Ndipo ndawerega 2 Timoteo...4 ves 14. Alessandro...wosula mkuwa anandicitila.zoipa zambili. Adzambwezera iye Ambuye. Monga mwa ntchito zache 15 ves Ameneyo. Iweso uchenjere naye ,pakuti Anatsutsana. Nao Mau Anthu....🙏
@Mrnaumi-bz4osАй бұрын
We love times tv not mbc
@ThomuChiwangaАй бұрын
Zoona zoona awuzeni Ku MBC mukuwona ngati mulipo nonkha muzachokapo kumeneko Ku mbcko
@WachiyawoWangalusaАй бұрын
@@ThomuChiwanga😮😮😮😮😮😢😮😮😢😢😮😢😢😢😢😊😅😢😢😮😮😮😮😢😢 30:44
@Andrew-mr5kpАй бұрын
@@ThomuChiwangato
@PrinceBlessings-bv5bsАй бұрын
😂😂😂😂 walasa
@OmarManjawira-up3nsАй бұрын
Keep the fire burning guys,, what re you saying here ndizoona zokha zokha we are expecting a better Malawi from different leaders osati zitsilu zamcp
@JimmieKatemaАй бұрын
What change can Joyce bring? She failed big time in her two years and that's why Malawians booted her out. She has been part of the tonse government as well but she failed miserably. I'm even surprised that you guys are not saying anything about why Malawians denied her in 2014 after only serving two years by accident. Don't give her hopes but instead advise her to serve the nation outside politics
@GiftMlindeАй бұрын
Ing'alulani kwambliii MBC, that's veryy useless station
@sthoramexjrsa902Ай бұрын
I like this guys coz muli zichewa za gwwwaaaa kkk😅😅😅😅😅😅😅
@VailetnyirendaShamahАй бұрын
😂
@JanaJovianАй бұрын
A mbc amapanga za mcp tawatuluka ittv ❤❤❤
@VailetnyirendaShamahАй бұрын
MBC is very usiless but time is good chanel you're very impressive guys for times go your head don't afraid with stupid people who kill us in our country and you guys you know how malawi now is with layer busterd goverment
@isaacimmantambala5294Ай бұрын
mtsukuluzi chifuwachi akut wadya za mera to support za kukwela kwa mafuta🤣🤣 kukulakwilani bwana wanga😂
@KumbukaniChimbalangaАй бұрын
Iyi ndi wailesi yanga yokondedwa yomwe ndimaimvera nthawi zonse osati kasakula radio yosogozedwa ndi mbuli kasakula
Kasakula zimvere mu mtolo, munatha msuzi....ikanipo ana oti will lose nothing pa MBC...kikkkk anthu zili mommuja ngati kale before 2020 anthu samvera MBC
@ShamimuBisaniАй бұрын
Kd MBC ilipobe ayu times oyeeeee
@RuthMkangalaАй бұрын
A MBC atha mapulani asiyeni azilumbwalumbwa😊
@Mrnaumi-bz4osАй бұрын
Mbc is wast of time
@gradsonmayira9336Ай бұрын
Alesandiliyo😂😂😂 the Alexander 😂😂😂
@JudithHappiness-y4mАй бұрын
Times TV ndi mwala
@PromiseMankhwa-cr5mwАй бұрын
Inu a mbc kagwereni uku tanasiya kuvera radio yanuyo
@Dauson-j5iАй бұрын
Ngati nthawi ya a Joice Banda zinthu zimayenda bwino chifukwa chani anagulitsa ndege munthawi yawo fuso langa
@falliotphiri688Ай бұрын
Komanso A Times, The Fact kuti anthu amakukonda I, Sizithanthauza kuti ndinu aneneri olondola Ai, Mukanakhala kuti mumanena zoona, Mwina a MCP Sakana lowa mboma,, MCP ndi Boma lero partly because of Brian Banda and George kasakula, osaiwala wonder Msisya,,, Onsewa a Mapanga campaign for Opposition.. KOMA akuyenera kukhala Non Partisan, to avoid conflict of interests
@JimmyRajab-o7nАй бұрын
Koma azungu andituma ija ndikuba ndizomwe amalakwisa
@YamzyAmosАй бұрын
Pdp woyeeeeeeee😂😂😂😂
@OmegaChingamukaАй бұрын
Ine MBC ndinasiya kuwonela ndimakonda Times tv
@giftmakoyo1441Ай бұрын
Brian mpaka nsalu yalekaleka😂😂😂
@isaacchiwaula731Ай бұрын
Mmm musazichemerere guys, Ineyo ndimakupanga praise koma zichepetseni musazikuze ai, azikukwezani ndiathufe not u, coz pamenepopo aliyense amayankhula zosangalatsa iye mwini, so musayankhulitse coz sizoonse zomwe mumayankhula zoona, in something mumalakwitsaso ndithu si ingopitilizani kupanga ma program anu momwe mumapangira nthawi zonse not kuzichemereraso nooo, ur wrong....
@HusseinBinali-z1sАй бұрын
MBC ndi nonsense tt. No. 1
@falliotphiri688Ай бұрын
Vuto la Times, komanso a Brian Banda amakhala Partisan,, amaonetsa mbali Imene Ali,, Mu 2019 election, anali ku mbali Ya MCP, ndipo panopa pakuoneka kuti Ali ku mbali Ya DPP komanso ndi opposition, Mwina akanakhala educative to Government, and Malawians, GOVERNMENT business is not personal. A times amakhala too personal,, and that's Unprofessional
@RuthMkangalaАй бұрын
Atsukuluzeni Ang,Lauren ana achibwana
@ElizabethMulindeАй бұрын
Alisakiliyo anatiphera chilima
@faroukmejah.9169Ай бұрын
Koma Brian ndi sukuluzi 😂😂😂😂😂😂😂
@chitanibenito1109Ай бұрын
Komanso Joyce banda aziyamika Dpp inamuchita expose coz akanakhala kuti Bingu samamukonda sakanamusakha kukhala vc president, Dpp ndichipani chokhacho chomwe chimayika anthu pa map same applies to the late chilima Dpp imakukonda yabwera mcp yangomupha basi mmmmmmm kuyika mtima.
@PaulMunukwaАй бұрын
Inu ndi madolo guys achina brain enao nd manyaka
@chitanibenito1109Ай бұрын
Others yemweyo kkkkkk achina Nankomyaaaa
@kingtiles-g6qАй бұрын
kodi kwabwera abusa relo kkkkkkkk koma Brain
@emilymasiye2674Ай бұрын
Eee koma kuli kung'alula😂😂
@raymondchilimba7010Ай бұрын
Guys muzikhalako serious pa TV hey!.... Mukamakambilana kwa nthawi yayitali muzikhalako ndi madzi pa front komaso imakhala ngati decoration..... Mwatani Kodi! be creative hey!
Times Radio adminstrator olo kuwapatsako madzi okumwa anthuwa? Mmmm thats cruelty to your presenters...work on this please anthu kutsamwa kungogwira pakamwa kusowa madzi????? be serious a Times