Appreciate the detailed breakdown! Could you help me with something unrelated: I have a SafePal wallet with USDT, and I have the seed phrase. (alarm fetch churn bridge exercise tape speak race clerk couch crater letter). What's the best way to send them to Binance?
@charlesmuwanya784514 күн бұрын
@@JuanCarlosGreta Hy. What are you talking about? Can you come out clearly?
@Auscarmbeye19 күн бұрын
Manganya ndimunthu wabwino Ena inu sanje zikiphani
@mchipengule18 күн бұрын
Mcp my vote!! Congratulations Vp.
@AmosShadreck18 күн бұрын
Hunger your vote aswell
@AugustineTheu-of6nv15 күн бұрын
Popesa u are all thieves
@FranksonKennethChipande15 күн бұрын
No matter what???? MCP my vote
@charlesmuwanya784514 күн бұрын
@@FranksonKennethChipande waste of time & public resources. Tonse alliance collapsed a long time ago. MCP is just in wonderland . A lonely wounded buffalo.
Nkhani yabwino no matter umapanga compain mwachinsisi iweeee
@LextonKuntaja10 күн бұрын
Im shadow councillor for Cz south mitumbira and Mp didn't help our area
@ummufareedah717319 күн бұрын
Amwanamveka sanachite bwino chimanga chikugawidwachi ndi Cha boma osati A vp ndiye ndale mudzisye uko
@HappyAutumnTrees-cd9ye18 күн бұрын
Agawa bwanji chimanga vp adodma apita kt,,
@charlesmuwanya784514 күн бұрын
@@HappyAutumnTrees-cd9ye Inde ntchito yogawa chimanga ndi ya DODMA. Usi akumalondola komwe DODMA yapita kuika ndale malo osayenera just to show Malawians his undesirable political relevance.
@YohaneMmorrah-k9d18 күн бұрын
Izitu sisatiiwalise mavuto,,,pakuyenera kukhala plan yoti tizikwanisa kuzifikila patokha..
@Mrc-w5w11 күн бұрын
Kulankhula ndiye uku kosadanisa anthu. Zikomo a vice president a dziko.
@phindiswatshibo710119 күн бұрын
Kodi chimanga cha dotima mwachilowesa ndale agalu inu
@AckimKasiya-u7q17 күн бұрын
Ndekut simuzitsata
@wisdom20mkango4915 күн бұрын
Kukhala chete ndikwabwino than kuzionesa uchisili
@officemoyenda-rj2hz18 күн бұрын
Micheal Usi is not manganya please address our VP with due respect
@monicagondwe22818 күн бұрын
I support
@MKANDAWIRE-z6s18 күн бұрын
mayikolo usi, ndi wadza kwambiri, nkhani ndiyakuti, ngati panali, akanisalala, oyimila delalo, that's fine, Chifukwa chani akulimbana ndi MP, Joseph mwana Veka? Komaso, MCP, ana tseka MA ADMARC, ndikubitsa. Chimanga chose , cholinga chawo, adzakopele anthu, pa nthawi ino, mchitidwe oputsa kwambiri, M'MALo motsegula mitsika ya ADMARC, Basi akunamidza anthu, kuti akugawa chimanga, Kodi chimangacho, chikwana anthu angati? Joseph mwana veka sikape ayii, ngati usi, kapena chakwela,, KOMASO nkhani yofunika, kwambiri, asegule mitsika ya ADMARC, MADELA ONSE, ADRMAC,
Manganya ndi Muthu wakulu mwanaveka muthawi yawo akamayenda aphungu azipani Zina samakhalapo kuzikonda basi
@PatrickKapendo18 күн бұрын
Amalawi tikuziwa kuti chilichose chimene andale amapanga chimatengedwa kuti ndi chandale ndipo amalawi apa ndim'mene amzitengela basi
@vinceynyone669316 күн бұрын
Uyu ndiwoononga zinthu, kuwombesa anthu Mitu
@HamiltonSinosi16 күн бұрын
Mukusowamo zochita mma office mwanumo eti
@WillyNyirenda-l7h17 күн бұрын
Mwanamveka has missed an opportunity for re election in ,2025.
@AugustineTheu-of6nv15 күн бұрын
Iwe usi unamupyetsa Chilima
@goodwinmtupanyama18 күн бұрын
Akuyesetsa nde kuti chani?.. ameneyo akuzilowetsa ndale zinthu zimenezo nde azingopanga zake ndi chipani chakecho asalumbane ndi anzake, komaso palibe lamulo lokakamiza phungu kuti akhalepo
@MoreenSemu18 күн бұрын
Manganya aku Chita bwino kusiya ofesi kumaka gawa chimanga ma mp opusawa amagawana katundu wa anthu osawuka pamodzi ndi a DC awo
@CleverChiumia19 күн бұрын
Lero mukubweretsa chimanga, mudali kuti?
@tasmania52719 күн бұрын
Kuyankhula mopusa kumeneku. Chili chonse chimayendera ndondomeko. Kupeza ndalama zogulira chimanga ndi ntchito yaikulu judging from the fact that dziko la Malawi silochita bwino kuyambira kale. Then identifying anthu ofuna chithandizo chifukwa pamalowaso chinyengo choti anthu ena ozikonda ndi oipa mtima amafuna ayike azibale awo kusiya osaukitsitsa. Then pali logistical issues- kupanga identify ma transporters opititsa chimanga kumalo kogawira. Warehousing is also taken into account. So, musamangobwebweta chifukwa chodana ndi boma ngati inu mungakwanise. Khalani anthu okoma mtima osati nkhwizi ndi chidani ndi anthu oyesa kuthandiza dziko. Chodabwitsa ndi choti , a opposition monga DPP amangodziwa kuyankhula ndale against government ndi kudzudzula pakathandizidwe ka anthu ndi chimanga chonsecho iwo ali ndi ndalama zomwe anaba ali m'boma koma sangagule chimanga kuthandiza kapena kugawira anthu ovutika ndi a njala- yimeneyo ndi hypocrisy ndipo Mulungu sakondwere nazo.
Usi, u can't tell Mwanamveka what to do,,, ulibe dziko lapansi VP yemwe amagawa chimanga never izi it has anthu ake omwe amayendetsa Usi u would have just say ogawa chimanga abwera date lakuti osati iwenso busy busy ndimatumba ako 10 wo nde look at anthu omwe alili as popo
@PeterPuluma18 күн бұрын
Matumba 13 okha abale serious 😢😢😢
@felistasbunu982415 күн бұрын
0:26
@HaroonFadweck-p5i9 күн бұрын
Avp mwalankhulabwino ndithu,simunanyoze munthu
@HenryMalikebu-i4g18 күн бұрын
KAMPENI MUKUPANGILA PA CHIMANGA CHA ULERE
@ManuelMagombo-m2u18 күн бұрын
Udindo osasankhidwa ndi anthu, olo u MP a manganya sanawinepo
@ChristinaMandala-j5u9 күн бұрын
Ngati sakugawira ndale bwanji sanangowasiira ma mp kuti aziyendetsa okha zimenezo.A dodma ali kuti
@rodricktwaya797718 күн бұрын
The guy is being realistic.........I love ❤ his energy.