Social media imajambula zimene kulibe? Nanunso umunthu udakuthawilani@@DesireMoyo-y8x
@ChristopherManase-s1f3 күн бұрын
Laona chiyani?
@ThomasJohn-d9rКүн бұрын
Umboni otani si zamuyayatu izi
@JoiceChisambi3 күн бұрын
Mukufuna umboni wachi zithu zawoneks ndimaso
@EvansEgra4 күн бұрын
Chaponda anaba chimanga uyu, chisiru chamuthu, wosamasewera ndi boma ai
@SebastianSauwa3 күн бұрын
Akamati phuma silabwino akutanthauza chani?? Izi sidzamuntthu mmodzi ndi MEC and NRB.Ayiniake ndi aMalawi what ever is happening aMalawi eniake adzidziwa china chilichotse kuti asamutsa office kupita uku.Kuti anthu asamadabwe.Why hidding things? Remember black box ijainasowa bwanji.what evidence are u waiting for????
@RuthChilobwe4 күн бұрын
A GEORGE CHAPONDA SADZIWA KUPANGA MFUNDO ZOTSUMIKIZA .KOMA ANAKAKHALA DALITSO KABAMBE OLO SAMEER SULEMAN OR NORMAN CHISALE CONVINCINGLY
@BrightZionga3 күн бұрын
Kazombo sikutitu iweyo wchita kutsika kumwambatu umakhala ndiukali ndi opposition bwanji osakhala pa neutral bwanji
Umbon Ndiokut malo ameneaja ndii osungila chimanga not ma ID n amakatani kkkk manyi amenewo ife ayiii
@nayyeguga7359Күн бұрын
😅⁰p
@NikolasNanawe3 күн бұрын
anthu osutsa ali ndi vuto boza kwambir fundo alibe km maboza bas guys perekan maomboni muva ukweche achaponda 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@SaidiMbawa-st6bj4 күн бұрын
Opposition yongona iyi tsete
@ShamilahSaizi3 күн бұрын
Koma kukula konseko mungamalembe zimenezi???? Zipatseni ulemu
@SaidiMbawa-st6bj3 күн бұрын
@ShamilahSaizi vuto lako ndi chani phone ndi yako
@ShamimuBisaniКүн бұрын
Sister pliz usamalimbane ndi ana asatana pliz ss love u so much dzitalikise kutali ndi asatana nthawi yatha enawa akuona ngt pamanda pawo padzalembedwa MCP ndye kuti akalowa kwa Mulungu@@ShamilahSaizi
@paulmartin816511 сағат бұрын
Boma ndilomweli zosithasitha ma pulezidet nd zomwe zikutionongela dziko
@AlicksonMakata10 сағат бұрын
Mulungu ali mbali ya boma dpp ndi chipani chosokoneza.
@edsonalfredmoya2605Сағат бұрын
Chaponda wa chimanga uja kuno😂😂
@MorrisMapiri-o4k3 күн бұрын
Anthuwo awapeza ndi ma printing machines, so what kind of evidence does ruling party want?, this is nothing else but intimidation to the rights and democracy.
@bs-malawi3 күн бұрын
No, there were no printing machines. Just computers and scanners. Ndi pamene umboni wavutila, Chifukwa achina Chaponda akuti NRB imachita print, koma printer munalibe, nde nkhani yavuta pamenepo Mukanakhala printer zinali za straight forward
@MolesBrown4 күн бұрын
Ukamafuna kulanda nkazi mwaphuma zimakupatsa mavuto adpp phuma kaya ndikukalamba kaya
@GitfIobodo3 күн бұрын
Komatu munu mmalawi mkhala nkhondo tiphana magazi ku magazi
@AusteenSumael4 күн бұрын
Which umbon,?
@DumisanPhiri3 күн бұрын
😂😂😂😂 chaponda mwapanga mwa panga bwanji apa nde akugwesanisotu
@jameskachulu81413 күн бұрын
Umboni ndi womwe Uja zinajambulidya zija
@KelvinBanda-s1s4 күн бұрын
President ndi chakwera enanu mukufuna mukabe musiyen mzanu apitilize mission bas
@JoyLuwanika3 күн бұрын
Mulungu akudalitseni anthu mukuwadzuzatu
@chifundochalowa53233 күн бұрын
Before evidence you supposed to find out what happened there,Mr sikala. nanga atakupatsani evidence yabodza? Mudzadziwa bwanji kuti ndiyoona kapena Ayi. Coz kumaloko simunapiteko kukaona kuti chachitika ndichani? Chimwendo akuti Phuma iyeyo anapitako ?
@ibrahimmumba3 күн бұрын
Wakuba ndi wakuba bansi
@tonnexScott4 күн бұрын
A Chimwendo mumandibowa kwambiri
@EvansEgra4 күн бұрын
Zitsiru mbuli, agalu a opposition, maka Dpp
@RosinaPatel4 күн бұрын
Mafumu..chimwendo akutenga ma id awanthu ndikumagawa ndalama
Maize get yamutsalira🤣🤣🤣🤣Ukakhara wakuba umangoona ngati aliyese ndiwakuba kkk Dpp ikufuna ikamalizitse kuba osati kudzakoza Malawi
@BrightZionga3 күн бұрын
Umboni ulipo zija taona zija nde umbonio
@RosinaPatel4 күн бұрын
Umboni ndi woti bwanji a NRB sanauze otsutsa kuti akupanga ma id ku kanengo?
@EDGARMPIKAMEZO4 күн бұрын
Speaker wa MCP uyu!!! Apart from the evidence there is also need of an explanation of what is happening there. Dont rash to evidence yet everyone saw those gadgets for both photographing, printing yet claimed to be for solting 😡😡
What evidence? They say they were using the hall for sorting IDs kodi mesa sorting amapanga ndi manja? Nanga ma camera amachitako chani??? The PRESENCE of cameras is a real evidence of theft period.. Cameras are supposed to be found in centers where people's faces are captured.. Why do you want to compromise straight forward things? Malawians are not fools. We are taking you out mcp
@bs-malawi4 күн бұрын
Kkkkkk zilikotu chaka chino
@GiftMuyungu4 күн бұрын
Achimwendo ndi nonse amcp mulibe manyazi kwanu mkupha kuba komaso kuwononga ntchito zasatana zagona mwainu koma kumwambaku kuli mulungu muzaziwona
Komaditu a MCP chikuwakhudzq ndichani. Chimwendo why
@FunnyKalimwayi3 күн бұрын
ayalukabe k
@GibsonBankha2 күн бұрын
Kkkk koma makadeti ya bpp kkkk
@CassimMbalaka4 күн бұрын
Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pokuyikani nose wokhudxidwa pa ifa ya chilima
@EvansEgra4 күн бұрын
Sizikugwiriza ai
@BrightZionga3 күн бұрын
Khaaaaaà
@tasmania5274 күн бұрын
Akuti DPP ndi system koma system yake yofoiraso, yikugwedezeka. Ma leaders a system akupangaso phuma, akukhala ndi mantha oluza zisankho, nde udolo wake uli pati?kkkkk. Gone are the days when DPP used to steal elections. This is the new era of sanity, VIVA MALAWI!
@SalatiKiddie4 күн бұрын
agalu amcp awa ndipo tikoma ndipo popano
@johnjoachim38204 күн бұрын
I think wina akutamba kumeneko zoona mukanikiranji ma vidio ali paliponse adzulo and u Mr sipikala usamankhale ndi mbali mache.....ako pati
@AmosiChauluka4 күн бұрын
Koma chimwendo iweyo uzazuzitsa banjalako
@KennedyKManda4 күн бұрын
Chimwendo Mboli yamako
@EvansEgra4 күн бұрын
Ukhalira zimenezo
@BrightZionga3 күн бұрын
@EvansEgra kodi iwe kape why you are busy attacking others iweyo kwanuko zilibwino mavuto akulilitsa amalawi iweyo zako zilibwino shame on you
@EvansEgra3 күн бұрын
@BrightZionga I fight my slf, sindimayang'ana zisiru za ndale ine ai
@ShamilahSaizi3 күн бұрын
Chikangawa son, ngt mukudya nawo za zipereganyo muzingokhala chete osati muziziwonetsa ngt inuo a nzeru apa
China chimangolimban ndi opposition ukhalira yomweyo garu iwee umbon wake akufuna utiwo zaziii kukakamira znthu zoti zakukanikan hehehehehehe mukalamul ndikumanda kkmwe