Bas ndizona nyanja yapitadii tasinthanisa ndi mafuta
@NOVABOUYКүн бұрын
Agulisa nyanja ndikugula mafuta 😂😂😂km boma ili lochekedi mu September umu😂😂😂
@SydneyNyasuliКүн бұрын
Mbuzi iwe
@NOVABOUYКүн бұрын
@@SydneyNyasuli mbuzi ndiwe ndi mcp yakoyo nyopakoso bwanji
@WysonChilongaКүн бұрын
eeee moti bomali lasinthanitsa nyanja ndi mafuta😢😢😢😢,koma yeah results of poor leadership 😢
@WysonChilongaКүн бұрын
@@SydneyNyasuliMbuzi ndiiweyo, can't you see kuti ndizochitisa manyazi zachitikazi,ine ndimadabwa Chakwera sanayankhulepo pa nkhani ya nyanja😢😢😢😢,eeeee September kwatalika
@NOVABOUYКүн бұрын
@@WysonChilonga boma ili ndi boma lorephere kwake ndikupha ndkuononga zinthu busy kuloza zitukuko za azawo ngt apange ndwo mu September akupakira awa panyapawo ndi omusatira onse