No video

Limpopo Vuu Ntanyiwa akatele watulukila ndi chi program chija nkhani ya lipoti ili umu

  Рет қаралды 46,284

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 309
@IsaaclBanda
@IsaaclBanda Ай бұрын
Ine nili ku Zambia koma nkhanga zaona sinipeza bwino ngati sininainvere.Comred ntanyiwa ni best
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Ай бұрын
A Mcp ankawona ngati akamudzimitsa Chilima nde kuti Mcp idzalowanso osadziwa kuti mpamene akutero po akudzichotsera mbvoti Pena tikhonza kumanena kuti Mulungu analora dala kuti zimenezi zichitike
@user-fm8ed7eo3i
@user-fm8ed7eo3i Ай бұрын
Muli boooh Mr mtanyiwa. I love you so much all team for Limpopo fm
@JuniorHala-vf9ov
@JuniorHala-vf9ov Ай бұрын
Ndiliphe kuno ku Pretoria ndi ntanyiwawu Kaya ena amamuda koma ine nde ummmmm I like this guy ndingot malawi first yonse
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Ай бұрын
Antanyiwa inuyo Mulungu anakonza mumatiyimilira lemu wanu❤❤❤❤❤
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Ай бұрын
Chakwera pokupha Chilima amkaona ngati azawina koma sizitheka apa anadzikalasila makala amoto heavyyyyyy
@Anni00Zungu
@Anni00Zungu Ай бұрын
More fire ntanyiwa mumatiyimilira keep it up
@HashimNyirenda
@HashimNyirenda Ай бұрын
Mulungu samaoneka ndimaso koma pamene ife tikuyenda or pamene takhala timakhala naye limodzi, Moti onse amene anapanga chipongwe chimenechi MULUNGU awaika pampalanganda. Shaaaaa ulemu wanu bigy potiziwitsa za lipotili Amen
@ListerBarsonBanda
@ListerBarsonBanda Ай бұрын
Ndizovuta kuti oyipawa kuti akupange chipongwe Ntanyiwa.coz mulungu wadzusa inu bigger kuti mupulumuse dziko lamaliwi all the best God bless you with more protection 🙏 🙌 anthu oyipa sasukunika ku malawi 🇲🇼
@user-hs4bm2yj8r
@user-hs4bm2yj8r Ай бұрын
Mtanyiwa the pangolin original, keep it up the good work brother man ❤
@RachelNkhoma-vn2jo
@RachelNkhoma-vn2jo Ай бұрын
mbambande padziko lapansi palibe chinsinsi mbali yakuno chinsaru Cha mkachisi chang'ambika tiyenazoni a Ntanyiwa ,wabisala mbatata msana ukuoneka aona moto a Mcp
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Ай бұрын
Kkkkk kkkk more fire man of God kumanga Mulungu asiyeni awakanthe😂
@HanaNyasulu
@HanaNyasulu Ай бұрын
Ndipo ine sindipuma bwino ndikapanda kunvera nkhanga zaona❤
@TwalikiWisiki
@TwalikiWisiki Ай бұрын
😂😂 😅😅😅😅 comrade inetu since morning ndakhala ndikufufunza nkhangabzawona osayipeza
@patrickdamalekani9863
@patrickdamalekani9863 Ай бұрын
Even me ase
@JohnChiwaya-ym5me
@JohnChiwaya-ym5me Ай бұрын
Mtanyiwa umakwana,,, We are proud of you!!, You are out and clear kuno ku BT , ku quarry
@SaidiAdamu-c6i
@SaidiAdamu-c6i Ай бұрын
Takunyadilanj a ntanyiwa mwatulukila coz m'bale wathu akasowa kwa 2 days tikumakhala ndi nkhawa coz agalu a mcp wa akutamangatu eeey
@HafsaAbwanali
@HafsaAbwanali Ай бұрын
Akangopita Ku German nkhanira imeneyo pibwerera Army mulande dziko ndikuzamangira pa airport akalowewe kundende life in prison kukanakhala Ku chilembenzo kwanthu chachisilamu tikanapanga sharia law aphedwe ,Koma asilikaliy dzukani musagone izi zachitikadzi zausatana ooopsa ndipo anandinyasa mene anali Ku chikokobe kumangochi kumanena kuti ati abale anthu akuziwa kuti anawapha lero siizi chifunga chapita dzuwa latuluka zaulira nde ati bwanji pamenepo☹️
@christinachikadza3760
@christinachikadza3760 Ай бұрын
Listening from Capetown South Africa. Keep the good work Mr ntanyiwa
@amoschataika7440
@amoschataika7440 Ай бұрын
Big up yomweyo Chikangawa
@collinsbanda8024
@collinsbanda8024 Ай бұрын
More fire 🔥 ntanyiwa we love love you all the way from south Africa 🇿🇦 ❤️ 😊
@PeterMillimbo
@PeterMillimbo Ай бұрын
Timakunyadilani a Limpopo FM komano nchifukwa chiyani asilikari athu sakukhala mbali yowateteza anthu?
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Ай бұрын
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa God bless you all the time.
@FatimanickisJaffer
@FatimanickisJaffer Ай бұрын
Km chakwera mpak kumupha chilima chifukwa cha kufuna kuimas upulezitent km chakwera ambuye akuchitire chifundo chifukwa uli chabe ulibe zelu ulipo ndipo iwey uzafa ngt mbalame sure ndakwiya nawe chakwera shem on you, chakwera must go 😭😭😭😭😭😭😭💔💔💔💔💔💔
@spargomw
@spargomw Ай бұрын
Mr Ntanyiwa koma mumaseka mopweteketsa moyo😂😂😂😂😂 Chakwera akamavera Limpopo i think thukuta limayenda kuchokera kumapazi kupita kumutu😂😂😂😂
@PhilipMatolino
@PhilipMatolino Ай бұрын
Mbambande comred ntanyiwa 🔥
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Ай бұрын
Ntanyiwa mumakwana, ndipo Limpopo FM ndi radio mbambande, No.1
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Ай бұрын
Osamvela nkhanga zaona mtima umawawa ngat chibwenzi Chako chatha 😂😂😂
@TakondwaSaidi
@TakondwaSaidi Ай бұрын
😅😅kungozuka timafikira Popa ntanyiwa oyeeee😅
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Ай бұрын
You are the best ❣️❤ Limpopo FM ndi radio yokha imene amalawi wonse amayikonda and we need report from black box ✊
@james-zd2nz
@james-zd2nz Ай бұрын
chilungamo chiyende ngati madzi opha mzake nayenso aphedwe watching from jhb
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj Ай бұрын
Mtanyiwwa ulemu wanuw km ndili ndi fuso bwanji ashankwela ankuyenda ndi amey yonkwana 4000 km shikangawaw anatumisa andu 8 onka bwanji sinankalla bwanji
@blessingcharo7669
@blessingcharo7669 Ай бұрын
Mumakwana keep it up
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
Omenyela ufulu a original akumalawi ❤😂😂 Ntanyiwa ❤
@FatimaBakali-v7q
@FatimaBakali-v7q Ай бұрын
Mfiti za mcp, asilikali akanangowalandapo dzikoli agalu amenewa miyezi yatsalai
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Ай бұрын
Ndipo inuyooo!!!
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 Ай бұрын
Asilikali akumalawi sangalande boma ngati momwe anachitila azimbabwe iwalani zimemezo
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Ай бұрын
@@viennasamuel2976 Ndipo mukunena zoona Asilikali aku Malawi mmmmmmmm ndi amantha koma kuzunza anthu mu njira zina ndiye amatha.
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Ай бұрын
Km nyimbo ya kayin ya kumapetoko ndiyoopsya kwambiri ndiyokhudza ngakhale mfiti imene ikhoza kufa ndi chikumbumtima.
@AliceJere-k9v
@AliceJere-k9v Ай бұрын
Ut reminds me of king Nebuchadnezzar...anazionatu ulemerero wa Mulungu utamuchokera.... from King to nobody kutchire mmmmhu
@crosbeygondwe5403
@crosbeygondwe5403 Ай бұрын
Comrade Ntanyiwa akubwela mwa coming 😂😂😂😂😂
@JessicaManda-zm1ug
@JessicaManda-zm1ug Ай бұрын
Kkkkkkkkk😂😂😂😂 chikangawa woyeeee satana achite manyazi sure more fire 🔥
@fedson2050
@fedson2050 Ай бұрын
Choyambilira tiyamika mulungu maka chifukwa cha Team iyi tikuti Limpopo Fm. Ndipo mulungu emweyo apitikire kugwira nanu ntchito imeneyo Tikowa mu Bible psalms 54 vs 17 Ves ilili ligwire ntchito pokutetezerani pogwira ntchito yanu Sir Comred
@HalimaDamiano
@HalimaDamiano Ай бұрын
Ntanyiwa moto kuti buuuuuu
@user-yu4np2wq4s
@user-yu4np2wq4s Ай бұрын
Ifetu Moni taulandili ndithu timakunyadilani ntanyiwa kwambili 👍👍🔥🔥
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj Ай бұрын
Mbambande Limpopo FM ndi ntanyiwa 😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤🙏🙏🙏🙏 Yomweyo chikangawa
@MebleNgulinga-hi6rg
@MebleNgulinga-hi6rg Ай бұрын
Palibe chinsisiiii padziko lapansili All evil plans back to the sender in Jesus christ name Limpopo with Comrade nthanyiwa woyeeeee
@LindaMakalani
@LindaMakalani Ай бұрын
Ine popanda kuvela comred mdimadwala kip de gud job God protect you en guide u aswel
@AlexHenere-r6l
@AlexHenere-r6l Ай бұрын
Asilikali pangani njira zimene mumapanga dziko ndilofunika lilandidwe mmanja MWA anthu away ndi okupha
@user-bi6pb5gc8t
@user-bi6pb5gc8t Ай бұрын
Kkkkk koma kumeneko chikangawa kunotu kuzomba tamuonesamo ground yonse anangokhalapo ndizibwenzizawo basi anyela agalu amenewa
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Ай бұрын
Ndipo ulemu wanu mwachita bwino galu ameneu ndipo mulungu amukathe
@PaulineKamwana
@PaulineKamwana Ай бұрын
Zomba mumatha ndazikonda kobasi zomwe munampanga chikangawa​@@user-eh1mg3ww6d
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 Ай бұрын
Mwaitha
@MandalaChaona
@MandalaChaona Ай бұрын
Ndalama akugawazo ndi za eni wake Amalawi kuzidya basi Koma Chidziwe mchipande powomola Maumboni ayambe kuoneka pa kusankha Ma khansala. Chikangawa boys you Will pay for what you did. Mwazi wa anthu 9 mwausamba thupi lonse. COMRADE NTANYIWA keep it up, keep moving🏃🏃
@macdonaldkorea2928
@macdonaldkorea2928 Ай бұрын
Ntanyiwa WOYEEEEEEE mukutiimilira ife olirafe, mcp yayaluka, amadutsa m'mbali
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope Ай бұрын
Kulakwa chakwera,,,,Ku Germany komwe akupitako kwapitanso amalawi ena amagulu omenyela ufulu nde ka akukapanga chiyani
@IgienacioPhiri
@IgienacioPhiri Ай бұрын
Akangonyamuka galu ameneyo kupita ku German kwakeko tiyeni panseu tonse mademo😊
@ThomasStephan-tg6ng
@ThomasStephan-tg6ng Ай бұрын
Inu Malawi fest mulengeze kuti pofika siku lakuti mupeleke 1 wiki kuti chakwera atule pansi udindo
@NoelBambala
@NoelBambala Ай бұрын
Mmakwanira a mtanyiwa ulemu wanu onse❤❤❤❤❤
@PollyLysonLutepo
@PollyLysonLutepo Ай бұрын
Ambuye apitilize kukudalitsani. Ndikukutsungani ndi moyo a Ntanyiwa. Ndimakunyadilani. Pitilizani ntchito yomwe mwayiyamba. Chilungamo chioneke. Don't give up.
@TakondwaSaidi
@TakondwaSaidi Ай бұрын
Aziyenda ma midzi Mo sinanga anthuwo alibe ma fn sakuziwa zomwe zikuchitika😮Koma Muthu amene Ali fn data angamunamize
@user-eo2hl9ug1h
@user-eo2hl9ug1h Ай бұрын
Antanyiwa....musatisiye...Mulungu..azikuyanganileni❤
@user-hs4bm2yj8r
@user-hs4bm2yj8r Ай бұрын
Asilikali please akanyamuka galu ameneyu, please a silikali take the office of President please
@user-qq1uj7ct6n
@user-qq1uj7ct6n Ай бұрын
Mulungu amve ma pemphero athu.. ulendo akupita Ku Germany aziwone mudzina la chiwanda chakecho. Amalawi chonde tiyen tizuke ngt ma Kenyan. Tiyen pa nseu😢😢😢😢😢😢
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Ай бұрын
Limopo FM Ntanyiwa imakuyenera kwambiri ❤, it suits you bro, keep it up bro
@ganizanimanyamba
@ganizanimanyamba Ай бұрын
More fire mr, comred ntanyiwa iweyo ndikatundu waboma olopano Brain banda pa times akunamano pale pale fisianadyamkazake🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 Ай бұрын
Tiyenda pa 31 pano pasewu
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona Ай бұрын
Come on mr muthwanyiwa bwela nayoni nkhani yonse timakunyadirani
@DonexNasenga
@DonexNasenga Ай бұрын
Osamaiwala bambo avick ku cape maclrear ku dwale muziziwaso kt amikonda kwambili amavela daily nyamata ameneyu
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Ай бұрын
Awawa antanyiwa penapake mutu wawo sugwira chifukwa pamene aku German amafika amati amene azapange kafukufuku saziwa chilichonse angowatenga ku butchery pano akut atulusa lipoti lenileni chifukwa chakwera akupita german kukakambanawo Kodi tinve ziti ,iweyo ndiwedi munthu waboza ndipo la 40 likukwanila chitsiru iwe
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt Ай бұрын
Chitsiru ndiwe wopanda mnzeru
@JowasiMasina-fy8ji
@JowasiMasina-fy8ji Ай бұрын
Matiyimira Mr Mtanyiwa ulemu wako
@SaidiAdamu-c6i
@SaidiAdamu-c6i Ай бұрын
Komaditu nane ndimazifusa kuti kodi chazulo ntanyiwa bwanji
@GoodsonfahardMaganga-qc2qk
@GoodsonfahardMaganga-qc2qk Ай бұрын
Ulemu Wanu mumatiyimilira inuyo ndithu ❤
@user-oj5ye6bj9q
@user-oj5ye6bj9q Ай бұрын
Morefire boss mtanyiwa mpaka amve kutentha afit amenewa
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i Ай бұрын
Ambuye pitilizani kusunga moyo wa antanyiwa ndiwose amenene akufunila ziko lomwe munatipasa zabwino musalole oyipawa kuti awononge myoyo yawo komaso atate langani athu amene akuwoneka ngati ndikhosazanu koma ilimimbulu yoyipa tikuziwakuti zosezi mukupangisa ndinu kuti satanayo ayaluke pitilizani kusunga mizimu yabaleathu ose amane anaphedwa kuchikangawa osayiwa SKC chilima tikulemphela kuvomeleza kuti munachoka pakatipathu 😭😭😭💔
@blessingsnyalo-rp9ko
@blessingsnyalo-rp9ko Ай бұрын
We are proud of you ntanyiwa
@cynthiandekhakatundu6890
@cynthiandekhakatundu6890 Ай бұрын
Palibenso kudikira 2025... Achoke ameneyo
@Atheeeefire
@Atheeeefire Ай бұрын
Ntanyiwa usamasowe chocho ife kumango check ma phone ngati notification ya limpopo hahaha respect always president ntanyiwa
@AubreymjBanda
@AubreymjBanda Ай бұрын
More fire 🔥 comliee!
@Chisomo-dh2gq
@Chisomo-dh2gq Ай бұрын
Fellow Malawian tiyen pa seu this coming Monday please Please this president he must go
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw Ай бұрын
Number one mtanyiwa
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 Ай бұрын
Inu ndi 1 basi iyaaaaaaaaaa😂 2 kuopa kuopa kupindika Shaaaaaaaa 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p Ай бұрын
More fire Mr ntanyiwa palibe chida chosulidwira iwe chidzapambana
@ruthkundwe7448
@ruthkundwe7448 Ай бұрын
UTM my vote
@ThomasStephan-tg6ng
@ThomasStephan-tg6ng Ай бұрын
Mademo apa 31tikupita konko kuli chakwera konko tikufuna axipita azikalima kwawo antanyiwa yokhayi yapweyeka Malawi MOTi Malawi sitideka akuchoka bs isanakwane 2025 Malawi zukani tiyeni tiyeni Malawi pansewu
@DanielSingano-bb7xq
@DanielSingano-bb7xq Ай бұрын
M'makwana bossman💪💪💪💪💪
@GertrudeLuciano
@GertrudeLuciano Ай бұрын
Ulemu wanu Nthanyiwa more fire
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg Ай бұрын
Ntanyiwa iweyo ❤❤❤❤❤ ndiwe mfumu basi
@PaulDaka-dc3re
@PaulDaka-dc3re Ай бұрын
Kuli bwanji ku Botswana, chikangawa yavuta pa nyasa🥱🥱🥱🥱
@JamesManjawira-yz4ji
@JamesManjawira-yz4ji Ай бұрын
Mr Ntanyiwa we're together ❤💪
@MandalaChaona
@MandalaChaona Ай бұрын
Through the blessings of God and God's Power One day Malawi First will Lead as Opposition Party representing Malawians Keep it up Comrade.
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 Ай бұрын
Inu ndi fire🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥ana achepa❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@patrickzembani4315
@patrickzembani4315 Ай бұрын
Moto kuti buuuuuuu aruta kontinyuwa comrade Ntanyiwa
@peterlowole7841
@peterlowole7841 Ай бұрын
More fire big man
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 Ай бұрын
Achilima anapita ifa yowawa ngati galu ophedwa ndigalimoto panjila koma mulungu anaona chilichose chinachitika kuchikangawa sizinakatheka ose kumwalila komaso inakakhala ngozi denge inakayaka
@user-sh5wq4uf6r
@user-sh5wq4uf6r Ай бұрын
Nkhani iyi yikundiwawa abale anthu kuchita kukhapa ndi zikwanje zoona? MCP what are you doing us? 😭😭 MCP ndi president wanu chakwela are you a Malawians? Why are you doing this? Because of money? Your position? Fokofu! God will punish you 😢
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Ай бұрын
This so called president will rot in jail
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 Ай бұрын
Amalawi tinagona kwambiri
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb Ай бұрын
Munthu kungophedwa just like that basi... Stronger, so energetic and Courageous man SKC, gone just like that.. MCP mwanya..
@cephasSainet
@cephasSainet Ай бұрын
Keep fire burning
@PollyLysonLutepo
@PollyLysonLutepo Ай бұрын
Antanyiwa Ambuye apitilize kuchita Nanu. Timakunyadilani.
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 Ай бұрын
Yoooooo abisala mbatata koma nsana ukuoneka Ambuye awakhululukire ndithu shaaaaaaaa 😭😭😭😭😭😭😭😭
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m Ай бұрын
Big up mtanyiwa
@feranjifeza6802
@feranjifeza6802 Ай бұрын
I was asking the same kuti kodi nganga zaona kulibe
@MISHECKBANDAH-m3h
@MISHECKBANDAH-m3h Ай бұрын
Mtanyiwa izi ndizimene timadikilira❤❤❤❤❤
@chiefjusticie
@chiefjusticie Ай бұрын
Anaphedwadi anthu aja chief Justice akhala akuyimba nyinbo pompano yozuzula
@KennedyKanyama-ce8lb
@KennedyKanyama-ce8lb Ай бұрын
U r number 1. Mtanyiwa timadalira iweo fire. Tifufuzireni pliz mutipatse zonse
@MarkinaJohn
@MarkinaJohn Ай бұрын
Boom!!! Wathu wathu ntanyiwa
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w Ай бұрын
Musamasowe big man ❤❤❤❤❤
@ThandoKunene-j9u
@ThandoKunene-j9u Ай бұрын
Mumakwanira mr Ntanyiwa !.Chikangawa yomweyo!! Galuiwe@. Kkkkkk timakunyadirani mr.🎉🎉🎉
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws Ай бұрын
Funso Langa kwa president chakwela,,,,,,kodi a vise President anapedzeka bwanji ovulidwa malaya??? Kodi tinene kuti ndege ndiyimene inanvula Malaya??
Just Give me my Money!
00:18
GL Show Russian
Рет қаралды 958 М.
when you have plan B 😂
00:11
Andrey Grechka
Рет қаралды 5 МЛН
So Cute 🥰
00:17
dednahype
Рет қаралды 43 МЛН
KUFA NDI NJALA UTAPHODA // DENIS MAHATA
29:56
MALAWI TODAY
Рет қаралды 13 М.
ZADZIWIKA ZIFUKWA ZOMWE BOMA LIMAFUNA KUTSEKA LIMPOPO FM NDI BAKILI TV
13:57
GWEDEGWEDE LERO PA 5 SEPTEMBER  2024 |
30:28
DZIWE TV
Рет қаралды 10 М.
BON KALINDO KUNG'ALULA MWA NYOO!! 5 September 2024
43:54
HOT 265
Рет қаралды 6 М.
NKHANI ZALERO KU TIMES 4 September 2024
19:35
HOT 265
Рет қаралды 18 М.
BON KALINDO LERO PA 6 SEPTEMBER 2024 |
16:10
DZIWE TV
Рет қаралды 4,5 М.
Just Give me my Money!
00:18
GL Show Russian
Рет қаралды 958 М.