Times 360 it's my best, Brian Banda and your Team pitilizani kutidziwitsa ndi kutivetsa kukoma, Brian Stanley Nowa, Capetown # from Monkey Bay chantulo
@gradsonmayira9336Ай бұрын
Brian ntchito muyigwira🔥🔥
@BrianMagangaАй бұрын
Mai chindevu mumakwana mwati Olira alile mwandisangalatsa
Times 360 mumatiimilira mumativesa kukoma zukachitika tivera kwa inu
@MandalaChaonaАй бұрын
" Pakuti Malamulo a Dziko lino amalora, choncho dzina langa likakatulukanso Ku Ballot, ine mkayimanso" Mr Lazarus Macathy Chikangawa ndinu munayankhula mawu amenewa pamaso pa yemwe munasayinira naye mgwirizano . Tulusani za kafukufuku wa ngozi ku Chikangawa simukutulusa. Pali ??????? Munthu woyipa iwe, M'busa okuba ndi okupha. God Will judge you evil man 👹🔨⛏️⚒️🔨👹. Lero zisangalala koma Amalawi sangayiwale Kuti unapha kufuna zonse zikhale zako.
@honourablebanda1961Ай бұрын
Times 360 is the best. Allan Banda pritoria(RSA) #ing'aluleni azibambo
@johnkatumbu6846Ай бұрын
Waitchela kale mwati kuluyo?🤣
@simonejose8925Ай бұрын
GWIRANI NTCHITO A TMS
@BlessingsSelemanАй бұрын
Kod brian unayamba mwazifusa chifukwa chomwe asilikali Ena mwati safuna kuti camera yaonese
@DanielKatengezaАй бұрын
Times ilengezenso kuti Brian Banda president wa Malawi nzakoyo akhale Vice President I think dzikoli liyenda bwino popanda corruption
@SelinaGamaliyere-q8vАй бұрын
Onse omwe anapha chilima asawine anthu oyipa
@user-hl3st3cc4vАй бұрын
Ubwino wake zomvota wochewa wokha wokha ndemukaluza muphanaso nokha nokha ma pb muzikomoka nawo zindalama mumamwaza zija
@pauljosephmakaula6835Ай бұрын
Katundu Vitumbiko Mumba all the best...new political dimensions
@FredPondamwalaАй бұрын
Vituuuuu
@SelemanSimoniАй бұрын
Thomas chibade
@ChifundoNinjeАй бұрын
Eeeee km times mukuigwila tchito yopambana
@user-ul1fb4yn5oАй бұрын
Times team mumakwanisa
@isaacgmcАй бұрын
Koma amalawi mukadali kuivotela MCP mmmmmm😂😂😂😂
@user-kh4qp1ji1iАй бұрын
Tea sitidya Brian 😂 timamwa!
@TriceGulaniАй бұрын
Kkkkkkkkkkkk zavuta achimwene amosesi
@CatherineKamsare-cy3yoАй бұрын
Kwachema🤣🤣🤣🤣
@user-ww9rj2wx8dАй бұрын
Bolani asamupheso Brian Banda mtola nkhani mbambande
@KingsleySymonАй бұрын
Nanga Nanu mtentha ndevuyo bwanj???? kkkkkkk am Kingsley Symon kusalima
@EnerstBanda-m4sАй бұрын
President sanalakhule bwino sungadzudzule opeleka ndalama tsiku lovota ai pomwe Anthu ataononga kale ndalama zawo akanawauza nthawi yomwe amapanga kampeni kuti asagwiritse ntchito ndalama komaso akanauza omwe amaletsa enakuti asaime nawo chifukwa sanakhale mu chipani zaka ziwiri izi zapangitsa atidye nawo mong Dausi, Brown Mpinganjira,Uladi Mussa ndi Ken nsonda kuti asapeze nawo mwai opikisana nawo zomwe President akanatha kuzikhoza before not tsiku la master mansakho kumenekuku wapangira kampeni ena wichs not good
@zacchaeusbvumbwe391Ай бұрын
Ntchito mwayigwira
@RichardChirwa-em6qjАй бұрын
Mkasa paja ankati sazatamandanso wa ndale waywala cruise 5 pa zodiac ndi joab, yedye
@NewtonSikweseАй бұрын
Koma kuyakhura chilungamo ndongotsolo lake likuyenda bwino koma mapeto ake Akala bwino