Mkwezalamba you have spoken very well indeed and that's true don't bite about the bush
@Fkaymw1Kadango-by5mu2 күн бұрын
Iwe Usi ndiwe osokoneza Kodi mmesa iwe ndiwe wa mcp, Uli ndi Dyera munthu oipa iwe
@OmegaChingamuka2 күн бұрын
Yusadi uyu akusunga ku mcp chifukwa akufuna kuti akoke anthu ku UTM kupita nawo ku mcp nde kwatsala miyexi ingati tiwona ngati atansungenso
@edsonndalama23342 күн бұрын
This was is insane. The UTM leaders dont need Usi's endorsement, they needed the endorsement of the delegates. This coward run away from the convention to avoid shameless defeat. He is an outcast, irrelevant and a confusionist
@LindaNkwazi2 күн бұрын
Iwe ngati ndani kodi??
@WakisaGodfrey-y8h2 күн бұрын
Ine ndine waku karonga kma zoti chikangawa azapeza voti ku karonga ndi kukayika ndi munthu modzi yemwe waononga dziko la Malawi
@KelvinChiwra2 күн бұрын
Kuli nkhondo ku islael please ma islael eni ake akuthawa please umphawi sumatha mukafera za eni
Michael Usi ndikape kwambiri, he is being a states man. If he doesn't want to be associated with the party, he would have just paved way for others. This mayhem will just bring division
@SalimmichaelNjobvuyalema2 күн бұрын
Sibwino
@natashamathala87152 күн бұрын
Wadyela iwe panga chimodzi asiye a utm panga za mcp zakozo dyela mkufupikako mutuowumawo
@viennasamuel29762 күн бұрын
Amanganya tasankhani chipani chimodzi mukutibalalitsa ife, nokha mukumati boma ndilomweli boma lake ndi liti?
@CharlesWitness-vp6dw2 күн бұрын
Kodi Anthu opita Ku Israel apita bwanji, ? Ku Israel kuli nkhondo mabomba aku phulika pena paliponse komanso eniake a Ku Israel akuthawako kupita kumaiko ena ,Anyamata muyenda bwanji? Mukafikira kuti?Nanga mukakhala pati? Chonde kuli NKHONDO Ku Israel pepani
@user-ux3ed3ni1p2 күн бұрын
Where are the factories and industries? Zitukuko is based on National planning and funding by the treasury using Misonka zathu. Not funding MCP Chakwera 70 trips.
@Muchipululu2 күн бұрын
Manganya nde wasinthiratutu....uyu analidi wa kongiresi mkale komwe, ndatsimikiza
@GiftLORENTI2 күн бұрын
Koma ndiwamisara using basi
@PatukanVincent2 күн бұрын
Okuba uyu
@user-ux3ed3ni1p2 күн бұрын
Usi let those people go and be productive instead of that nonsense. I thought kuli njala?
@AdamJames-x7x2 күн бұрын
usi ma battery Ako , upange zako ndi chikangawa party yakoyo, zolimbana ndi utm usiiletu pamtumbo pako iweeee
@MavutoUliah2 күн бұрын
Ndipo manganya akubowa he always over exited
@AdyasiMaulana2 күн бұрын
Kodi yeyu akuyikakamila utm bwanji chonsecho Ali kale ku mcp koma nama drama
@KellyNyangulu2 күн бұрын
Basi kutuluka basi
@dominicmphepo-jk8lk2 күн бұрын
Tangopitani ku MCP ko bwana usi mwatikwana ndi ma drama anawaaa aaa
@ENOKMAKONDI2 күн бұрын
Michael usi akupanga ngati sanapite ku xul pena bwanji. This is not TIKUFERANJI when you are not happy with UTM why using their brand. You could have also stopped people wearing their colours and using their brand. You are fueling the downfall of the party.