M’BUSA WINA WAFOTOKOZA ZOOPSYA ZIMENE ZINACHITIKA AKUONA EKHA ATAPITA KUPHIRI LA SOCHE KUKAPEMPHERA

  Рет қаралды 83,337

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 125
@patrickkadzeya3020
@patrickkadzeya3020 3 ай бұрын
The Holy Spirit is our awesome power and advocate, intercessor, He protected him and his prayer team, keep it up .
@Maxielyies
@Maxielyies 4 ай бұрын
Powerful, the holy spirit is really working all the time, thanks for the words of encouragement from this man of God ❤❤❤❤
@lusostudio
@lusostudio 4 ай бұрын
Osama ikapo bodza paza murunguzi
@mwizamalanga6102
@mwizamalanga6102 4 ай бұрын
@IsaacMoses-s2u
@IsaacMoses-s2u Ай бұрын
Tandipangen like guys ndiwonere bwino bwino mawa please guys 🙏🙏🙏🙏
@PastinaHope
@PastinaHope 3 ай бұрын
Amen❤❤
@MercyMakhala
@MercyMakhala 4 ай бұрын
Powerful words keep it up my brother .May the Lord be with you
@BLUR-p6c
@BLUR-p6c 4 ай бұрын
Mumphetsa apeze Malo ena opemphelela
@LouisKapange
@LouisKapange 4 ай бұрын
Amen
@chixo-gz7pw
@chixo-gz7pw 4 ай бұрын
Hahaha petulo anauzidwa kuti bwenza lupanga mchimake. Sanauzidwe kuti ataye kutanthauza kuti mu nyengo iyi sichikuyenela kugwira ntchito koma ifika nthawi yoti petulo atulutse lupanga mchimake kuti agwiritse ntchito. M'busa mbambande uyu
@MaryrappozoRappozo
@MaryrappozoRappozo 3 ай бұрын
Amen ambuye ndi number one
@JoyceMatendeu
@JoyceMatendeu 3 ай бұрын
Our God is God of war, Hie is a great. Warrior, He was with David an Samson, Praise the Lord.
@tiwongehojaney5873
@tiwongehojaney5873 4 ай бұрын
Amen.ambuye ndiwabwino
@RuthSmart-r6g
@RuthSmart-r6g 3 ай бұрын
That's powerful umboni
@NellieChikuse
@NellieChikuse 3 ай бұрын
Very powerful
@EnetChiomba
@EnetChiomba 4 ай бұрын
Amen God is wonderful
@VictoriaWilly
@VictoriaWilly 4 ай бұрын
May God bless you man of God 🙏
@JoanahGam
@JoanahGam 3 ай бұрын
Powerful
@FrancisKalavina
@FrancisKalavina 3 ай бұрын
Pastor kutema muthu 😂😂😂😂
@MAYESOCHIBWEZA
@MAYESOCHIBWEZA 2 ай бұрын
The God's power saves
@REXCHARLESKAJAWO
@REXCHARLESKAJAWO 3 ай бұрын
Kodi kukumana ndi zinthu? Heheee😂😂😂
@BEATRICEMAULIDI-f7k
@BEATRICEMAULIDI-f7k 4 ай бұрын
Amen Man of God
@DalitsoAlufeyo
@DalitsoAlufeyo 4 ай бұрын
Chomwe chiri mwa azibusawa ndi azimayi qmachiziwa okha😂😂😂😂
@DoliceChapita
@DoliceChapita 4 ай бұрын
God is wonderful
@SmartBanda-f9l
@SmartBanda-f9l 2 ай бұрын
Zaboza ndine Jackson kono kuzambia . koma atuper azwina mwava nose uko .zikomo
@ZefaniaChadza
@ZefaniaChadza 4 ай бұрын
Nyimbo ikhale ya Ndirande Anglican Voices "choka choka"
@kiddyphiri4203
@kiddyphiri4203 4 ай бұрын
This is very true and i onve met this tjinh at Soche mountain in 2006. It has been a long tendancy from these thugs
@IqrahSikweya-wm5mn
@IqrahSikweya-wm5mn 4 ай бұрын
Mwat anakuuzan ndi Mulungu kut mzikapemphera ku phiri koma abale... Mukumseweretsa Mulungu 😂. Inu kuyankhula ndi Mulungu 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Mulungu akukhululukiren Abusa 🙏
@HappyAnt-uz5je
@HappyAnt-uz5je 4 ай бұрын
Athu opanda chikhuulupiliro inu mulipobe Kodi zikhuthuleni mwatuthu mudzaona zomwe mulungu amachita pephero lodzikhurhula mwini Moyo salinyoza amamvaa
@IqrahSikweya-wm5mn
@IqrahSikweya-wm5mn 4 ай бұрын
@@HappyAnt-uz5je oh kkkkkkk komat At aZabwra onynga...... Mummadziwa iyemwa anayankhulanapo ndi Mulungu direct??????? Iyeyo ndindan pofika mkuyankhulana, kumvana mau ndi mlengi komatu ohoooooo
@FrancisEnock-e7n
@FrancisEnock-e7n 4 ай бұрын
Ambuye alemekezeke pokutetezani
@mayamikozimanyeta8633
@mayamikozimanyeta8633 3 ай бұрын
Muloleni Mulungu akhale Mulungu
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 4 ай бұрын
Azilipati talondolozani zachikamgawa
@Annie-c5g
@Annie-c5g 3 ай бұрын
Good news ndipo mwandisangalasa nchifukwa chani akumusiya galu ameneyu Mr chikangawa osafufuza za ndege koma chakwela ayi zikomo asazafe azangolowa pasi wamoyo
@patriciagondwe2934
@patriciagondwe2934 2 ай бұрын
Abusa apa mwapanga ndewu mulape
@FrancisKalavina
@FrancisKalavina 3 ай бұрын
Kkkk pastor kubisa ndlama
@BeatriceChilembwe
@BeatriceChilembwe 3 ай бұрын
Eshhhh zobvuta kwambir bt God it's not Aman indeed they were leap what they sow
@SimeonAbraham-u2j
@SimeonAbraham-u2j 4 ай бұрын
Azimayi take care
@InnocentAlligator-ll8fj
@InnocentAlligator-ll8fj 4 ай бұрын
God is good
@TabiahWisick
@TabiahWisick 2 ай бұрын
Ambuye ndiwabwino, ukaima pachoonadi Mulungu amakhala nawe ndithu .
@Annie-c5g
@Annie-c5g 3 ай бұрын
Mulungu akusogolereni abusa, Mulungu simunthu
@SMXBOYZAMBIA
@SMXBOYZAMBIA 4 ай бұрын
Mr speak m,busa wabwino Zambia mwati abusa analiphana nichigawenga ok koma ndalama niyovuta abusa kusiya bible nikusata cakhumi sorry koma m,tumiki niwovuta kwambili job 2:1-5 samalani kwambili ndinthu
@KingstonMahamba
@KingstonMahamba 4 ай бұрын
Aaaa unali ndi azimai okha okha nthawi yimene azimayi ankalandidwa matewela unangokhala chete koma nthawi yimene amafuna kukulanga chakhumi ndipamene mphamvu yamlungu yinakupeza.
@yamikaniloti
@yamikaniloti 4 ай бұрын
😂😂😂😂😂
@LevieMwanayaya
@LevieMwanayaya 4 ай бұрын
Kkkkkkkk koma abale
@AggieMayor
@AggieMayor 4 ай бұрын
Zosayendatu
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 4 ай бұрын
Kkkkk eti eti kkkkk
@archangelwycliffe4083
@archangelwycliffe4083 4 ай бұрын
Women!! women !!😢😢 hey!!
@JaneNgwira-d7t
@JaneNgwira-d7t 4 ай бұрын
Eee azimai funani Yehova weni weni okhala kumwamba mosamalitsa osangopusistsika ndi izi zaumbavazi ndi ziwerewerezi aiiii
@IddieMwanyali
@IddieMwanyali 4 ай бұрын
Kkkkkkkk😂😂😂 Vumbuluso lake lochokera kumidimalo😂😂😂 akuti tumiki😂😂😂
@NickUpoche
@NickUpoche 4 ай бұрын
Aaaaa kupedxa Bala chifukwa cha 5000mk,singapange zopusazo komaso chomayenda ndi adzikazi a eni ndichani,mamuna kukhala wekha
@EnifaHamiton
@EnifaHamiton 3 ай бұрын
Enifa hamiton
@CharityMhone-uk9ym
@CharityMhone-uk9ym 4 ай бұрын
Ndpo maboza azibusa amatsiku ano..kumapita ku phiri ndi akazi bwanji osapita ndi amuna anzako..ukuyeneladi kukhapidwa mwanyanya
@m-tedgustavo
@m-tedgustavo 4 ай бұрын
Kulengatu kulenga
@JECKYGREY
@JECKYGREY 4 ай бұрын
Watedzera iweo
@Momweekly
@Momweekly 4 ай бұрын
Ndalama zizakuphani abusa😅
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 4 ай бұрын
Zikungofanana ndi m,"busa uja amagonana ndazimai uja ,ndendendee ,bwanji akuti panalibe anyamata kapena azibambo ,koma azimai okhaokga ,kapena kuti atsikana zamasiku omaliza
@UseniMailosi
@UseniMailosi 4 ай бұрын
Akuti ndimayangulana ndimulungu koma anthu Inu
@IbrahndemangaIbrahndemanga
@IbrahndemangaIbrahndemanga 4 ай бұрын
Komaso inu 😂😂😂😅😅
@HamanjaManyela
@HamanjaManyela 4 ай бұрын
Yes he was speaking with God do you know the meaning of pray
@SelemaniAdam-q4d
@SelemaniAdam-q4d 4 ай бұрын
Wasowa zoyankhula uyoooooo
@VenançioZocueza
@VenançioZocueza 4 ай бұрын
Ndiwe wachigololo zilango amuna anzako osalalikira mphongo bwanji.
@JoanahGam
@JoanahGam 3 ай бұрын
Kutumikira mulungu ndikulimba mtima tisafooke ndipo tikhale olimba mtima
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 4 ай бұрын
Kkkkk Koma ndaseka bwanji, Abusa zowona kulimbana ndi nkhondo ya thupi ndi mwazi? Malemba amati chani Kodi?yesu anawuza Petro atamudula khutu munthu kuti: longedza lupanga nchimake chifukwa nkhondoyi siyathupi ndi mwazi,chomwe munakapanga Inu mukanangopereka zinthuzo basi ndipo lanu linayenera kukhala pemphero
@omargrey6500
@omargrey6500 4 ай бұрын
In my understanding about this ndikuona ngati it's just created story simple chifukwa nkhaniyi palibe kutchulidwapo police komaso ndikupita kuchipala pomwe ma department awiri amenewa amafunikiranso mu statement yakeyi in short ndiwe galu kwabasi
@StevenBestonDovu
@StevenBestonDovu 4 ай бұрын
Naweso ndi chigawenga choopysa
@ChikondiJobe
@ChikondiJobe 4 ай бұрын
Koma azimayiii,inuuuu,kutengeka.azimunanu amaziwa zomwe mmachitaa,kupusa,akanakukhapani koma,mukanaona polekera
@m-tedgustavo
@m-tedgustavo 4 ай бұрын
Eti mzimu oyera ananditsogolera ndikukhapa zigawenga kuteteza chakhumi Aah 😂😂😂
@RazaqMandondo
@RazaqMandondo 4 ай бұрын
😅😅😅😅
@lusostudio
@lusostudio 4 ай бұрын
Bora muzinena zowona2
@davidjoemalungah6338
@davidjoemalungah6338 4 ай бұрын
Ndizowona ineso anandi tenger ma 4n
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 4 ай бұрын
Mmmh chabvuta nchankhumi kuchiteteza kkkkkk
@RoseMcDonaldSinclair
@RoseMcDonaldSinclair 4 ай бұрын
Kmtu abaleee pena azimayi fe tikuzuzidwa nd azibusawa,mmalo mongopeleka chakhumicho kmtu ayiii ndithu mpaka kukhapana nae munthuyo ,mukanangopeleka bwezi kulibeso kuvulalako,km Ambuye atithandizile koposa
@GraceHarrison-qm2px
@GraceHarrison-qm2px 3 ай бұрын
Tsopano anali ndi azimayi okha bwanji azibambo bwa?
@CliveChikaphonya
@CliveChikaphonya 4 ай бұрын
Ma Prophet onyenga awa ndpo masku osiliza awa ndpo anthu akusocheresedwa omwe sakuwerenga Bible
@archangelwycliffe4083
@archangelwycliffe4083 4 ай бұрын
Petulo analetsedwa kuchita nkhondo ndi chida. Inu Mzimu munenayu ndiye uti? 😅😅😅
@yamikaniloti
@yamikaniloti 4 ай бұрын
😂😂😂
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 4 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 aaa koma Iwe eshiii 😂
@GeophuliesHarry
@GeophuliesHarry 4 ай бұрын
Aaaaa zazii ndiye umafuna asabweze aphedwe? Mzeru ulibe eti
@GeophuliesHarry
@GeophuliesHarry 4 ай бұрын
aaaa ulibe mzeru eti
@GeophuliesHarry
@GeophuliesHarry 4 ай бұрын
Mulungu anakumenyelani nkhondo pastor... Glory to God
@PLANBDAMZY-c7n
@PLANBDAMZY-c7n 4 ай бұрын
Amen 🙌
@chifundochiphwanya6859
@chifundochiphwanya6859 4 ай бұрын
Mulungu adalitse utumiki umenewu
@MadalitsoMofolo-k4m
@MadalitsoMofolo-k4m 4 ай бұрын
😭😭😭😭🙏
@JOHNOlesmasCosmas
@JOHNOlesmasCosmas 4 ай бұрын
Aaah bodza leni leni kukhulupilira ku phiri cholinga mukapakule basi mzimu udandiyankhura motan dyabu😂😂😂😂 Adakuchita bwino
@MarvellousTech-kz6no
@MarvellousTech-kz6no 4 ай бұрын
Mphavu ya chipambano mupambana mu nzose ,
@BLUR-p6c
@BLUR-p6c 4 ай бұрын
Osaopa abusa kumapitabe
@Littlefair7
@Littlefair7 4 ай бұрын
Mumakaziputa dala, kumuyesa Mulungu, tsiku lina mudzakumana ndi zinyama zoopsa. Aneneri a fake ndi amene mukulimbikitsa umphawi.
@claralewis9574
@claralewis9574 4 ай бұрын
Correct
@EdwardPhiri-n1e
@EdwardPhiri-n1e 4 ай бұрын
Kodi zimatheka bwanji inu azibusa nthawi zambiri mumakonda kupita Ku mapiri ndi akazi okha okha mumatidabwisa kwambiri
@nditumenichagunda4192
@nditumenichagunda4192 4 ай бұрын
Mbusa wanji otema anthu
@PetersenMjaliva
@PetersenMjaliva 4 ай бұрын
Kkkkk mlungu atsogolele
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo 4 ай бұрын
Moti dera lime be elo apolice a Ku uyudziwa nkhani imeneyi chifukwa anthu inu mukumatinamiza kwambiri
@towerankhoma1380
@towerankhoma1380 4 ай бұрын
Kukanizatu chakhumi kkkkkk
@MercyMwale-wc4lr
@MercyMwale-wc4lr 4 ай бұрын
Kkkkkk
@hopembendela
@hopembendela 4 ай бұрын
Komatu komatu inu umayankhulana ndi mulungu iweyo? ulape mwachangu ada usamasewele ndi mulungu
@MaryBanda-n3h
@MaryBanda-n3h 4 ай бұрын
Etieti ziwanda zimenezo 😢😢😢😢😢
@Mtonga-m9b
@Mtonga-m9b 4 ай бұрын
M'busa ochekera chikwanje
@SimeonAbraham-u2j
@SimeonAbraham-u2j 4 ай бұрын
Not impressive at how come the church has got only ladies men not in attendance
@YusufYusuf-k5k
@YusufYusuf-k5k 4 ай бұрын
ndiwe onama upeze China chinchita
@KennedyKutembo
@KennedyKutembo 4 ай бұрын
Koma ameneyo mutuwake ukugwila
@SurprisedCells-ny6gx
@SurprisedCells-ny6gx 3 ай бұрын
Mulungu sataya wake
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 4 ай бұрын
Azibambo bwanji kunalibe
@EdwinRabson-qn4sz
@EdwinRabson-qn4sz 4 ай бұрын
Utumiki wa aximai ndi atsikana
@kingsleySeda
@kingsleySeda 4 ай бұрын
Chakhumi
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 4 ай бұрын
Komatu azibale ake achakwera inu mumatikaikitsa mmmmm
@SaadiJannah
@SaadiJannah 4 ай бұрын
Ndiwe galu kwabas
@MphonoMatube
@MphonoMatube 4 ай бұрын
mbava iwe chachikhumi amakaperekera kuctchire
@jumaninyasulu5273
@jumaninyasulu5273 4 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 my thoughts as well
@MartherJack
@MartherJack 2 ай бұрын
Mb,usa uyu siwabwino ayi akanataya moyo wake chifukwa chachachikhumi komadi ndalama ndiyoopsa ndichifukwa chake yudasi anampeleka yesu chifukwa chandalama
@BenadettaThom-n8n
@BenadettaThom-n8n 4 ай бұрын
Glory to God
@ANGANILEMwenefumbo
@ANGANILEMwenefumbo 4 ай бұрын
Kkkk
@saidimwanyali8969
@saidimwanyali8969 4 ай бұрын
Maboza palibe amayangula ndi zimu wamulungu maboza basi
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c 4 ай бұрын
Komatu Pena muziyankhula bwino, mutenga nazo matemberero
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 4 ай бұрын
Azimayi kutengeka pa zithu Zina
@claralewis9574
@claralewis9574 4 ай бұрын
Stop this goin to mt nonsense if Yu have to pray stay in your homes. GOD is in you not in mt or building. Africans wake up
@RuthBothah-n8w
@RuthBothah-n8w 4 ай бұрын
Abusa okonda azimai awoo😂
@DolophyBlackson
@DolophyBlackson 2 ай бұрын
Very bad
@JoanahGam
@JoanahGam 3 ай бұрын
Powerful
@EnifaHamiton
@EnifaHamiton 3 ай бұрын
Amen
@LonjezoNkhoma
@LonjezoNkhoma 4 ай бұрын
Glory b to God
@ThrezaStanleyPhiri
@ThrezaStanleyPhiri 4 ай бұрын
Glory be to God
@EnifaHamiton
@EnifaHamiton 3 ай бұрын
Enifa hamiton
@EnifaHamiton
@EnifaHamiton 3 ай бұрын
Amen
@JpmwanaBoy-q1n
@JpmwanaBoy-q1n 3 ай бұрын
Amen
Every team from the Bracket Buster! Who ya got? 😏
0:53
FailArmy Shorts
Рет қаралды 13 МЛН
The Lost World: Living Room Edition
0:46
Daniel LaBelle
Рет қаралды 27 МЛН
Mafia King ft Ka Sir Blanca_  Know we bad(official music video)
3:44
Mafia King_ 1genna🥷🏿
Рет қаралды 11 М.
Em direto: 15 de Janeiro de 2025 - Jornal da Manhã
DW Português para África
Рет қаралды 1,4 М.