So it means such stuff is everywhere. In Zambia too there is much talk about Yo Maps and Chile One, Mr Zambia. The only difference though is that these guyz do not go public word-stoning one other but it's the general public that somewhat promote or proliferate the so called competition, earning themselves a name: "THE DISCIPLINARY COMMITTEE" In the world of sports it's 'Ronaldo or Messi'
@sammalvitha Жыл бұрын
Hahahaha .... Am happy to have you brother from Zambia
@caiuskesly516 Жыл бұрын
Lulu is a Legend......to those who follow Lulu and Namadingo you have to listen nyimbo imene these two anayimba limodzi.....it will prove it all.... Lulu is the Best....and very humble with his talent....Big Up Mr. MATHUMERA
@thomasmwitiya1447 Жыл бұрын
Lulu ndidolo kwambiri pamayimbidwe,,,very humble person
@davemasanjala6499 Жыл бұрын
Lulu ndi dolo
@danieltvsrepairs1315 Жыл бұрын
Namadingo ndidolo
@beatonchingapa5868 Жыл бұрын
Tikationeso nyimbo zanamadingo ndizongovera basi koma sungati upita ku live show ya namadingo ndikukasangalala njee...king of live show ndi lulu ndinyimbo zake zabwino.... Lulu ndi humble guy Jah bless Lulu
Amwene anthuwa or atadana sikuti apangitsa kt adane ndi amalawi ai koma namadingo ndi amene ali very stupid chifukwa choziva kukoko lulu ndi munthu odekha kmanso kuyimba amatha
@richardmbondoma4846 Жыл бұрын
I believe they are all musicians and all are Malawians, Why should we waste time with things that wanna not help us?? Let's make them become best friends than before..... tikhale anthu achikondi tisamasonkhezele nkhani ayiiiii....ndi udindo wathu kulanditsa ndeu anthu akamamenyana, ndikuwayanjanitsa... Let us be like Jesus Christ... Philadelphia
@sarahsakala1549 Жыл бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣Lulu olotaimba guitar ndi Mano 🤣🤣🤣awe ndaseka anyway Lulu he is the best I still love his old songs and I love his dunce tiganize nampula itavuta tikutchola timadunce
@sammalvitha Жыл бұрын
Ganiza bwino tinyamuke 🤗
@chimzyalifoso Жыл бұрын
I like the way lulu answered namadingo
@magnificentmatchere706 Жыл бұрын
Ngat kwaine Magnificent Matchere.....ondikonda amandtchura kut GINTY....Lulu ndidolo kwambili komaso ozichepesa keep it up Lulu...
@hamdanmasuku4800 Жыл бұрын
Kkkķkk inu namadingo sangafike pa Lulu . Imeney nd mbuzi ya munthu
@bersonnyambi8370 Жыл бұрын
Lulu ndi muthu wamkulu and he is a humble man music anaiyamba kale enawa Ali ku primary std2 so ulemu umafunika
@frankmauzauza3819 Жыл бұрын
Bwana Sam luso lotambasula nkhani. ! muli nalo km vuto lanu ndikut pena mumaonesa mbali , ngat apa zikuonesa kut mwakwera Lulu .
@blessingskutchuwi8635 Жыл бұрын
Uli ndi Mbali AISE.... NAMAFAN TEAM Doc Ovaya palibeso..... NAMADINGO ND G.O.A.T.
@frankmangani1067 Жыл бұрын
Namadingu ndidolo ine lulu olo nyimbo zake sindingavele
@evancesteven97556 ай бұрын
The guy is taking side Indeed in his analysis. Chibwana🚮
@billy5866 Жыл бұрын
lulu is very humble and amatha kuimba siwalero komaso
@CathyKanthiti-e2p Жыл бұрын
Lulu ndi dolo👏👏👏eeeee straight up 🤟😅
@azunguauskay4903 Жыл бұрын
Lulu ndi machine, Namadingo kwake ndikulubwalubwa
@judithchitukwi165 Жыл бұрын
Namadingo ndi mwana mu music industry. Lulu ndi dolo.
@SamuelJoshua-qd4nn7 ай бұрын
I just like how this guy called lulu xpress himself to the entire Malawian nationa. Lulu v machine!!! Music that fit everyone-any age! 8:49
@fadsonkatasobanda Жыл бұрын
Namadingo ndidolo posatengera kt oyambilira kuimba ndindan nama alindiluso even kunja akuziwa pomwe saona hedge lulu mukumuziwa kwa mwenyekondo ndi kubangwe kawamvula basi aaa
@wangachindeya8577 Жыл бұрын
Sudziwa sakha kukhara chete lulu amatha kuimba ndipo ndioimba wamkulu mangalande imadziwa zalulu lulu ali pa map
@AhmmadAwali Жыл бұрын
Every one should respect legend Lulu nd lagend
@spencerukonde8259 Жыл бұрын
Anamadingo mwatani kod Inuo mungafike pa legend Lulu
@EgesLosa3 ай бұрын
Lulu ndidolo basi
@lesterchaula7850 Жыл бұрын
Lulu ndi more and it's ulemu ndiofunikadi mu industry imeneyi l love that point 👉
@wisdomsadyalunda2001 Жыл бұрын
Lulu Is a matured guy then he shouldn't allow every Jim and Jack to disturb him We know the way namadingo started his career and how he was supported If anything akanakhala munthu ozichepa .so he can't learn to humble himself he will humiliated Sizofuna zake
@chrismatekenya6084 Жыл бұрын
Zimangovuta azathu akunja amakonda ma Artist, Mikangano umabwelesa udani.... Thus why Upcoming Artist called Chris Matekenya , He said on his quote “I think music in itself is healing. It's an explosive expression of humanity. It's something we are all touched by. No matter what culture we're from, everyone loves music." #tag ~ Chris Matekenya
@blessingskutchuwi8635 Жыл бұрын
Uli ndi Mbali AISE.... NAMAFAN TEAM Doc O
@fwigo905 Жыл бұрын
Umatha
@jamesngaunje9790 Жыл бұрын
Koma adah awaa amafusa timafuso tawo, tachibwana🤣🤣🤣
@mulanjehydro6684 Жыл бұрын
Kuyimba kulingati politics ife timangomvela zalunja basi amalawi akatchuka always matama basi
@janenkhoma6447 Жыл бұрын
Anthuwa chilipo akulimbana si nyimbo zokha ayi
@emmanuelwakuluernest9372 Жыл бұрын
Lulu ndiwakuluzedi,ndimunthu amene SAdakhaleko ndinthawi yolimbana ndimunthu,ndiye uyu mukunuti namadingo wangokula ndi unyopoli basi ,ife nganganga pambuyo pa Lawrence khwisa LULU
@madalitsokazembe9569 Жыл бұрын
Inu a Sam mavithaso ndinu amtopola mukukolezera zoyankhula za anthuwa kuti tizidanisa anthuwa Inu ndiausilu ndakuonani.
@WanaBabez Жыл бұрын
Komatu zimangovuta...I wish they could work together
@zadomusictesfaye7511 Жыл бұрын
Namadingo ndi kape kombili palibe chomwe akudziwa chitsilu
@shinekaipa639810 ай бұрын
Lulu is the best ever❤
@GraciousSisal-tb2pe4 ай бұрын
Ndakuomani muli ndi mbali😂😂😂
@reubensamu5642 Жыл бұрын
Komano tikatengera mmayimbidwe Lulu ndi dolo kwambri. Komaso Namadingo wayamba liti kuyimba ali pa chipasula iyeo amamvera nyimbo dza Lulu nde Lero akukwera mtengo
@victorngwazi228 Жыл бұрын
Lulu ndi amuna namadingo anagwa mu mpingo afuna agwetse lulu wachepatu size yake ndi faith mussah dadawa asiyeni ndi mtendele wao
@mafulekav1225 Жыл бұрын
Dakter anavaya aixeee ,,, lulu ndi iweyo nonse ndinu ana ,,, pitani mkavine kwasakwasa uko
@GraciousSisal-tb2pe4 ай бұрын
Komabe Lulu ndi faddah🔥
@samuelmiwawa6422 Жыл бұрын
Muthu sakana kale Lake zikakhala6 zayenda.
@4waysphonetech Жыл бұрын
I like the way he answered Namadingo
@GaniMaononga-i8yАй бұрын
Onsewa ndi oimba omwe ine ndimakonda koma pali number one ndipo ndi Lulu
@FelistusTaulo2 ай бұрын
Lulu osamataya nthawi ndi kapeyo wabwera liti mu music industry kuti azikazikweza
@georgemilazi3935 Жыл бұрын
Lulu ndi founder i support him so much
@sutheen Жыл бұрын
A Namadingo aja 🤣🤣
@Judah-zb6sl5 ай бұрын
Bg🎉🎉🎉🎉🎉
@championntchana1343 Жыл бұрын
That's why I like you Lulu
@rashidsalanje4352 Жыл бұрын
Lulu is a legend than the so called Namadingo
@raphaeldzinyemba5693 Жыл бұрын
Lulu ndi legend basi olo Ena afune olo asafunei
@felixwachilundi1284 Жыл бұрын
Lulu ⭐⭐⭐
@mablekaombe2258 Жыл бұрын
Lulu ndi mphuzitsi Namadingo angovomeleza basi coz choonadi akuchidziwa muntima mwakemo
@kosisinoya6952 Жыл бұрын
Namadingo Legend
@tfhhhgfgju236 Жыл бұрын
Ulemu kwa lulu more 🔥🔥🔥🔥
@yvonnegwalidi1638 Жыл бұрын
Lulu ndiodekha sazipopa koma ada a Namadingo mmm kuzifila kumachuluka
@georgechambo3552 Жыл бұрын
Lulu amatha and dolo ine namadingo kuyimba kwake sindimakuona anatchukila ma mash uyu
@allanphiri2368 Жыл бұрын
Eya ndizabwino coz iyeyo Amanama kut sanakhalepo pafupifupi ndi Lulu yet waphunzira zambir kuchokera Kwa Lulu
@danieljulius2522 Жыл бұрын
Lulu number one iwe mbambande
@aaronchimbalanga4081 Жыл бұрын
Doc anavia athu mungochedwa aaaaaaa za ziiiii
@caphyasibu501 Жыл бұрын
Eya ndizabwino chifukwa Lulu nayenso ndi munthu amamva kuwawa
@justinedamson8862 Жыл бұрын
Lulu ndi machine kukhan yoyimba . Olo namadingo akulubwa lubwa pot anat munthu sayamika
@pscvideoz Жыл бұрын
The problem of being a judge who's already prejudiced, this KZbinr is like that, Honestly speaking namadingo is a talented artist, so is LULU, both of them are also too pompous, that's the undeniable fact.
@chrisysuwedi2754 Жыл бұрын
Lulu ndi mbambande awowo afuna akwiye anyanyale azipitaso Ku Zambia kkkkk
@andymtema5517 Жыл бұрын
Lulu ndi Biggy mwanayo muuzeni apeze size yake. Osamayamba zoti sangamalize kkkkkkkkkkkkkkk
@lawrenceblacktealyson8015 Жыл бұрын
Lulu much love you kudzichepetsa kuli mwa iwe
@dicksonbanda5731 Жыл бұрын
Dwaa samanena LULU if you follow bible thats a pure bible story there is no any kind of diss in that song and when you talk about zaku BICC Lulu ignited the fire he was the first one to answer and kukhala pafupi ndimunthu its a context of literature sikuti kukhala pafupi in physical appearance anyway LULU ndi dolo
@Ponex0001 Жыл бұрын
Inu nkhani idzitha. Mufuna anthu atani?
@moffatkadwa2598 Жыл бұрын
namadingo dzichepetse lulu ndi madala nzakoyo amajambula yekha nyimbo pamene namadingo amachita kujambulidwa ma audio
@JossamSteven8 ай бұрын
Lulu ❤
@WarriorKB-u3k2 ай бұрын
Ndikakhala ine nyimbo za malawi ndinasiya ndilibe nanu ntchito enanu munalowa satanic nde aaah basi ndi mmene munathele panopa ndimangovera lucky dube ndili phee