OYENDA NDI LUPANGA/CHOIPA CHITSATA MWINI - NZWANYA CHARLEY PATACHE

  Рет қаралды 5,334

Mpungwe-Pungwe mw

Mpungwe-Pungwe mw

Күн бұрын

Пікірлер: 30
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 4 сағат бұрын
Alimoyo Chakwera koma yekha ngt alindi nzeru adziwe kuti anthu atopa nae chfukwa munthu akamwalira anthu amalira osati amaseka ndikunyadra
@CosterMustafa-m6h
@CosterMustafa-m6h 4 сағат бұрын
Koma ndy kulli kalelangatu nyimbo izii zilipo kom ndy yomweyo dj 🎉🎉🎉😂😂😂😂😂
@WilliamNyirenda-xq4km
@WilliamNyirenda-xq4km 4 сағат бұрын
Mixerxo ya akupita awo abwana ndi ulendo
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 4 сағат бұрын
Alimoyo sangafe kwacha agwesa ndani akafamo ngongole ija abweza ndani sakuthawatu ameneyo alimoyo ndthu Chakwera alipo
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 4 сағат бұрын
Chakwera yamba kukhal bwino ndi Amalawi nawo ndi anthu amafuna zabwino ichi chikhale chisadzo ngt uli ndi umunthu sintha khalidwe pliz pliz
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 2 сағат бұрын
Choipa chitsata mwini Ulemu Wanu mwatikumbutsa kale 💃💃💃💃💃💃❤️❤️❤️❤️❤️
@JOHNKANYALA
@JOHNKANYALA 4 сағат бұрын
Yomweyo dj😂😂😂
@kekeaufi9834
@kekeaufi9834 4 сағат бұрын
Lero kukutuluka nyimbo zodabwitsatu kwatani Kodi 🤔🤔🤔🤔
@WilliamNyirenda-xq4km
@WilliamNyirenda-xq4km 4 сағат бұрын
Tiguliseniko zikuti bwanji Kodi 😂😂😂😂😂😂
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 4 сағат бұрын
Aaaaaa ine nditenga mpando ndiwandikire basi zikuti bwanji?
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k 4 сағат бұрын
Mwambo wowona nkhope tikachitira mchikangawa guys yomweyo garu iwe
@HandissoneMaquina
@HandissoneMaquina 4 сағат бұрын
Mzimu WA chilima ndi anthu ema aja ine pheee
@HoseKatsekera
@HoseKatsekera 4 сағат бұрын
yomweyo, malawi ali boh, tiwuchape bas 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@HandissoneMaquina
@HandissoneMaquina 4 сағат бұрын
Chilima kupezeka wopanda nsapato nkumati inali Ngozi ààààa
@atanazimvuyekure955
@atanazimvuyekure955 4 сағат бұрын
Bola asazafe wa pandege ndiopa kuwonongetsa ndege yina
@ElizaJoseph-q9w
@ElizaJoseph-q9w 4 сағат бұрын
Malawi wavuta lelo anthu amwa wa mkaka ngati zili zoona zomwe ndikunganiza
@JohnWalekana-z2f
@JohnWalekana-z2f 4 сағат бұрын
Yashuta
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 4 сағат бұрын
Tiuchape tiutafune mahule mahule omwa fanta abwele pano.awuse muntendele bwanawo
@LinlyMatheweKufakwina
@LinlyMatheweKufakwina 4 сағат бұрын
Hmmm koma people aaa pliz polani moto
@Paul-q2p
@Paul-q2p 3 сағат бұрын
Mungoyika zofanana lelo ngati mukuziwapo nenani mutsatithele nthawi
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 3 сағат бұрын
Nice song
@LafickDickson
@LafickDickson 55 минут бұрын
Mcp achakwela alikuti
@gizzykondwani865
@gizzykondwani865 3 сағат бұрын
😂😅😅😅😅😅 mr patache inu mumakwana
@PatriciaAlomwe-oz8wc
@PatriciaAlomwe-oz8wc 3 сағат бұрын
Yomweyo galu iwe
@HarryKandani
@HarryKandani 4 сағат бұрын
Kkkkk koma timva nyimbo
@PaulFrank-tj2mc
@PaulFrank-tj2mc 2 сағат бұрын
Anakonza
@babranzima8120
@babranzima8120 3 сағат бұрын
Khasu lali fupi limudikirira nayyo😂
@ahmedmsume1489
@ahmedmsume1489 4 сағат бұрын
Koma sound imeneyi 😢😢😢😢
@JOHNSANGWALI-r2m
@JOHNSANGWALI-r2m 4 сағат бұрын
Iiiii zikuti bwanji Kodi Okay Dili Ku mastand kuvesera
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 2 сағат бұрын
Chakwera ngati uli moyo change please dziwa kukhala bwino ndi anthu, waona momwe ena akusangalalira za maliro? Please Apure sinthani
SANKANDILORA KUTULUKA PANJA - KANGAUDE PART2 WITH GOD KNOWS
55:02
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 13 М.
ABWANA PAULENDO - BLESSINGS CHIMANGENI
5:20
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 32 М.
Incredible: Teacher builds airplane to teach kids behavior! #shorts
00:32
Fabiosa Stories
Рет қаралды 12 МЛН
规则,在门里生存,出来~死亡
00:33
落魄的王子
Рет қаралды 29 МЛН
Chikuchitika ndichani Amalawi 🤔
2:21
Malawian Cameras
Рет қаралды 39 М.
E20 : MALAWI ON THE ROAD, FROM CHIKWAWA TO BLANTYRE
7:47
Gypsy Wheels
Рет қаралды 2,8 М.
COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM - DISO NDI DISO NDI PATRICIA KALIAT
16:58
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 39 М.
GT hardrock  Cafe and food
18:14
Bunny toocoolGY
Рет қаралды 5 М.
African abraham church
1:25
Moffat Mdhluli
Рет қаралды 2,5 М.
6  DZUKA  WOMENS   M'BANDA KUCHA
5:11
Khumbo Kaliwo
Рет қаралды 1,1 М.