KUCHITA KUUNIKIRA NDI MA TORCH!

  Рет қаралды 3,685

Malawi Lero🇲🇼

Malawi Lero🇲🇼

Күн бұрын

Пікірлер: 47
@MemoryZiyaya
@MemoryZiyaya 2 сағат бұрын
Mulichokoka mwaPeter eeish... Ambuye amukomere mtima🧢💙💙
@Frederick-s4h
@Frederick-s4h 3 сағат бұрын
Much more fire postar munthalika ameneyu nde busa osati razalo mesiya wakumalawi apm ndlkatundu pachitukuko amakwana anakoza mesiya wakumalawi dpp oooza my vote
@BistonMacheso
@BistonMacheso 58 минут бұрын
APM yanyamuka muto kuti buuuuuuù boma ilooooooooooo
@AdamuKasimu-x5o
@AdamuKasimu-x5o Сағат бұрын
Chakwera bp ilipat😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 adad oyeeeeee
@raytavares2256
@raytavares2256 3 сағат бұрын
Mudzi wopanda nkharamba sumakhala wokhazikika chifukwa ana ndi mbumba pakhomo pamakhala posowa nzeru kuchokera kwa nankungwi.
@ThokoMsonkho-hy4uc
@ThokoMsonkho-hy4uc 3 сағат бұрын
Ine PETER MUTHARIKA loko atakwana zaka 100 nditha kumuvotera ndiwanzeru Komanso amaganizira anthu akumudzi. Munthu oti ankaphunzitsa ku American siwamasera CHAKWERA ndi ife sitingafikireko. Chakwera ndi munthu osowa zochita nchifukwa chake anali m'busa APM my vote
@MilliumZacharia
@MilliumZacharia 2 сағат бұрын
Koma ndiye kunachema 😂😂❤
@BeatrinceChanza
@BeatrinceChanza 16 минут бұрын
Munthu wabwino uyu okonda dziko lake president okonda anthu Ake ❤❤❤❤
@BunnahAdamh-n7s
@BunnahAdamh-n7s Сағат бұрын
Nkhalidwe limakusata iwe mwini❤
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf Сағат бұрын
The chosen one ✝️🕊️
@LovemoreSambuke
@LovemoreSambuke 2 сағат бұрын
Nde wina abele zizakubvutani😂
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi Сағат бұрын
President wozichepesa
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 22 минут бұрын
Adad mcp tsikugona nanu tulo God bless you
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Сағат бұрын
Chonena ndilibe ndithu mmm ayi 😅
@BrightonChidzalo
@BrightonChidzalo Сағат бұрын
Zonsezi adad mwanva za athu koma matching oberamavuti Accokeek asazagwile ntchito chifukwe chakwera sakugona tulotu adad
@Frederick-s4h
@Frederick-s4h 3 сағат бұрын
Kkkkkk palibeso ndiyemweyo bas much more fire muthallka
@BakhePaliso-h8h
@BakhePaliso-h8h 2 сағат бұрын
Boma iroooo❤
@Frederick-s4h
@Frederick-s4h 3 сағат бұрын
Mmmmmmmm km yaa muthallka ndlkatundu oloatapanda kumayenda dpp oooza my vote
@raytavares2256
@raytavares2256 3 сағат бұрын
Greetings from North London UK, thank you for your educational vedeos.
@Malawitoday265
@Malawitoday265 3 сағат бұрын
You are very welcome
@Frederick-s4h
@Frederick-s4h 3 сағат бұрын
Km zikuenda muthallka samasewela pachitukuko amakwana anakoza mesiya wakumalawi apm
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 2 сағат бұрын
Uyuyu ndiosankhidwa ndithu
@InnoMalikebu
@InnoMalikebu 3 сағат бұрын
❤❤❤❤
@AgnesNjikho
@AgnesNjikho 2 сағат бұрын
Hhhhhhhhh kuyamikila zinthu ngati mwawola kale sizavomerezatu Inu kurephera kwanu
@Jafari-s3c
@Jafari-s3c 2 сағат бұрын
Whether you like or not, Peter munthalika is going to rule again this country,people like you will be the witneses.
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w 2 сағат бұрын
A name mulibo mulibo muzawina mwa nyooooooo
@RoseThindwa
@RoseThindwa 2 сағат бұрын
Zonyadirisa mstogoleri kukondedwa ndi Malawi's tikukumbukira time ya dpp anthu amasangalala woyee💙💙
@HyTy-r3m
@HyTy-r3m 2 сағат бұрын
Ambuye amusogolere kumanso ambuye phupani anaanu pamoto
@dreetosh8502
@dreetosh8502 Сағат бұрын
DPP woyeeeee🎉❤😂😅
@oswardzenizeni1458
@oswardzenizeni1458 Минут бұрын
Mpaseni mpata big man muthalika boma limene tikudikira adadi mumutumize bushili akayakhe murandu. Kuno ku joni
@LennieNyirenda-w6p
@LennieNyirenda-w6p 2 сағат бұрын
Boma ndilomweli tingosintha otenga chiongolero 🎉🎉🎉🎉boma iloooo
@BakhePaliso-h8h
@BakhePaliso-h8h 2 сағат бұрын
DPP mtesa nuala woyeeee
@oswardzenizeni1458
@oswardzenizeni1458 11 минут бұрын
Uyu ndiwosankhidwa ndi Mulungu
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 Сағат бұрын
Koma kubwelela kudwambwe ndikowawa kwambili mmmm
@omarajibu860
@omarajibu860 2 сағат бұрын
Bwanji manyazi? Pangani resign mwina pang'ono muzalemekezedwa.
@oswardzenizeni1458
@oswardzenizeni1458 4 минут бұрын
Kapitani kwanu kwa malembo
@oswardzenizeni1458
@oswardzenizeni1458 5 минут бұрын
Kachimutu kumene uliko bwanji wayamba kutsekura mmimba ndi chikangawa wako
@oswardzenizeni1458
@oswardzenizeni1458 8 минут бұрын
Kupangisa mspkhano azanu ndi usiku koma osagendedwa mulibe manyazi achikangawa
@kekeaufi9834
@kekeaufi9834 2 сағат бұрын
💙💙💙💙💙
@oswardzenizeni1458
@oswardzenizeni1458 10 минут бұрын
Ayambedi kumanga katundu adadi
@oswardzenizeni1458
@oswardzenizeni1458 9 минут бұрын
Kukubwera adadi
@StevenDastan-f5y
@StevenDastan-f5y 14 минут бұрын
Our hope
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 14 минут бұрын
Mcp mwaona aini dziko? Kuenda paliponse, nthawi iliyonse,kwina kulikonse imeneo nde dpp ameneo nde APM 2025 boma!
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 Сағат бұрын
Mulungu akaloza chala chimakhala chaloza basi amalawi alila kwambili ndipo pemphelo lathu lanveka tikufuna tiziwe yemwe anagwesa ndege uja
@DamianoYohane
@DamianoYohane Сағат бұрын
A Chisale alipati,,,!
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 2 сағат бұрын
Chakwela akuyenela kupakiladi
@Aisha-db6ds
@Aisha-db6ds 2 сағат бұрын
Chikangawa akuti uyambetu kumanga zinthu zako ku state house ko
Syrian army retreats as rebels storm into Aleppo | DW News
17:17
Senzo Meyiwa Murder Trial | 2 December 2024
SABC News
Рет қаралды 12 М.
The IMPOSSIBLE Puzzle..
00:55
Stokes Twins
Рет қаралды 197 МЛН
كم بصير عمركم عام ٢٠٢٥😍 #shorts #hasanandnour
00:27
hasan and nour shorts
Рет қаралды 11 МЛН
How To Choose Mac N Cheese Date Night.. 🧀
00:58
Jojo Sim
Рет қаралды 110 МЛН
Senzo Meyiwa murder trial | 2 December 2024
eNCA
Рет қаралды 894
Why will soon everybody get Parkinson's disease?
15:26
Universiteit van Nederland
Рет қаралды 1,4 МЛН
Nkhani Mmawa | 2 December 2024
22:57
Malawi News Update
Рет қаралды 505
The IMPOSSIBLE Puzzle..
00:55
Stokes Twins
Рет қаралды 197 МЛН