Pa prophet amenewa ndi a pansi pa nyanja za moyo wa munthu aliyense amaziwa ndi Mulungu long life 🧬🧬 Peter Mutharika God continue protecting you and good health
@WarriorKB-l3i2 күн бұрын
Bale mukunena zoona ndichifukwa ndimanena kuti ma prophert ndi mbuzi za anthu, a satanic maprophert onse kuphatikizapo mcp afune, asafune 💙💙💙💙💙💙 chaka chino boma!
@JohnmjigoMalinda2 күн бұрын
Muwu abwno zoonad ndakunyadilani kwambiri
@abgi.doctor.august2 күн бұрын
Olo wina anyoze Peter Muthalika koma amewu ndiyemwe akutenga boma lino mu September 16 DPP woyeeeeeeeeee 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤❤
@EnerstManess2 күн бұрын
Chisale he don't have time to play my brother
@AyamiMustafa22 сағат бұрын
Dpp woyeeee my boma batsi
@TrizaBaile2 күн бұрын
Kungochoka pa Chitakale chimvula ichoooo...adad ndi mdalitso inuuuu🥳🥳🥳
@NEDGIFT-p5t2 күн бұрын
Akamuna ❤❤❤
@alexjeremanuel25412 күн бұрын
I like the way Chisale and his teammates behave these guys look that they're professionals
@MussaZimba-p3e2 күн бұрын
Koma nomani chitsaleyo azimuwonjezela moyo ndikatundu kwambili ❤❤
@PrinceBlessings-bv5bs2 күн бұрын
Olo wina anditseka maso kut msaone koma blue kuoneka patali ndichongi❤❤
@JackMulima-p4wКүн бұрын
ADAD WOYEEE❤❤❤❤ MY VOTE
@trymooTv2 күн бұрын
Wachipani china akuchita manyazi kupanga LIKE comment Yanga 🧥🩴🧢🩲👗🥿
@lacksonsiyadi9436 сағат бұрын
Wa mcp wakhalira nsomali
@BlessingsFredd2 күн бұрын
Team yonyoza muno ayi ngati sizikukukondani muzikachemelela Satan wa mcp ...... Ife athu ❤❤❤❤ adadi
Munthu wakulu. My vote enanu muzichedwa kunyoza chocho
@HendeRabson2 күн бұрын
Machine awa🙏
@yunusuPhili2 күн бұрын
❤❤❤ vote
@PatriciaBanda-e3v2 күн бұрын
I see Bingu in You😢😢Dad titengeni kubwera Mozambique
@RabbiNyirenda-g8g2 күн бұрын
No way
@CharlesmilanziliheraКүн бұрын
Wa bakili TV uja ndamuona lero😎
@MavutoFodya-p1u2 күн бұрын
Chivomelezi tsopano pangoline katundu weniweni
@WarriorKB-l3i2 күн бұрын
Mpulumutsi wa a malawi okonda dziko lino ndichifukwa taganiza kuti chaka chino mavoti athu onse tiwapatse adad program ili choncho palibenso kusintha 💙💙💙💙💙💙💙💙💙 mo fire palibe kutekesekanso ai .
@chimwemwechimwanza2 күн бұрын
zoonadi
@RabbiNyirenda-g8g2 күн бұрын
Chakwera wins
@WarriorKB-l3i2 күн бұрын
@RabbiNyirenda-g8g ukudzichinda ndi chala aise mcp ngakhale ana a ku khonde sakuifuna, dziko lopanda mafuta,feteleza,chimanga, forex, kobili kobili mungoba , dzinthu dzakwera ndi chakwera the chikangawa, munapha ndege kuchikangawa black box ili kuti? Lero mudzikati boma ndilomweli! La manu? Inu dzisilu kwambiri chaka chino boma likubwelera mufune, musafune mukuona ngati smart matic igwila ntchito panyoo panu mwauponda.
@ThoccooDuwa2 күн бұрын
Apm my vote 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙
@YamikaniYamikani2 күн бұрын
adad oyeeee🤝🤝💃💃💃💃💃🤝🙏🙏🙏
@GracieRejoice2 күн бұрын
Dpp woyeee❤❤❤
@honmitrus2 күн бұрын
Our pangolin
@VeronicaMatiyaBanda2 күн бұрын
Adad my vote
@DONNEXKhama-bk1gy2 күн бұрын
Boma kma ili 😂😂😂 my vote
@YasinterKapinga2 күн бұрын
Apa tizingochotsela my vote 💙💙💙
@HappyMajo-l3q2 күн бұрын
Apm my vote
@MemoryChikakudaКүн бұрын
❤❤❤❤❤ My vote APM
@FrancesPeter-xw3vb2 күн бұрын
Ambuye amukudzire malire Peter monga anakudzira malire a Yabezi Ambuye amukumbukire monga Ezekiya
@WysonKalimbuka2 күн бұрын
Adad woyeee❤❤❤
@MosesChazima2 күн бұрын
❤❤❤❤ My voti apm
@UmaliDaili2 күн бұрын
Adadi ❤🎉
@InnocentHassan-m3r2 күн бұрын
Big up big up Mr APM
@JACKSONHULUWA-j2n2 күн бұрын
My heart is blue
@HappyAbyssinianCat-xt2bm2 күн бұрын
Apm my vote💙💙💙💙💙
@EdwardTembo-n4w2 күн бұрын
Boma ilo👍
@FreedahKabaghe2 күн бұрын
APM my vote
@Staphelsavimbindhlovu2 күн бұрын
My vote❤❤❤
@MerryWayson2 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤woyeeeeeé
@TrizaBaile2 күн бұрын
My vote🔥🔥🔥
@EdsonNansambo2 күн бұрын
Mulungu akutetedzeni Mr muthalika
@RoseMsonkhoMaleleКүн бұрын
Moto kt buu
@MoniLodge2 күн бұрын
My vote🎉
@MussaAli-h4i2 күн бұрын
Fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 🏡 dpp woo yeeeeeee
@Pangolinimw2 күн бұрын
Dpp❤❤
@ChomboNgosi2 күн бұрын
My vote APM from lilongwe
@MarryMartin-z6u2 күн бұрын
❤❤❤❤
@FaroukSaliemКүн бұрын
Me too from Lilongwe, but APM is my vote 2025
@HamuzahRobenКүн бұрын
Achewa odzikila ❤❤❤❤
@ChaibuBabson2 күн бұрын
My vote apm💙💙💙💙💙💙💙
@GiftMuyunguКүн бұрын
Ukumva bwanji wa mcp simukomoka munya zikuvotelani zikwanje Miguel zambiri😅😅😅😅
@hackwellkagolo6614Күн бұрын
wakwiya ndi chiifiti. neighbour wakwiya chifukwa just give like basi sanje simanga dziko
@LawrentBanda-i8u2 күн бұрын
Makwana sir Dpp woyeee
@highcallingglobalministries2 күн бұрын
YOU CAN JUST FEEL THE LOVE N HOPE IN HIM
@BoscoChimveyi2 күн бұрын
Katundu omanga ndimawaya kukalamba sichifukwa koma nzeru
@QueenWaheraКүн бұрын
Komano Peter chimulilenji sakumutenga bwnj chimulilenji🤣🤣🤣🤣🤣
@NdaonaMsowoya2 күн бұрын
Oooooooy❤❤❤
@DOMZYMW-z4d2 күн бұрын
Adada more fire😂😂😂😂😂😂
@KwathaLester2 күн бұрын
My vote 💙💙💙💙
@Hambalisphiri2 күн бұрын
APM MY VOTE
@chifundocharles2348Күн бұрын
Boma silaaathumbidwa ayi😢😂😂😂😂😂
@HamidImed-p1g2 күн бұрын
❤🎉🎉🎉
@MarcusLucius-j7d2 күн бұрын
Chitakale pa deni😅
@TiyanjaneMkwate-we8gu2 күн бұрын
Chakwera watizunza mokwanira. Bola tibwerere ku iguputo kuja chifukwa timadyako.
@ReginaKasemaКүн бұрын
My Dad where are you take us out of this😅😅😅 regime
Mmmmmmmm muli mphumatu man kkkkkkk Inu chikangawa inakupeteni kale basi
@EsnartGirivin2 күн бұрын
Chakwela amva madzi 3025 bola othowedwayutu Kusiyana ndi chikangawa😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Apm my vote ❤
@hafeezenterprise2 күн бұрын
Ubwino wophunzira ndi umenewo adad skul yanu ndi phindu la ife a Malawi pamene enawo skulu yao ndi yoononga miyoyo ya wanthu, mpaka miyoyo naini adad woyeeeeee
@HamitonFrank2 күн бұрын
Kkkkkkk wakwiya zake APM BOMA 16,SEP,2025
@frankiechasokoneza58022 күн бұрын
@HamitonFrank kkkkkkkkkk ndipo nde zake zakeditu kkkkkkkk