PLAN YOFUNA KUPHA APM YAPHEDUKA _ COMRADE CLIFF CHINYAMA 22/12/24

  Рет қаралды 16,805

MPUNGWE-PUNGWE MW

MPUNGWE-PUNGWE MW

Күн бұрын

Пікірлер: 132
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 17 сағат бұрын
Takumvani Comred May the Almighty God bless you.Malawi adalitsidwe kopambana
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 3 күн бұрын
Keep it up good work 😇 comrade cliff may God continue keeping you safe
@ThoccoChimbali-h6g
@ThoccoChimbali-h6g 3 күн бұрын
Rulling a country with an iron fist and expect people to be quiet is a completely fallacy
@MandalaChaona
@MandalaChaona 4 күн бұрын
Weldone Brother Cliff. Mwayiyalusa Game, keep it up Brother zoopsyezana palibe this is 2024 not 1940 God be with you
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 3 күн бұрын
Living in a country of democratic freedom while colonial attitude is blastinb a ver long spell
@gladysmanthimba7851
@gladysmanthimba7851 3 күн бұрын
Comrade chinyama thank you for the updates
@AlexanderTraffick
@AlexanderTraffick 4 күн бұрын
Koma chitetedzo chomwe chili Kwa APM muzakwanitsa.kkkkk ngati mukumurephera Gangata amene wateketsa mu Lilongwe kkkkk
@IshmaelNgeyani
@IshmaelNgeyani 3 күн бұрын
Wadziwa kale norman chisale kuli citetezo cokhwithima kwa apm kuposa ca cakwera
@Miracle1979Mike
@Miracle1979Mike 20 сағат бұрын
Nabadwilanji kumalawi ine
@EvasonThupilifana
@EvasonThupilifana 4 күн бұрын
Kod a Malawi chakwera tikumusungilanji munthu okupha ngati amenei 😅
@MveraNambala
@MveraNambala 8 сағат бұрын
Ndipo
@MorrisOwenSeleman
@MorrisOwenSeleman 17 сағат бұрын
Kodi asilikali athu mukamva zimenezi mukumapangapo chani?
@natashamathala8715
@natashamathala8715 3 күн бұрын
Osati anthu 9 koma 10 ndi kasambala yemwe
@clairelewis5309
@clairelewis5309 Күн бұрын
Zoona 10 ,Kasambara our Hero RIP.
@natashamathala8715
@natashamathala8715 Күн бұрын
Eya kaya tisamangoona za chilima ndi anthu amu ndege ayi, kasambala komaso anthu ena onwe akuphedwa everyday mwachinsinsi kaaa
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 22 сағат бұрын
Anaphanso sidiki mia
@nawenaconstruction
@nawenaconstruction 4 күн бұрын
Chisale awonjezeee security yamphamvu kwambili kmaso yolorela mafelano
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di 3 күн бұрын
Apm sakufa mpaka atenge boma 2025 adzalisiye kwa oyenela basi afune asafune komanso panopa adani a apm ayambe kuswana okha okha mudzina la yesu
@MandalaChaona
@MandalaChaona 23 сағат бұрын
@MaryChavula-jz3di Amen and Amen 🙏🙏
@MatthewKaliyati
@MatthewKaliyati 23 сағат бұрын
Amen
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 22 сағат бұрын
Mau
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 19 сағат бұрын
Zandikhudza bwanj izizi mulungu achitepo kanthu bravo comrade chinyama.
@KelvenNakhalare
@KelvenNakhalare 16 сағат бұрын
Bravo
@EdwardMathuwa
@EdwardMathuwa 4 күн бұрын
God bless you my brother
@catherinekadwala3839
@catherinekadwala3839 2 күн бұрын
Comrade osaopa kumangong'alura Ali dziko Momo,God bless you bro
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 4 күн бұрын
Mcp ikudziwa kuti 2025 APM ndi amene akutenga dzikoli sakugona nae tulo.APM ndiyemwe a malawi tikudalira moti 2025 tizamuvotele.Nkhani imenei ndiyona ndawuzidwa ndi msilikali wina wa MDF ku lilongwe kuti APM akufuna aphedwe komano mcp isamale sikudziwa comwe cikuganiza anthu cifukwa APM anthu amamukonda. Mcp inu ndi makape tidzakuma komweko.
@RosinaPatel
@RosinaPatel 4 күн бұрын
Ndipo live..mulungu amuteteza APM
@AlexKaunda-w7l
@AlexKaunda-w7l 2 күн бұрын
Mkaka nyini yamako yosameta
@YusufMoyo
@YusufMoyo 4 күн бұрын
Ndipo ndikamamva zimenezi ngati ndiagwile pakhozi Anthu oyipawa ambuye atithandize nkhondo yakula tonkha sitintha
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 3 күн бұрын
anthu ngati inu akulu ndipemphelo langa Mulungu azikutetezani ndithu
@alexsumani6823
@alexsumani6823 4 күн бұрын
awa ndi akatundu omangs ndi mawaya
@JamesPhiri-h7p
@JamesPhiri-h7p 4 күн бұрын
Big up crif
@LoydKamtedza
@LoydKamtedza 3 күн бұрын
Akufulatire YAA ALLAH Nothing happened to u clif
@NdaizwaChipeta-cp5fs
@NdaizwaChipeta-cp5fs 3 күн бұрын
Ure a strong citizen
@InacioCement-t7n
@InacioCement-t7n 3 күн бұрын
God ndiye mwini zonse asatana ndi olephera iwonso azafa
@JoyceKasongo-s8k
@JoyceKasongo-s8k 22 сағат бұрын
Apha angati kodi,angotimaliza tonsee
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 4 күн бұрын
Bravo brother❤
@collengoma6542
@collengoma6542 4 күн бұрын
ine or ndikamawona chakwera ndimakhala ngati ndikuwona chiwanda chakwera ndi munthu oyipa osati masewera ndipo palibe chabwino chomwe angatichitire a Malawi koma ine ndikubetcha ngati chakwera azafike tsiku lovota
@MandalaChaona
@MandalaChaona 4 күн бұрын
Ine ndimafika pochita Mseru ndikamuona Blood sucker Ameneyi ndi Chimwendo,Za satanic Izi
@BlessingsGama-j3r
@BlessingsGama-j3r 3 күн бұрын
Muzing'alula Nyumba komwe kuli zigawengako ndikuti Osaopa
@EnockMawaya
@EnockMawaya 18 сағат бұрын
Mulungu wathu wakumwamba musakhale chete chonde mutetezeni APM mumphimbeni kunsi kwa mapiko Anu chonde ambuye pa masalimo 91 mutetezeni APM ku mulili osakaza chonde ambuye chonde
@RosinaPatel
@RosinaPatel 4 күн бұрын
Adad woyeeeeee
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 4 күн бұрын
KAFUKUFUKU WANGA AKUNDUZA KUTI CHAKWELA ADZAMWALIRA PA 17JULY 2025 10 AM AMALAWI TISATAYE MTIMA CHONDE MULUNGUVALINAFE
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 21 сағат бұрын
Rip in advance
@BoscoKalua
@BoscoKalua 2 күн бұрын
Wokumba dzenje adzagweramo yekha
@joebrown1158
@joebrown1158 4 күн бұрын
Devil 😈 is in the details, ana a njoka akusaweluzika kuyembekezela chiweluzo
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy 4 күн бұрын
Ndipo these devils 😡😡😡
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera 4 күн бұрын
MCP azipanga misonkhano ku Lilongwe konko osati ma region ena chifukwa ndizisilu zigewenga.
@AlexanderTraffick
@AlexanderTraffick 4 күн бұрын
APM sakuyenda kulikonse .maka maka pa Centre Region.osadabwa kuti zigawo zina nayenderako kale.Chosale amaziwa zosezo.bwanji sanaime panthawi yomwe amapita kumpoto kuja.Centre Region Azingozungulira Anyamata bansi achina Gangata ndi adzawo
@katalamajames4947
@katalamajames4947 4 күн бұрын
Komatu peter kungoti wafa mosadziwika bwino Richard chimwendo banda ndi chakwera munzanya muzaonaso kuti amalawi akwiya tidzakuchotsani mbolo dzanu aphwanga
@BoscoKalua
@BoscoKalua 2 күн бұрын
No secret under the sun God says
@zayedmitawa8345
@zayedmitawa8345 22 сағат бұрын
USA, Biden ankafuna kupha Trump mmalo mwake kunali ngati kumpangira campaign,anawina mopanda chikaikonso.
@Christopherchapeta-q2j
@Christopherchapeta-q2j 4 күн бұрын
Kodi ndiye kuti am7ganiza kuti azikhala ndi moyo ndiokhawi a chikangawa party koma APM simungamukea ise
@ManjeUphl
@ManjeUphl 13 сағат бұрын
Chakweranso aphedwe lamuro likutero lamulungu
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 9 сағат бұрын
Mulungu alipo kunja kuno munya muwona mutadzafe ndi inu osati Peter muntharika, Mcp kunyadatu ngati kunja kuno kulibe Mulungu munya sizidzatheka ndinkona chilichonse chikungowululika
@Dellingsmunthali
@Dellingsmunthali 10 сағат бұрын
Ozayanbisa phokosowo malume anga chisare please please onesani luso lanu please please chonde tiuzeni zochita anthu awa atitora
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 19 сағат бұрын
NGATI KWADZIWIKA KUNYUMBA KOMWE KUKUSUNGIDWA ZIGAWENGA BWANJI KUTENGANA A MALAWI KUPITA KONKO NKUKAWAGWIRA NKUWAPANA NDI MAFUNSO ALOWA BWANJI MONO NANGA ACHOKERA KITI NANGA AKUZATANI TIUZENI KULIZIGAWENGAZO
@joebrown1158
@joebrown1158 4 күн бұрын
Koma ndithu a Malawi kufika pasayizi yimeneyi kodi kwa Mulungu mudzakati chiyani patsiku lachiweluzo? Anthu yinu muli ndi tsoka lalikulu kwambiri pamaso pa Mulungu.
@GiftMathewe-fr3kn
@GiftMathewe-fr3kn 4 күн бұрын
❤❤
@RoseThindwa
@RoseThindwa 4 күн бұрын
Zoona boma ili lakupha it make sense now za kuchikangwa anthu onse aja chifukwa cha seat zomvetsa chisoni
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson 3 күн бұрын
Kod mukuti chakwelayo tikumulolelanj kulamula mdziko la malawi mpaka pano?
@ManjeUphl
@ManjeUphl 13 сағат бұрын
Ukumakhala ukuonangati wamuyaya ask kamuzu banda alikuti u not safe chikangawa do u think state house is safe place Ufa infa yo wawa ugwa padegenso nawenso
@HawaHussein-o5k
@HawaHussein-o5k 3 күн бұрын
Ambuye akhale mtetezi wa a p m amene wakumba dzenje agwelamo yekha nde pemphero langa
@AlexKaunda-w7l
@AlexKaunda-w7l 2 күн бұрын
Mukuopaso nyumbayo yilikuti
@chimwemwechimwanza
@chimwemwechimwanza 11 сағат бұрын
asavutike olo adad atapanda kupanga misokhano ife tidzavotelabe dpp basi ndipo adad safa
@JonesBenNgaiyaye
@JonesBenNgaiyaye Күн бұрын
Comrade Cliff ambuye akupatseni moyo wautali komanso apereke chitetezo chokwanira kuti dziko lidziwe choonadi
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 8 сағат бұрын
Boma lapangidwa ndi ma vampire, achina dausi, omwe anali bodyguard wa dictator, kamuzu
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 3 күн бұрын
MULUNGU alinawo adad, kodi chakwerayu akuganiza iyeyu ndimulungu ? kuti azipha anthu
@KiaJohnson-wi9kx
@KiaJohnson-wi9kx 3 күн бұрын
Kod iwe chakwela iwendibhuzi eti chomwe umaziwa ndikupha chomwe ungaziwe ndichot pitha alindi mulungu wava tayelekeza uwone kupha tizakupha
@MatthewKaliyati
@MatthewKaliyati 22 сағат бұрын
Chakweratu ndi mulungu wakumidima ndi chifukwa chake sawelenga zochotsa moyo wamunthu. Nthawi ikwana yoti ayaluke mothelatu very soon
@MalickMkweche
@MalickMkweche 3 күн бұрын
Koma chakwera malo.moyendesa bwino ziko busy kufuna kuchosa moyo wanzawo iiiii
@AlfredSemani
@AlfredSemani 4 күн бұрын
Nonsenu mwalankhula mwanzelu kwambili ine chomwe ndngalankhulepo nchakut ngati zili choncho awo ndimalingalilo awo kapena kt chikonzelo chawo chabe kma ine ndikuona kt amenewo ndimaloto omwalila sangakwanise
@GOSH-c8y
@GOSH-c8y 4 күн бұрын
kodi afuna aphe anthu angati kuti akhalebe pa udindo,
@OssmanAbubaker-v7t
@OssmanAbubaker-v7t Күн бұрын
Zoonadi brother chilungamo osaopa osafooka osatopa
@JimmyMhone-b5p
@JimmyMhone-b5p 3 күн бұрын
Chakwera ndi mfiti yopanda manyazi
@RosinaPatel
@RosinaPatel 4 күн бұрын
APM akukumvetsani pain
@JosephGabriel-y7w
@JosephGabriel-y7w 4 күн бұрын
Kod guys chakwela osamungwila pakhosi bwanji
@BusisiweMakhoba-d8o
@BusisiweMakhoba-d8o 21 сағат бұрын
Osawasekelela anthu oipawa
@OwenNyangu
@OwenNyangu 16 сағат бұрын
Osamawakhulupilira anthu amabodzawa. Anthu oyambanittsa awa
@FrancisKenneth-i4p
@FrancisKenneth-i4p Күн бұрын
Nchewa opusa kwambili eme😂neyo atipha tonse mwachita bwino kuyin'galula ankolo
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 23 сағат бұрын
Ndipo awa a mcp ine kukhala ndimadziwa ufiti ndikanalodza chakwela sure
@SPEARJAMES-r7y
@SPEARJAMES-r7y 14 сағат бұрын
Kodi iye saziwa kuti ena sakodwa ndi kuzuzidwa Kwa abale awo sakukondwa nawo panopa tonse tilimaso chomwe chingabisike ndi angapange yekha basi pitilizani kitiuzazinsisi
@MarySinjirani
@MarySinjirani 16 сағат бұрын
Kodi iwe chikangawa chakwela ngati kufa kuli kokoma bwanji osafa iweyo ukufuna utimalize usale nalo wekha dzikoli ndi mkazi wako onyasayo
@LawrenceMsango
@LawrenceMsango 4 күн бұрын
Chimwendo chifukwa chake amayimba nyimbo kuti peter asowe pamusonkhano . Chimwendo akufuna amwalile nayo.
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 19 сағат бұрын
MULUNGU NDIYE AKUULULA KOMA VUTO A MALAWI TULO CAUSE NGATI ZAZIWIKA KUMENE ZIKUKHALA ZIGAWENGAZO KUNALIBWINO KUPITAKONKO NKUKAWATENGA AULULE CHOMWE ABWERERA
@OmarNseula
@OmarNseula 20 сағат бұрын
Zimayamba chomchi kumene kenako umva zina
@joebrown1158
@joebrown1158 4 күн бұрын
Kodi a Malawi munakgalabwanji wosadzuka ndikupanga chinthu chakuti dziko lapasi lidziwe chikuvuta ndi chiyani wosagwiliza chimodzi.
@MacxwellStuarts-h9r
@MacxwellStuarts-h9r 8 сағат бұрын
Asilikali akumalawi ndi a chipani cha mcp osati aziko
@MaupoMhango
@MaupoMhango 23 сағат бұрын
Zina mkunamapo apa
@InnocentHassan-m3r
@InnocentHassan-m3r Күн бұрын
Kumango ng'alura basi a MCP Anya nayo
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx Күн бұрын
APM sakuphedwa mu dzina L yesu akumuteteza pali ponse akuyenda ndipo aPita ndi iwowo mwazi wa yesu ugwira ntchito ayaluka tu amene wa akong*on tha anthu nawoso ndi manja asiyeni
@JoyceKasongo-s8k
@JoyceKasongo-s8k 22 сағат бұрын
Afa ndiiwowo
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy 4 күн бұрын
Koditu chakwela 2025 akufa
@MatthewKaliyati
@MatthewKaliyati 22 сағат бұрын
Afendithu satana ameneyo, chilombo chanyangachi
@stalickkafera3454
@stalickkafera3454 4 күн бұрын
Kodi mumangoyakhura zopeka eti
@ezekielchingoma5345
@ezekielchingoma5345 2 күн бұрын
Akukuuza izizi nde ngabodzatu. Munthu ukunenayo what would he benefit from killing nkuluyo.??
@futurekanjanga1290
@futurekanjanga1290 13 сағат бұрын
What he benefited from killing Chilima and other?
@TiyaMtete-l7t
@TiyaMtete-l7t 13 сағат бұрын
Iweyo ndiwee galu
@HappyWilliams-k6n
@HappyWilliams-k6n 4 күн бұрын
Km chakwera akufuna chan, mfiti imeneyi tinalozedwa chan kut akhale pa mpando
@MemorieMwasinga
@MemorieMwasinga 4 күн бұрын
Padzavuta heavy asayelekeze
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 9 сағат бұрын
Osangopita kukangoyiyatsa Nyumba yo bwanji? Nde olo mutamupha Peter muntharika angakumbvotereni ndani inu a Mcp? Nde bola nso kukabvotera kabambetu
@MaxwellChisi-k2e
@MaxwellChisi-k2e Күн бұрын
Shame mcp lion of killing .
@EdwardMathuwa
@EdwardMathuwa 4 күн бұрын
Kodi bansi mcp mumangoganiza zokupha bansi
@GabaBogyi
@GabaBogyi Күн бұрын
Mavoto kwatu
@ElsaMalunga
@ElsaMalunga Күн бұрын
Mutayerekeza komariza kamene mukufuna kupangazo kd Inu ndi ana ifenso takozeka dziko mukungonya ndarama za aMalawi guys musamare
@aaronziyeretsa6420
@aaronziyeretsa6420 4 күн бұрын
Mbuzi ya munthu
@YamikaniLekani-mo2vo
@YamikaniLekani-mo2vo 3 күн бұрын
Chakwerayo?
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 22 сағат бұрын
Akuyankhulay kapen Chakwera? Oooooohhhhhh
@ChifundoBeston
@ChifundoBeston 4 күн бұрын
Zabodza izi
@MatthewKaliyati
@MatthewKaliyati 22 сағат бұрын
Zowona ndizakozo ndiye wabweleranji ku comment m'malo mobwelesa zako, akutuma eti unditukwanisatu iwe mwana wa satana chikangawa
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 22 сағат бұрын
Mupindula chani mukapha Peter?muuzan kut nthawi yolap machimo ino sizausru anthu amagazi manja
@DoreenBanda-hg7oe
@DoreenBanda-hg7oe 2 күн бұрын
Eeeeeee koma musayerekeze plan yanuyo mudzaziona
@MynessChirwa
@MynessChirwa 21 сағат бұрын
Koma mcp mmm ndaituluka
@joebrown1158
@joebrown1158 4 күн бұрын
Amalawi muli ndi tsoka kwa mbiri mukulimbirana zotsala zaka nthawi kochepa kwambiri
@VinGenerators
@VinGenerators Күн бұрын
Although thawi ndichepa koma sumangawonerere zoyipa zikuchika tose tikuva kuwawa
@FrancesPeter-xw3vb
@FrancesPeter-xw3vb 22 сағат бұрын
Kkkkk mwapanga bwino kuphulisa ndukhulupirira kut ku page ku aona
@ManuelMataya
@ManuelMataya Сағат бұрын
Zosakhala bwino mmmmmmmmmmmmmmmmmmmm
@IbrahimMatola-k9p
@IbrahimMatola-k9p 3 күн бұрын
Inu atamwalire ndi chakwela yemweyo Tikama Vote kukala kulibe ameneyo ndipo mulungu apanga pepho Ili munthu oyipa ngati ameneyu ma pulani Ake Daily kumango ganidza zoyipa zoka zoka basi amenewo apita mulungu samakukonda wekha anthu 21milion avutike chifukwa Cha anthu ochepa ngati amenewa or 20 osakukwana
@brightkwenje-ib7yo
@brightkwenje-ib7yo 11 сағат бұрын
Wankhuta machende uyu inu mcp singaluze anthu timavotera chipani ngakhare titagona ndi njala koma mcp 🎉🎉🎉 sakuchoka chakwera
@aaronziyeretsa6420
@aaronziyeretsa6420 4 күн бұрын
Kkkkk akulu awa ndiopusa Propaganda a Dpp mwafika nayo pa ugalu Bakili muluzi adakambapo Mntanyiwa adanenapo izi Achisale ine ndi bwana ako kumene
@aaronziyeretsa6420
@aaronziyeretsa6420 4 күн бұрын
Inuyo ngati mukuyidziwa kuti anthuwo akugona kwakuti osapita komko bwanji Mulibe fundo ndi ubulutu wanowo bwanji
@VeronicaTime-jn7fp
@VeronicaTime-jn7fp 4 күн бұрын
Munyelabe achitsilu Inu waing'alilabe mulungu sakulila mwapha aja akwana
@MandalaChaona
@MandalaChaona 4 күн бұрын
Bulutu yomweyo Koma waulura zinsinsi Zanu zopusazo. Kodi mulipo ambiri amphyoza Magazi mix Mikodzo. Muyalukatu simunati. AKAZIKWANJE
@IbrahimMatola-k9p
@IbrahimMatola-k9p 3 күн бұрын
Kodi nawoso amenewa akuyikila kumbuyo manyi achakwelawo ochedwa MCP Pali chadzelu chomwe chikuchitika Malawi muno saposa kuononga agalu Inu ndamene mukunyatsisa zikoli mumango chikila kumbuyo zoyipa dzikuchitika chifukwa choti angokupasani ka 2000 anthu osowa chochita Inu
@DoreenBanda-hg7oe
@DoreenBanda-hg7oe 2 күн бұрын
bulutu la munthu
@JafarWiati
@JafarWiati Күн бұрын
😂😂😂mmozi wayiwo ndiiwe wayalukatu sunapilile wati uyankhe
@ChomboNgosi
@ChomboNgosi 3 күн бұрын
❤❤❤❤
Мясо вегана? 🧐 @Whatthefshow
01:01
История одного вокалиста
Рет қаралды 7 МЛН
Арыстанның айқасы, Тәуіржанның шайқасы!
25:51
QosLike / ҚосЛайк / Косылайық
Рет қаралды 700 М.
Сестра обхитрила!
00:17
Victoria Portfolio
Рет қаралды 958 М.
Senator Akpabio Asks Nigerians To Show Love, Unity
0:33
TVC News Nigeria
Рет қаралды 1,3 М.
MUSIYE ZOMANDIOPSEZAZO ANYAPAPI INU A MCP __COMRADE CLIFF CHINYAMA 23/12/24
11:58
Ответы на вопросы журналистов
20:49
COMRADE NTANYIWA 21/12/24 WAZAMBATUKANSO NDINKHANI YODZIDZIMUTSA
38:52
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 30 М.
COMRADE CLIFF CHINYAMA WADZANSO NDI KUKHADZURA KWANTUNDU WINA LERO 19/12/24
20:13
Мясо вегана? 🧐 @Whatthefshow
01:01
История одного вокалиста
Рет қаралды 7 МЛН