Well spoken mama and we understand every single point of ur message and keep it up you're opening our brains
@LukasBamus2 ай бұрын
Always on my mind uncle God bless you wisely and continue to reviled more sicrets in this world
@jameslifah79092 ай бұрын
Strong woman ever,you stand by the truth. Let love lead❤
@Yungjoe7862 ай бұрын
I salute you aunt The TRUTH eish
@LindaMalunjika2 ай бұрын
U are right zimene wanena.....anakakhala kuti ndi iweoyo chimwendo unali mu ✈️ ndi anthu ena Chilima anakakhala okathandiza anakakhala SKC.....why coz anali ndi umunthu....ndeeee who did ever did tha to Chilima ili ndi dziko ndipo limatembenuka
@HalimaMussa-j6t29 күн бұрын
Mulungu sachedwa azawaika poyela dziko lizadziwa
@MercyChimaliro-fi6mv2 ай бұрын
Well spoken Aunt ❤️ 💗
@howellbandah82112 ай бұрын
Be protected ur a blessing mama not just to the Malawian but to whole world ❤
@AllanTamula2 ай бұрын
Your comments towards Malawi politics is just great.
@0wenNkhambule2 ай бұрын
Good message Mayi Chimwendo ndiwakupha ndi Chakwela
@EllenKUMWENDA-b2z2 ай бұрын
I kove the spirit u hv mamie.Malawi shld hv more ladies like u....💪💪💪
@ReyonAndrewBanda2 ай бұрын
She is not in malawi remember.
@BrightKuyaka2 ай бұрын
Chemwali ndinkanyalanyaza zainu koma ndayamba kukumvetsani, more fire big woman
@SpencerKadewere-cd5ok2 ай бұрын
You deserve respect mumm continue fighting for the truth until these crocodiles🐊🐊🐊 repent there seens
@JosephGama-v7r2 ай бұрын
Mama you are a true freedom fighter
@PatriciaTikhiwa2 ай бұрын
Ndipo zoona chilima eishiiii ngt zabodza ndege hooooo zosaveseseka😊
@WelemuSayizi2 ай бұрын
Koma azimayi ngati amenewa ndi mwana wathu koma Malawi ndi yodala mayi uyu ngakhale azibambo 10 muli mu mcp simungafanane naye iron lady more fire!!!
People like this woman must be abandant, keep it up mama
@HajiAslam-nd9xq2 ай бұрын
Big up Mai mukhalise inuyo 💯💯💯💯
@alexjeremanuel2541Ай бұрын
Another example is Kondwani Nankumwa who was expelled from DPP but alive but MCP will never leave you alive
@Sabina-hw4js2 ай бұрын
Oh yes a woman of truth
@JamiluSunday2 ай бұрын
❤❤❤ ulemu wanu mama
@NickUpoche2 ай бұрын
Keep it up mm,proud of u
@QueenMoses-c1n2 ай бұрын
Big up mama u really encourage us
@EmmanuelDanitsa2 ай бұрын
Great message Moom..
@ThomasNChinseu2 ай бұрын
Nice touching to u nurse in USA keep it up
@RidgieGondweАй бұрын
Well done mamie
@ÑaloWembaАй бұрын
Wow 😮 chilungamo ichi
@KhumboNyerenda2 ай бұрын
Good message mum
@UfuluManondo2 ай бұрын
I silute you dear mommy mwaima pachilungamo,ambuye abise Moyo wanu pomwe a mcp isauone❤
@EliasManthenga2 ай бұрын
Mummy mukazafika ku South Africa zandizwsen tizadye kota limozi, kuima pa chilungamo amalawi aziwe ❤
@geeman-p9dАй бұрын
Abiti mukunena zoona tonse tikudziwa zoti Saulos anaphedwa. Anali ndi ntchito yabwino osati ku chipiku. Tikulirabe ndipo tidzalira mpaka kalekale. Anali wa ndale nde tikukambanso za ndale apapa. Mwayankhula bwino abiti zikomo
@Sabina-hw4js2 ай бұрын
Wise woman.
@MussaChilembwe2 ай бұрын
Chimwendo banda chakwera kunkuyu namajekete wankulu wa army manganya athu amenewa ndi amene anapha athu onse 9 aja koma thawi yawo yatha sopano mcp yamagazi crocodile 🐊
Dan Lu naye imukhuze nkhani iyi kulondola kosekose athu osakhazikika😂😂😂😂
@ChimwemweJoelKajawoАй бұрын
🤣🤣🤣🤣 Koma ndi osekesa kwambiri apa Pali cha nzeru chilichonse chomwe munthuyu wayankhula, even izizi sizikupeleka evidence or proof yoti munthu anaphedwa kapena Kuti inali movie
Abiti ndinu fire. Mau opanda chigamba. Zikomo kwambiri tili nanu limodzi
@gearardphiri69042 ай бұрын
Thanks my sister
@MikeMtunduwathaАй бұрын
Zoonazake zimenetikudziwa
@GlynLumbe2 ай бұрын
Muti ineyo Ku Namwera Ndiye kwathu kumudzi kumachemba MOTi timatsikila galimoto pa chesailesi kumapita ku machemba tiyakhulileni Kwa Anthu wathu osowa chikondi wa kuno
@AnniePetro2 ай бұрын
Chilungamo mama
@franciscomalola922 ай бұрын
aunt sizobisa apa anachita kumupha ndipo umboni ulipo pamene panagwera ndege simalo oti munthu angasake kwa 1 hour ayi ,,
@MiddayDeleza2 ай бұрын
Yes timukamba kumene anafa imfa yowawa SKC ndi ena wonse aja ulemu wanu mama
@JoyceZimba-pc4du2 ай бұрын
Good point mama
@WakisaNjeghenje-i2n2 ай бұрын
Ndizoona mama❤❤❤❤
@dewasicmalunga33742 ай бұрын
I salute you kusyeto wakumangwetu
@GlynLumbe2 ай бұрын
Mama takumvani ndi zoona zake ndipo ku Malawi kuno tikuliladi une so mwanache njenu
@IvanRoux-vl8gu2 ай бұрын
Thats true Mam
@Halima-i4x2 ай бұрын
Zoona mama osaposa 🙏🙏🙏💪💪💪
@ErnestChansa2 ай бұрын
Point point anamumpha chakwela ndi fit anthuwa a MCP
@HendrixBraveАй бұрын
Eeeeeeeeeeeeh Koma yaaaaa ine ndili pheeeeee ena kuseliku akungosegura mmimba
@AlexanderKamanga-i2l2 ай бұрын
Chakwela ndi mbuzi
@PercyRoosАй бұрын
That is true mamma
@IvanRoux-vl8gu2 ай бұрын
True ma Mamu God be fi
@EssauChimpangoАй бұрын
Truth being told
@CarolynBandA-bb6cn2 ай бұрын
True❤
@PeterMlowoka2 ай бұрын
Iyayi apa palimbetso zoti bwanji iyi inali plan yao same size Thambani akunga kuti Amalawk ndife opusa ,ifa imakhala ndi malonji
@wonganimwase9881Ай бұрын
Even if a child is late coming from school, the parents don't wait for an hour to atart searching,, talk less of saying that the search will resume the next day. Every flight has a manifest and a whole pesident couldn't didnt have the correct list of passengers on the plane.
Mmmmm mzoopsaaaa zinachitika zija, anthu analimba mtima 9 people mmmmm
@Halima-i4x2 ай бұрын
MCP ndichiman chakupha chifukwa chilowelen MCP boma onan Malawi anthu mene akumwalilila eeeee chakwela akuononga dziko labwino bwino ndi 2 😢😢😢 koma one day is one day
@phillipstamaley79012 ай бұрын
Kkkk aaaa za azimayidi ndithu kkkk
@MarthaChikandira-yr1yeАй бұрын
How can a download this video please
@HajiraMustapher2 ай бұрын
Chimwendo,chakwera,kumkuyu,zikhale nonse tsiku ili lidzakupedzani mufune musadune
@cynthiandekhakatundu68902 ай бұрын
Ndipo kambani Mamie anthu awa anatipweteka ...
@YusufGafa-s3jАй бұрын
Black box inasowa bwanji mundenge ngati inali ngozi chabe eeeee koma a MCP inu mmmmm only God knows
@RobertLuka-wy9cl2 ай бұрын
Auzeni mayi achimwendo ndi chitsilu chopusa
@MussaChilembwe2 ай бұрын
Komaso anachita kuphedwa athu onse aja ndege sinagwe ayi koma anachita kuphedwa basi straight point basi chakwera anachita kukonza kuti afe athu onse aja anapha basi chakwerayo
@montfortwoka28962 ай бұрын
Ndipo osamaika mau akuti mwina akanakhala ali moyo akanapita mwachangu ayi answer ndiyakuti anachita kupha awa anthu oipa kwambili tichotsa oipa onse next year ino . SKC anali president wanga.