu aaah nakakhala ndi ufiti ndinakaona kuti ndipanga bwanji
@frankmake
@frankmake 19 күн бұрын
Chakwera mutu ngat manyi oponda😊
@Martha-m6e
@Martha-m6e 19 күн бұрын
😂😂😂😂ifa ija anthuwa apenga ndithu.
@YusufuMasakho
@YusufuMasakho 19 күн бұрын
Kungoti bwana chakwela mutu mwawo sizikuyenda bwino koma iwowo sakuziwa kuti mizimu ya anthu 9 aja zimuvuta ameneyo .koma akunama
@WilliamMisoya-g3z
@WilliamMisoya-g3z 19 күн бұрын
Osadandaula amalawi zitsiluzi 4:42 zichokatu chifukwakungowina adadi
@petrokagona1708
@petrokagona1708 19 күн бұрын
Kkkkkkkkkkkkk. Masamu ake ndiwovuta kuwamvetsa. Austerity measures, kkkkk.
@ubs7030
@ubs7030 19 күн бұрын
Inu akugulani, Kodi mukuyiwala kuti DPP idali ndi ma minister 45? Simunenapo bwanji?
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 19 күн бұрын
Mwazi wamunthutu supita pachabe😂😂😂😂😂chakwela akupenga koma sakudziwa mwiniwakeyo,,,,Madotolo chonde mukanakamuyezatu koma Munthu m'Mutu mwake😂😂😂😂😂
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 19 күн бұрын
Chakwera sadziwa zochita, mutu sukugwila, palibe chomwe wachita, poor Malawi, Cabinet mpaka 31 ministers. Aaaaaaah kuwononga ndalama.
@veronicamalisero2671
@veronicamalisero2671 19 күн бұрын
koma Achunga akanakhala ali n amzawo ahot current aja,ndikuona ngati samamasuka bwinobwinoyi
@petrokagona1708
@petrokagona1708 18 күн бұрын
Have you ever tried to interview the President on such issues? Maybe he can clearly explain the mathematics behind this. How can anyone expect austerity measures to work perfectly while simultaneously maintaining a bloated cabinet like this? Things are not adding up here.
@henryphiri6100
@henryphiri6100 19 күн бұрын
M'busa waonjezera nkhosa mu church yake kuchoka pa 27 kufika pa 31 Church ikukula ndithu. Zikomo mulungu
@limbanibandah4022
@limbanibandah4022 19 күн бұрын
Government for kamajekete not for people
@SamuelKhumbiwa
@SamuelKhumbiwa 19 күн бұрын
Achakwela ndi time yao ku mcp akutsazika zizindikiro zake ndizimenezi,munthu akamafa sasankha pofela amafela paliponse.mmalo mochepetsa akuonjeza,Malo motinthandiza ife amphawi omwe tikuvutika kt tipeze mankhwala kuchipatala,kt tipeze fertilizer ,chakudya ndipamene Iwo akukhutisa mimba zao,talimba kale mitima tachoka kutali kwatsalaku mkochepa ,atimpha kale azipita bas atitopesa
@MichaelKachiboo
@MichaelKachiboo 19 күн бұрын
Palibe chabwino
@ShakiraJackson-x8w
@ShakiraJackson-x8w 19 күн бұрын
Where is brian banda
@SamuelKhumbiwa
@SamuelKhumbiwa 19 күн бұрын
Chakwela mutu wabayizika ,munthu akatembeleledwa zochita zake sizimagwira,
@patrickdamalekani9863
@patrickdamalekani9863 19 күн бұрын
Kod chakwerayu alibe makolo ake akhale nae pasi? Chifukwat szooonayi zomwe amalawi akuwachita
@henryphiri6100
@henryphiri6100 19 күн бұрын
Nyau sikhala ndi kholo 😊
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 18 күн бұрын
Athuwa mutu simukugwila asiyen tiphopa
@PiassDayit
@PiassDayit 19 күн бұрын
ndikukhufuna ndifuse ndani amene Akumufuna chakwela ayimike manja
@MosesChauluka-f9r
@MosesChauluka-f9r 19 күн бұрын
Kodi times mwiniwake ndindani??
@henryphiri6100
@henryphiri6100 19 күн бұрын
Chakwera
@StoreNkhoma-ii2lo
@StoreNkhoma-ii2lo 19 күн бұрын
Times TV imadana ndi aChakwera inuyo simungakwanitse kutsogolera dziko anthu atsankho osafuna mgwirizano àchipongwe inuyo osayamika
Une nouvelle voiture pour Noël 🥹
00:28
Nicocapone
Рет қаралды 9 МЛН