KODI OIPAYO NDI MUTHARIKA KOMASO ATUPELE KAPENA ILI NDI BODZA?

  Рет қаралды 8,479

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 91
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 2 ай бұрын
Musalimbane ndi peter komanso Atupele ...pakampeni paja amaneneratu poyera kut MUSAVOTERE MCP ...nde anthu sanamve akut umafuna change...This is the change..the change can be positive or negative....asiyeni a MCP alamulire chifukwa ndie zimene munavotera...tichimine kaye a malawi...Pena Mulungu amapanga zoti anthu aphunzire kwambiri
@MaureenMaonga
@MaureenMaonga 2 ай бұрын
Zoonad anthu amageya mwano kwambiri akuti tisithe zithu ndie zasithaditu
@RiteRoderick
@RiteRoderick 2 ай бұрын
Koma boss ndiiwe ozindikira koopsa keep it up, mavutowa tinachita kubwelesa tokha. Anatiuza ndipo anatilangiza koma kusanva ndipo ananena Peter Muntharika kuti mukupanga inuzi akubwerawo muona Nyekhwe. Lero ndiizi kaaah
@DanielZitande-y1d
@DanielZitande-y1d 2 ай бұрын
Zoona brother uyu walankhura odiyo iyi ndi mbudzi ya Mano kunsi, ndipo samadziwa chomwe amanena. I love you u ndipo mau anga mwandinenera ndinu❤❤
@JohnAsendi
@JohnAsendi 2 ай бұрын
Zikomo amwene papani Mr pita ndi Tupele muzitikhululukila zoona vuto ndi ife ndithu🙏🙏🙏🙏🙏
@LeonardChinomba
@LeonardChinomba 2 ай бұрын
Abwana osaganiza ndi inuyo don't trust akunena zoona apeter ndi atupele ndi anthu osathandiza anthu akulephela kutuluka kulimbikisa anthu boni kalindo akulimba naye ekha sakumuona mzawo uja chihana akuyenda kumalankhula pa steji dziko ndi kumamva koma peter ndi atupele ndipamene kubisala iwo akuti aopa kuphedwa ndi mcp kodi mufuna muzangonyamulilidwapo pampandopo muzidya misonkho ya amalawi
@macrinenduna1024
@macrinenduna1024 2 ай бұрын
Good comment. Truly these two Gentlemen are real country men.
@MonicaSteve-t5p
@MonicaSteve-t5p 2 ай бұрын
Good correction sir ❤❤
@WayneWinterbottom-y6s
@WayneWinterbottom-y6s 2 ай бұрын
More fire mr D takunyadilani kwambiri mwalankhulabwino
@PetroMatias
@PetroMatias 2 ай бұрын
Ase wayankhura bwino mmanja mwako 🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🤝🤝🤝🤝🤝🤝
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 2 ай бұрын
Ameen Iweyo mulungu akudalisene moyo ukuyangula zabwino mau amuna asitero amavuna dala athuwo
@LovemoreSalima
@LovemoreSalima 2 ай бұрын
Thanks D phiri Auzeni ana amahurewa, Ndiomwe atifikitsa pa manyiwa. Bu shit, anthu amanyi amenewa. Azimuloza Chala ntambo.
@EdsonKamwendo
@EdsonKamwendo 2 ай бұрын
Mai woputsa iwe umafuna azingoyenda wamba iweyo siukuziwa kuti mcp ili ndi chiwembu chachikulu kodi mcp yakutuma ? Ugaluwako
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 2 ай бұрын
This is true boss,, atupere or munthalika asiyeni mavutowa ndiifeyo amalawi kusamva lero ndi izi
@FisherAction
@FisherAction 2 ай бұрын
Ndiye ngati akutero kut samatengapo gawo nkwabwino asayime asiye omwe angamathandizire kumamenyanawo nkhondo bcz we are in democracy no words kupembezana
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 2 ай бұрын
Mr phiri .mwandizizilitsa mtima mwarankhura bwino kwambiri.nditamva vn yonyodza ija ineyo mtima unawawa
@HezekiahItz
@HezekiahItz 2 ай бұрын
Zoona kuyankhur mosacheuka bwana komaso chilungamo anthuwa tithanenao tokha Peter and atupele asiyeni ananyozedwa ngat alibe mitu ngat alibe uzimu asiyen imfa ya saulosi chilima yaripweteka Ndye mikono yanthu tikutsamir kwa a2 awawa Ndye njara ikatikhaulitsa ndipamene tingapite pa mseu
@Freedomchennl47
@Freedomchennl47 2 ай бұрын
Kmaso number one ozikonda ndameneo akuyakhulayo waku mangochiyo ndamene ali adyela
@MaggieCement
@MaggieCement 2 ай бұрын
Ndipo Muthu ndiobvuta ndithu tinya ndizomwe tinkafuna ngati ana akhanda oti nkhongelesiyo yabwela lero hahahahaha
@mozesaine6677
@mozesaine6677 2 ай бұрын
Pure answer
@IshumaerWazakile-u5d
@IshumaerWazakile-u5d 2 ай бұрын
Chachikulu ife amalawi sitikufuna kukhutitsi pazimene Dr piter amatipangira ndiye anthu athira kuwiri
@OscarChandema
@OscarChandema 2 ай бұрын
Moti inu mwavotelaso mavuto aaaa zikozeni nokha kumeneko Peter atupele siwolakwa
@MrsNankhumwa
@MrsNankhumwa 2 ай бұрын
Ndipo APM anatiuza kut mukavotera MCP muzalira, lero nzimenezi munkafuna anyamata paja, ulemu wanu akulu mwayankhula bwino kwabas,
@zaidimussa
@zaidimussa 2 ай бұрын
Muiyu afuna kukoza mbili yachakwela kodi Apm sadanene kuti mudzaona nyenkhwe atupele ndi apm sindikuwapeza ndi mulandu ovulala ife bandi akamange atupele ndi apm ndizoona
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
Peter wakalamba sangathamange osazemba ai ndipotu inuyo mukakakamila peter ndiye zolowa boma iwalani ndithu
@ElizahMadi
@ElizahMadi 2 ай бұрын
Kusankha kwanu a Malawi , muziwona konko. Iwowo analemela kale awa ,mabvuto ndife
@IbrahimUseni-p8f
@IbrahimUseni-p8f 2 ай бұрын
D.phiri wanena zoona,,,ife tinalakwisa
@lutfieabrahams1465
@lutfieabrahams1465 2 ай бұрын
Ndpo zoona bro mwayankhula bwino
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt 2 ай бұрын
Good correction
@LindaMakalani
@LindaMakalani 2 ай бұрын
Chisilu ndamene anavotela mcp yo ine ndinavotela my lovely dad Mr p ndiposo pano it's my vote no matter wat
@FisherAction
@FisherAction 2 ай бұрын
Ayi ndizakale zomwezija ndikwabwino azilankhulapo asakhale zii
@JuuuKomba
@JuuuKomba 2 ай бұрын
Ndipo Apm ndi atupele 2025 anatisiya tikhaule tinapanga chipongwe tokha
@ElizahMadi
@ElizahMadi 2 ай бұрын
Malawi ngakhale wuyifele ,aaa ,chilima anapita ,nkhani yake kufera Malawi . Malawi si woufela
@MoosaDawood-l5c
@MoosaDawood-l5c 2 ай бұрын
Musiyeni uyo wadya banzi walandila ndalama.Mangochi singavotele mcp ai
@HUMPHREYBALANGWE
@HUMPHREYBALANGWE 2 ай бұрын
Tiyeni tingoyang'ana kutsogolo Munthu amadikira chopereka church kuti akhale ndi ndalama ndie mumaganiza kuti angalamulire dziko Lero ndi izi dziko latsala masanza okhaokha
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm 2 ай бұрын
Powerful 👊
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 2 ай бұрын
Tinalakwisa tinavotela ena ndiyekuti tisadzudzule? Usanena kuti musakonze ayi ,,wa Aodio sanalakwise,,,tisawagwadile Oro kuwachonderela,,Iwo nde azamwe mkaka,,
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 ай бұрын
Sanayankhule di bwino bambo amene aja Peter ndi atupere komanso former president Bakili Muluzi anayankhula po za mcp koma anthu kusambva lero ndi izi nde akamayankhula aziyamba aganuza kaye osamangobwebwetuka
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
Mungobvutika boma ndilomweli ndipo sitikusintha apa mungotaya nthawi kulongolola palibe chomwe mungachite
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
Alomwe muli patchito chakwela ndukuzani pano simungamuchotse mulakhula mutopa chitsazo ma by election mukungoluza daily
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka 2 ай бұрын
Walandira ndarama za mcp amenyo
@SellinaSanena
@SellinaSanena 2 ай бұрын
Kusamva kwathu. Don't put the blame on Peter and Atupele. Tinavota tokha
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 2 ай бұрын
Iyeyo akuona ngati a opposition angokhala? A Peter ndi atupele TU siopusa akumuwelenga kaye chakwela yu AKUFUNA amlize kaye uchitsiru wakewo kenako adzuke koditu campaign sinayambe kukhala zinthu a opposition mukuwanyozawo simuwafuna
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
Tsono mukuona ngati mcp ingachoke boma ndi kutukwana kwa ma akitivisinu anthu muli ndichibwana kwabwasi tiye nazoni mukhala ku kotsutsa konko
@Maweya-e5e
@Maweya-e5e 2 ай бұрын
Choka ukuyankha zosaveka azako akuti kampeni osati zimene mukuyankha ndizina zimene akunena aazanu ndi kampeni
@ShearstonNyirenda
@ShearstonNyirenda 2 ай бұрын
Kagwileni ntchito mupeza nalondalama boma lachakwera koma mulesi alipamavuto
@Maweya-e5e
@Maweya-e5e 2 ай бұрын
Peter amapanga kampeni
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
Mcp 2025 boma cadet akhaula ndipo iwe cadet ukanalila musobva😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 ай бұрын
Peter muthalika ndi nkhalamba munthu oti akuziyipitsira yekha pomwe akhala angapange kampen
@EsnartMartin
@EsnartMartin 2 ай бұрын
Amene uja machende ake ndipo ozikonda ndi iye uja ndi chakwera wakeyo
@Mahamudu-q6b
@Mahamudu-q6b 2 ай бұрын
❤❤❤
@YasmeenYalabi-b2c
@YasmeenYalabi-b2c 2 ай бұрын
Bodza len leni ifetu sitikupanga complain chifukwa chilungamo tikuchidziwa inu izi mukuzitenga kut
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 ай бұрын
Ulemu wanu guys mwayakhula bwino kwambili mulungu adzikhala nanu thawi zose onyazao asiyeni azinyoza amachita kutumidwa ndi chakwela kuti adzisusa athu akayakhula chilungamo chachikulu tiyeni tiike zise m, manja mwa chauta akuva kulila kwathu chakwela akadapanda kulamulila dzikoli mukanakhala khondo yoopsa kwambili koma mulungu adalola kuti kutelo kuti ukulu wake uonekele 🙏🙏
@MustapherLino
@MustapherLino 2 ай бұрын
Zoona man, mai awa ndi hule wachabe
@MalungaSteven-i2o
@MalungaSteven-i2o 2 ай бұрын
Mau akulu akoma akagonela
@HassanMbalaka-gb5sv
@HassanMbalaka-gb5sv 2 ай бұрын
Sitinva ife Anthony awa Antananarivo don't vote ❎ theme ife makan
@MaikNkhoma
@MaikNkhoma 2 ай бұрын
Ndiwekape munya 2025 bomasitokusintha
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
Akulu inu mulibe zelu ndipo zomwe mukunenazo chipani cha dpp udf ngati akhala ndimaganizo akowo basi dpp yapita sizalowaso boma ndiwe chisilu basi dpp ndaituluka kuli zitsilu ndichifukwa chake mukongoluza zisakho shupit
@ThulaniPrince
@ThulaniPrince 2 ай бұрын
Koma amalawi tilindimavito, chonyasa chija chayamba kuoneka chabwino kkkkk akangolowa adadi. Muzayambe kunenaso kuti bora chakwera
@ChiefJustin-cl8jl
@ChiefJustin-cl8jl 2 ай бұрын
Ndi mbuzi imeneyo mutharika ndi atupele ndi sogolo la dziko lamalawi
@EnerstManess
@EnerstManess 2 ай бұрын
Wa mcp ameneyo akufuna kut a peter ndi atupele atuluke akawaphe a mcp wabunya
@YusufuUsumani
@YusufuUsumani 2 ай бұрын
Chakwela ndi wamizala wamanyi
@francebanda-du9yk
@francebanda-du9yk 2 ай бұрын
Zonadi. Zimenez O
@patassonelucaszovuta3431
@patassonelucaszovuta3431 2 ай бұрын
Ndie ngati ali ndi mantha asiye ndale kuti akhale moyo wautali umene akuufunao
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
Iwe usabvutike anthu sangabvoteleso dpp kulibe ndipo ndukuuza pano dpp sizabwelelasi boma pezani zina zochita izi mutayanazo nthawi
@AustinMhone-r3s
@AustinMhone-r3s 2 ай бұрын
Ndare za nepotism ku Malawi we need federal system of government otherwise no change to people that's why Malawi is the poorest country in the world.
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 2 ай бұрын
Ndi munthu opepera iyeyo ngati wapatsidwa ndalama azingodya
@StellaCharles-dq8db
@StellaCharles-dq8db 2 ай бұрын
Amai amene aja atumidwa inu satipusise ife eetu ndpo alikomweko kwachakwerako
@shazirahJafali
@shazirahJafali 2 ай бұрын
Kma ndiye akuchita kuonekadi kuti awapatsa kenakake chifukwa nde akulubwalubwatu
@JusticeKawilira
@JusticeKawilira 2 ай бұрын
Mwayankhula bwino kwambiri
@AshanAlexx
@AshanAlexx 2 ай бұрын
Watiyakhulila mwene
@AlliSaiti
@AlliSaiti 2 ай бұрын
Uku nde kuyakhura mopanda nzeru😅😅😅😅😅😅 kod adpp abalalika eti
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 2 ай бұрын
Zoona Peter atupele si ozikonda vuto ndife amalawi ovota mitu inawuma mtanyiwa kalindo bakili TV Peter atupere ndi ena ofunila Malawi zabwino alankhula za mcp koma sitinave. Panopa mukuona mcp ikugwirisa ngongole and ikugawa ndala and amalawi tawona mumene wafera chilima ndi abale athu koma still tikusapota bomalo amalawi tili ndivuto loganiza bwino. Munthu kuti mumuziwe kuti zeru alibe boma kuyakhula mwamatama kuzikona kupereka ndalama kuti anthu amuvotere
@GiftJulius-ro9ev
@GiftJulius-ro9ev 2 ай бұрын
Choka mboliyako...mkamwa mopindikamo...
@VarietyNkhata
@VarietyNkhata 2 ай бұрын
Kma iwe ngati ndiwe mukazi ndiwe hule wangoifuna Boro yaminthuyo asa😊
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness 2 ай бұрын
Tinawakana amapha ma albino amenewo asiye akalamba panopa sitikumvako kuti agwira ziwaro za anthu boma la peter linalibe security ndiposo wakalamba wapume zina mumangonama mulizambiri mu malawi panopa tikuwona zachilendo kale kunalibe ngati ndikukwera kwazinthu si malawi yekha ife tikufuna chitukuko basi zimene mukulankhurazo sizikumveka bora chakwera ndi anthu anuwo
@MohammedAriesa-j4x
@MohammedAriesa-j4x 2 ай бұрын
Opusa
@LovemoreSalima
@LovemoreSalima 2 ай бұрын
Gulu la mahure opanda mzeru ndimanena aja ndi m'modzi mwaiwo ndiweyo. Hule
@yotamumahomed1313
@yotamumahomed1313 2 ай бұрын
Komanso umuuze kut watikwana
@shazirahJafali
@shazirahJafali 2 ай бұрын
Izi nde ndizoonad osapanga complain pa anthu awa ayi vuto ndamene anachotsa dpp kukavotela mcp
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w 2 ай бұрын
Muuze chimbuzi chimenechi mmesa amakuuzani kusamva kwani
@RiteRoderick
@RiteRoderick 2 ай бұрын
Ndipo big amai amenewa ndi chimbuzidi zedi Amai opanda nzeru
@yassinn5634
@yassinn5634 2 ай бұрын
Zaka 84 angathamange.? Anthu osazindikira inu Peter akanangotuluka tsiku limodzi mukuganiza khansala wa DPP akanaluza? Tulo basi
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n 2 ай бұрын
Nzeru ulibe
@yassinn5634
@yassinn5634 2 ай бұрын
Iwe ukuyankhulawe ndi Peter muthalika kapena Atupele akupatsa chani chitsiru iwe kagwade wekha kupepera eti kuzolowera kunyambita nsapato .Khala pansi asiyire anthu ozindikira aziyankhula. IWE SINNENERI WA ANTHU AWIRIWA
@yassinn5634
@yassinn5634 2 ай бұрын
Asiye ayankhe okha
@KestonNGUBO
@KestonNGUBO 2 ай бұрын
A dpp mbuzi yagalu iwe ukuyakha
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td 2 ай бұрын
Tsono iwe wadya banzi ya pitala munthu wadyewa uku one kuziro 2025 mukunya chakwera bomaaa iwe mulomwe mwachepa achewa ndayao atumbuka simuwatha komaso ozindikila alomwe ena Asari Ngati iwe samuvotera pitila DPP yatha Palibe akuifuna tanganizani Mangochi zikumvekanso Kuti mwina pitala akhoza Ku votela chakwera😂😂😂😂😂😂
@LeonardChinomba
@LeonardChinomba 2 ай бұрын
Abwana osaganiza ndi inuyo don't trust akunena zoona apeter ndi atupele ndi anthu osathandiza anthu akulephela kutuluka kulimbikisa anthu boni kalindo akulimba naye ekha sakumuona mzawo uja chihana akuyenda kumalankhula pa steji dziko ndi kumamva koma peter ndi atupele ndipamene kubisala iwo akuti aopa kuphedwa ndi mcp kodi mufuna muzangonyamulilidwapo pampandopo muzidya misonkho ya amalawi
@LovemoreSalima
@LovemoreSalima 2 ай бұрын
Inutu ndiye munyee, mukhaule agaluu Inu.
Крутой фокус + секрет! #shorts
00:10
Роман Magic
Рет қаралды 41 МЛН
Cool Parenting Gadget Against Mosquitos! 🦟👶
00:21
TheSoul Music Family
Рет қаралды 19 МЛН
Зу-зу Күлпаш 2. Бригадир.
43:03
ASTANATV Movie
Рет қаралды 752 М.
How to whistle ?? 😱😱
00:31
Tibo InShape
Рет қаралды 12 МЛН
DD News Mizoram - Chanchinthar Langsar | 17 October 2024 | 3:00 PM
5:21
DD News Mizoram
Рет қаралды 2,4 М.
Iran threatens US, allies ahead of Israel retaliation | LiveNOW from FOX
15:13
Israeli Army Special Forces
1:00:36
Investigations et Enquêtes
Рет қаралды 597 М.
MAFUNSO A ATOLA NKHANI KU PRESS BRIEFING YA OPPOSITION PARTIES
15:31
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 7 М.
TIKU 30 JUNE 2018 B
27:20
Edson Gunsalu
Рет қаралды 222 М.
Крутой фокус + секрет! #shorts
00:10
Роман Magic
Рет қаралды 41 МЛН