We need person like u mah , u ar such special for Malawians who suffering bcs of this government of mcp we love u mah for gd dissection
@brothermanjamkhosi14792 күн бұрын
A real man does the right thing because it is right and pleasing to God no matter what people say or write. So Malawians let's learn to be honest in making decisions.
@GideonNkosi-i4n3 күн бұрын
An excellent development. Life matters though, she only needs to be protected. If you are working with carnivals and cannibals, it is good to prepare your Armada.....
@TonyMhone3 күн бұрын
To me Agnes is a Hero in all ways. Umunthu alinawo kuposa enawa omwe sanaonetse kukhudzidwa ndi infa ya SKC.
Welcome development Agness Chikangawa party yatopetsa
@DavidPhiri-s6r3 күн бұрын
Wishing you a long life mama. You know the pain that the woman feels when giving birth. I want many of you in our country for the future Generations coming.
@MayamikoJeke-d5m4 сағат бұрын
Mai oganiza mwanzeru kwambiri ❤
@WilsonMalingamoyo-z5x3 күн бұрын
Mai Nyalonje ndi munthu wa ma principals ake ,ngati munthu siuli comfortable ndi Malo uli
@Chikulamayembe573 күн бұрын
Jonah's analysis is brilliant!
@EssauChimpangoКүн бұрын
Setting best example
@EmmanuelSimthole3 күн бұрын
Mai oganiza bwno kwambili coz is same like pa banja ngati latha nkati mwaana ena mumakhala chkumbu mtima chamu2 yemwe mawakonda ngati anali bambo amapita kwa kwa bambo ngati analiso mai amapita kwamai ndgwlizane nao ao omwe anena kuti or kuxul kumakhala mphunzitsi wina oti akati akuchokapo pa xulpo ana ena amachokaso chilima anali mu2 yemwe wina aliyense sazamuiwala koma okonda a2 ake
@ElizabethMulinde3 күн бұрын
Zoonadi
@hesbaluku72813 күн бұрын
Mai aja ndimuthu wakulu woganiza boo alibe dyere ngat nduna zinazi ma yudasi
@DickinsonLikhoma3 күн бұрын
aululana anapha chilima asala pang'ono
@esthermafaiti35563 күн бұрын
Amaiwo akukhudzidwa ndi imfa ya Chilima 😢 Mzimu wa Chilima ukuwasowetsa mtendere
@AnorldKamponda3 күн бұрын
Inutu ndopepera
@PrinceThom-pe6ie3 күн бұрын
Kum'yini Kwa amako nyau iwe.kodi womwe adapha chilima siwukwaziwa iwe nakumtumbo
@TadalaMtipe2 күн бұрын
Good idea mum
@CHARLESMSAMSON2 күн бұрын
Congratulations
@AchinaKellz2 күн бұрын
Amayenera kulandira chifukwa adauzidwa adikire kaye apule chifukwa adali ali mu system, that woman is smart and good
@SylvesterLikumba2 күн бұрын
Aulusi, m'zoona zomwe ayakhula mr wo
@mabvutomichaelpanagona19493 күн бұрын
Maiyu akuopa kuti,pangapite nthawi ya italibwanji nayeso adzamupha ngati Dr chilima RIP wachita mantha ameneyu apite ndi mtendele kusiyana ndi kuti amwalire mukumudziwa chikangawa amamenya nkhondo ya pansi adzamusowetsa wachita bwino wachoka ndi moyo.
@DelubyMarko3 күн бұрын
She is telling us how hard it is in this government coz this is not what we are expected to this government according the promises we were told.
@RobertLuka-wy9cl2 күн бұрын
God bless Agnes🙏🙏🙏🙏
@TriceBeib-e6x3 күн бұрын
Well done Ag
@WhyteSmart3 күн бұрын
Good sound zikumveka
@MakabaBauleni-c2i3 күн бұрын
Bola akhale otetedzedwa cz atha kumuphaxotu kufuna kusokoneza umboni ,Mai uyu akuonesa kt akudziwa china chake za imfa ya Chilima
Afufuzidwe coz akhoza kutipatsa ka umbon ka ngoz ija
@GodfreyWhayo-hh1dm3 күн бұрын
I was listening to a clp yesterday on KZbin where they were talking of the 10 most rich people in Malawi and our president LMC is the richest person in Malawi ( 300 million USD ) My concern is to know how much he had declared on taking the presidency .
@YohaneNthala-n9p3 күн бұрын
Anthu amapanga kungofuna kut ena aziganiza molakwika
Honestly speaking unlike Kamtukule, Nyalonje was a non performa if anything she might have been keept just to balance up representation in the alliance.
@KelsonThom3 күн бұрын
President analakwitsa kuchedwa kuvomeleza chifukwa,chomwe mayiwa ankasiila udindi zilingati anawa tsekeleza zomwe ankafuna atanena mu nthawi yake