Kodi Tonse Tavomeleza Kuti Mayi Annabel Mtalimanja Ayendetse Chisankho? Blessing Chaima Lozalio

  Рет қаралды 2,703

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Күн бұрын

Пікірлер
@StevenMasamba-y1p
@StevenMasamba-y1p 2 күн бұрын
Ameneyo asiiretu asakhuzidwe ndi za mavoti
@AlicksonMakata
@AlicksonMakata 2 күн бұрын
Inde tavomeleza ndipo we ❤❤❤❤❤❤❤❤ her.
@ChidaPhiri
@ChidaPhiri 12 сағат бұрын
Achotsedwe sakuyenela kuyendetsa chisankho cha 2025. Achotsedwe basi
@MwaiChagaga
@MwaiChagaga 2 күн бұрын
Good msg bhudy
@ChristopherKadawati
@ChristopherKadawati Күн бұрын
Ine ndimaganiza kuti zipani za opposition zipite kukadandaula ku court against SMARTMATIC machine.
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 2 күн бұрын
Ameneyu achoke ndithu ndipo machine a smartmatic aotchedwe
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 2 күн бұрын
@@alexjeremanuel2541 Ifetu we’re all about the rule of law….the MEC chair was appointed accordingly and smartmatic is what non partisan house of Assembly chose in line with their mandate of representing the people. Let’s take emotions out of the equation.
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 2 күн бұрын
Eya tavomeleza iwe umati?
@DanielNangoma
@DanielNangoma 2 күн бұрын
Smartmatic isagwire ntchito komanso Anabel mtalimanja ndi wamkulu wa RNB atule pansi udindo sitikuwafuna ayi, ife tikufuna chisankho Cha mtendele
@Bbbbwesgtcjoug
@Bbbbwesgtcjoug 2 күн бұрын
Ayi ine sindikulola koma a DPP ayendetse zisankhozi popeza anazolowera kuba ndiye ali ndi experience yobera zisankho kuphatikizapo iweyo wabweretsa nkhaniyi uyendetse nawo zisankho zimenezo zikomo anthu olungama inu
@MarySinjirani
@MarySinjirani 2 күн бұрын
Anabel achoke smartimatic ichoke chisankho chiyende mwanthawi zonse
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba Күн бұрын
Malamulo akulu adziko lino avomeleza iwe ndi ndani??????
@MarySinjirani
@MarySinjirani 2 күн бұрын
Ndipo kalemberayu akuyenera kuti akhansulidwe anabel, msambo komanso smartimatic zichoke chifukwa zinthu zimenezi zikuoneka kuti zikhala ma virus chisankho chathu
@ChristopherManase-s1f
@ChristopherManase-s1f 2 күн бұрын
Ukutaya nthawi yako iweyo. MEC chair sakuchoka.
@ManjeUphl
@ManjeUphl 14 сағат бұрын
Achoke bwanj jen anachoka nayenso ngati sitikumufuna nayenso achoke
@GeoffreyMarko-v3s
@GeoffreyMarko-v3s 2 күн бұрын
Sitikuvomereza
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 2 күн бұрын
Ai ndithu asazayendetse Chisankho Chifukwa Choti aonetsa kulephela kwake pa nyengo yolembetsa za Uzika amawaikila ku mbuyo ANRB pame anthu tinali ndimadandaulo ambiri pamene timalembetsa
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 2 күн бұрын
@@LilianKachala-yz2xf let me help you. First of all kulembetsa unzika is NRB’s jurisdiction, kulembetsa kaundula wa vote 🗳️ is MEC’s responsibility. As of today we have over 7 million registered voters more than in the last election cycle. You’re an intelligent man I’m assuming, do the math
@TakalaniGlenda
@TakalaniGlenda Күн бұрын
Dzina lokhalo Abel ( anabel) ntalimanja eish eish nlovuta kwathu akati munthuyu ndiwantali manja meaning ndiwakuba ndiye zisankhozi azabela😂😂
@StevenMasamba-y1p
@StevenMasamba-y1p 2 күн бұрын
Zikoli zadzidzi pa nkhani ya wamtalimanja, Kodi simudziwa kt munthu amene amanenedwa kt ntali manja ndi okuba?
@EnochSamuel-o5e
@EnochSamuel-o5e 2 күн бұрын
NO....!!! WE DID NIT ACCEPT HER TO BE OUR MEC CHAIR BECAUSE SHE'S INCOMPETENT. 😖😔😟😞😞
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 2 күн бұрын
@@EnochSamuel-o5e Akulu take time to follow proceedings of your country…as the Arabs say “Ikra” take time to read what the law says! Osamangoyankhula mchimbulimbuli
@felixjoseph8161
@felixjoseph8161 2 күн бұрын
Mwana wa MCP John Tembo sangayendetse bwino chisankho Mai ameneyu kunyini Kwa Mai ake John Tembo mbole yake chakweraso mbole yake akufuna akufuna kusokoneza dziko amalawi tulo kuseka too much mbole Za Manu nose a MCP
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick Күн бұрын
zosatheka,kalembela,kuyambilaso
@YusufJulius-q2o
@YusufJulius-q2o 2 күн бұрын
Mawu ogwila mtima kalembela akuyenela kuyambilaso ndipo anabelo achoke msambo achoke
@AdamKay-q1l
@AdamKay-q1l 2 күн бұрын
No no no achoke
@SaimonDavide
@SaimonDavide 2 күн бұрын
Zoonadi akulu,anthu aiwala za Anabel koma achoke basi chifukwa adzakondera mbwiyacheyo chakwera ,achoke,achoke,anabel
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 14 сағат бұрын
Ayi
@FrankChanza-z7z
@FrankChanza-z7z 2 күн бұрын
azipita ameneyo ife sitimufuna ayi
@Kasimu-d3i
@Kasimu-d3i 2 күн бұрын
Ai sitikuvuna achoke
@GiftNorton
@GiftNorton 2 күн бұрын
Koma akuluwa akufotokoza chilungamo chokhachokha
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick Күн бұрын
anabe,sakuchoka
@EstherMaonga
@EstherMaonga 2 күн бұрын
Ndipo zoona
@AdyasiMaulana
@AdyasiMaulana 2 күн бұрын
Am watching from south Africa we are not agree that my final answer
@PatrickMalenga-h5m
@PatrickMalenga-h5m 2 күн бұрын
Inu ndiye mukugwetsa athu kut asakadule mavot mziko lamalawi sitingapange khondo ndirantendere
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick Күн бұрын
tose,tinavomela,anabe,kuyendetsa,zisankho
@EllahChikwatu
@EllahChikwatu 2 күн бұрын
Ai sitinavomereze
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 2 күн бұрын
Zipani zina zatopa ndikugwilisidwa tchito ndi DPP ngati UDF basi tasiya tikukonza chipani chathu the agenda for DPP is to get back into government through other political partys ngati UDF ikakhala chete masapota a DPP akumati ya join MCP pepani a DPP zimeyeleni khondo nokha ife a UDF tilindi 2 % tisiyeni 😂😂😂😂
@ChidaPhiri
@ChidaPhiri 2 күн бұрын
Ai achotsedwe mzimai oipa uyu
Azizi-  Talowa Tonse (official music video)
1:47
Azizi Mit Crouzy Mw
Рет қаралды 8 М.
A MCP Kugulitsa Nyanja Ndi Uchitsilu Opitilila Muyezo   Jonathan Phiri
10:38
99.9% IMPOSSIBLE
00:24
STORROR
Рет қаралды 31 МЛН
Каха и дочка
00:28
К-Media
Рет қаралды 3,4 МЛН
Cheerleader Transformation That Left Everyone Speechless! #shorts
00:27
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 16 МЛН
A Malawi Chipembedzo Ndi Ndale Ndi Zinthu Zosiyana - Dan Zakoleka
6:51
A Malawi Musadandaule Nyanja Ilipo - Country Man & Uncle
20:39
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 8 М.
99.9% IMPOSSIBLE
00:24
STORROR
Рет қаралды 31 МЛН