COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM - CHAKWERA WAKAKAMIZIDWA KUTULUKIRA POYERA NDI ABOMA LA MCP

  Рет қаралды 12,457

Mpungwe-Pungwe mw

Mpungwe-Pungwe mw

Күн бұрын

Пікірлер: 121
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 4 сағат бұрын
Mr Comrade ntanyiwa more fire comrade Osaopa osatopa osafooka Allah alipo mpaka tituluke mukaporo tilinawo pano
@AuphieBannet
@AuphieBannet 2 сағат бұрын
Awuzeeeniii Agwelemo okhaa😂 More 🔥 fire Mr NKHANGA ZAONA
@JOHNKANYALA
@JOHNKANYALA 3 сағат бұрын
Akulu ine ndimakhulupilila koma ndinu onama aaaaa ndakutulukani
@horacechera6978
@horacechera6978 2 сағат бұрын
Ndi mbuli izi amwene zimafuna atani munthuyo pamene sadaoneke mumati wamwalira pano watulukira ku gulu akuchulutsanso zokamba
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 2 сағат бұрын
​@@horacechera6978Ntanyiwa sananene zoti chakwera wamwalira
@jameschiwanga
@jameschiwanga Сағат бұрын
Ife timaziwa kale Kut uyu ndiozungulila Mutu uyu anthu openga awa maboza tooo
@rhodamaunge-uq5dz
@rhodamaunge-uq5dz Сағат бұрын
Ntanyiwa sananepo kuti chakwera wamwalira ayii
@AllanNdovie-e4j
@AllanNdovie-e4j 58 минут бұрын
Tasiya ku khulupilila nd redio Yakoyo kaya ndiwe wa UTM kaya dpp peza zina zochita
@WelingsLongwe
@WelingsLongwe 2 сағат бұрын
Inu munthu wodwara amathamanga kapena kuyenda ndawala kumangofuna kupasa anthu zoyakhula ndimaona ngati zimene mumanena zimakhara zoona koma apa ndiye eshii nkuku iwe bodza usiye mlungu akukhululukile umuziwe yesu
@MphatsoGeorge
@MphatsoGeorge 2 сағат бұрын
😅😅😊😊😊😊😊fn
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 4 сағат бұрын
Chingofa chimenecho basi waononga dziko ra Malawi ameneyo crocodile Tonse tizafa palibe amene azakhala pa dziko rapansi
@Martha-m6e
@Martha-m6e 3 сағат бұрын
Zowonadi zake oro pamene akuthamangapo amai ali pafupi popo kuti atatiagwe awagwile❤❤❤❤.
@wisdom20mkango49
@wisdom20mkango49 2 сағат бұрын
Ulibe manyazi zoona mmayi iwe😂😂😂😂
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 2 сағат бұрын
​@@wisdom20mkango49ndipo or pang'ono alibiletu 😅😅😅
@jameschiwanga
@jameschiwanga Сағат бұрын
Chakwera NDI munthu wanthazi uja
@RuthZimema
@RuthZimema Сағат бұрын
Iwe president amamugwira ndi mkazi wake akafuna kugwa? Uwafunse adad kuti anakugwirani ndani mutangwa podzala mitengo? 8:13 8:13 8:13
@SmartMajola
@SmartMajola 3 сағат бұрын
Iwe chisilu Cha munthu ,panopa ndy ulibe manyadzi wasowatu choyankhula,ndipo iwe si Yahweh,chakwela more🔥🔥🔥
@DytonPhiri-bd1yl
@DytonPhiri-bd1yl 2 сағат бұрын
Comrade ndimakudalila koma na apa watiwonjeza iwetu dzulo umati chkwela Ali ndi stroke mpaka yafika ku mtima Ali pakati pamoyo ndi imfa lero chakwera uyo akupanga ma push ups ku bt Iweyo ndakutuluka ndatulukaso dpp ndailowa MCP pano
@BrightLuciano
@BrightLuciano Сағат бұрын
Ndinu a mcp ndi kale musatikwanepo apa
@Onex-z6s
@Onex-z6s 5 минут бұрын
Comrade Ntanyiwa mumathana chifukwa choti simunanenepo kuti chakwela wamwalila potengela kuti anachita dala kuti anthu asamakukhulupilileni ndiye munachita bwino osanenapo kalikonse za nkhani yomwe imafalisidwa yoti chakwela wamwalila sono ife tili nganganga pambuyo panu.
@jomochirwa
@jomochirwa 3 сағат бұрын
Inu ndi amene mudzaluzitse dpp ,tima radio tanuti mukuchulutsa ma bodza nkhani zopeka ndipo anthu panopa akutulukilani.inu dziwani kuti nthawi imene chilima ankamwalila anthu mmalawi muno adakayika ngati mcp ingadzapange misonkhano .koma pano anthu adabweza mitima ya mkwiyo kwa chakwela chifukwa atazindikila kuti nkhani zanu zambiri mukungopeka kuwonjezela .
@IsaacKulongwe-ol5mx
@IsaacKulongwe-ol5mx 3 сағат бұрын
Amisala atha kumamvera zokamba za inu .Ngati ndi umphawi pezani zina zochita.
@WelingsLongwe
@WelingsLongwe 2 сағат бұрын
Nkulu uyu muli bodza alibe zochita
@GibsonBankha
@GibsonBankha 3 сағат бұрын
Iwe gologolo wamuthu umangidwekumene ndimabodza akowo gulugunyinda wamuthu
@PatienceHarry-z7h
@PatienceHarry-z7h 17 минут бұрын
Uremu wanu comrade nyanyuwa osawopa osafowoka kuswakuswa
@MarkoMayuni
@MarkoMayuni 3 сағат бұрын
Inunso ngati mulibe chonena khalani chete
@GrecianWyson
@GrecianWyson 3 сағат бұрын
Zazi Ngatitu mulibe umboni okwanila please osamaikapo comments mwatipusitsa Ife timakudarirani hv
@mikekamanga45
@mikekamanga45 25 минут бұрын
Komatu mukuti odwala anapanga ma push ups Mr comrade
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 4 сағат бұрын
Achina Ntanyiwa inu mwapusisa fans dzulo ndi bodza lanu kunama za imfa,si choncho sibwino,mwazusa BP kwa omukonda President komaso mwa panga zosangalasa adani mwawa lumphisa pachabe
@IbrahimPhiri-ky5jk
@IbrahimPhiri-ky5jk 3 сағат бұрын
Panyapako pamozi ndi amako omwe
@AaliyaKalembo
@AaliyaKalembo 2 сағат бұрын
Koma zaifa sanakambe koma anati akudwala
@MicyThobve
@MicyThobve Сағат бұрын
Inenso ndapombonezeka mmm ali ku hospital RSA now ali ku blantyre, compromising indeed
@GeoffTchezan
@GeoffTchezan 3 сағат бұрын
Panyopako iwe wanva,,ukusokoneza a Malawi pantumbo pamako fwetseki hiyaa
@GracePhiri-f2u
@GracePhiri-f2u 3 сағат бұрын
Dzulo mwatiuza ziti alikuchipatala Ku South Africa lero mukuyiuzaso Zina Mmmmm koma
@SmartMajola
@SmartMajola 3 сағат бұрын
Wanamidzi nthundu wa Malawi kokwanila,panopa nthawi yako yatha,uwone pa ma robort po mg 1 akutchita ma push ups mpaka kugonjetsa a nduna a information,ndy ulibe manyadzi,galu wamunthu
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem 59 минут бұрын
onama iwe!! watinamiza mmawa omwe uno!! tadziwonela tokha kuti munthu aili bho bho
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson 3 сағат бұрын
Zabwino kuti amalawi akazionele okha akama komoka popeza masiku ano ali nga kafadala.
@Thewarrior7093
@Thewarrior7093 15 минут бұрын
Apa Ntanyiwa wambwita. Intelligence yako yabodza
@IsaacKulongwe-ol5mx
@IsaacKulongwe-ol5mx 3 сағат бұрын
Afiti nose pano chitani manyazi musayese gogo wanu othyoka manja uja komaso opanda Mano
@WilsonChiumia-bi3oy
@WilsonChiumia-bi3oy 3 сағат бұрын
Wabodza iwe sumati wamwalira pano wabwera ndi ina azikukhulupila ndi omwewo unanamaso za Pitala
@AaliyaKalembo
@AaliyaKalembo 2 сағат бұрын
Zomwalira sanakambe koma amati wadwala
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 3 сағат бұрын
Kodi inu.mulungu Alison.His eyes are open
@RonaldSaee
@RonaldSaee 43 минут бұрын
Zopeka zabodza ena ndi aja mukuti akalindo kumangotiuza zabodza kulimbana ndimuthu odzedwa ndiphavu yamulung mudzapeza nazo mathemberero osatha izo mwaxiona dzulo kutinamiza namiza lelo muthu akuthamanga mudwararo inu thenda yofaziwarao
@MabushPaulo
@MabushPaulo Сағат бұрын
Umanena wekha kuti ali south Africa,wadwalalika kwambiri ,komaso nkhope za anthu kumeneko ndi zachisoni,Kodi nthawi yomweyi abwerako ku Garden City ku chipatala kuja??????
@JaneMoyo-b7i
@JaneMoyo-b7i 45 минут бұрын
Kabambe ngwa dpp ntanyiwa ngwa dpp Kani Ali against Mayi Kaliati
@wisdom20mkango49
@wisdom20mkango49 3 сағат бұрын
Iwe sizulo umalankhula zopusa now what are you saying... You supposed to go to school and study journalism maybe you could have some sense Coz apa baba mukupenga
@StevenLikukuta
@StevenLikukuta Сағат бұрын
Mtanyiwa iwe ndi chitsiru zulo watokota kuti ali ku garden city hospital ndiye wachokera kuchipatala kupita ku Blantyre. Iwe mbuzi ya munthu ukusocheresa amalawi opusa anzako
@munikabambe7625
@munikabambe7625 3 сағат бұрын
Ndetimve ziti poti dzulo mwatiuza zina?.. Mxieew
@wisdom20mkango49
@wisdom20mkango49 2 сағат бұрын
😂😂😂 Mbuzi iyi amwene
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 3 сағат бұрын
Malawi is in a bad state
@ChettoSongeah
@ChettoSongeah 3 сағат бұрын
Singachite kutaya nthawi yanga kumuikizi satan ameneyu
@wisdom20mkango49
@wisdom20mkango49 3 сағат бұрын
Iwe mtanyiwa ndichisiru kwambu mbuzi galu bankha mbewa
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 сағат бұрын
Ntanyiwa ndiwe waboza mesa umat chakwera apita ku s Africa ku garden city ,munthu wodwala angapange ma push up chitsiru Cha munthu iwe
@VioletMbale
@VioletMbale Сағат бұрын
Koma nanuso too much mabodza nde ku America wabwelako liti president? Koma dzikoli mmmm ayi
@jameschiwanga
@jameschiwanga Сағат бұрын
Dpp chipani chokumpha ichi basi tiziti chibwerereso mboma pamene akulimbikisa kumphana ndi kuontchana
@whatsonbanda4277
@whatsonbanda4277 2 минут бұрын
Iyi channel ndi channel ya mfiti ndithu uzinamiza mfuti zinzako.
@RonaldSaee
@RonaldSaee 47 минут бұрын
NDinu abodza zd mumangotithera madata athu zazih muziuza athu zabodza ife taona tokha akuthamanga kupanga phushapu muthu odwara zd angapange zimenezo
@MphatsoGeorge
@MphatsoGeorge Сағат бұрын
Abale amusiyaso uyu osafa asaa ambuy mtengeni chakwela tipume
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 2 сағат бұрын
Atanyiwa pekani lina bodza ili lamvuta muwuzane ndi bakili muluzi tv mukagwere 😅😅😅😅😅😅
@PatrickMalenga-h5m
@PatrickMalenga-h5m Сағат бұрын
Antanyiwa takutukani ndinu wabodza lanjere kkkkk manyazi ulibe lero ukukamba zina mmmmm mukufa ndibodza abambo inu takutulukani mumayakhula zopanda zeru ukulakoseko kukhalira kunama bas😅😅😅😅
@ConlardNkhoma
@ConlardNkhoma 3 сағат бұрын
Mwasiwa chonena kkkkkk😂😂😂😂
@StevenKupheka-k6b
@StevenKupheka-k6b 3 сағат бұрын
Koma mwatenga ma Jacksen okwanila
@ChawingaMwaseteza
@ChawingaMwaseteza 2 сағат бұрын
Koma anthu sitimafunilsna zabwino,,inu munthu amanenedwa kuti wafa nkonoyo mene wapangila ma push muja munthu odwala angatelo,,,aaaaa Amalawi tiyeni timudziwe yesu masikuwa ndiwomalidza
@FrancisKampira-h6s
@FrancisKampira-h6s 2 сағат бұрын
Sindisapota Congress.koma mabodza saafunika.if you have no news remain quite.nzanu wadya ma push ups
@DysonTummiesSajiwa
@DysonTummiesSajiwa 4 сағат бұрын
Mmmmm inu musamapotoze anthu inu pantumbo panu ndithu munthu odwala amapanga ma push Up
@SaviourNyimbiri-qk1qh
@SaviourNyimbiri-qk1qh Сағат бұрын
Poyamba timakukhulupililani koma panopa takutulukani ndinu onama mungotithera bandle bas
@ChomboNgosi
@ChomboNgosi 50 минут бұрын
❤❤❤❤
@RabeccaChiumia
@RabeccaChiumia 3 сағат бұрын
Ndafulumira ndibweraso
@AugustineChimaliro-e5i
@AugustineChimaliro-e5i 4 сағат бұрын
Asiye aziwona
@HenryNanthuwa
@HenryNanthuwa 3 сағат бұрын
Dzulo mwatinamidza inu iyaaah
@MasekoKalimanjira
@MasekoKalimanjira Сағат бұрын
Ase mulungu adzakulanga ndipo zmene mumakamba zamabodza zakoz umapindura chan ndkutuluka
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 3 сағат бұрын
To prove what now?
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 4 сағат бұрын
Onse amene akuwafunira zoipa athu kuti afe nayeso azafa palibe wamuyaya Allah akulangani fast
@thomaswyson-e2q
@thomaswyson-e2q 4 сағат бұрын
Alanga amako
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 4 сағат бұрын
@@thomaswyson-e2q iweyo mayakowo ndi bambo ako
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 3 сағат бұрын
@@thomaswyson-e2q umaona ngati kupha muthu kapena kumanga muthu ndi udolo naweso uzafa wamva nonse amene mukupanga zimenezo Allah akulangani mwachangu
@WilliousNyirongo
@WilliousNyirongo 43 минут бұрын
Mulungu sàmasangalala ndi bodza,ikakwana la 40 umayaluka nalo kuti anthu adziwe chomwe uli.
@Onex-z6s
@Onex-z6s 4 минут бұрын
Wayaluka bwanji ngati ananena zoti chakwela wamwalila?ufela limozi ndi MCP yakoyo
@SaviourNyimbiri-qk1qh
@SaviourNyimbiri-qk1qh Сағат бұрын
Zaa ziii kungosowa zochita basi mnthu ali bwino bwino uja
@DavieTombozi
@DavieTombozi 4 сағат бұрын
Komano zosokoneza maganizo izi bwanji wachita ma push up ndabalalika ine abale
@EmmanuelMpalagule
@EmmanuelMpalagule 4 сағат бұрын
Eeeeh chatuluka amwene chimunthu chija mpaka ma push up mmmmmh ichi mchamangolomela eti?
@tasmania527
@tasmania527 2 сағат бұрын
Kkkkkk koma. Amwene khalani a chikondi ndi leadership, Mulungu akudalitsani.
@HarryChindiwo
@HarryChindiwo 2 сағат бұрын
Ngati sakudziwapo kanthu za anthu 9 aja sa afa koma ngati akudziwa kuti anachitipo kanthu mulungu zioneseleni nokha
@GanizaniBishop
@GanizaniBishop 3 сағат бұрын
Apa mwayamba kutinamiza inu
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 8 минут бұрын
Nde simunafotokonzenso kut wabwera bwanji mmesa mmati alikunja
@LeonardNdhlovu-x4t
@LeonardNdhlovu-x4t Сағат бұрын
Chaboza icho chilibe ndimanyazi chitanyiwa ichi
@GiftMangani-od4dq
@GiftMangani-od4dq 2 сағат бұрын
Galu iwe
@AliNtolera
@AliNtolera 55 минут бұрын
Ada inu mukunama bwanji bodza loteleri
@horacechera6978
@horacechera6978 2 сағат бұрын
Boma ndilomweli komanso president ndiyemweyu sitikusintha ma propaganda anuwa sakuthandizani dzikalimani uko mu ulimi muli phindu anthu a mwanja lende ndi amene akulimva kuwawa dzukoli pitani ku madera kumene anthu amalima mukawapeza apa akukololanso chimanga cha kudimba.Mbuli za anthu inu forsake
@louiskagona
@louiskagona Сағат бұрын
Mapazi anu man, mulowe mu ⚰️ ndinu
@AmosMussa-v4q
@AmosMussa-v4q Сағат бұрын
Mmm inuso penapake mufuna muzitinamiza 😂😂
@BasielBanda
@BasielBanda 4 сағат бұрын
Pambuyo panu Mr
@CyprianoSandalamu
@CyprianoSandalamu 3 сағат бұрын
Antanyiwa dzulo mumati a president amwalira apita nao ku garden city ku south Africa,ndipo apitilira nao ku America ukapanga embamu thupi lao,ndye lero mukamba Zina ,ndinu abodza ndipo izi sizikuthandizani gwilani ntchito kuti mupeze zosowa zapanyumba izi sizikuthandizani,tiyeni kudimba tikagwile ntchito osati zamabodzazi,
@annabelmunyenyembe-u7v
@annabelmunyenyembe-u7v 3 сағат бұрын
Anati sakupeza bwino musanamepo apa
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 2 сағат бұрын
Ndipo ananenanso kuti ayenela kuti wabwera dzuro lomwelo sananene zoti wamwalira nawonso ndiabodza
@AaliyaKalembo
@AaliyaKalembo 2 сағат бұрын
Zoti amfa sanakambe Inu munamva mwapuma eti aaa Siyani bonza
@AgnessMatchado
@AgnessMatchado 7 минут бұрын
Achewanu matako amayi anu sadanene kut wamwalira anena kut sakupeza bwino
@StevenLikukuta
@StevenLikukuta Сағат бұрын
Ngati DPP izaluze ndiweyo chifukwa amasatila mbuzi ngati iwe
@HenryNanthuwa
@HenryNanthuwa 3 сағат бұрын
Bodza iyaa
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 сағат бұрын
Satana ameneyu palibeso yemwe akukufunani zabwino
@vincentmumbwe2571
@vincentmumbwe2571 2 сағат бұрын
Akuphe kumene pa mtumbo pako
@OlivaPhiri
@OlivaPhiri 2 сағат бұрын
Ntanyiwa kkkkkkkk mutu ngat choswela malambe
@melnisachagwamnjira6082
@melnisachagwamnjira6082 2 сағат бұрын
Mmmm bodza ilo mwangosowa zochita agalu inu
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 17 минут бұрын
Agwatu awa!!!!
@NamuleriKafa
@NamuleriKafa 38 минут бұрын
Uyuyu amatinamiza wausilu uyu
@fredlemani
@fredlemani Сағат бұрын
Wabwera liti ku chipatala?
@FionaKhoma
@FionaKhoma 13 минут бұрын
Chikudwara kumene
@FunnyKalimwayi
@FunnyKalimwayi 2 сағат бұрын
musavutike loboti imeneyo
@LizzKaunda
@LizzKaunda 2 сағат бұрын
Akusakedi, ndi maboza ako,iyaah
@finchiadriano
@finchiadriano 2 сағат бұрын
Akulu inu ndi abodza kwambili
@BlessingsCperumal
@BlessingsCperumal 2 сағат бұрын
Ichi chitsiru😂
@BrendaKawinga
@BrendaKawinga 2 сағат бұрын
Mmmmh ndinu abodza
@Zaliro87_Frank
@Zaliro87_Frank 2 сағат бұрын
Kodi ada awa ndionamadi
@CrispalKachingwe
@CrispalKachingwe 2 сағат бұрын
Tiyenazo😂
@MynessChirwa
@MynessChirwa 40 минут бұрын
❤❤
She's very CREATIVE💡💦 #camping #survival #bushcraft #outdoors #lifehack
00:26
My Daughter's Dumplings Are Filled With Coins #funny #cute #comedy
00:18
Funny daughter's daily life
Рет қаралды 24 МЛН
ДЕНЬ УЧИТЕЛЯ В ШКОЛЕ
01:00
SIDELNIKOVVV
Рет қаралды 3,7 МЛН
LIVE - Malawi, Kenya president’s address 79th UNGA session
43:30
Malawi President Lazarus Chakwera Addresses 78th UNGA
13:39
VOA Africa
Рет қаралды 13 М.
President Ramaphosa hosts Malawian President Chakwera on a working visit to South Africa
29:21
The Presidency of the Republic of South Africa
Рет қаралды 10 М.
BON KALINDO - ANTHU ANAKONDWERA ATAMVA KUTI ANKOLO ANGA AKOMOKA
16:17
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 2,5 М.
Stories of Grace with Lazarus Chakwera
3:06
sapres
Рет қаралды 46 М.
OYENDA NDI LUPANGA/CHOIPA CHITSATA MWINI - NZWANYA CHARLEY PATACHE
6:16
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 12 М.
O‘zbekiston Prezidenti Ashxobod shahrida bo‘lib o‘tadigan xalqaro forumda ishtirok etadi
5:18
O'zMTRK O'zbekiston milliy teleradiokompaniyasi
Рет қаралды 6 М.
She's very CREATIVE💡💦 #camping #survival #bushcraft #outdoors #lifehack
00:26